A Kalindo Musalimbikitse Umphawi - Shaffie Hassan

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 29. 08. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, One Shaffie Hassan speak to Comrade Ntanyiwa, Bon Kalindo and DPP.
    Ku Nyasa VoiceBox, One Shaffie Hassan alankhula ndi Comrade Ntanyiwa, Bon Kalindo ndi DPP.
    #malawi

Komentáře • 55

  • @MarkinaJohn
    @MarkinaJohn Před měsícem +1

    Ukati azapanga ulimi azithira mikozo Malo mwa fertilizer??

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx Před měsícem +1

    Bon Kalindo, Ntanyiwa munkanena zoonadi kuti alipo aganyu a MCP omwe adziyankhula zotsusana ndi inuyo. Lero ndi awa

    • @user-bd5kw8oq1r
      @user-bd5kw8oq1r Před měsícem

      Ngati kalindo wabodza komanso wa ganyu wa DPP 😅😅

  • @FelleCasim
    @FelleCasim Před měsícem +2

    Mukutipangitsa manyazi jomba akututesya soni😊

  • @Cathy-oc7vd
    @Cathy-oc7vd Před měsícem +1

    Zikomo kwambiri chifukwa cha mau anu anzeru zakuya.. Bon Kalindo wakula ndi umbuli ndi dyera. Ndipo Kalindo akuchulusa bodza mukuyakhula kwake kupangila campaign DPP.

  • @thulambale2836
    @thulambale2836 Před měsícem

    Excellent audio iyo adada wane

  • @gilamwelekedwa4889
    @gilamwelekedwa4889 Před měsícem

    Video yamzeru pa ma audio onse pa Malawi 🇲🇼 a comrade Nganga mwayakhula bwino kwabwino kwambiri Zikomo 🙌🏽👏🏽👏🏽👏🏽🙌🏽

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před měsícem +1

    Ukunena zoonadi big

  • @dontreybanda278
    @dontreybanda278 Před měsícem +2

    Nganga yausilu

  • @SandraBanda-hd1li
    @SandraBanda-hd1li Před měsícem

    Gaga. amenewo..... timadabwa... nao..... analandila ndalama. ... amenewo ... Zanziii

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg Před měsícem

    Sikukula kwa muthu kumayendetsa dziko ndi zeru zomwe zimaendesa dziko lazalo mnyamatayo akulephera bwanji???

  • @MathewsChitsulo
    @MathewsChitsulo Před měsícem

    Akulu mulibe nzelu kodi cholinga chanu chimakhala chotani mukamabwela kuzatsutsa zomwe anthu ena akufufudza ? Bwanji osakamba Zina bwanji.

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx Před měsícem

    Koditu anthu aganyu simusowa. M'malo momvera chisoni agogo Anu omwe akuvutika uli busy kulimbana ndi ma comrade amnzako

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg Před měsícem

    Ndikuuona kuti zomwe mukutiuuza inu nganga ndizoona koma kalindo pakukhara president waphawi sakulimbikitsa uphawi koma akuimilira wathu omwe sangathe kutumiza audio ngat momwe mwatumiziramo

  • @Yahiya-wm8nd
    @Yahiya-wm8nd Před měsícem

    wanganyu uwu mbuzi

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před měsícem

    Adpp amadana ndi chilungamo asiyeni atulutsa part 2 atibela 2025 anganga mau amakhala amphabvu koma ku dpp safuna kuwauza zoona asiyeni mau anuwa adzawakumbukila

  • @AllyMilanzi-h2t
    @AllyMilanzi-h2t Před měsícem

    Ndizona mwalakhula komano anthuaza Lima bwanji mbeu zadiba zintuzikuvuta koma nozinthu zonsezikutizite khani ndi president akufunika kuti anthu avekukoma ndekuti inu zomwe zikuchitika Malawi kukwela kwazinthu ndekuti inu zikukusagalasani.

