Limpopo FM shaa akukamuphela ku Nkhatabay Kalindo Kamlepo kumuphela ku Mchinji Ntanyiwa wayiphedula

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 21. 06. 2024

Komentáře • 101

  • @elizasingano
    @elizasingano Před 5 dny +11

    Washing from SA but following you everyday keep up good work and God protect you , born kalindo ,kamlepo kaluwa and all malawians we are together in this situations

  • @ChimwemweMagombobanda
    @ChimwemweMagombobanda Před 5 dny +8

    Keep updating us comrade mtanyiwa we proud of you.

  • @FloridaMakwinja-eq2ek
    @FloridaMakwinja-eq2ek Před 5 dny +5

    In my prayer every day
    Love you always Bro Bon
    Mwana wolimba mtima

  • @MustapherDavie-su3nk
    @MustapherDavie-su3nk Před 5 dny +8

    Bakili Muluzi tv ikuti anthuwa akatuluka ayezedwe poison

  • @OssmanAbubaker-xu7ql
    @OssmanAbubaker-xu7ql Před 5 dny +6

    Zoonadi Chakwera sanali mbusa koma ndi mfiti

  • @RobertKingsleyMarevon
    @RobertKingsleyMarevon Před 5 dny +3

    Thanks Mr comrade for your update

  • @CollinsNthete-kq8td
    @CollinsNthete-kq8td Před 5 dny +6

    We love u mtanyiwa

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 5 dny +5

    Eeeeeee koma Malawi mukuyenda satana ndi mapazi zoti Mulungu alipo anaiwala ali busy kudzikundikira chuma ngati adzapita nacho kwa Mulungu help us lord

  • @EllenMphangamu
    @EllenMphangamu Před 3 dny

    Thanks mr comrade for ur update

  • @FrancisMbewe-xn2pl
    @FrancisMbewe-xn2pl Před 4 dny

    The dangerous child will come back I live 💪🔥

  • @MustafaHenderson
    @MustafaHenderson Před 5 dny +7

    We need our Kamulepo n Bon kalindo now don't kill our heroes pls

  • @DianaKachina-ws4hm
    @DianaKachina-ws4hm Před 5 dny +2

    Your protection upon us Lord we need you more than before Malawi waola uyu

  • @GibsonDamzy-ek8vg
    @GibsonDamzy-ek8vg Před 4 dny

    Ntanyiwa umanena zoona zake keep it up

  • @HomeBoyKauta
    @HomeBoyKauta Před 5 dny +1

    We've to proud of you bro comrod

  • @MbisaOngani-g6o
    @MbisaOngani-g6o Před 5 dny +1

    Umandikumbutsa early 90s aKamlepo pa Chanel Africa kuiphwasula MCP ndi Zondani Sakala

  • @EvanceLumeyo
    @EvanceLumeyo Před 4 dny

    Malawian never rest campaign yokonzekera zisankho zamu 2025 tiione kuti iyende bwanji

  • @augustMag
    @augustMag Před 4 dny

    I believe Mr DC and Kamulepo he is back home alive ❤ Limpopo FM radio 🔥🥳

  • @TryceMagombo-sh7kb
    @TryceMagombo-sh7kb Před 5 dny

    Timakunyadira heavy and we are following u

  • @josephkuseke4166
    @josephkuseke4166 Před 4 dny

    Rise Malawi we can not be prisoners in our motherland.

  • @ZaccheousPetrol
    @ZaccheousPetrol Před 5 dny +1

    Try your best comrade.... Kaluwa komanso kalindo.... Update.

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Před 5 dny

    The best Radio station in southern Africa..

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz Před 4 dny

    Ayelekeze kuwapha zingooneka zokha Malawi muno

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Před 5 dny

    abon nkalindo mulimanja mwamulungu yenkayo ndamene ankudsiwaw sawmoyyo wanuw mtanyiwwa good brress you orrowyess we will love you every day every time

  • @coollife-is7ir
    @coollife-is7ir Před 5 dny +3

    Ku nkhata bay police ndi prison ziri pa musipa tikamuona

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 Před 5 dny

      Pangani zomwezo bro, lets all rescue our heroes bon Kalindo and kamlepo kalua

  • @Imrandaniel683
    @Imrandaniel683 Před 5 dny

    Big man mtanyiwa mumakwana brother

  • @user-gx3xc9lk8x
    @user-gx3xc9lk8x Před 5 dny +1

    Malawi wanga akupita kut kodi😢😢

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 Před 5 dny

    Chakupha ichi antanyiwa uyu sanalibusa ndi wagule nyawu mboli zawo agalu panyapawo asadzuze mwana Nyooooooo the DC kalindo

  • @user-pf5hu2pd2b
    @user-pf5hu2pd2b Před 5 dny

    We respect you brother

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti Před 5 dny

    Zikomo bwana, following.

