JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 6. 10. 2023

Komentáře • 212

  • @charlesmuwanya7845
    @charlesmuwanya7845 Před 8 měsíci +19

    Mr John Kapito has given a true account of the real situation in Malawi. He is a senior soothsayer. He is always for the whole truth. He doesn't mince words & his desire is to set things right.

    • @user-ym9eg6qg6t
      @user-ym9eg6qg6t Před 8 měsíci

      Jst straight to the point

    • @JafaliAkimu-ll1bf
      @JafaliAkimu-ll1bf Před 13 dny

      chakwera ndi chitsiru cha munthu mdziko muno mbava

    • @user-bq9rj2mi4h
      @user-bq9rj2mi4h Před 21 hodinou

      koma maiko anzathu zimachitika ngati zimachitika kwathu kunozi kapena nkhani ndiyathu kunjaku....malawi wafika penipeni pomvesa chisoni mmmmm Mulungu atithandize

  • @EdwinMabviko
    @EdwinMabviko Před 8 měsíci +11

    Malawi needs such people to develop!!!

  • @PatrickTembo-lm1ih
    @PatrickTembo-lm1ih Před 18 hodinami

    Koma apapa mwayankhula chilungamo ngakhale msogoleli alindimaganizo amenewa likhoza kukhala boma mkhoza kuyendesa boma bwino ❤❤❤❤

  • @user-xi2vo4gc4u
    @user-xi2vo4gc4u Před 3 dny

    Mr Kapito a man himself he doesn't fear nothing .He is so intelligent

  • @user-vt5cf3dw1l
    @user-vt5cf3dw1l Před 4 dny +1

    Good explanation without taking politics but only justice ⚖ landilani ulemu Mr John Kapito😊😊😊

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk Před 8 měsíci +7

    Big up Bwana Kapito, you are indeed a great man, I have really enjoyed your explanations 🔥🔥🔥🔥

  • @user-fg8zw2bf4m
    @user-fg8zw2bf4m Před 8 měsíci +3

    Very clear message Mr Kapito may God bless you and your family and God bless Malawi country

  • @mkhulukinyata5198
    @mkhulukinyata5198 Před 8 měsíci +2

    Well spoken Mr Kapito..Indeed Malawi tikufuna anthu wolankhula dzokupsa ngati momwe alankhulira Mr KAPITO apamu

  • @AllanMwakalenga-wn5ib
    @AllanMwakalenga-wn5ib Před 8 měsíci +2

    Kapito umakwana... If possible mungoyima pa u president.. we will vote for you

  • @alicekalupsya7149
    @alicekalupsya7149 Před dnem

    Ur a man full of wisdom.

  • @user-iy8vi7nn8r
    @user-iy8vi7nn8r Před 8 měsíci +4

    Good explanation sounds like izeck somewhere (kukagwirana ndi azungu 😅😅😅 nice one Mr kapito

  • @jonas-xh4hz
    @jonas-xh4hz Před 9 hodinami

    thank you sir kapito for your explanation

  • @williamskondowe8795
    @williamskondowe8795 Před 8 měsíci +3

    Respect Mr kapito otsaopa ,otsapweketsa we're all malawian don't fear lf there's justice

  • @user-hu7qs5be4j
    @user-hu7qs5be4j Před 14 dny +2

    Mr kapita you're true leader

  • @jaydee1236
    @jaydee1236 Před 8 měsíci +1

    Brilliant ❤ Mr John kapito

  • @user-id9df1kn1i
    @user-id9df1kn1i Před 8 měsíci +2

    Kapito your e a big man ayi pano ndiye ku Malawi sikulibwno ayi.

