CHIHANA NDI NANKHUMWA AVUTA UKU |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 21. 06. 2024

Komentáře • 123

  • @Edson-sj8vn
    @Edson-sj8vn Před 5 dny +11

    Mawa lisathe kalindo amasulidwe chakwera &usi tionana 2025

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt Před 5 dny +7

    Nduona ngati akuopaa kkk ufulu weni weni tilibe kweni kweni

  • @ChristinaLigomeka
    @ChristinaLigomeka Před 5 dny +5

    Amene adzapite ku mapephero amenewo mutu wake suyenda bwino mwalo mopangitsa mapephero olapa mudzikapephera chani Mulungu akamva zimenezo magazi akuyenda Malawi mo simukuwawona, mwazi wa anthu osalakwa ukufuulawo simukuoona mapephero achani mudziwerenga bible before kuchita zithu za ziiii mudzikapha Ana azanu ngati khuku mtendere simudzaupeza mpaka mutabwera poyera kulula

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri Před 4 dny +4

    Big up Mr Chihana though sinamveere zomwe mwayankhula ndangowona anthu akuyamikira

  • @JohnsonRannel18
    @JohnsonRannel18 Před 5 dny +10

    Ufulu wake ndiye wutiwo mungomanga adzanu ndi kuphaso azanu

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 5 dny +4

    Dzaka 60 really 😢😢😢 Malawi udzakula liti 60 years still kuvala pampaz shame on you kunkuyu

  • @JIMMYWATHONJE
    @JIMMYWATHONJE Před 5 dny +3

    Straight to the point Mr Chihana

  • @user-jd9yz5hp7y
    @user-jd9yz5hp7y Před 5 dny +3

    Anthu amenewo ofufuzawo pls Mr Chihana muwonetsetse kuti asachokele ku Butchery kumene amatinamiza kuja kuti akagura Feteleza anthu akuba awa ndi kupha oyipa a MCP

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf

    Memories will remain fresh even after 100 years. Let's remember them in a special way and continuously pray for their Souls to rest in eternal peace.

  • @PaulMwachande
    @PaulMwachande Před 5 dny +3

    Nankhumwa wayamba kulankhula chifukwa sanamusankhe kukhala vp

  • @BillyKalambo-jx3vf
    @BillyKalambo-jx3vf Před 4 dny

    Nkukuyu ungotaya nthawi kulankhula zopusazo asakuziwa kuti Chakwera ndi nsogoleri ndani sangalalani ndi gulu lanulo LA uchigawenga mcp 😭😭😭😭😭🐊🐊🐊🐊

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 5 dny +3

    Good Mr Chihana

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Před 5 dny +4

    Akuna adzakondwerere kuti zomwe.amafuna zatheka pokupha chilima

  • @user-zi8pj5ey4t
    @user-zi8pj5ey4t Před 5 dny +3

    A kunkuyu mzimu wa witika muli nao pamutupo

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před 4 dny

    Aaa atenga anthu osadziwika cholinga choti adzattwudze mabodza ANTHU AKADZAMANENA KUTI CHILUNGAMO ACHIBUTSA ADZIMANGIDWA NDE MCP IMENEYO NDEGE YOTI DZIPANGIDZO DZINA ANACHOTSA MO MA PHONE KUTENGA KUMAFUFUDZA POKAPELEKA MA FON AFUTAMU CHILICHOTSE AAAAA amalawi mufunilanji omboni wina apa zawoka dzokha kuti chiwembu chokodza MR CHIHANA THANKS U SO MUCH KOMA A MCP AKATULUTSA BODZA LAWOLO ngati inu mudzayankhule potsusana a MCP mudzayembekedzele kumangidwa CHIFUKWA PANO DZIKO LA MALAWI LAFIKA ULAMULILO WACHIPANI CHIMODZI CHAKAKA NYALENDA NDADZANU ENA MUNATILAKWILA AMALAWI MUDZIWE DZIMENEDZO

  • @EdwardMukholi
    @EdwardMukholi Před 4 dny

    Nanga anthu amene mukuwamangao mukutathauza kuti mukulira bodza bwanji Mr president

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před 4 dny +1

    Kodi ufulu ulikuti, ku malawi kulibe ufulu chifukwa achina kamulepo ndi kalindo mudawamanga chifukwa chomenyera ufuluo, komatu Boma ili litipweteka ndithu