  • @JerryChain-cz8ru
    @JerryChain-cz8ru Před 5 dny +2

    Muzitiwuza momwe zilili

  • @kayzeesambani7153
    @kayzeesambani7153 Před 4 dny

    Ubusa wake wodyetsa ng'ombe

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em Před 5 dny

    Viva Ntanyiwa, ur a Hero

  • @user-hg2cw1om1p
    @user-hg2cw1om1p Před 4 dny

    Proud of you mtanyiwa

  • @alicegama8138
    @alicegama8138 Před 4 dny

    Kalindo atuluke ndimoyo akangomwalila pazavuta

  • @Jaydee-mw4
    @Jaydee-mw4 Před 4 dny

    Mfiti ngat chakwela sindinaionepo ai galu yamunthu chakera

  • @BrightonKamwendo-db1ci
    @BrightonKamwendo-db1ci Před 5 dny +1

    Koma chakwerayu akuziwa kuti posachedwapa akhala munthu wamba!!!!! Zonsezi anthu azawabwezera mulungu simunthu and sangalore Wana wake azuzike chilango ichi

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Před 5 dny

    Ambuye tetezani m, bale wathu born kalindo

  • @JUMAHSabiti
    @JUMAHSabiti Před 5 dny

    Maso ndimakutu athu ali pa limpopo fm please let us know everything 🙏 ❤ ♥ 🙌 😢

  • @janemanyamba7201
    @janemanyamba7201 Před 4 dny

    Mulungu atithandiza

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Před 5 dny +1

    Za ubusa aaaaa ndakaika mwina kapena zomwezo za Bushiri zo mwina

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 Před 5 dny

      😂😂😂😂😂😂😂, ndemwati zandani akulu !?

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs Před 5 dny +2

    Koma abale kumalawi ndichan kwen kwen eshiiiii

  • @jangiya03
    @jangiya03 Před 4 dny

    Afuna aphe anthu angati tikulilabe mizimu ya anthu 9 afuna apheso anthu ena Mulungu alowelelepo ndithu

  • @JhdaLifi-vu9sd
    @JhdaLifi-vu9sd Před 5 dny +1

    Wellcome ntanyiwaaaa

  • @MusaAllain
    @MusaAllain Před 4 dny

    Update us everyday

  • @HazlathAdmack
    @HazlathAdmack Před 4 dny

    Km guys kwavuta ndikumalawi asa mupha athu bwanji ngati mbuzi😢😢😢

  • @PatrickMangani-p2r
    @PatrickMangani-p2r Před 3 dny

    Ummmh life in Malawi is so bad.

  • @AdamLano-sj1gv
    @AdamLano-sj1gv Před 5 dny

    Limpopo no 1

  • @StanleySabantinegamah

    Km comrade ulemu wanu

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo Před 5 dny

    Km akangofa kuvuta

  • @CollinMkhonza
    @CollinMkhonza Před 5 dny +1

    Koma ndife amalawi atundu wanji omangoyang,anila zinthu zopusa Ngati izi, .....not even take action

    • @PaulineKamwana
      @PaulineKamwana Před 5 dny

      Ndipo ineyo funso limeneli likundivuta Moyo mwanga😂, Ambuye imvani kulira Kwa ana anufe😂

  • @MoosahTiger
    @MoosahTiger Před 4 dny

    Mumakwa ntanyiwa

  • @patrickscott9086
    @patrickscott9086 Před 5 dny

    Kma ndye aliyese wonena chilungamo azisowa bas? Malawi wokomela tonse ujaa😢😢😢😢😢😢😢

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Před 5 dny

    Mtanyiwwa osawopha bwanji ngani yonkusana shikangawaw tiutseni soona sandege}

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 3 dny

    Boma ilili ndilirakupha ndithu bwanji akamumanga munthu amangomuyendesa wuku ndi wuku cholinga Kuti amuphe bwino MCP ndi akupha mopanda manyazi

