We really need to light the candles daily but my question is where we we get the money to buy the candles and lighters on daily basis? Do we really have the power to make the spirit of the dead rest by showing our love, allegiance and good works of the deceased?
Kalindo Anthu amamutenga ngat ndiwosokonedza Km ineyo ndikut ayi ndikalindo yemweyu amayidzudzura dpp koma ali momwemo komano ifeyo ndi amene sitimupasa support yokwanira
But then this guy bon kalindo is a true hero of Malawi.. Long live sir
Dc we love you
We love you DC
Good point Bon kalido@@AnockyDavidd
Never to see person like kalindo ❤❤mulungu akudalise kalindo.. Bwedzi ena anasiya Kale Kale koma kalindo amatiyimira❤️❤️
Tavaso kuti chakwera anaphaso m'busa nzake wa assembulesi ndi fiti yachikhalire😢😢kudziko
Muthuyi ndi fiti
I love you sir this true leader who shows the way and follow the way 💪💪💪💪
We love you the DC ng'alulani tikufuna kudziwa amene adakhudza thupi la VP wathu Chilima ,,, his soul continue rest in peace
Your a true son of the soil Bon Kalindo osaopa osatopa keep the fire burning chilungamo chiyende ngati madzi
Bon kakalindo wa limpopo akumawanchura anthu live km inu simukuwa nchura amkhazuleren aziwikire ndikuba kwawo ndikumpha kwawo timakudalilan nose awili ❤
The DC of the world number one ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Mulungu apitilize kukutetezelan DC moyo wauta❤
We love you The DC'S mwana woooopsa kwambiri akhalise Malawi chilungamo chiyende ngat madzi.
Tilinawerimozi chilungamo tidalila kwayinu kms Ana ntema chilima timuziwe
Uremu wanu the DC ❤❤
.
Listening from Capetown
Dc we stand with you akuphawa tigwetse basi
Mmmmm koma inuyo ambuye akudalitsen kwambiri mwaimiladi ife osauka zikomo
Your talking true bro
Mdima umadana kuwunika
Awululeni aziwe okha
Kalindo ndi munthu osawopa ndipo akati sindimaopa tigwirizane naye (1) Ali mziko mommuno (2) amanena mpanda mantha (3) samabisala akamasakidwa (4) amatha kusiya udindo umene wapasidwa (5) samahongedwa (6) amawayalusa anthu amene sayenera kuyalusidwa (7) alibe mzache amamunena aliyense amene walakwisa (8) umoyo wake nthawi zonse umakhala pa chiwopyezo
Ndipo zoonadi😊
Ndipo zoonadi😊
Ndipo live l love like this guy😊
Koma vuto amati abwino sankhalitsa zikumandinkhudza kwambili zomwe zikuchitika mu Malawi muno
Timakukondani kwambiri the DC
We really need to light the candles daily but my question is where we we get the money to buy the candles and lighters on daily basis? Do we really have the power to make the spirit of the dead rest by showing our love, allegiance and good works of the deceased?
DC we support you!!! We pray for you and God cover you with his blood
We stand with you
DC thanks for representing us
We the whole malawi support you the DC
We stand with u our freedom Fighter ❤
Love dc kalindo ❤❤❤
Respect to you the Dc
The DC our own independent journalist
The DC plz we love pitilizani kutiyimilira monga president wanthu wa amphawi more fire the Dc
Keep up mr we are proud of you
❤ we love you man of vision
Timamvela zoona kuchoka Kwa inu bwana kalindo mmakwana long leav❤
Obvious Mr president let's fighting together
DC the number one 💪🧢🔥
Proud of you the DC ✨☀️
We love you Bon k the DC more fire!!!
The DC keep the fire burning...
Ulemu wanu bwana DC God bless you
The DC umàkwana iweyo mr president wa anthu osauka 😂😂😂 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 Osaopa osatopa
Mumatiimilira mr DC pitilidzani kung'alura !.
Palibenso, Bon kalindo ulemu wanu, Respect
I support you bon kalindo ❤❤❤❤❤
Tili nanu a Bon may God protect you
Go ahead
Ndemwati msing'angayo wapasidwa ma drip kunyumba ya m'busayo 😂😂😂😂
keep it up my DC❤❤❤❤❤❤
I like the ending..."iweyoo?" 😂😂😂
Ulemu wanu Dr DC president waife osauka l salute you 😅😅
DC. ❤❤❤
We stand with you even though we are forced to be quiet
More fire Mr president
The DC mmatidziwitsa zomwe sitikanazidziwa real man
Big up Mr dc no fear no body😅😅
Mumatilimbitsa mtima kobasi the dc🎉🎉🎉🎉
Iweo mulungu azikudalisa ndi moyo wawutali❤
Longlive Boooooooon Kaliiiiiiindooooooooo....brave man
The DC mwana oopsa kwambiri 🔥🔥🔥🔥
Dc we love you❤❤❤❤❤
Long live Mr DC
Kkkkkkk tiuzeni wadwalira kwa bus wake wa kuti akalindo tiuzeni timve nawo kkkkkk
More fire 🔥 Booooon kalindoooo 🔥 🙌
We love you the DC
Mbambande DC👏👏👏
❤❤❤mtili nanu bwana 💪💪
Bwana DC auzeni chilungamo anthu oipa amenewa
Mr DC mulungu azikudalisani kwambili ndipo azikutetezani kulikose komwe mukuyenda ndie mwati mizimu yatani
MULUNGU AZIKUTETEZARANI MR DC
Our own spoke person
❤❤❤❤ God bless you big
Dc ndimakunyadirani❤❤❤
Adyeletu agalu amenewa akuona ngati azilubwalubwa forever sikumasintha zinthu masiku ano taonela zisikumatenga nthawi ayi
Chilungamo sichiphedwa Bwana stand on your feet
The DC. !!!🔥🔥🔥🔥
❤❤❤❤ Kalindo🔥🔥🔥🔥
Chilungamo chiyende ngati madzi ❤❤❤❤❤❤
Ndipo uyuyu ndi mwala mwala💪
Kalindo Anthu amamutenga ngat ndiwosokonedza Km ineyo ndikut ayi ndikalindo yemweyu amayidzudzura dpp koma ali momwemo komano ifeyo ndi amene sitimupasa support yokwanira
Sure anthu mumasatopa ntambo ndi chakwera poononga katundu wa Amalawi lero yakwiya ndi mizimu
😂😂😂 Koma a president more fire
Love you DC🎉
Big up Mr Dddddcccccc
The DC mwana ooooooophya kwambiri 😊
DC anakonza more fire
Powerful kalindo ❤❤❤
Our own DC.
Kkkkk, the DC mmatiimirira inuyo
DC we love u
Mulungu yemwe timapembedza si onama komaso sakhumudwitsa😭😭
Machine The D.c bonnie kalindo🔥🔥🔥
Ngozi yabwanji kumaopseza anthu akayankhula?
Ifetu zonse tasiya kwa Mulungu chifukwa ndiye mwini zonse.🙏
tiyenawo Bon kalindo osaopa ❤
We are love you fadah
Following the DC
DC much love
Dc I love you
ena mwina tungotsatila, Kalindo is not accusing anyone while okumva tikumva ngati he is accusing someone
Bwana ❤❤❤
We still follow you dc
Kalindo ndiwachilungamo ngati anali against ndi chipani chake cha DPP showing chilungamo
Respect a DC
Thanks born karindo