Jomo wamukana Bon Kalindo

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 29. 08. 2024
  • "Count me out" says Jomo

Komentáře • 22

  • @FachiMalilima
    @FachiMalilima Před 20 dny +2

    Winiko spresident nanu okuti angasinthe dziko, osimtha dziko simukuwaona, winiko amangoying'alula boma likamalephera kugwira ntchito

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Před 11 měsíci +2

    Well done Jomo, mademo a Winiko mutu wake ndi kumanidwa udindo kwa Kalindo.

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga Před 20 dny +1

    a JOMO INU...NDINU A MANTHA CHABE😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @BlessingsmadalitsoShumba

    Ayiso ajomo nanu 😅 mumaikonda inu mcp kuti izivutitsa anthu

  • @katalamajames4947
    @katalamajames4947 Před 11 měsíci +1

    ndiposo jomoyo machende amake iye migodi yoyitani ndichaniso osasaka ndzochita bwanji chifukwa choti sanapite kuxool mkona akufera migodi yoitanira nanga mene wakulira yeyu azinena dzoyitanira ndi mbuziso imeneyi eti

  • @user-tn4xm2dc2n
    @user-tn4xm2dc2n Před dnem

    Galu ameneyu akutipusitsadi

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg Před 6 měsíci +1

    Iwe Jomo usalowese chibwana, MCP ikumwaza ndalama kugula anthu m'malo mochita zomwe analonjeza lero a Malawi ambiri akuvutika iwo ali busy kugula anthu kut azinyoza DPP pali nzeru pamenepo??????

  • @mphatso2976
    @mphatso2976 Před 11 měsíci

    Mene wayakhulila jomoyo mwaona bwaji mau ake dimagulu ugulisa amalawi didalama olomene akuonekela sagakane ndalama jomo upeleke ulemu kwa anthu opephape diwechisilu sukuziwa chimene ukuchita ufela zani

  • @PeacefulWildFlowers-sl8er
    @PeacefulWildFlowers-sl8er Před 7 měsíci

    I am warning you 😂😂😂😂

  • @harrymbelenga8614
    @harrymbelenga8614 Před 2 lety +2

    More fire nkharango

  • @MozesKamwambi-iu4ox
    @MozesKamwambi-iu4ox Před 11 měsíci +1

    Ver good magyz

  • @user-lt3xl7cv5n
    @user-lt3xl7cv5n Před 6 měsíci +1

    Kodi akalindo dziko la malawi mukufuna kuyambitsa nkhondo, alomwe inu mumadzitenga ngati ayani? Mmalawi muno muli mitundu ya anthu ambiri mbiri koma kumanvela alomwe wokha, boma simudzalionaso ndi umbuli wanuwo

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg Před 6 měsíci

      Ukamati alomwe ukutanthauza chani? Pafika zinthupa akuvutika nd alomwe okha, sugar wakwerera alomwe okha? Iweyo suziwa kut alomwe ambir anavotera boma ili koma palibe cha nzeru ikuchita. Mind your mouth.

    • @LuciusMaison
      @LuciusMaison Před 15 dny

      Iwe ndiye ndani kakapetheee ngati iwe

  • @lyiemax
    @lyiemax Před 11 měsíci

    That's a big warning, take care don't involve mademo ndi zautsilu za achina Jomo

  • @ThandiePotah-qq6ox
    @ThandiePotah-qq6ox Před 8 měsíci

    Mulungu adalitse malawi

  • @user-wz8jo7fj2b
    @user-wz8jo7fj2b Před 9 měsíci

    Zoona d big

  • @manuelmalunga8763
    @manuelmalunga8763 Před 4 měsíci

    Chakwera ndi MCP Mulungu azakuweruzani yekha

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg Před 6 měsíci

    Koma kunyasaland kwavuta

  • @mederinausain6913
    @mederinausain6913 Před 11 měsíci

    Kkkk

  • @AndrewDamson
    @AndrewDamson Před 19 dny

    Ur lie