  • @user-ur2pf9ts2p
    @user-ur2pf9ts2p Před 7 měsíci +1

    Thank you Mr kapito mwanena zothandiza ziko la malawi Kodi achakwera mkuva please pasto mrungu akuyang,oneni

  • @user-eu1qs1eu5q
    @user-eu1qs1eu5q Před 8 měsíci +5

    Mr kapito ukunena zoona koma nkhani yimozi yonkha ndiyankhepo.
    Chilima sangayendese boma ndimunthu wonama kwambiri. Ndiye ngati mutsogoleri ali ndiboza sangatumikire anthu.
    Chilima ndi chakwera ndichimozimozi.
    Chilima ngati akanankhala kuti akufunila zabwino amalawi bwezi atatuluka mu MCP chifukwa akanamuwuza chakwera kuti zimene tinauza anthu kuti tiwachitira sizikuchitika naye ali mphee
    Choyamba kuyendesa ziko ukhale wa zeru and kuzichepesa kwa amene anakukweza. Kuopa Mulungu.

  • @lame8
    @lame8 Před 8 měsíci +2

    Zimangovuta koma chaka China tizapeza wabwinoyo❤ msogoleli wabwinoyo is our hope tizabowoleza tili ndi anthu azelu kumalawi ambiri

  • @JUMAHSabiti
    @JUMAHSabiti Před 5 dny +1

    Good explanation posatengela ndale ❤ koma chilungamo chokhachokha

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y Před 8 měsíci +1

    Good explanation uncle. The Country need people like you not Chakwera,He must go back to his church not rule the country. The citizens are suffering alot because of him.

  • @stevenchidathas4477
    @stevenchidathas4477 Před 8 měsíci +1

    I like this Man, Mr Kapito keep on😊

  • @greymasha838
    @greymasha838 Před 8 měsíci +1

    God bless you and keep it up and this is well said

  • @MikeMadeya-xm4uy
    @MikeMadeya-xm4uy Před 8 měsíci +2

    Mr kapito please 2025 please stand for people

  • @EliahLetulo
    @EliahLetulo Před 7 měsíci +1

    Kma mr kapita you are the great man ❤😂

  • @allanbanda4388
    @allanbanda4388 Před 8 měsíci

    100% Mr man matiimilila ifeyo anthu amene tilibe kuthekela kofikitsa nkhawa zathu koyenela kupititsa nkhawa coz anthu tilinazo zolankhula zodzadza mitima komaso chilungamo dziko lamalawi lofunika fix kugwedeza kukhutchumula nyansi tikhale ndiatsogoleli osadzikonda moonjeza amene amalimbikitsa timbamva ma offence ndicholinga chofuna kukhututsa mimbazawo kumamupsinja munthu angakhale olimbikila paiye yekha km Mmmm oky god bless you Mr kapito please musakakhale pansi mubweleso kumalankhula osaopa please thanks

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 Před 8 měsíci +2

    Bravo kapito!...respect

  • @douglasturner2992
    @douglasturner2992 Před 7 měsíci +1

    You deserve to be a leader...

  • @LovelyAzaleaFlower-uc8vr
    @LovelyAzaleaFlower-uc8vr Před měsícem

    Well explanation, Malawi needs such people

  • @user-ej5mc5cj8f
    @user-ej5mc5cj8f Před 8 měsíci +1

    Big up boss man... you're a great man

  • @CeciliaKamanga-mx9dc
    @CeciliaKamanga-mx9dc Před 19 hodinami

    Bravo kapito 100% agree 👍

  • @FernandosLuciano-bb9or
    @FernandosLuciano-bb9or Před 8 měsíci +4

    Uwuwu ndi kantho kapena chilango cha mulungu pochosa msogoleli wabwino peter ndijuika mbava ngothi ndizisilu zones zili mu tonse palibe chomwe chisinthe mpaka 2030

  • @MuhammadSamson-yz1kl
    @MuhammadSamson-yz1kl Před 8 měsíci +2

    Respect kapito osaopa achakwera ndi nyani

  • @petertukula1649
    @petertukula1649 Před 8 měsíci +1

    Mr Kapita Bravo.... awa ndi mau

  • @user-vf9oz7jq6r
    @user-vf9oz7jq6r Před 2 dny

    Bwana kapito kuzang"alula khokhooo

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr Před 13 dny

    True Malawian, Mr Kapito. Okumbira mnzake dzenje, adzagweramo yekha. Lero anadzikumbira okha dzenje ku IMF.