  • @user-kr4wb2th9i
    @user-kr4wb2th9i Před 4 dny +1

    Anawo akhala osabereka

  • @HeedsonJere
    @HeedsonJere Před 4 dny +1

    Chihana anamumana udindo ku tonse allias

  • @OmarManjawira-up3ns
    @OmarManjawira-up3ns Před 5 dny +1

    Chihana well spoken,

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před 4 dny +1

    Iwowa mituyao sigwira kunkuyu ndi chakwera wakoyo ndinu mbuzi mukati ufulu odziramulira what do you mean? Momwe mukuyendetsera boma lero mukuona ngati dziko liri pa ufulu popeza muli busy kupha anthu komaso kumanga anthu omwe akukudzudzulani ndiye nkumati dziko liri pa ufulu inu agalu kwabasi zigawenga

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Před 5 dny +1

    Agalu mumuziwaso Mulungu

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Před 5 dny +1

    Muchoseko zaka 4 zomwe mwalamulilaz kulibe ufulu ndiye kt tili ndi zaka 56 xaufulu

  • @user-hp4rl8cv3h
    @user-hp4rl8cv3h Před 4 dny +1

    Chihana very good

  • @robertnambazo9936
    @robertnambazo9936 Před 4 dny +1

    Akuziwa kuti anthu sazapitako awatuluka anthu awa

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Před 5 dny +1

    Agalu kumkuyu mapwala ako

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p Před 4 dny +1

    Bodza limenero manyazi achakwera

  • @GRACIOUSKENAN
    @GRACIOUSKENAN Před 5 dny +6

    Boon kalindo ndikumufuna osat inuo,chokan apaaaa

  • @LamieTiger-ff7cj
    @LamieTiger-ff7cj Před 5 dny +1

    Chakwera mukanangot kukhala Za satanic metsa inu ndi satana

  • @ulemujumbe8501
    @ulemujumbe8501 Před 4 dny

    Bring back Bon Kalindo

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa Před 4 dny

    Dzaka 60 za democracy minus 4 ya chakwela tikusangala dzaka 56 coz dzaka 4 za chakwela kulibe ufulu

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet Před 5 dny +2

    Iwe mukuyu matako yako wapulika chakwel nayo pathako pake

  • @GiftManuel-er7yh
    @GiftManuel-er7yh Před 5 dny +1

    Amaio akunama mwana sangabadwe kutha miyedzi 6 asanamupitenao ku chipatala ku scale

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 Před 4 dny +1

    Mwamasukatu mpaka zikhulupiliro zosakhala bwino? Globe vaccine akukupatsani thandizowo ndi ayesu? OK.

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Před 5 dny +1

    Ukuona ngati anthu akukukhululukini mwanya akupha

  • @chimwemwekamwana787
    @chimwemwekamwana787 Před 5 dny +1

    Mukuopa kut anthu akutukwanani.. nanga mmene mukuoneramu amalawi tili pa ufulu ifeeee.. ai muli ndi manyazi ndithu

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 3 dny

    Musatinyasepo apa ufulu womwe mukunena ndiye wuti Malawi wake wuti womwe Muli wufulu za ziiiii

  • @JacksonChayibu
    @JacksonChayibu Před 5 dny +2

    Ife tikufuna bon kalindo mawa atulusidwe

  • @JamesOsman-cz9cw
    @JamesOsman-cz9cw Před 5 dny +2

    Mcp people machende anu nonse

  • @yusufbakali
    @yusufbakali Před 5 dny +1

    Kukhuyu zikhare chimwendo chakwela osewa adyeretu chaka chamawa chawoo palibe anthu tinavota kare kufa kwa chilima

  • @user-rd2ft5uk3q
    @user-rd2ft5uk3q Před 5 dny +2

    Ufulu wake utiwo

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před 2 dny

    Kunkuyu uzipemphela kwambili kuti boma lisasinthe ...boma kungosintha iwe uzafela kumdende ....unapha allan witika chifukwa cha mkazi .....munthu wopusa iwe kwambili mbuzi

  • @eliaskhofielias8152
    @eliaskhofielias8152 Před 5 dny +1

    Ngakhale atapanga zokoma bwanji a mcp kuphiphilitsa za imfa ya chilima even atati apereka nseu wot chilima road sadzawinabe awa.ndinu okupha okupha basi munapha nzanu mbili sizafufutika.

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 Před 4 dny

    Ziko la Malawi lakwanisa zaka 60 pokweza pasogolo umphawi wathu

  • @storytambala6088
    @storytambala6088 Před 4 dny

    Hmm iwe Kunkuyu, ndi Chakwera musatiputsitse apa.

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 Před 5 dny +1

    Iweyo Kumkuyu ndi Chakwera wakoyo God must punish you, Mukukamba za kukhudza Maliro a Dr Chilima chonsecho mukungotiphimba kumaso.