  • @PreciousPhiri-jr4sd
    @PreciousPhiri-jr4sd Před 5 dny +1

    Kma zinandiwawa ndkamaganiza zaimfa yachilima

  • @user-bu5gt7qu2h
    @user-bu5gt7qu2h Před 5 dny

    They'll pay for it one day

  • @RabsonSabit-nc5ds
    @RabsonSabit-nc5ds Před 4 dny

    Komatu zaonjeza kumalawi

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 5 dny

    Amalawi mumkafuna kusintha , lerotu ndendizimenezi mukuti bwa!?, kkkkkkkk, koma kumenekoo galu iweee

  • @user-bc3tx3wp1i
    @user-bc3tx3wp1i Před 5 dny

    Why malawi wanga ine 😭😭

  • @GodfreyMitiyani
    @GodfreyMitiyani Před 5 dny

    Eshi! God knows

  • @TryceMagombo-sh7kb
    @TryceMagombo-sh7kb Před 5 dny

    Asayerekeze kufa kalindo kuvuta

  • @SimonLikwangulo-xq9oz
    @SimonLikwangulo-xq9oz Před 5 dny +1

    Noooo dzikoli ndilatonse koma mcp ikulakwitsa serious apha angati

    • @user-rf4br1fv2z
      @user-rf4br1fv2z Před 4 dny

      Amwene kupha munthu sichithu chapafupi munthu si khuku ai zinazi mmmmm

  • @EphraimMokwebo-yo7fs
    @EphraimMokwebo-yo7fs Před 5 dny

    Tikayasa moto nyumba ya namachende chakwera

  • @user-em1qi8kj9h
    @user-em1qi8kj9h Před 5 dny

    Malawi akumvesa chisoni mu Africa muno....pa chikhalidwe chomwe akupanga abusawa.....ngti akutelo pa nations pa kupha anthu...nanga bwanji ku mpigoko anathako anthu angati?

  • @KondoweAmini
    @KondoweAmini Před 5 dny

    Kodi mukudikila afe nde muziti tichite bata zachani tiyeni koko

  • @tulab-447
    @tulab-447 Před 5 dny

    Malawi Malawi zikolankakandiuchi lija

  • @AubreyKantenga
    @AubreyKantenga Před 4 dny

    Km malawi waopsa abale

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 Před 5 dny +1

    galu mtanyiwa kunamiza mbulu zako izo😊

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před 5 dny

    Lakanika kuyaka moto chilima atamwalila bwanji munali kuti akulu inu muzilakhula bwino koma aaaa

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi Před 5 dny

    Koma kalindo musiye amalawi anadalila kupotaa mcp

  • @twavysibale4751
    @twavysibale4751 Před 5 dny

    Anabweletsa asilikali akurwanda 500,why?

  • @user-jd9yz5hp7y
    @user-jd9yz5hp7y Před 5 dny

    Mademo amenewo adzakhala olujika ku State House kukapanga mmphindikilo kumuchotsa Chakwera munthu oyipa kwambiri

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 5 dny

    Koma bomali likidziwa kut kuli Mulungu wamphamvu yonse?

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 Před 5 dny

    Galu kwabasi nkhankhankha uyuuuuuuuuuuu ndimapulani awo opusawo abvutika okha eeeeee

  • @user-kl9id7kx3m
    @user-kl9id7kx3m Před 4 dny

    Osamanamiza anthu ndi zinthu zopanda umboni zanuzi, magaye. Shupiti! 😠😠😠

  • @CharlesChilembwe
    @CharlesChilembwe Před 5 dny

    Komatu please musatibweletsele chisokonezo nikhani zanuzo ndinu atola khani kapena andale?ingoyambitsañi chipani osati zomakhala ngati atola khani muli andale ingotulukani poyela

  • @RamseyWilson-c5v
    @RamseyWilson-c5v Před 4 dny

    This is not pastor at all

  • @GiftPilan-pt9or
    @GiftPilan-pt9or Před 4 dny

    Koma mabodza omwe mumafalitsa apapa inu alimpopo fm mukafika nawo pat????ndimanyazi omwe mulibe shame on you

  • @GibsonBakha
    @GibsonBakha Před 5 dny +1

    Kamabodza iwe uzinamiza zitsiluzomwezi kkkkk

  • @HazlathAdmack
    @HazlathAdmack Před 4 dny

    Km guys kwavuta ndikumalawi asa mupha athu bwanji ngati mbuzi😢😢😢

  • @PatrickMangani-p2r
    @PatrickMangani-p2r Před 3 dny

    Ummmh life in Malawi is so bad.

  • @HazlathAdmack
    @HazlathAdmack Před 4 dny

    Km guys kwavuta ndikumalawi asa mupha athu bwanji ngati mbuzi😢😢😢