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv Před 2 měsíci

    Great ones Mr kapito

  • @Mfwanayo
    @Mfwanayo Před měsícem

    This Mr Kapito why he's true and direct like this.......shaaaa ndipo ndamkonda bwanj.....in Malawi we also have brilliant and straight people this like

  • @user-zj2dr2rp1e
    @user-zj2dr2rp1e Před 8 měsíci +3

    Brian ndi bambo kapito, boma ili ndi masanje eni eni, ndipo ukunena zoona bambo kapito, Chakwera sankhadziwa kuti angalamule dziko, mu mutu muli gwa! Sadziwa chilichose.

    • @charlesmuwanya7845
      @charlesmuwanya7845 Před 8 měsíci

      The real situation. Mr kapito is a soothsayer. He doesn't mince words. He calls a spade by its name.

    • @natashayohane
      @natashayohane Před 7 měsíci

      Zowona m bomamu muli nyasi

  • @ammaarahkhota7939
    @ammaarahkhota7939 Před 7 měsíci +1

    ACHAKWERA AKUFUNA KULEMERA SINANGA AKUDZIWA SAKHALANSO PA MPANDO. PALOWANSO ENA .NDIYE OSAMADABWA RATE YAKUNJAILI KUTI .UTSOGOLERI SASITHA NGATI MALAYA .MAPETO AKE ALIYENSE AZINGOLOWA CHOLINGA CHOTI NDILEMELELETU SINANGA CHAKA CHAMMAWA AKULOWA ENA. AWA NDI MAVUTO AWAYAMBA DALA. VUTO NDI IEFE OKHALA KUMUDZI.

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 Před 8 měsíci +1

    More fire mr Kapito🔥 🔥 🔥

  • @George-zd5le
    @George-zd5le Před 8 měsíci

    Sir Kapiti ndinu munthu wanseru. Genius man

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w Před 8 měsíci +7

    We're together mr Kapito

    • @user-qg6su9rx2k
      @user-qg6su9rx2k Před 7 měsíci

      Kodi akapito amagwira ntchito yanji kodi abale

    • @user-qg6su9rx2k
      @user-qg6su9rx2k Před 7 měsíci

      A brian banda mulibenso nzeru ndiyesa ndi mankhwala oyeretsa thupiwo mwina ,kodi ndege ku malawi zinasowa liti?

  • @ChomeNgondolo-uh5mu
    @ChomeNgondolo-uh5mu Před 8 měsíci +2

    😂😂kugwilana zanja ndi mzungu mkumatinamiza ife kuti zinthu ziyenda 😂😂😂

  • @chikaonekarh
    @chikaonekarh Před měsícem

    Our own KAPITO mumatiyimilira koma kunsanva a President,ndakusokosela mkulinga utava!
    Zayekha adaviyika nsima madzi musiyeni timuona 2025 Chakwera

  • @ChristinaNyirenda-zb1if

    Good Mr kapito

  • @jeffchikwapata6933
    @jeffchikwapata6933 Před 13 dny

    I like Mr kapito's explanation

  • @MikaNamwada
    @MikaNamwada Před 13 dny +1

    Well said kapito🔥🔥🔥🔥🔥

  • @DoreenAllan-tg1dz
    @DoreenAllan-tg1dz Před 8 měsíci +1

    Mr Kapito muyakhura chilungamo

  • @FanscioDancun
    @FanscioDancun Před 11 dny

    This man is speaks the truth

  • @MahmoudZebron
    @MahmoudZebron Před 5 dny

    Ndilibe mau mbili bwana kapito you're good man you're a m'dala 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @Goliath461
    @Goliath461 Před 8 měsíci +2

    Paja nyau yonunkha manyi ija amati zinalake chani?la chakwera tachosa koma la nyau yonkha ija😂😂😂

  • @DannieChimenya
    @DannieChimenya Před 13 dny

    Mr kapito God bless you sir

  • @AndersonChimwala-hz4so
    @AndersonChimwala-hz4so Před 8 měsíci +2

    Big up mr kapita malawi need people like you.

