BAKILI MULUZI TV 21 JUNE 2024 CHIGAWO CHA USIKU ..Political Prisoners in Chakwera's Police State

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 20. 06. 2024
  • Be active and listen and watch what is happening around the world 🌍
  • Zábava

Komentáře • 113

  • @rexphiri7242
    @rexphiri7242 Před 5 dny +22

    Zobisika mumatipatsila ndiinuyo wankulu Mulungu azikudalitsani nthawi yose tipatsen mphavu komaso apatsen uthenga anthu oti akwiye zen zen please boss

  • @YousufKadwala
    @YousufKadwala Před 4 dny +2

    Number one bakili muludzi tv

  • @powercharios2087
    @powercharios2087 Před 5 dny +4

    Bakili muluzi TV is a best we always love you

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 5 dny +8

    Bakili TV number one ❤

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Před 5 dny +3

    I support Bakili Muluzi TV.

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk Před 22 hodinami

    May God bless and protect you comrade, long live Bakili Tv

  • @NoelLangwani
    @NoelLangwani Před 5 dny +4

    Zobisika timadziwa chifukwa chainu boss naye chakwela amwalila adzamusata chilima 😭 😭😭😭

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 5 dny +7

    Ndipo a Peter Mutharika adapilila minyozo ndipo mulungu adalitse Mutharika. Sanamange munthu. MCP ndi yakupha, ndipo sitilora dictator.

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 Před 5 dny +1

    May Allah bless you ine or mutawulura zoipa zichits bambo anga sindingskusiken. Long live The Dcccc mcp amanga Akaluwa to threaten fredokisi

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 6 dny +4

    Can't wait bro, always listen to ur station alongside limpopo FM ❤

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před 5 dny +5

    Munthu akamumanga ndiye kuti akunena zoona tasiyeni achina Bon kalindo, mukamamanga anthu choncho simukudziwa kuti mukuonjezela mkwio kwa malawi, choti mudziwe mudzachoka pamenepo, nanunso adzakumangani 😮

  • @user-ku3gk4fz5i
    @user-ku3gk4fz5i Před 3 dny

    Ndipo inu bakili muluzi,ine pemphero langa ndiloti musadzafe mpaka ambuye adzakupezeni muli moyo, muwelenge yohene 11:25-26 kuti muchite umboni

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 Před 5 dny +4

    Koma ineyo azikhalewa andisekesa,😂😂😂😂akut anaoneka bwino atawaika makutu afisi😂😂😂😂😂

  • @ChikuMega
    @ChikuMega Před 4 dny

    Big up brother pitixan kutiphuzisa achinyamatafe ngt mne amatiphuzisira achilima❤💪

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 5 dny +3

    Iwe wukutukwana apa zeru wulibe ngati ndiwe WA MCP tangokhara chete anthu akupha inu zisiru

  • @Anthonymendos
    @Anthonymendos Před 5 dny +2

    Zonse paja greci Chinga adayankhula zokhuza zokhuza kulanda u plezident, ndi asatanic a MCP

  • @cephasnkhoma2301
    @cephasnkhoma2301 Před 4 dny

    Powerful TV

  • @marygoza1205
    @marygoza1205 Před 5 dny +1

    Mu kuononga ndalama za anthu osauka zomwezi mpaka kuyitanitsa anthu from mapiko kunja kuti azafufuze are you serious Mr minister? Bakali muluzi ndi Munthalika akhala akujambulidwa a cartoon komanso kuyimbidwa mu nyimbo sanayambe amangapo munthu. Even Jacob Zuma mwakhala akutukwanidwa even kupangidwa cartoon but sanamangepo anthu.
    Osayiwala kuti ukakwera pa nsanga pa njovu osamati kunja kulibe mame. God is watching at Malawi one day is one day

  • @MussaAsidi
    @MussaAsidi Před 5 dny +1

    I pray for you
    God bless you

  • @MalikiAlex-wn8jc
    @MalikiAlex-wn8jc Před 5 dny

    Yeah Kodi osamadzitenga ngati madolo amenetu muli mu bomatu yeah ❤😂🎉

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 5 dny +1

    Awatutse a Kamlepo Kalua ndi Bon Kalindo, tili mu democracy. Chakwera ndi boma lake la MCP lalephera, tatopanawo.

