OSAMACHITA NTUZU NDI MULUNGU - ULALIKI UMENE WALALIKIDWA PAMASO PA CHAKWERA LERO KU MANGOCHI

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 5. 09. 2024

Komentáře • 332

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Před měsícem +24

    Za wulurika zoti Chakwera Ndi Gulu lake ada mverana Ndi ma Israel agwetse ndenge muda kwera Chilima Ndipo ada Chita kuwa ombera nkuwa maliza mowatema nchi kwanje, Chakwera Yehova wolenga zonse amudalitse Ndipo wamvetsa manyazi mulengi wolenga Zonse koma Yesu adati wakupha ndilu panga nayenso azafa ndilu panga masiku achepe achuluke Chakwera azafa monga m'mene ada phera Wanthu amene adafa kuchi kangawa

  • @julietbanda5203
    @julietbanda5203 Před měsícem +1

    Chakwera wakupha,ndipo mulungu amukanthamula, power message 🙏🙏🙏🙏 May bless this word

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi Před měsícem +9

    Ndine msilamu Koma ulaliki iwuwu mmmm muli utenga wabwino moti inetso wandikuza kwambili. Ndipo ndaphuzira zambiri.ndipo ngati Chekwera anali m'busa wachoonadi ulaliki uwu awugwilize ntchito 😢😢

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa Před měsícem +9

    Ndiye chakwela akupha anthu omwe sanamulakwire mulungu amulange ndithu

  • @ElphinaChirwa-qk3cy
    @ElphinaChirwa-qk3cy Před měsícem +11

    Wakhutu wamva
    Powerful msg
    Straight from God

  • @user-nt9go2fz3k
    @user-nt9go2fz3k Před měsícem +28

    Ulaliki uwu ngat Ali ndi nzelu munthu umasintha machitudwe akee ndikuona kut zikolino anthu akut chaniii

  • @WezzieChimuzi-ek7bk
    @WezzieChimuzi-ek7bk Před měsícem +3

    Ameeen abusa uthengawu ogunda mtima kwabasi .... koma tipemphe chimodzi nyimbo ikuimba pansi pansiyoo ikulakwitsa ojambulanu plz muzadzaikenso tikamavera ulaliki

    • @DuncanDestiny
      @DuncanDestiny Před měsícem +1

      Ulaliki wabwino km nyimbo imenei ndadana naye opangayo

    • @WezzieChimuzi-ek7bk
      @WezzieChimuzi-ek7bk Před měsícem +1

      @@DuncanDestiny Ndimaona ngati ndilindekha amene ndadana ndikanyimbo kaoko bola kakadakhala ka uzimu.... coz moti tinvetsele ulaliki tikunvetsela kanyimboko kaye kuti kakuti chani Mwaona? Pena ngati kaja amaika mma filimu osakhala bwino ... hope sadziikaso kanyimboko tikuwafunila zabwino zonse potipatsa ma program

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 Před měsícem +1

    ❤❤❤ ulaliki uyu mwayankhula ndi moyo Dr chikangawa akwiya osaseka olo kuyankha mpaka azikanda posayamba ....Amen abusa chakwera koma.wamva bwino bwino ulalikiwu ndi wako kufuna zako osabwerako ...😭😭 rest in peace chilima...pano chakwera alimbe mwedzi ❤❤❤ abuse ambuye andalise uthengawu Amen

  • @franciscomalola92
    @franciscomalola92 Před měsícem +6

    Amen apo chakwera akumva Koma akuonangati dziko likuyenda

  • @fradrickMuvula
    @fradrickMuvula Před měsícem +3

    Truth n worthy preaching, Amen

  • @MaryNyalapa-u2t
    @MaryNyalapa-u2t Před měsícem +8

    Amen Abusa mwalankhula ndi moyo wanga.
    Funso langa Likupita kwa Chakwera ndi Monica…Kodi kuti mukhale pamene mulipo tsiku lalero chifukwa cha ndani?
    Kodi kupanda Chilima bwenzi Uli president?
    Kodi achina zikhale Ngoma kuti azikhala a position yomwe alinchifukwa cha ndani?
    Kodi ukanakhala kuti sunawine bwenzi aliposition yomwe Ali?
    Chikondi ulibwanji zikhale ngoma ndi a nzake at abwera ndi nfundo yokhupha chilimaukanawalesaa pokumbukukira zimene chilima anakuchitira.
    Munthu oipa okupha koma u call urself aman of God
    Monica ndiiwe Jezebel amupha munthu Kamba ka malo ake omwe.
    Muli ndi Tsoka