  • @phillimonzgambo1663
    @phillimonzgambo1663 Před 8 měsíci

    Good speech kapito

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 Před 8 měsíci +1

    A chakwera Ali ngati chipilala 2angokhala mu office ndiye zinduna zano zimangobwela zainani apa chakwera ku zaina palibe chomwe akuziwa dzikoli akuyendeza ndi zinduna pamodzi ndi banja lawo

  • @bigmount563
    @bigmount563 Před 13 dny

    I am sorry for my self I missed this program, but I koma Mr kapito Mulungu azikudalisani ngati chakwer a sakumva ixi afe ndithu

  • @ChimwemweMarkBanda-yj7yk
    @ChimwemweMarkBanda-yj7yk Před 8 měsíci +2

    Pempho Mr Brian Banda. Would you please visit anthu anchimidzi kuti muone how pple are suffering and see how they are surviving with every days life. Anthu amene adavota akufatu😢

    • @innocentkapachika6591
      @innocentkapachika6591 Před 8 měsíci

      Take this comment very seriously. Take a chance and visit voters in the the remote areas. For example, come and visit Dedza South Constituency the most Least Developed Constituency in Malawi

    • @user-zz3lf9qd5m
      @user-zz3lf9qd5m Před 8 měsíci

      Eish ndipo very pain full vote lako lomwe kumagona osadya😢

    • @alexdausi5167
      @alexdausi5167 Před 8 měsíci

      ​@@user-zz3lf9qd5mkoma Mesa amati tizidya katatuh everydey

  • @user-tn2qg1vs9j
    @user-tn2qg1vs9j Před 8 měsíci +1

    Appreciate bwana kapito

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 Před 8 měsíci +1

    Boma lavuta ili pangolini amanena zoona respect the DC

  • @user-zg7iw8kq4r
    @user-zg7iw8kq4r Před měsícem

    Mr kapito please imilani u president pano mboma mwazaza a yes bwana okhaokha anthu a mamina mmutu

  • @user-hu8vp4wt7j
    @user-hu8vp4wt7j Před 8 měsíci +1

    Mr kapito i respect you 🙏

  • @natashayohane
    @natashayohane Před 7 měsíci +1

    Zovetsa chisoni mmene yatulukila maina oti apindule ndi zipangizo zotsika mtengo pa fumu dzina limodzi

