A DPP Ku Parliament Mupite Okonzeka - Bon Kalindo

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 10. 02. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo continues warning the Democratic Progressive Party (DPP) ahead of Parliament meeting this week in Lilongwe.
    Ku Nyasa Voicebox, Bon Kalindo apitiliza kuchenjeza chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) pamene Nyumba ya Malamulo ikukumana sabata ino ku Lilongwe.
    #malawi

Komentáře • 52

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt Před 5 měsíci +1

    This is reality the first thing is leader of opposition do not allow parliament to Biggin without the leader of opposition if it is so postpone the meeting of parliament until the leader have elected the second thing, make sure the DPP party have a diolegue between them to hit the nail on there head because you're the eyes of Malawian may good God be with you and protect you during the meetings thank you

  • @JosephMwenyali
    @JosephMwenyali Před 5 měsíci +1

    Dpp,mps u need to stand strong

  • @user-qm1qb2jp4s
    @user-qm1qb2jp4s Před 5 měsíci

    Dccccccc 🔥 nankhumwa ndi chakwera watikwana ambuye tichotseleni

  • @oliviamphande1900
    @oliviamphande1900 Před 5 měsíci +1

    The only one freedom fighter Mr bon kalindo

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Před 5 měsíci +1

    Rest in peace Kondwani Nankhumwa

  • @user-hw9gg9nd9u
    @user-hw9gg9nd9u Před 5 měsíci

    Ndizoona aphuzitsi asavomele kumasonkha ndalama

  • @user-uf4db7im7d
    @user-uf4db7im7d Před 5 měsíci

    I totally agree with Bon Kalindo's advice.please DPP, do not accept Nankhumwa, to lead delegation in the house otherwise adjourn the house and get injunction.we want better Malawi

  • @user-dk6yc8pl2m
    @user-dk6yc8pl2m Před 5 měsíci +1

    ❤❤❤ the DC

  • @clintonnyirongo438
    @clintonnyirongo438 Před 5 měsíci

    Zaziii munthu aziyakhula mawu akuti ndine wowopsya wokhwima kkkkk

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 5 měsíci +2

    Akalindo ndalama zikupwetekesani nthawi zina mulungu azakwiya nanu chifukwa anthu amene mkuwanyozawo alibe nanu chifukwa

  • @FelixBMcdonard
    @FelixBMcdonard Před 5 měsíci

    Koma ngati a DPP mungokhara chete dzikoli lithapo
    Mr chihana mulikuti

  • @hendrymasina4014
    @hendrymasina4014 Před 5 měsíci

    Bon kalindo akunena zoona DPP, UDF,and AFORD segulani maso ndimbava zakuzungulilanizo segulani maso chifukwa zomwe akunenazo akalindo ndizoona ndinayamba kumusatila kale zose zimene amaya nkhula akalindo zimankhala zoti akuziwa zimene akunena zosezi zikuchitikazi anaziyankhula kale kale komano poti timamusatila bwino sizimatizizimusa kwambiri a DPP segulani maso

  • @user-qd2uy9fp9v
    @user-qd2uy9fp9v Před 5 měsíci

    Kalindo wumakwana ndipo chipani zotsusa ukuziwiza zoona zokhazokha

  • @user-od8gi6mj1d
    @user-od8gi6mj1d Před 5 měsíci

    Ndizoona akunena the DC able a DPP akugonana analanditsa Boma 2019 panopa Adina arhetse chipanichi

  • @user-fp5qn5ci2v
    @user-fp5qn5ci2v Před 5 měsíci

    Iwe bon kalindo usamayankhule mau ochita frustrate anthu ndi maganizo ako opusawo wamva nkhani zotembelera DPP timadana nazo kaya amachita kukutuma izo ndi zako

  • @thomasmalupi6624
    @thomasmalupi6624 Před 5 měsíci +1

    Bon Kalindo only the last standing man in Malawi. Mwana wa kwathu ku Mulanje kwa T/A Mabuka

  • @user-bq5ev7de1l
    @user-bq5ev7de1l Před 5 měsíci +3

    Apm my vote ✊

  • @user-vc4kz3yk8p
    @user-vc4kz3yk8p Před 5 měsíci

    Zoonaditu koma ofunika akonzekere bwino zochita a dpp

  • @user-mg1gu3ec6n
    @user-mg1gu3ec6n Před 5 měsíci

    Akunena zoona palibe chimene akulakwa akalindo mcp Akuma khalila Kuna miza anthu bas achoke Siti kuwa funaso feteleza panopa tikuma Gula 85000 thawi ya Peter tima Gula 22 ,500 chakwela asiye udindo

  • @user-ko1lk3br4r
    @user-ko1lk3br4r Před 5 měsíci

    imilani DPP KT zikhozeke coz khoti simuiopa mkulu

  • @mcdonaldchirwa3182
    @mcdonaldchirwa3182 Před 5 měsíci

    Keep on fighting Malawian Mr Bon Fighter Kalindooooo

  • @JumaAlli-vf6jp
    @JumaAlli-vf6jp Před 5 měsíci

    Kalindo akunena dzoona ndithu a d.p.p. asamale ndikuchenjera komwe

  • @user-dc7qq9yz3v
    @user-dc7qq9yz3v Před 5 měsíci

    Komano amavera DPP

  • @mchipengule
    @mchipengule Před 5 měsíci

    DPP mwayithetsa nokha, nanga kumangouyambana? MCP 2025 Woyeee!! Mwachitaya basi kutukwana chonchi? Mulungu sakudalitsani inu!!!