  • @JoybJohn-s6t
    @JoybJohn-s6t Před 5 dny +1

    Ku Malawi kulibe freedom of expression 😢

  • @user-gg6uh2wo4x
    @user-gg6uh2wo4x Před 5 dny

    Best tv

  • @sanuhabdullah5998
    @sanuhabdullah5998 Před 5 dny

    Anduna awa di ambutuma kuyitana anthu kucha za nkhani imeneyi malo molimbana Dziko litukuke cmc

  • @brightcharlie2396
    @brightcharlie2396 Před 5 dny +1

    Angoni analakwanji km RIP legend chilima 😭😭😭

  • @alexmkolongo3089
    @alexmkolongo3089 Před 5 dny +2

    Awa zimene akudziwa ndikugwetsa kwacha basi

  • @shayrafernandeslatif9556

    MTSRIP 🌹,we are all mourning with you the families ifeso takhudziwa kwambiri,imfa yosayiwalika😢

  • @user-cu8wy9rz3b
    @user-cu8wy9rz3b Před 5 dny +2

    Boss you should be making your own vids koma. Leave bakili tvs videos to his channels, thus the problem yaife ku malawi...we take someone's song n put pa channels yathu😊....it's not own

  • @DinopianoVascoPianoVasco-m3g

    Otukwana bakili muluzi tv simuthu ndi satana komanso ndi khumba

  • @DizayaLikhunye
    @DizayaLikhunye Před 4 dny

    Kkkkkk ifeyo tiripo mr kkkkkk akunama

  • @NoelKhwimba-bh3ts
    @NoelKhwimba-bh3ts Před 5 dny +1

    Inutu akumanga bakiri muluzi TV sinu mungofuna ma views

  • @ChisomoKandikole
    @ChisomoKandikole Před 4 dny

    My God prossed keep kuti muzitiuxa zambiri

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Před 5 dny +1

    Maiko USi wamupereka chilima mm zimu wa chilima use mutendere😭

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe7633 Před 5 dny +1

    Kkkkkkkkkk Skelton ngoma😂😂😂 yahhhh Malawi wanga ine

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m Před 3 dny

    Apato Boma Ngati lamanga kamulepo kaluwa ndiye Kuti nawoso nkulu wasilikali amangidweso sinanga kamulepo amumanga dzimene ananena

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 Před 5 dny

    Malawi on 🔥 🔥 🔥 🔥

  • @AngellahPhiri-wy6xl
    @AngellahPhiri-wy6xl Před 5 dny

    Ambwiyewa tidawavulira kare chipewa

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve Před 5 dny

    Chakwera tamusiyeni kamulepo kaluwa ndi boni kalindo, chakwera uziwe Kuti una Wana vamachero vikumanyikwa Yai , Wana wako chakwera wazamuwa pa suzgo musogolo tizamuwa Landa Chuma chose Dtn without Try, ziko ili lapasi likuzungulira .uzalira Lazarus takusungila mawng

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 Před 5 dny

    We belong to Allah and to Him we shall return 😥😥😥

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx Před 5 dny

    koma siwonse angakhukonde ayi. anthu ena njoka ndthu ndipo bambo chilima anafera zaini

  • @johnmiselo2230
    @johnmiselo2230 Před 4 dny

    😢😢😢😢😢😢 continue giving us good news 🗞️ like this

  • @chimwemwemorris6827
    @chimwemwemorris6827 Před 5 dny

    Zoonadi usi analinthira kuwiri kwamwalira kwachilima sitinanvepo chomwe anayakhura kaporoamenei

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h Před 6 dny

    Iwe watukwana bakili tv naweso pathako pako nyawu mwapha chilima ndinu ndipo ziko likusawuka zinthu zamuvutani mu kuwona ngati anthu azakuvotelani palibe never never munthu, akamakususani basi mwayamba kumutukwana basi nyawu inu 2025 kuphana kuphana mu kuwona ngati tukuwopani iyaa

  • @AladenKachewere
    @AladenKachewere Před 6 dny

    👍

  • @user-ku3gk4fz5i
    @user-ku3gk4fz5i Před 3 dny

    Ndizoodi mwanenazi achimwene

  • @ArabJames-de7fx
    @ArabJames-de7fx Před 5 dny

  • @Thewarrior7093
    @Thewarrior7093 Před 5 dny +1

    Agalu amenewa aonjeza

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 Před 5 dny

    Vyachitima chomene titimalenge tosa

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve Před 5 dny

    Chakwera uzamuli pulika kuwawa ziko lapasi tizakulanda Chuma chose ndi nduna Zakozonse

