Constitution yimati president asankhe vp ngati vp wamwalira. Sono mugwirizano wa utm ndi Mcp unaliwoti bwanji. Kodi akanamwalira chilima Ali mboma kodi ndani akanakhala president????? Or zikambidwe muti bwanji Michael Usiyu ndi Automatic.
Komano inuyo mmafuna vice president akhale ndani poti vice President anatisiya otsatila wa vice president anali micle usi mukuwona kuti adakasankha ndani ? Kuti akhale vice President za imfa ya a chilima i think tiyeni tinsiye mulungu akhale mulungu okupha ndilupanga nayenso adzaphedwa chimodzimodzi kulibe wambewu kudziko lapansi
Complete nonsense, akanakana nthawi yomweija Chilima alipo coz eniake amkavana and anayendetsera limodzi chipani from the grassroots. Izi zitayeni. Touch real things not this trash
Oyankhula ndi Peter Jegwa
Ndipoo olo kupeleka ulemu kwa SKC,ineso ndi nadabwa,kwa ine a Micheal Usi sanawoneke kukhudzidwa, ndi kuti aluza munthu wofunikila pawokha
Zavuta basi bwerelani ku APM
Nkhani nayipulika makola chomeni, suzgo la UTM, Uchisepuka, ngunandi,ntchindi zingawamo yayi, , Mulongozgi Chilima wanguwa wachali kusambizga wakumulondola wake,so ntchindi mulije mu UTM, and kuzenga mulije
Manganya ndimfiti ndipo musaloredi
Micheal Usi is a traitor he joined MCP long ago so Chakwera should not lie that he has taken his vice from UTM.
Mmmmm amalawi muchedwa nazo nthawi zonse miseche basi walakwanji Michael usi
I'm following
NDIPO MANGANYAYO NDI GALU NDIOMWE APHA CHILIMA ZIKHALE CHIMWENDO CHAKWERA NDI AFITI
Live from south Africa cape town kuvesera mwachidwi
We follow u
Komaso anayenera kunkanila chakwera ngatidi anali wa UTM
Ndani angakwane udindo
Anthu sakumfuna Manganya usi
You. Don't need to be liked by the people to be a leader... A leader will always have traitors against him
Anthu sangamupase wule usi chifukwa ndi udasi ndi amene anamupereka chilima
It's too early to start fighting, Chilima chose Michael Usi as his deputy, let's give him a chance.Dyera some leaders in UTM.
Dyera,dyera,dyera,miseche,miseche Yesu akukuonani
Mmm... koma mwati tipita chitsogolo? Ija ndi ngozi tivomeleze
Usi ndi oipa uyu simunthu timuwona ngati alimbe iyeyo
Choka apa naweso miseche amanena ziko rikunva ngakhare yesu zinthu zikarakwika amawa uza ophunzira ake ndiye ngat mukuti miseche kufuna kt zinthu zikarakwika anthu azingo penya nkawona chakwera akuku zunzani choncho chifukwa wawona nayeso kt ndinu anthu womango wombera mmanja bas kuthekera muribe ndemunya zeni zenitu simunat chifukwa nde akuchita kuwoneka kt sari mochezaso naye
Sakumufuna bwanji munthu skc anamukhulupilira,njala nthenda sanjeeeee.
ZOTI MANGANYA NDI WA U T M UZIWA NDIWE INE MULIBE
Constitution yimati president asankhe vp ngati vp wamwalira. Sono mugwirizano wa utm ndi Mcp unaliwoti bwanji. Kodi akanamwalira chilima Ali mboma kodi ndani akanakhala president????? Or zikambidwe muti bwanji Michael Usiyu ndi Automatic.
Manganyayo ajudziwapo Kanthu ndi mfiti manyi ake mkolo wako pa make ndi chikwelaniyo mbobo yake ya Monica nkholo wake mfikti wamake
Zoona uyuyu siwa utm ayi samalani inu UTM mutheka chipululu ngati simusamala mangadya akutengelani ku bagamoyo njoka saweta mcp ikukhazulani
Micheal utsi sakukwanila the late chilima was number one
Mthamangiseni galu ameneyo ndi mfiti
Eish
Poti mwaziwa kuti manganya ndamene anapha nawo achilima,timaona ngati simukuziwatu mfiti iyi
Ine ndikuwona ngati Usi Alibwino. Koma chakwerayo amuyipitsira mbiri yake .
Usi Sitikuyenera kumuwelengera kut amapanga za Chilima cos infa ya Chilima Usi ndili Shure kut amadziwa zachiwembuzi amadziwapo khanthu
Sakumufuna bwanji yet munthu anali VP ku utm.
Akutumani eti usi wakhala liti akupanga za utm? Usi ndi vise president wa mcp
MANGANYA NDI WA MCP KOMA ANAKAJOINA UTM MOTUMIDWA NDI CHAKWERA POFUNAFUNA NJIRA YOPEREKERA CHIRIMA UYU NDI GALU
Ndipo nkhope yake inali yowuma Gwaaa ngati yachakwela
Ndipo amkachita kunyokodola kukamwa kuonesa kuti zomwe amalankhula anzawo kwaiwo zinali zopanda pake chilipo chomwe amadziwa.....
Komano inuyo mmafuna vice president akhale ndani poti vice President anatisiya otsatila wa vice president anali micle usi mukuwona kuti adakasankha ndani ? Kuti akhale vice President za imfa ya a chilima i think tiyeni tinsiye mulungu akhale mulungu okupha ndilupanga nayenso adzaphedwa chimodzimodzi kulibe wambewu kudziko lapansi
Mkunena zoona
Manganya ndi m'thira kuwiri moti zonse zachitika zija akuyenera kuyankhulapo kanthu.
Wadya zake alibe mulandu kkkk
Vautesi,,,
Uyuyu wadya za chakwela galu uyu
Manganya ndi mfiti uyu galu wachabe chabe
Kudelera basi
Karma will know their addresses ,time is coming.
Utsi is betrayer we don't need him in utm
Apodi zoona ndithu,mau amenewo
Jelasi basi mukanakha inu mukanakana
Zilibe umboni kuti utm yamkana usi dikirani osalubwalubwa apa awo ndimaganizo anu
Zoona anthu akungoyankhula timve okha osati anthu aaaa
Complete nonsense, akanakana nthawi yomweija Chilima alipo coz eniake amkavana and anayendetsera limodzi chipani from the grassroots. Izi zitayeni. Touch real things not this trash
AKulankhula ma nonsense paliponse kumangofuna kuipitsa munthu
Traitor