We Are In The Age of Politics of Ideas - Kamlepo Kalua
Vložit
- čas přidán 26. 08. 2024
- On Nyasa VoiceBox, Rumphi East Member of Parliament Kamlepo Kalua proclaims that Malawi has entered a new political age characterized by the Politics of Ideas, not the politics of intimidation, killings, political violence, and political arrests.
Pa Nyasa VoiceBox, phungu wa ku Rumphi East a Kamlepo Kalua walengeza kuti dziko la Malawi lalowa munyengo yatsopano ya ndale yomwe imadziwika ndi Politics of Ideas, osati ndale zoopsezana, kuphana, ziwawa za ndale, komanso kumanga ndale.
#malawi
Powerful words Veteran Kamlepo ndipo chakwera pamodzi ndi Chipani chake ca MCP akuyenera kudziwa kuti 2025 ndi Ulendo wa kundende bas coz Malawi sadzalora kuti Nyau imeneyi tidziyiwona koma iye ndi nduna zake onse waku maula..
Powerful message Mr kamulepo.your matured in politics and you come from far with it.and I wish all politicians must listening to this message especially oppositions,there is a sense in this massage.mr Bakili muluzi,Mr chihana of afford,peter mutharika,and other Presidents of parties come together and join your friend to take back this nation to democracy.we need piece in Malawi not what mcp need.may God Bless Malawi and rescue to evil spirits from MCP government.we are patriots.God we seek your help in Malawi.
You're the icon and true meaning of democracy in our country.
If they have ears to hearing, let them hear your message but if they choose to be stubborn, then God, will strike and plunder them.
Mwana wa John Tembo iwe ku MEC komwe uliko, as Malawians, we all know why Chakwera elected you to be on that position with the aim to help him win the elections simply because you're both MCP fans and also that you meet underground. You've already proven it with your speech at the press briefing which you held previously that no 🆔 no voting. That's nonsense.
Be very careful of the deeply wounded Malawians. You will run away from Malawi if you try to a messenger of Lazarus Chakwera.
Be warned
Bravo Comrade Kaluwa we're with you
Good message Mr Kamlepo
Good Messnge Mr Kamulepo ❤
Liabunya analandila kale zoti azibweletsa zanyoo
Powerful!!!!
Amadana ndi inu ndi zigawenga bigman ma plan akupha otsutsana nawo ndiko kulepherako osaopa osatopa bigman.
Awa MCP tisamvele za ID iwowo akudziwa kuti ma ID alembetsa achewa okha nde pokuti adzinena kuti alipo 14 million chonde chonde chonde amalawi dziwonetselo a ma ID ayi mukalola otsusa chanu palibe ndinthu komatso muyika malawi 🇲🇼 pamoto 2025 itsaluwetso boma mcp koma zoti opanda ID ASALEMBETSE AMALAWI TISALOLE TIKUFA 2025 NDI MCP IYI
Listen up
Kuyankhula kwa nzeru
Tamva
Odana ndi kamlepo wadya banzi
Akamulepo munali kale munatha inu.panopa mungokhalira maboza
Nthawi ijaso unkanama kuti dpp yakupanga kidnap pomwe it was staged by yourself.panopa ukuti mcp through zikhale akufuna kukupha how special are you? Munabalalika inu thats why andale anzanu sakukufunani chifukwa they dont trust you.muja munayamba ndale ndikale kwambili bwezi simukufumabe sympathy kwa anthu.pangan retire madala fundo mulibe panopa mwatha.