  • @lukeshawa-mv6ed
    @lukeshawa-mv6ed Před 8 měsíci

    Yea man of confidence

  • @gkay-striker
    @gkay-striker Před 7 měsíci +1

    Chakwera Ndi Galu Kwambili We Are Tired Of Him

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf Před 16 dny

    Bambo Kapito now you are Talking. Keep it up

  • @user-oh6qd3xx4i
    @user-oh6qd3xx4i Před 7 měsíci

    Bravo Mr kapito

  • @MaxwellMustafa-ec8fc
    @MaxwellMustafa-ec8fc Před 8 měsíci +4

    God bless you sir Mr kapito

  • @user-yl5gk4od3s
    @user-yl5gk4od3s Před 12 dny

    Good one

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 Před 8 měsíci +1

    Respect Mr kapito

  • @user-fk3vw7ck3z
    @user-fk3vw7ck3z Před 7 měsíci +1

    Us Malawians we need to have readers from over seaze

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 Před 8 měsíci +1

    50 years plus depend on foreign aid....i wish bingu was alive

  • @user-dr7ct2zt8n
    @user-dr7ct2zt8n Před 12 dny

    Mr John kapito keep on trying to assist the blind

  • @madalitsokalulu2720
    @madalitsokalulu2720 Před 12 dny

    Mr Kapito katswiri

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Před 8 měsíci +1

    M'manja mwa akapito pwa pwa pwa

  • @mariezorgen7735
    @mariezorgen7735 Před 8 měsíci

    Thanks alote

  • @mphatsocaseywilson9113

    Big up

  • @HanishaissahKagansa
    @HanishaissahKagansa Před 8 měsíci +3

    Ndizoonadi alowa m,boma alibe Maso mphenye then nsamadziwa kuti kuyendetsa dziko ndichinthu chomvuta

  • @blessingsphiri878
    @blessingsphiri878 Před 7 měsíci

    True about fac leadership

  • @khalifacalvinajass9998
    @khalifacalvinajass9998 Před 8 měsíci +2

    Akulu awa ndagwilizan nawo kwambir

  • @user-jg9ec5dw3j
    @user-jg9ec5dw3j Před 7 měsíci

    Bele munayamba inu a Kapito tilodala.

  • @alexvwalika2242
    @alexvwalika2242 Před 6 měsíci +1

    Mr kapito inutu inutu mukukamba dzeni dzeni

  • @user-qm1qb2jp4s
    @user-qm1qb2jp4s Před 7 měsíci

    Bravo kapito chakwera and his government they have failed to read 🇲🇼

  • @frankiechasokoneza5802

    Nde wina adzikati Chakwera yemweyoooo akhomedwa

  • @user-hq6dq7zr1e
    @user-hq6dq7zr1e Před 13 dny

    Izizo ndi zoona,Koma ku malawi sikudzatheka muika bwanji munthu osaphuzila Kukhala president,inu mmaona ngati m'busa ndiwomukhulupilira kwambili,munatilakwila kwambili ndipo mulungu azikukhulukilani anthu inu

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před 8 měsíci

    Kkkk kugwilana chanza ndi mzungu ,koma a Kapito

  • @alexanderkhomera8154
    @alexanderkhomera8154 Před 8 měsíci

    Nice Kapito

  • @user-np3ko4mc4q
    @user-np3ko4mc4q Před 7 měsíci

    Exactly 💯

  • @user-tw9nl6ks9d
    @user-tw9nl6ks9d Před 7 měsíci

    True talk

  • @YohaneChimkango
    @YohaneChimkango Před 5 dny

    Mr kapito mumakwana mukunena zoona

  • @andreabrighten301
    @andreabrighten301 Před 8 měsíci +1

    That's true mr kapito

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 Před 8 měsíci

    That's true chakwera has failed eeeich Malawi 😢 need good leaders

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 Před 8 měsíci +2

    How can you say Chilima has not been tested and yet he was arrested for thieving yet still working getting payed on Malawian tax payers? Was he not suspended?

  • @user-tm1gm4dg2s
    @user-tm1gm4dg2s Před 8 měsíci

    Truth only, kapito wabwera

  • @user-re5of7tl2o
    @user-re5of7tl2o Před 8 měsíci +2

    Palibe angamutsutse mkuluyu

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Před 8 měsíci +3

    Cakwera ndi wasatanic sAngamve china chiri conse sangaone Kuti anthu akuvutika akufuna anthu afe ndi njala kumidimakupite magazi ambiri

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela Před 5 dny

    Time to say truth has come

  • @mkhokholasamuzonda5094
    @mkhokholasamuzonda5094 Před 8 měsíci +1

    iwe chakwera ndi chilima mboleizamanu anthu anga akubvutika kwambiri mwanva...

  • @StabbingsJenda
    @StabbingsJenda Před 4 dny

    He is agreat man

  • @user-lg2oq6nd2l
    @user-lg2oq6nd2l Před 8 měsíci +1

    Kapito machine