  • @MasterAkidu-cz4fb
    @MasterAkidu-cz4fb Před 5 dny

    Malawi defence Army ikungoyang'ana?...zachamba zokha zokha... Malawi ikhala ngati Sudan...zoona akulu akulu andale akungoyang'ana zimenezo

  • @DennisDonework
    @DennisDonework Před 5 dny

    Koma bakili muluzi tv mmmmm usazafe sanga

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py Před 5 dny

    Chakwera asatirat chilima ngat akuona ngat iye ndiwa panazare tiona achakwera thawi yanu ikafika mufera nyumba inuyo

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h Před 6 dny +1

    Panji nikuyowoyele muchitumbuka pamatako pako ulichindele chomene nkhana vimavi vako we love bakili muluzi tv our best Chanel ise luta waka uko kutali ungatikwitiska

    • @rachelkaunda
      @rachelkaunda Před 5 dny

      Akulu Inu kutuka nthena yayi please fear God musanayulutse Mau mkamwa mwanu think about God first there is judgement day after this life your words are too much before it is too late receive Jesus Christ

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Před 5 dny

    Mumatenga ma audio mochedwa
    Iyi inatuluka dzulo,inu mwapanga upload lero

  • @ChipilipiroMtsukwamwale

    Big mutipatsireko mbiiri ya asing'anga abwino kumalawi kuno, mwina tiyeseko matsenga abwino.
    14:36

  • @MackCent-ee8ys
    @MackCent-ee8ys Před 5 dny

    Zimenezo ndie zoona bwana

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9d Před 5 dny

    Kod chakwera ndi mubusa otani wankhaza chonchi??

  • @augustMag
    @augustMag Před 5 dny

    Chilungamo chokha chokha Bakili Muluzi TV ndiyokhayo imatiuza zoonadi zokhazokha kuposanso Ndipo pitilizani osaopa kuyima pachoona Mulungu Ali kumbali yanu nthawi zonse kukutetezani mpaka kuyitanisa anthu Kuja kuti azakucheni kuti kodi angakupeze kuti sangaone kuti Mulungu samalira kuti anthu amene amayima pachifuniro Cha Choona Samawapereka mmanja mwa adani awo? Amphunzirepotu pamenepo sangakupezeni kapena kudziwa kumene Inu muli Ambuye wazatheka bwanji apitilize kuchitisa khungu mmaso mwao amenewa

  • @WilliamChunga-jv5lm
    @WilliamChunga-jv5lm Před 5 dny

    Kkkkkk

  • @SelemaniAlie
    @SelemaniAlie Před 5 dny

    Osadandaura wakulu mulungu alinanu thawizonse

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Před 5 dny

    Chakwera wakupa wapa chilima palibeso kubisanaso apa

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Před 5 dny

    Afit mwachuluka et ndin mwapha vc takuonan mulungu achita nan

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před 5 dny

    Club junta don't imitate bakili muluzi tv you are down grading yourself and you not go far

  • @user-xj9uy6wz7b
    @user-xj9uy6wz7b Před 5 dny

    😢😢😢

  • @johnlameck8366
    @johnlameck8366 Před 4 dny

    😭😭😭😭

  • @JaccobMwenye
    @JaccobMwenye Před 4 dny

    Malo mopanga zitukuko ntchito Ku manga anthu bas

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před 5 dny

    Is this real

  • @user-oq5rg5mz7q
    @user-oq5rg5mz7q Před 5 dny

    Manganya ndi amene waphetsa chilima

  • @WisdomBlack-uu7zt
    @WisdomBlack-uu7zt Před 5 dny

    Ulemu wanu bigy mumati tsekula maso 🤔🤔

  • @laurentbutao4084
    @laurentbutao4084 Před 5 dny

    Politics so evil,nobody is clean in politics

  • @user-yj2dz5ej7r
    @user-yj2dz5ej7r Před 5 dny

    Osaphunzila uyu chimidzinso chili momcho

  • @GreenBadani
    @GreenBadani Před 5 dny

    🤦😢

  • @PreciousPhiri-jr4sd
    @PreciousPhiri-jr4sd Před 5 dny

    Kma dzkolanthu ili😅

  • @omarjustin5518
    @omarjustin5518 Před 5 dny

    MCP yazaza ndi mbuli ndi mphamva

  • @emiliaumali8360
    @emiliaumali8360 Před 5 dny

    Akusowa zochita awa

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc

    Koma bomali mmmm ayi zikomo

  • @MaggieChiomba
    @MaggieChiomba Před 5 dny

    🤣🤣😂😂😂azikhale andisekesa

  • @petrokagona1708
    @petrokagona1708 Před 5 dny

    Mukumatenga zomwe a bakili muluzi TV akamba kale inu mkumapangirapo ndalama. Izizi tamva kale kuseriku, inu mwangopanga repost. Fotseki.
    Sakani nkhani zanu mutiwuze