  • @ElizabethKhosa-gx3wt
    @ElizabethKhosa-gx3wt Před 4 dny

    Chingawenga choopya cha chakwela panopa chikufuna kuphe bon kalindo

  • @user-tn2qg1vs9j
    @user-tn2qg1vs9j Před 5 dny +1

    Inu nosenu ndinu agalu kwabasi ifetu tikungo funa kuti bon Kalindo wathuyo tipaseni achainiyakefe

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 5 dny +1

    Mukut mulira maliro nanga chowangira anthu mukulira maliro ndi chan?

  • @DennisDonework
    @DennisDonework Před 5 dny +1

    Afiti inu palibe ufulu nanga born kalindo akutani ku selo

  • @ShaliyaMusa
    @ShaliyaMusa Před 4 dny

    Ndiwomwewo mfiti. Chikwelayo paribe kikna

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py Před 5 dny +1

    Ofufuza akhare a independent osati oziwana ndi mcp ai sipamveka black box ili kutiko choyamba?

  • @josephchirwa-jt7jx
    @josephchirwa-jt7jx Před 5 dny +2

    Kodi ku malawi kuliso ufulu?

  • @feehasaidid.r.d
    @feehasaidid.r.d Před 5 dny +1

    Wanena zoona chihana

  • @dysonfysonchifundo2284
    @dysonfysonchifundo2284 Před 5 dny +1

    Ndipo ofufudza sakuyenera kuitanidwa kuchoka ku boma cos ndiwomwe analephela kupulumutsa anthu, in other way, boma ndilimwe lapha anthu

  • @QueneteCatundulo
    @QueneteCatundulo Před 5 dny +1

    Good

  • @user-nn7sv5yb8h
    @user-nn7sv5yb8h Před 5 dny +1

    Kunkuyu udzinena kuti presdent wakoyo wanena kuti osati walamula ai

  • @richardManemba
    @richardManemba Před 4 dny

    Ayii akupangila kt ufulu wa amalawi uchoke km osalola kungolola bas zabwelela zakale

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet Před 5 dny +1

    Inu ti onana 2025 mukutuluka inu

  • @VanPaul-sv9yx
    @VanPaul-sv9yx Před 4 dny

    Nanu tazingodurani nkhani zofunikirazo ndikumaponya apa osati ndi nkhani zopoira zomwe

  • @GeraldMkwewu-gd5eb
    @GeraldMkwewu-gd5eb Před 5 dny +1

    Chakwera ndi lwe nkukuyu agalu nose mapemphera achani fiti lnu nose ndi manganya tikulira chilima wanthu lnu mumumasure bon kalindo ndi kamulepu boma lakhaza lri mwayiwara kt mupeze ma udindo ndi chilima nose 😢

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Před 4 dny

    Akuopa kuti akakuwidwa ku 6 July 😂😂😂😂 mwabalalika makape

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt Před 5 dny +1

    Koma kachere anachulukitsa kulibe dzina lina

  • @user-mk3fy9nl2u
    @user-mk3fy9nl2u Před 4 dny

    Inunso mukuziziwa zimenezo

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před 2 dny

    Mulila bwanji poti mwachita kumupha chilima koma ndizokhumudwisa kwambili

  • @user-xm3zl5cg6x
    @user-xm3zl5cg6x Před 4 dny

    Muvesen akunena ufulu obela a malawi galuyu okukuda kukeqma

  • @TwayibuChimbama
    @TwayibuChimbama Před 5 dny +1

    Kusilamulila kwake kopa anthu

  • @mussakathumba128
    @mussakathumba128 Před 2 dny

    Komanotu kunena chilunga amalawife tikufatsa kwambiri plus ulemu too much.chakwera wationjeza akungopha anthu ngati khuku tinayenera kumuchotsa before mavoti

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll Před 5 dny +1

    Opemphera ake ndani zigawenga inu?

  • @ThomasMunyolowa
    @ThomasMunyolowa Před 5 dny +1

    Osati kuopa ku kuwizidwa

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 5 dny +1

    Chokani ana amahule inu kungokhalira umoyo wauchigawenga

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 5 dny +1

    Dzaka 60 yoh bwanji dziko lili paumphawi 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 shame

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms Před 4 dny

    Akuti muli wufulu m'malawi zoona

  • @user-nr4mi7pt8g
    @user-nr4mi7pt8g Před 4 dny

    Ma billion chikondwererowo nde tigawanepotu sizausiru apa

  • @princedetbozsmallboy1749

    Zaziiii

  • @user-nl5nk2wx1q
    @user-nl5nk2wx1q Před 5 dny +4

    KOMA BOMA LA MCP 😢😢😢
    AWA SI ANTHU KOMA AFITI ASATANIKI

  • @MatiasChimsakasa
    @MatiasChimsakasa Před 4 dny

    Komano bwanji anthu anasangalala polumbilitsa olemekezeka a vp koma 6jly ayi Kodi undiuthenga wanji mukupeleka kwa ife achinyamata