  • @user-hd7wq2yc6m
    @user-hd7wq2yc6m Před 5 měsíci

    ADPP choyamba musanayambe zokamborana zanu munyumba ya malamulo muyambe kaye mwakhala pansi mu nyumba yanuyo ya DPP kuuzana kapena kukambirana zokachita ku parliament ko leader of opposition first budget second ndizimene anthu amene tilikumodzi kuno tizizamva chifukwa ndipamene tizawonere kiti ndinudi opposition ya mphamvu asakutoleni a mca ndi yonse allaoance yawo yo iyayi.chonde chondr chonde ndipamene tizakikhulupitilani amayi Navitcha mukawonese uzimayi wanu ndipamenepa chonde kuno ku Muzi chikhulupiliro chathu chili mwa inu a DPP

  • @mchipengule
    @mchipengule Před 5 měsíci +1

    Zaziiii, moti anthu apange adjourn Pariament chifukwa cha uve wanu? Pariament ndi ya anthu.

  • @ConfusedAtv-bs4gc
    @ConfusedAtv-bs4gc Před 5 měsíci

    Kodi Mesa Ben longwe Ali kumalawi tatifunsilekoni Kuti zokoka zamayi yolamu zija amazinena zija wayamba kuzikoka pano chifukwa alinazo pafupi muja anali kutali

  • @wellingtonmtoso2074
    @wellingtonmtoso2074 Před 5 měsíci +1

    Za parliament zithela ku parliament. Za chipani zithela ku chipani.Otuminidwa amathela kwa omutuma.

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga Před 5 měsíci +1

    ukumva kuwawa sunati kalindo ukumva peni wen weni

  • @tafawakawonga6275
    @tafawakawonga6275 Před 5 měsíci

    Kkkkkk kuganiza ngati nkhuku

  • @user-od8gi6mj1d
    @user-od8gi6mj1d Před 5 měsíci

    Rubish people s are supporting MCP anthu adyera

  • @muhammadjuma3317
    @muhammadjuma3317 Před 5 měsíci +1

    Ukhaula iwe udzakhala kunja kwa boma mpakana kale kale . President wa amphawi alipo kale ndi mkasa. Adzako adakutuluka kale chifukwa chakuti ndalama umangodya wekha

    • @user-xn2dt2eu8x
      @user-xn2dt2eu8x Před 5 měsíci

      akulu mukulankhula palibe chipani cha MCP zikupanga iwo zikukutsangalani anthu opusa amene mukuyikira kumbuyo MCP the DC ndi omenyera ufulu ku mtunda wa amalawi osauka

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga Před 5 měsíci

    paja adayambira kugura lweyotu usaiware

  • @jomochirwa
    @jomochirwa Před 5 měsíci

    Katundu kapena zinthu zakwela mtengo kumayiko onse makamakaso mayiko amene ali ndi chuma.chitsanzo kuno ku southafrica katundu akudula zeedi koma chikhalile katunduyo akupangidwila kuno.ku mozambique anthu wogwila ntchito za boma maka police ,asilikali pano 4 month no salaries.kukwela ntengo sikumalawi kokha ayi.koma mtsogoleli wathu akayesa kupeza njila zabwino zochepetsela mavuto komanso katangale.anthu sitingavomeleze zakudula kwa zinthu pamene atsogoleli anthu akungokhalila kuba komanso ma alawasi akulandila ,masalale awo sadadulidwe.

  • @user-hu5su2ys7k
    @user-hu5su2ys7k Před 5 měsíci +1

    Kalindo mbuli

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 5 měsíci

    Kusakuyankhani pazimene mkuyankhula sikut ndiwopusa ayi koma anawona uchisilu wanuwo ugalu

    • @user-qv4ko6ps4j
      @user-qv4ko6ps4j Před 5 měsíci +1

      Ugalu opose wakowo mwana hule iwe.mwana oleledwa ndi agogo mai ako ali ku bar,chitsilu, mbuzi ya munthu ngati mkotero bwanji ukawafunse agogo akowo kut kodi dziko likuyenda bwanji,,,,,,, umve iwo mkutheka za bon kalindo siukumva ndipo ngati ndi chamba or tindalama tonyenyekato ta MCP m'phwanga tikupweteketsa ukalimbana ndi bon kalindo ulidziwano dziko ndipo choti udziwe ma bwana ako a MCP onse ndi ana kwa kalindo, iwe mantha ai ,monse adayambila kulimbana ndi boma muja akutaninae? Wamba wamba bwenzi ataphedwa kale koma uwu ndi mtunda,,,,,, dikila akayamba misonkhano tiwagenda mapwala awo!

    • @user-gx5ht9gm3z
      @user-gx5ht9gm3z Před 5 měsíci

      Sugayakhe coz ndiwe mwana wangon buzi sml boy 😊

    • @user-qv4ko6ps4j
      @user-qv4ko6ps4j Před 5 měsíci

      Cjay lucky,,,,,,, chitsilu cha MCP ndipo nonse munya 2025

    • @user-mx3rw2dt4z
      @user-mx3rw2dt4z Před 5 měsíci

      Ndimwana oti anaphulika chishango patumbo pa make akanyoze the DC wachilungamo

    • @user-qv4ko6ps4j
      @user-qv4ko6ps4j Před 5 měsíci

      The DC machine original than all

  • @henryhenry6632
    @henryhenry6632 Před 5 měsíci +1

    Nonsense dzimaphwala dzanu alomwe

  • @user-nw6ie3xx8b
    @user-nw6ie3xx8b Před 5 měsíci

    This man is hopeless, and u can see from far this man is hungry now he has joined dpp

    • @user-gx5ht9gm3z
      @user-gx5ht9gm3z Před 5 měsíci +1

      Ndiwe sml boy ndiye chifukwa ukunganizil zolakwa