  • @user-lv9vf6rf8r
    @user-lv9vf6rf8r Před 5 dny

    Boma ili lititha m'thambo aliko adziwe kuti watiika m'mavuto poika boma ili m'boma.

  • @user-mz8nw6nx6p
    @user-mz8nw6nx6p Před 5 dny

    Inuyo ndiye big man ndimakutsatani not enawa akuti Athanyiwa amangopanga za nonsense

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s Před 5 dny +1

    Eeeeeeeee km abale kd inu aboma munthu uyu amamuti Azikhale Ng'oma munamutenga kt? iiiiiii edit mpaka kuidabwa.
    Kd tiziti smartphone mwayamba kuigwiritsa ntchito ndi Mcp yomwe km zinaz mukumatichitisa manyaz

  • @EmanuelMlenga-sb5kw
    @EmanuelMlenga-sb5kw Před 5 dny

    Uziwuza amako zimenezo galu lwee

    • @CiprianoBindissone
      @CiprianoBindissone Před 5 dny

      Choka iwe galu

    • @SharifahWillardChampionn-rn8cm
      @SharifahWillardChampionn-rn8cm Před 5 dny

      Mmm watibwanji iwey pls ngat sukumafuna kumavera bakili muluzi TV pls just skip don't talk nonsense respect yourself manyi akwanu mbuzi

    • @SharifahWillardChampionn-rn8cm
      @SharifahWillardChampionn-rn8cm Před 5 dny

      Mmm watibwanji iwey pls ngat sukumafuna kumavera bakili muluzi TV pls just skip don't talk nonsense respect yourself manyi akwanu mbuzi

    • @SharifahWillardChampionn-rn8cm
      @SharifahWillardChampionn-rn8cm Před 5 dny

      Mmm watibwanji iwey pls ngat sukumafuna kumavera bakili muluzi TV pls just skip don't talk nonsense respect yourself manyi akwanu mbuzi

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 Před 5 dny

    Stupid president 🙄

  • @chadreckchibwithala1493

    LIMPOPO USANAMIZE ANTHU IWE ULI GALU FOSEKI ISE KU NORTH NO DPP UWONASO TILIBE NTHAWI YA CHIPANICHA SANKHO . ALOMWE MKHAUKA

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 Před 6 dny +1

    Pathako pamako muluzi tv watsala ndiwe kumangidwa, mmadzitcha anthu omenyela ma ufulu, ufulu wa kumatako kwa Munthalika dzitsilu nyelo zanu

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d Před 5 dny

      Mukhaula agalu inu mudziwaso simunati, pathako pabambo ako galu iwe

    • @EllahChikwatu
      @EllahChikwatu Před 5 dny

      Opepera iwet ukuwatukwana amako osat amuthalika koma ukuzitukwana wekha manyaz ulibe

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 Před 5 dny

      @@EllahChikwatu you what iweso panyelo pamako, kodi inu ma refugees mmafuna mudzitisowetsa mtendele mudziko lathu why

    • @EllahChikwatu
      @EllahChikwatu Před 5 dny

      Ziko lake liti lomwe ukusowa tenderero kapolo iwe ... Akusowa tendere ndamene akuyakhula cilungamo kumagidwawo ndpo bambo opanda zeru iwe

    • @CeniaMayeni
      @CeniaMayeni Před 5 dny

      Eeeeee akulu mwamasukatu,zonse zomwe watukwana zipite kwa azibale ako uwagawanisa wekha, kukhala nyau ndi mavuto ndithu ntchito yozola manyi

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Před 5 dny

    Zovesa chisoni Malawi wafika Pena pale zinthu sizikuyende kungovutika

  • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw

    Tikumvera ndithu, mutesi atitha mkutinjata

  • @GreenBadani
    @GreenBadani Před 5 dny

    🤦😢

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Před 5 dny

    Zoonadi ndithu, ife timadabwa kuti, oipawo amadziwa bwanji mapulani achilima