  • @stevemtambalika
    @stevemtambalika Před měsícem +4

    Muoneni maso ake ngati chikangawa chakwera yu

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před měsícem +15

    Apule mudakapuma Kaye kumatchilitchi enawa, kodi yanu ija mudatseka, chifukwatu kwinaku akukudzudzulani mulaliki, ndiyesa mukudzimvera 😮

    • @ManzyNgoleka
      @ManzyNgoleka Před měsícem

      😂😂😂😂

    • @fradrickMuvula
      @fradrickMuvula Před měsícem

      @@MisheckAselo Zonse ndi Nthawi dzidikira nyengo, Mulungu amaona zonse, Amen

    • @MisheckAselo
      @MisheckAselo Před měsícem

      @@fradrickMuvula Ndipo sagona satopa sapumula ndiye mulungu ameneo 🙏

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e Před měsícem +37

    Kodi president akukangalika kumapita ma church akuona ngati a zibusa sakuona momwe a Malawi akudusila munyengo zowawa ndi MCP....😅😅😅😅

    • @macdonaldkorea2928
      @macdonaldkorea2928 Před měsícem +1

      Wabalalika komanso akufuna kuziphimba ngt ndi khritu ndipo sanakonze nawo chiwembu....ati tiiwale tiziti ndiwabwino iyeyu

    • @NeemaMatewere
      @NeemaMatewere Před měsícem

      ❤ exactly my question,akuzivutisiranji pilizi,ndendiiyo maulaliki akungopherezera iyetu zovesa chisoni Zochititsa shame.

    • @BeatriceRobert-jq6ci
      @BeatriceRobert-jq6ci Před měsícem

      Chikangawa anali dendekere ngati akumva

    • @RoseNyoni-b5d
      @RoseNyoni-b5d Před měsícem

      Abusa mwafutsa bwino kuti chikangawayo anamulakwira chani chilima?

  • @bosheenhakhomba
    @bosheenhakhomba Před měsícem +1

    BRAVO my uncle kuima pa chilungamo osaopa. Uncle amwana makwana🎉🎉

  • @ruthkundwe7448
    @ruthkundwe7448 Před měsícem

    Achimwene zaziko lapansi nzosata,zisiyeni mulandile yesu pakuti palibe ngakale omozdi oziwa siku lake,satana asakuumiseni mtima,mwa yesu muli mtendele,amen pastor

  • @MussaAndreQuenessi
    @MussaAndreQuenessi Před měsícem +5

    Tamuuze chakwera akuchita manyadzi akuopa kunthawa yemweyo galuiwe

  • @ZakawiroNkhoma-qs7nq
    @ZakawiroNkhoma-qs7nq Před měsícem +2

    Power messeg...God bless u pastor

  • @gersommalama
    @gersommalama Před měsícem +3

    Wise advice to Mr President. Thank you man of God. I am sure Mr President was strengthened in fight for the National unity

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Před měsícem +2

    Amen abusa umeneu umatchedwa udani opasirana imwe akazi anga amalalika dairly kuti udan opasirana Ido very very dangerious ndipo ilo maubale amavuta kwambiri thank you pastor

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 Před měsícem +4

    Kuseli pa unai wawo akupangana kuti akupangire chiwembu.

  • @user-iz4yo2sj1d
    @user-iz4yo2sj1d Před měsícem +1

    Some one told me that when the gospel is coming take it as God is speaking to your own life not to some one

  • @kelvinchola739
    @kelvinchola739 Před měsícem +1

    ❤❤ Ambuye Mulungu akudalitseni pofukula malemba ngati awa, ndipo ndaona bwino kuti a Chakwela ndiozindikila pa zinazake iwo anachita polimbana ndi akapolo a Mulungu. Mulungu sanyozeka kapena coloration, Tsoka limafika tsiku la Mulungu lowawa!!!

  • @safaliallid
    @safaliallid Před měsícem +3

    M'busa uyu amalalikira hvy Shalom pastor

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Před měsícem +1

    Chakwera Nzeru ulibe ndithu ntima wako oopanda chifundo unapherani chilima? Unaputa nkwiyo wa Mulungu unapangiranji zimenezi? Mulungu yekha akudziwa za mkati mwako continue Rest well Chilima 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @VictorNgwira-w3b
    @VictorNgwira-w3b Před 26 dny

    God bless you man of God

  • @DanielChipasula
    @DanielChipasula Před měsícem

    AMEN....DZIKO LIMANYENGA! TIYENI TAZILAMBIRA MULUNGU MOWOONA. AMBUYE AZITIDALITSA.

