ZOMWE AYANKHULA VICE PRESIDENT MICHAEL USI.21 June 2024

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 20. 06. 2024

Komentáře • 472

  • @JacobBanda-s1f
    @JacobBanda-s1f Před 5 dny +10

    Your words DR Sir has deeply touched me,may the good LORD direct you.Mwalankhulazi ndizimene timati nzeru

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r Před 6 dny +7

    This is what God normally does when he chooses a man to Lead congratulations mr usi komabe ena salephera kukuwa angakhale a mnyumba mwawo momwemo muwona anthu umbuli unawapangitsa khungu amafunabe balaba kusiya yesu 😊😊

  • @user-pl6yh4ip6j
    @user-pl6yh4ip6j Před 6 dny +16

    My the soul of Dr klausi chilima and sadik Mia continues to rest in peace

    • @williamsalexmbonga
      @williamsalexmbonga Před 5 dny +1

      Nkhani yake yomweyi ?

    • @amourvido8027
      @amourvido8027 Před 5 dny

      Amalawi a nsanje amwene aaaah😂😂. Zugwirizana bwanji

    • @amourvido8027
      @amourvido8027 Před 5 dny

      ​@@williamsalexmbonga😂😂😂

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa Před 5 dny

      Mulibe nzeru mukuyikira kumbuyo inu munthu wanzeru akat sakuopa kukhala pa mpando kwa tsiku limodziro ayambe kuchuluka nzeru kkkk mau amat komwe kwasala tchire ndkomwe kumapita moto just wait n see u believe me

  • @MatiasChimsakasa
    @MatiasChimsakasa Před 6 dny +9

    Nyimbo ikhale adzakuiwala udzasanduka dothi kaya adaimba uja ndani 😊

  • @Lexkasonkanji
    @Lexkasonkanji Před 6 dny +31

    😢chilima wanga😢

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd Před 6 dny +7

    Mcp is happy because chilima amawapatsa mphuma...nkhani ya ngwirizanoh!!!!!!

  • @rashirdbanda8204
    @rashirdbanda8204 Před 6 dny +7

    Chilima tikusowani chifundo chinaphesa

  • @DianahMatiki
    @DianahMatiki Před 6 dny +19

    Ayi ndithu dziko lizatiyiwaladi😢

    • @suprianomgalla5512
      @suprianomgalla5512 Před 6 dny

      Ndipo inuu😢😢😢, eti anthu kusangalala mpaka ana achepa

    • @SamuelJoseGaviteni
      @SamuelJoseGaviteni Před 6 dny +1

    • @Xris241
      @Xris241 Před 6 dny

      The dead shall b forgotten and b replaced by the alive,so better accept it,the world has to move even though we mourning

    • @kingzack8999
      @kingzack8999 Před 3 dny

      @@suprianomgalla5512 wina ndikutenganso mkazi wako

  • @towerankhoma1380
    @towerankhoma1380 Před 6 dny +5

    Zikhale Ng'oma kusekeleratu mission yatheka 😢

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Před 6 dny +7

    Chilima amakunyansani chani azikhale ng'oma koma ngati udzitumidwa kumapanga zopusa Maga uwamva kuwawa alomwe anzako

  • @user-gw8oo4ty2e
    @user-gw8oo4ty2e Před 6 dny +11

    My name is Stanley Baluwa, let me thank the President Dr Lazarus Chakwera for appointing Dr Michael usi to be the Vice president of Malawi, this shows that there's is a great wisdom in the Mind of President, lastly don't worry about what people are saying about you, Mr President God will help you ❤

  • @alinuswengwira-yu6mg
    @alinuswengwira-yu6mg Před 10 hodinami

    Manganya💪 Dr Michael za nzeru zimenezo mpaka ma Judge anaseka mkuluyu anakonza

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Před 6 dny +14

    Zanu wapita mwapha Inu mukusangalala

    • @fxmw
      @fxmw Před 6 dny

      Ndiwe kape

    • @BlakRedGrin
      @BlakRedGrin Před 5 dny

      Mumafuna kuti ku mwambo olumbilitsa anthu aziliranso? There's time for everything

    • @user-xc5sd3qe8z
      @user-xc5sd3qe8z Před 4 dny +1

      Kodi mumafuna anyamule bokosi

  • @vitumbikomunthali8185
    @vitumbikomunthali8185 Před 5 dny +1

    Looking forward to what you can offer Dr Michael Usi..All in all congratulations Dr Manga, wishing you all the best man🎉

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Před 6 dny +19

    Ngati kulotatu,anachita sewelo,la kamuzu banda lero ndi izi.congra

  • @manzimatekwe8808
    @manzimatekwe8808 Před 5 dny +2

    Am so happy that the chosen vice president mr usi, is so good for the people of Malawi, lets hope and trust that he will work well for the people of Malawi, good luck mr usi.

  • @mosesbwalya1305
    @mosesbwalya1305 Před 6 dny +3

    Wishing you Sir all the best in your new post and May the God Lord protect you in that office

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np Před 6 dny +8

    Good Mr usi...kulankhura mwa mzeru mowopa Yehova 🎉🎉🎉🎉

  • @sultannatha5556
    @sultannatha5556 Před 4 dny

    Very very very and very good speach. This man is going to do his best. Let's help him. From Mozambique.

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem Před 6 dny +19

    Malawi omvesa chison ndithu

    • @fxmw
      @fxmw Před 6 dny +1

      Mmafuna asankhe bambo Ako?