  • @user-nq2ih6xl5z
    @user-nq2ih6xl5z Před měsícem

    Kodi ukuti iwe ndi nganga osangokhala chete bwanji, pali nzeru iliyonse yomwe ukukamba pamenepo, musiye kalindo ndi Ntanyiwa aziyankhula ndi ife amalawi ngati sufuna kuwamvesera ungosiya osamamvesera, kaya akutuma a mcp zimenezo ndi zako

  • @ShavielSiment
    @ShavielSiment Před měsícem

    iyi ndi mbuzi

  • @user-nq2ih6xl5z
    @user-nq2ih6xl5z Před měsícem

    Kodi mmene adad ankatisogolera mu 2019 iwe unali kuti, sukuona wekha kuti mcp ikupha anthu njala nkhanza, zimenezi zinaliko,iwe usazavotere dpp votera mcp yakoyo machende akonso

  • @edenbelievemseteka5197
    @edenbelievemseteka5197 Před měsícem

    Koma za APM ine ndikugwirizana naye munthu uja wakalamba

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Před měsícem

    Jomba chopusa iwe utulukambwanji mavuto ndalama ilikwani

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy Před měsícem

    Nde omwenyera ufulu inu ndichaninso mutsutsana ndi anzanu mmalo mothandizana nzeru mutiombole ku mavuto omwe tilinayo

  • @user-nq2ih6xl5z
    @user-nq2ih6xl5z Před měsícem

    Iwe adad kuyenda kukuwavuta, iwe ndiwamisala khala ndi mcp yakoyo

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz Před měsícem

    Ameneyu ndiopusa kwambiri bdi radio itiyo mmalawi muni inakuuzapo zoona?, nee munthi akan ena zoona wagwesa mphwayi bwanji, ukufuna tikalembetse okubawo agwiritse mavoti athu? DPP peter mutharika adina. Bhati muline mzeru khala ni chete. You think what they see life ma silent listeners simaona? Musamatithere bundle kumaona ngati ndizanzeru ifesotu zimatiwawa

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 Před měsícem

    Machende anu notse alandila ndalama amaneyo amamuyadira ndani iwe kapena iwe pa liololenu

  • @NONELWANAMANYI
    @NONELWANAMANYI Před měsícem

    Ndi mbuzi ya MCP imeneyo

  • @user-hl5ey8bs5s
    @user-hl5ey8bs5s Před měsícem

    Tiye uko galu iwe akudyetsa chi banzi etii? Iwo amangoyankhula zimene zikuchitika bas.
    Iwesotu apa zaonetsa kale kut ndiwe wa MCP oputsa iwr

  • @LumbaniNeba-d9n
    @LumbaniNeba-d9n Před měsícem

    Wopusa iwe akupatsa mabanzi et!

  • @MasegoModukanele-xg2hj
    @MasegoModukanele-xg2hj Před měsícem

    Awuze kuti ave apitadi limodzi amenewa apitadi zoona akhaula asiye dpp singalowe mboma ndikuuzs iiiiiiii koma ayaluka ndi athuambili ndi apulezident oyimila anthu osauka apitola limodzi komatu afanrns kuti mmalawi siomufela kaya ayiwala bwaji inu moti mkumati dpp ingagwetse boma athu wake ndani akunama nfale xapamalawi dakuzidziwa adpp sadazolowela kupatsidwa nfoye ziwavuta awapatseyo ndani adachitika mwayi ku udf ndi pp koma mcp songa wapatse akadalila kuja kwa boma

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Před měsícem

    Petongo penupo bwanawe mmwe mbwa

  • @NONELWANAMANYI
    @NONELWANAMANYI Před měsícem

    Ngat watumidwa unya galu iwe shaf

  • @user-ti2ct8ts8d
    @user-ti2ct8ts8d Před měsícem

    Tiye uko iwe opusa kwambiri,Ife tikudalila ntanyiwa ndi kalindo ungatiuze chani iwe kape fokofu.