  • @NeemaMatewere
    @NeemaMatewere Před měsícem

    ❤ powerful gospel
    Ambuye yekha azudalitsani chifukwa cha mau awa,Amen

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Před měsícem

    Uthenga wamphamvu uwu chakwera ngati uli nawo Mzimu wa Mulungu udziwe chimene Nzimu Woyera akulakhura ndi iwe Abusa Ambuye akudalitseni koposa uthenga wamphamvu uwu 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌😳

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v Před měsícem +23

    Azibusa oyima pa chilungamo osati kumangodya ndalama ayi lalikilani dziko limve

    • @AliceChipeta-pc3nb
      @AliceChipeta-pc3nb Před měsícem

      Ifetu chilima sitikaziwa kuti amapita Ku church. Tinaziwa atapitati or tsiku lofela kuti amapita Ku church asembe ananenatu, lelo zikutani nanga

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d Před měsícem

      @@AliceChipeta-pc3nbmutichani kodi inu

    • @NeemaMatewere
      @NeemaMatewere Před měsícem

      Mposoo

  • @johnmponda9070
    @johnmponda9070 Před měsícem

    It's my testimony God bless you pastor 🙏

  • @RitaKainga
    @RitaKainga Před měsícem +3

    Kkkkkkkk mkudzachita chomudzidzimukila Amen"yo😂😂

  • @isaacmtambo3511
    @isaacmtambo3511 Před měsícem

    A great representation of a man of God........May God Bless you

  • @GraceGowelo
    @GraceGowelo Před měsícem

    Powerful preaching Man of God 🙏

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před měsícem +4

    Ameeeeern limbani mtima achakwela adani a.ene muli nawo inuyo simnapunep amen

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d Před měsícem

      Chakwera anapha Chilima palibe kupuma ameneu kumatako kwake kukutetha moto

    • @user-hx6jl2jq9j
      @user-hx6jl2jq9j Před měsícem

      A limbe mtima ndani

    • @getbusy7173
      @getbusy7173 Před měsícem

      chakwera wake utiiiiiiiiiiiiiiiiii haha mfitiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii

    • @doreendzimuuzani7180
      @doreendzimuuzani7180 Před měsícem

      😂😂😂😂😂😂

    • @ZionekaMember
      @ZionekaMember Před měsícem

      Kupempha kupasa usiru umangoombela m'manja zilizose

  • @Chrisy-n1o
    @Chrisy-n1o Před 6 dny

    Powerful message

  • @PhilbertoChaimah
    @PhilbertoChaimah Před 23 dny

    Go deeper man of God

  • @JumaGadaff
    @JumaGadaff Před měsícem +3

    Akulu akulu ng.oma yokweza mawu sichedwa kusweka perekani miyezi iwili wina wake abwela poyera kunena zaifa ya skc mnzimu wa skc ulipo

  • @JacksonSoko-yf3gj
    @JacksonSoko-yf3gj Před měsícem

    Amen power message Ali ND khutu anve God bless u pastor

  • @julietbanda5203
    @julietbanda5203 Před měsícem

    Powerful prayer 🙏🙏🙏🙏

  • @janetbyson
    @janetbyson Před 5 dny

    Amen unthengs wamphamvu

  • @user-kd5zi7cc8z
    @user-kd5zi7cc8z Před měsícem

    Amen powerful massage from above

  • @user-ck7eb7tb7v
    @user-ck7eb7tb7v Před měsícem +1

    Ulaliki wochokera ka Mulungu.... Nzeru

  • @user-ez1kc7zp9m
    @user-ez1kc7zp9m Před měsícem +1

    Ican even see Chakwera showing his sympathetic nerve by looking at the pastor

  • @AubreyMitta
    @AubreyMitta Před měsícem

    Powerful message my pastor

  • @Frank-c6k
    @Frank-c6k Před měsícem

    Amen amen ndipo chakwela ngt alindi nzeru watengapo phunziro

  • @maxonkumpama4173
    @maxonkumpama4173 Před měsícem

    Powerful lecture!!!!!!

