GWEDE GWEDE 27 JUNE 2024 ...OTSOGOLELI MULIBE DZIKOMO MUNO

Sdílet
Vložit

Komentáře • 33

  • @MartinezSpoke
    @MartinezSpoke Před 2 dny +2

    Ine chiyambire kumvera gwedegwede pg imenei ndyomwe mwandyankhulira zakukhosi kwanga❤❤❤❤❤.Ma ministers chilichose chopangiridwa mix salary pwapwapwa.

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Před 2 dny +2

    Ndipo mulingo umenewo chakwera azanyera pogona asakufuna ndipo apolisi zitsilu zeni zeni bwanji zikungolora zinthu zaziiii

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 2 dny +1

    Kodi anthu oyankula chilungamo mudakalipobe may the good Lord bless you ❤❤

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy Před 2 dny +1

    Muli bho guys ..Mr chikangawau kapena Kuti chifungau NDI a police Ake nkhumba Za anthu kusaphuzira kuseku kuzolowela nyau

  • @DafterKhungwa
    @DafterKhungwa Před 2 dny

    Mr Banda keep up the good work,kumeneko ndiye kulankhula

  • @thomasbodo4099
    @thomasbodo4099 Před 2 dny +1

    Mwati munthu ameneyo anali Busadi ka pena anagobisalirapo I think fisi koma chikopa cha nkhosa

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 Před 2 hodinami

    Chikondi tilibe a Malawi, tikadzayamba kukondana Malawi adzasintha koma ndimene zilipanopamu even tizisintha maboma nothing can change

  • @MubarakMatembah
    @MubarakMatembah Před dnem

    Bambo Banda mulungu azikudalitsani ndi moyo wautali ndiwa thadzi mumati imilila

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 Před 2 dny +1

    Rule one: don't be friends with a criminal party
    Rule two: obey Rule one

  • @GanieAlidih-gu7no
    @GanieAlidih-gu7no Před 2 dny +1

    😂😂😂😂. Zilipati kod zama mega kkkkkkkkkkk😅😅

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Před 2 dny

    Dziko la Malawi likuyendetsedwa ndi munthu osadziwa chochita

  • @thomchiphale-bm6tj
    @thomchiphale-bm6tj Před 2 dny

    Adzitenga madzi akumwa akutinyasa

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v Před 2 dny

    Malo mozilemekeza achakwera angotukwanidwa ndi ana omwe zoona izii kungochoka komvina zinyawu kukhala sogolere wa ziko yooooo

  • @user-oq5rg5mz7q
    @user-oq5rg5mz7q Před 2 dny +1

    Chakwela wanyanya guys, waonjezakwambili

  • @otiblestudios
    @otiblestudios Před 2 dny +2

    Makamaka wachitrauza ngati parachute uja,ndimasuit ake ngati Apollo ii, kuipa nkhope ndi mtima ngati Bermuda triangle

  • @user-lb5gt4uv3s
    @user-lb5gt4uv3s Před 2 dny

    Tipangano za ku kenya soon

  • @homeremedys3748
    @homeremedys3748 Před 2 dny

    Apolice ambili ndi mbuli ma loya ndophuzila kwambili, Apolice ambili ali certificate ya standard 8 to MSCE.
    Mabuzi Anu Apolice Nonse

  • @thomasbodo4099
    @thomasbodo4099 Před 2 dny

    Dzikomuno kulibe president dziko lili pa Auto pilot ili aaa

  • @EmmanuelMoyo-hy5ni
    @EmmanuelMoyo-hy5ni Před dnem

    Chinese Bus or cars parts are very expensive..

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Před 2 dny

    Well spoken guys

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w Před 2 dny

    Eti 2minamina sugar wakwera mafuta forsake

  • @user-cb5me8wp1k
    @user-cb5me8wp1k Před 2 dny

    Kutereku chilungamo chayakhulidwa apachi wina zamuwawa

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zs Před 2 dny

    Mukunena zoonatu kwambili

  • @user-gb2sl1jt4s
    @user-gb2sl1jt4s Před 2 dny

    Zowonadi bwana

  • @JerryChain-cz8ru
    @JerryChain-cz8ru Před 2 dny

    Apa mwalankhula nkhani zamisonkho zimenezi zingafike bwanji kwa adindo?

  • @MartinMsimuko
    @MartinMsimuko Před 2 dny

    Timanena kuti ifa ya biyeni muyaluka nazo izi mkungomanga anthu without real reason

  • @user-gb2sl1jt4s
    @user-gb2sl1jt4s Před 2 dny

    Mumatha guys

  • @ellahmwams831
    @ellahmwams831 Před 2 dny

    Boma ili yalephera basi

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Před 2 dny +2

    Achakwera awauze anthu awo oipawo amene awazungulira kut zisankho zikubwera ndipo anthu amenewa adzakhaula ndithu

    • @FraserNamaona
      @FraserNamaona Před 2 dny +1

      Woyipa ndi Chakwela yo, iye akusekelera zopusazo bwanji? Inuyo ndi anzanga mukuziwa kuti ndine wakuba komano muli nane phatiii opepela ndi ndani?

  • @user-oq5rg5mz7q
    @user-oq5rg5mz7q Před 2 dny

    Chakwela wanyanya guys, waonjezakwambili