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před měsícem

    Galu iwe usatitayise nthawi

  • @RaphealKwelani
    @RaphealKwelani Před měsícem

    Kd iwe zakukwela ntengo zakatundu ukuziziwa km jomba murungu akukhululukilen ife tivotelabe adadi galu iwe

  • @MasegoModukanele-xg2hj
    @MasegoModukanele-xg2hj Před měsícem +1

    Kulakhula kuti anthuwa ave mchifukwa zolakhula akalindo ndixa umbuli mbuli kalindo ndimbuzi

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba Před měsícem

    Kod ayao muliso ndi athu opusa kwanuko ndati uyu

  • @Andrew-nz9sh
    @Andrew-nz9sh Před měsícem

    Zazii why don't you leave them we love them like that as they are

  • @user-jj3oo6jh1l
    @user-jj3oo6jh1l Před měsícem

    Chikuni chautsi mchimene chimasunga moto nde mukati peter wakula mufuna kunena kt chiyani?

  • @braveglorymwanzagolah4899
    @braveglorymwanzagolah4899 Před měsícem

    Galu wachabe chabe iwe walandila chibanz chophaka jam basi

  • @GRACIOUSKENAN
    @GRACIOUSKENAN Před měsícem

    Iwe kamdala iwe ukufuna akutame ndat?? Unalikut mmene achilima ndi anzao akamwalira muja??
    Bwanji mzelu zakozo sunaynkhulepo galu ukulimbana ndi ma warriors idiot iwee, ukulimbana ndi ma battle field why?
    Bwanji sukumufufuza chakwela kanganga iwe waninkhidwa chan iwee?
    Ungalimbane ndi DC? Ungalimbane ndi Mr nkhanga and bakili tv, shot up your mouth 👄 kagwere......
    No interegent idea hereeee
    Kod mukati ndale ndikuthamanga kapena readership??? Kma iwe usandikweze bp

  • @RashidNgalinje
    @RashidNgalinje Před měsícem

    Iweyo anganga kodi akupatsani chiyani a mcp ndalama Iweyo ngati ukudya bwino ndi ana anu ndi zanu pantumbo panu amatchende iwowo akuphela ufulu ife amalawi mwina Iweyo si m'malawi uchoke pa voice po ukutibhowa manyi ako opanda nzeru ndi iweyo ukuganiza tonsefe tizikalima kwanuko muli ndi malo inu fack you mjomba

  • @user-ql8nf2vb8s
    @user-ql8nf2vb8s Před měsícem

    Manyi awa ashaf akuti waunsilu ameneyo

  • @YusuJames
    @YusuJames Před měsícem

    Ukatero akupasa ndilamatu maphwala ako iwe ndikwatali manja kwanuko ulibetso fundo bwanj

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga Před měsícem

    Ndiponso mapwala a bambo ako shaf iwe

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w Před měsícem

    Mapwala ako srs

  • @jamusnamwino-br2iz
    @jamusnamwino-br2iz Před měsícem

    Jomba opusa uyu sakuziwa zimene akuyankhula

    • @user-bd5kw8oq1r
      @user-bd5kw8oq1r Před měsícem

      Akulankhula zaphindu keep it up mbuli inu ndi kalindo wanuyo

  • @ThokozaniChadza
    @ThokozaniChadza Před měsícem

    Zazibasi asagokhalachetebwanji

  • @SilenceChepiano
    @SilenceChepiano Před měsícem

    Zoduka mutu basi chilingamo chioneke basi

    • @HASSANHASSANTDL
      @HASSANHASSANTDL Před měsícem

      Jomba ngati mwalandila ndalama muzingodya mwasowa zoyakhula mukukhala ngati sena kupusa kumeneko iweyo ndi mozi wa kuba watumidwa chiyani iwezo kumangochi usamuke

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Před měsícem

    Galuiwe akumtuma