  • @dorothywillard2442
    @dorothywillard2442 Před měsícem

    Uthenga wamphamvu mulungu akudalitsen Abusa

  • @ChifundoSangatale
    @ChifundoSangatale Před měsícem

    Amen abusa Chirwa uthenga wanu wandilimbikisa kwambiri👏👏👏

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Před měsícem

    My Advice to the President ,bwelelani mmanja mwa Mulungu ,zadziko ndidzosala ,ndinu mtumiki kapitilizéni utumiki

  • @ImanRashidi-so4oo
    @ImanRashidi-so4oo Před měsícem

    Powerful massage ❤

  • @user-ik5sz8hc6f
    @user-ik5sz8hc6f Před měsícem +3

    Abusa.Ngakhale mwameta mbali komabe lalikilani ndithu za nyengo

  • @martinmoyo4211
    @martinmoyo4211 Před měsícem +2

    Abusa awa akulirikira bwino. Sakularikira monyoza a president. Ukundiyekusamvetsetsa ulaliki.

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 Před měsícem +1

    Why is Chakwera busy visiting Churches and mosques??? He must stop testing God,,,

  • @RajabuMuhamad
    @RajabuMuhamad Před měsícem

    Nanga choti mangaya alikut anakamva nawonso uthengawu😢😢

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Před měsícem +5

    Koma abusawa akuluwika mbavayi tuuuuuuu

    • @user-be5fc3ed1i
      @user-be5fc3ed1i Před měsícem +1

      Zoona abusawa alarikira mu njira Ina yoti wakumva bwino aziwapo chomwe akutanthauza koma mulungu dalisani malawi ndiposo invani mapemphero athu

  • @NelsonJames-r4m
    @NelsonJames-r4m Před měsícem +3

    Sound yanuyo (background) ikumasokoneza .......ndipo mukanaichosa

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em Před měsícem

    Amen , amazing message

  • @FloneySipondo
    @FloneySipondo Před měsícem +5

    Chakwera samva

  • @GraceGowelo
    @GraceGowelo Před měsícem

    Mizimu yonse ikumampeza ameneyo that's why akuenda ma church tsiku lina adzafuna mamasulidwe a Mulungu uyo miximu inachuluka ya anthu

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 Před měsícem

    Misonzi yomulilira chilima ndi nyengo chabe. Tiyeni tithamangire kwa Yehova atiuze tivote motani. Tingayambe kuvotera amaleki

  • @BrianAmbeswa
    @BrianAmbeswa Před měsícem

    Amen amen tsikulina mulungu azayankha ❤❤❤

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya Před měsícem

    Koma ngati mizimu yakuchikangawa ija ena sapenga misala, ndiye kuti Malawi zoti chaka cha mmawa tizavotaso zimenezo tiiwale, cz Mulungu akutiyankhula ndithu kupyolera mwa anthu ochuluka

  • @user-qo6ru2nb9r
    @user-qo6ru2nb9r Před měsícem

    Powerful man of God

  • @InnocentNkhwazi
    @InnocentNkhwazi Před měsícem

    David sanali oti ine mdzaimanso atapangana Zina ndi Jonathan anali osunga pangano that's why zake zimatheka

  • @hendkachibowo9672
    @hendkachibowo9672 Před měsícem +4

    Abusa mukaweluka mukawelenge YEREMIA 9 vs 25_26 pali nkhani yanu

  • @LindaNkwazi
    @LindaNkwazi Před měsícem

    Amen abusa preach on

  • @user-ol1hf7ru1v
    @user-ol1hf7ru1v Před měsícem

    Mai chikangawa muziwauza zanzeru amuna anuwo osamangokonda ndalama ai muli ndwiiiiii ngati akugwilani nyanga