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b Před 4 dny

    Mufika kumeneko nonsenu kumeneko za chamba 6 July muzakhalamulibe moyo inu agalu eti mboloyako

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma Před 4 dny

    Masiran born kalindo kaye mukubisa chan pomumanga iyeyo

  • @user-fh7sd6gp3f
    @user-fh7sd6gp3f Před 4 dny

    Mapemphero ake ati komanso abusa achokera mpingo uti
    Please leave God alone please

  • @AndrewMukhwapa-qj4vo
    @AndrewMukhwapa-qj4vo Před 5 dny +2

    Very good a Chihana

  • @user-lr2wx5xd9d
    @user-lr2wx5xd9d Před 5 dny +1

    Following

  • @JosephKuyeli-rc9on
    @JosephKuyeli-rc9on Před 3 dny

    Or mpunga wa nyama tisadyenso?? 😢😢😢

  • @yusufbakali
    @yusufbakali Před 5 dny +1

    Mbudzi iwe

  • @DawoodIssah-mp1yi
    @DawoodIssah-mp1yi Před 5 dny +2

    Stupid you guys in chakwera team
    Mwapha chilima anthu inu mukukayankhula zautsiru

  • @user-xf6dn7pv9b
    @user-xf6dn7pv9b Před 4 dny

    Chakwera ndiwe mbuzi wamva , galu , nyani chittsru cha munthu

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Před 5 dny +1

    Well done Enoch chihana utsogoleri ndiumeneo. Tikufuna tiwaziwe anthu amene achoka ku Germany ofufuza za ngozi ya vice president ndi azathu 9. Awapeza bwanji anthu aku Germany owo aboma anene.

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem Před 4 dny

    Iwe kumkuyu ndiiwe mbuz et ufulu wake ulikut popeza mungomanga aliyese brushit zako

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Před 4 dny

    Anthu tili ndi mafunso kumene

  • @louisgolden
    @louisgolden Před 3 dny

    Kodi July yili Liti Koti muyambe kunena Za 6 July

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před 2 dny

    Kunkuyu panyapako galu iwe

  • @charlesvenacio9773
    @charlesvenacio9773 Před 4 dny

    Malawi muno mulibe umfulu

  • @ClementMinyanga
    @ClementMinyanga Před 3 dny

    Ufulu wake ulikut???

  • @user-kk4uj8ko8k
    @user-kk4uj8ko8k Před 5 dny +1

    😂😂😂😂😂

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal Před 3 dny

    Ufulu wake utiwo?????

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py Před 5 dny +1

    Inet imfa yachilima ndalota utsiku tapephera mosweka mtima akundilakhula kuti pangoz damulumuka koma anthu adandipha pondikhapa mendo zanga ndiy achakwera musamalet enafe ndi daniel tikapephera mulungu amayakha kumaloto athu mudapha inu pomukha chilima ndi zikwanje munyaaaaa nane daniel omasulira maloto kuuulurani

    • @ChristinaLigomeka
      @ChristinaLigomeka Před 5 dny +1

      😭😭😭 Km kulakwatu uku ayaluka awa akusewera ndi Mulungu km😭😭😭😭

    • @ManifoldPhiri
      @ManifoldPhiri Před 5 dny

      Usatchure dzina la mulungu wako pachabe mingochimwa nazo izi

    • @ChristinaLigomeka
      @ChristinaLigomeka Před 5 dny +2

      @@ManifoldPhiri atchula pacha be pempherani nanu mosweka mtima Mulungu sapepusa PEMPHELO losweka mtima Koditu amakani nu choona muchidziwa posachedwapa mwazi ukufula ohoooo wanthu 9 mmmmmm anthu mimba zamangidwa kufuna kudziwa choona chochoka kumwamba anthu kukugonedwa mapili kufuna kudziwa nchoonadi chochoka kumwamba inu ngati mafoloko alimanja daily musaganize ngati dziko lonse anthu avula dzuwa liliphweeee mukucheza ndi Mulungu

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr Před 5 dny +1

      ​@@ChristinaLigomekakunena zoona imfa iyiyi sikundigonetsa tulo ndizowawa ndipo ngati bodza Chilima kulibe zoona. Mulungu munaloleranji? 😢 ndikufuna tidziwe zoona

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w Před 5 dny +1

    Mbolo zanu

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma Před 4 dny

    Akunkuyu machende

  • @Sugerman-tw4do
    @Sugerman-tw4do Před 4 dny

    Zopusainu

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 Před 4 dny

    Kulibe ufulu ku malawi mcp is fokolo