  • @KhaliluGiftMasala
    @KhaliluGiftMasala Před měsícem

    Abusa ometa mbali😢😢😢

  • @CharlesKamanga-f4g
    @CharlesKamanga-f4g Před 24 dny +1

    Zanyengo

  • @IssahAluba
    @IssahAluba Před měsícem

    Chakwera akanagovomereza, mawuwo akuchoka kwamulungu

  • @FriddyMwaiphi
    @FriddyMwaiphi Před měsícem

    Strong words

  • @vivianmkwate8536
    @vivianmkwate8536 Před měsícem

    Amen pastor 🙏🏾🙏🏾🙏🏾🙏🏾 mau mau

  • @vivianmkwate8536
    @vivianmkwate8536 Před měsícem

    😂😂😂😂 ulaliki uwu wandigwira mtima pastor amen

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i Před měsícem

    Amen amen chakwela mukuvwa bwanji kumeneko

  • @SbaniCaros
    @SbaniCaros Před měsícem

    Amen n amen

  • @chisomomakavalo9232
    @chisomomakavalo9232 Před měsícem

    Who is this man of God

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e Před měsícem

    Powerful

  • @EdwinHowardmkandawire
    @EdwinHowardmkandawire Před měsícem

    Chakwera my vote basi

  • @user-mm3wq8qp2q
    @user-mm3wq8qp2q Před měsícem

    chakwera chilima anakulakwira chani 😢😢😢

  • @RebeccaMaluwa
    @RebeccaMaluwa Před měsícem

    Kodi mpaka mukulephela kutabwanya iPad 😂😂😂

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před měsícem

    Chikuyankhuladi chi chakwera kuti "mdani ameneyo alipo"lol 🤣iweyoka

  • @AaronWilliam-tm6mu
    @AaronWilliam-tm6mu Před měsícem

    NThawi zonse tiava mau AMULUNGU timayenela kuwava kuti MULUNGU akulankhula ndine, ukapeleka kwawina umachoka opanda kathu,ndilimbikitsa

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h Před měsícem +3

    Ulaliki uwu ukanamupeza skc chilima mwina bwezi chakwela sanakwanise kumupha ndithu

  • @user-fp1ki1gp7h
    @user-fp1ki1gp7h Před měsícem +3

    Ngat abusa akumeta mbalimbali ine ndindan kut ndisamete😂😂😂

  • @merviselias6230
    @merviselias6230 Před 23 dny

    Amen🙏🙏🙏🙏🙏

  • @RabbecaChirwa
    @RabbecaChirwa Před 9 dny

    Amen

  • @macdonaldkorea2928
    @macdonaldkorea2928 Před měsícem

    Koma mkaz wa Chakwera ndiy ndinkhwangwatu....ndalama alinazo akudya koma ngat wakumudzi mmmmm zinqngokumana amenewa akuoneka kut amkauluka(ufiti) amenewa

  • @HappyFyson
    @HappyFyson Před měsícem

    Chapapiyo wazibera yekha zufunika kulapa kt tikloe ufumu wakumwamba

  • @user-wi8xw9qh7n
    @user-wi8xw9qh7n Před měsícem

    Mulungu wathu ndiwowona tikulira mulungu tiomboleni

  • @NysonStandy
    @NysonStandy Před měsícem

    Nyengo zapa 10june,24.kumalawi stdzaiwala mpakana Mulungu atactapo ukulu wake

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před měsícem +2

    Ameni abusa mwayankhula moyo wanga

  • @WAKISANJEGHENJE
    @WAKISANJEGHENJE Před měsícem

    😭😭😭🤣🤣🤣 mmmm nzaulendo uno abusa nampaka kumeta mmbali kkkkk

  • @giftmakoyo1441
    @giftmakoyo1441 Před měsícem

    Amen uthenga wamphamvu uwu

  • @StellahMsodoka
    @StellahMsodoka Před měsícem

    Achitireni chifundo pakuti sakudziwa chomwe akuchita...mau onsewa mukumupasa Chakwera wa olo asazawinenso koma tsiku uzawafuna koma osawapeza samala bale ikudza thawi ndipo sikale ndipo palibe dziko lapasi kusitha kulikonse komwe tidzakuwone popanda kuchirimika pa wekha...chisoni chikumandipeza Maka kwa ana Ang'ono amene mutenga gawo lovala matemberero pa mau a Mulungu...koma ngati inuyo muli oyera kwa thuthu ndimawona ngati ndinu amene mungaliyike dziko li pabwino chifukwa Mulungu siwamasewera...ndipo sapanga nawo za tchezerazo... komanso amene akukutumaniwo ana awo anachita bwino kale ena Ali Kumaiko akunja koma Inu ndi ine mmmmmm busy kumangoyakhulapo..tayeserani kupanga zanu muone zimene Mulungu akuchitireni Ambuye akuthandizeni

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 Před měsícem

    Good pastor

  • @BrainSankhulani
    @BrainSankhulani Před měsícem

    Powerful msg

  • @HappyFyson
    @HappyFyson Před měsícem

    Musiyeni wazierayekha ameneyo

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před měsícem +1

    Amen Chakwela wava

  • @sayidimisessa
    @sayidimisessa Před měsícem +2

    Kkkkk hallelujah yatulukauku yowasiyisa achakwera kugona