    • @user-ue2st6zw5w
      @user-ue2st6zw5w Před 5 dny +1

      Once a comedian always a comedian the presidency does not really matter

    • @fxmw
      @fxmw Před 5 dny +2

      @@user-ue2st6zw5w and people forget that before becoming VP he was also a VP wa chilima. And anali chilima yemweyo amene anamusankha. He has all requirements for being a VP and he's well educated kuposanso chakwera. Anthu akuona manganya osati Michael Usi that's the problem

  • @user-rn7wv8ze3v
    @user-rn7wv8ze3v Před 6 dny +7

    Mavuto mu Malawi alipo

  • @user-es4jt6ds8m
    @user-es4jt6ds8m Před 6 dny +6

    Usapiteso Ku UTM galu

  • @AlexHanyana
    @AlexHanyana Před 23 hodinami

    Mr president I love your sepich god bless you 🙏

  • @bekithembasibanda8096

    Very very very Good words God is leading him .. according to his words u feel confidence..thats great too

  • @BrendaMalunga
    @BrendaMalunga Před 4 dny +1

    Nice chining'a

  • @Jerry-vm6mo
    @Jerry-vm6mo Před 6 dny +3

    Ukuyankhula zopusa ndizomwe umafuna

  • @SlajihMeria
    @SlajihMeria Před 6 dny +4

    Malawi ziko lomvesa chisoni kwambiri 😢😢😢😢😢

  • @user-rr3il1vg7f
    @user-rr3il1vg7f Před 6 dny

    ❤❤❤ motooo kuti buuu congratulations Bambo asikhono

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Před 6 dny +10

    Ndikulumbira,pali Mulungu .
    Sangalalani kwa kanthawi kochepa
    Ife amalawi ena tilibe atsogoleri
    Km a MCP.
    Mulamulira mpaka chaka cha 20000000000000000000000000000000000000000000000
    MCP WOYEEE

    • @GodwinKatunga
      @GodwinKatunga Před 6 dny

      😢😢😢😢 Malawi tizikhala ndi umunthu Mary chirima afila bwanji? 😢😢😢😢

  • @TryceMagombo-sh7kb
    @TryceMagombo-sh7kb Před 6 dny

    Ur our celebrity manga we love u ulibe mbiri yoipa yako ndi Geri basi umatha kucheza

  • @user-xz3qn5zh2u
    @user-xz3qn5zh2u Před 2 dny

    Well spoken. Put God first

  • @pamelachirwa427
    @pamelachirwa427 Před 6 dny +2

    Amen! Man of God.

  • @IssaZiyada
    @IssaZiyada Před 6 dny +3

    Thats very stupid,, sometimes do not trust anyone else chisoni chinaphesa nkhwali,,ndipo mawanga its not a symbol of goodness

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo Před 5 dny +1

    Kkkkk l am not satisfied ndingonena kt mulungu atipatse utsogoleri wabwino Masha Allah

  • @LatifahDavid
    @LatifahDavid Před 6 dny +1

    All the best Mr Michael Usi❤❤

  • @user-zq3uf5bc8v
    @user-zq3uf5bc8v Před 6 dny +8

    Izi akungomphimba Maso utm usi ndiwa Congress asatipusitse

  • @ElizabethKuputu
    @ElizabethKuputu Před 6 dny +12

    Michel usi you are very intelligent and ontop of that Iwish you all the best in this new office

  • @ZainthwaSikelo
    @ZainthwaSikelo Před 6 dny +9

    Akamalumbira chonchi with Bible zimaoneka ngati pali uMulungu km ndithu ndithu ndithudi,palibepo Mulungu pamenepo

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Před 6 dny +2

    Manganya sekerera kucola lwa achilima 2 days yomweyi mwamuiwala chilima rip chilima asiyeni manganya akondwe

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js Před 6 dny +2

    Imagine laughing and shouting like that instead of finding another way of congratulating him.Oh you evil people

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z Před 6 dny +3

    Rip my vice president chilima mudalibe ulemu wa u vice President .kkkkkomasesa mu church haaa rip

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o Před 6 dny

      Aaaa kuyankhula kwa bwanji ngakhale bible linalemba zichesepeseni pa maso pa mulungu u vice president ndi mau a mulungu chachikulu ndi chani kodi???

  • @StevenMjMbama
    @StevenMjMbama Před 6 dny +1

    All the best Mr usi plz do ur best for malawians ndipo ausi finyani onse amene akutsokoneza Malawi ndikatangale plz muma office aboma Mr usi awonetseni nyekhwe onse opanga zibwana muma public sector plz plz our people are suffering

  • @DytonMission-iz5rn
    @DytonMission-iz5rn Před 2 dny

    All the best Mr usi🎉🎉

  • @OwenDoctor
    @OwenDoctor Před 4 dny

    Amighty God please help Malawi and put mercy in Malawi 🙏

  • @doreenchirwa-ry5yt
    @doreenchirwa-ry5yt Před 6 dny

    All the very best sir ....May God guide you

  • @MarkManyowa
    @MarkManyowa Před 5 dny +1

    Ndakatulo ikhale ya Robert Chiwamba "Muzafa Imfa Yowawa"
    🇹🇿

  • @EphraimJoevino
    @EphraimJoevino Před 4 dny

    All the best, politics munayamba pakanthawi big..pakamwa mukutulusa funds zanzeru

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 Před 6 dny +3

    Kutchura dzina la Mulungu pa chabe

  • @user-us6sf3rn5y
    @user-us6sf3rn5y Před 5 dny

    Congratulations Mr Usi put Allah first zinazo pambuyo but one more thing don't forget that any good or bad coming from God almighty ndakonda momwe mwayankhulira

  • @HassanMbalaka-gb5sv
    @HassanMbalaka-gb5sv Před 6 dny +3

    Koma inu nzikomuno chikuchitika ndichan wina andidzuse mwina ndikulota ndilintulo

  • @GraciousBeyard
    @GraciousBeyard Před 5 dny

    Once Evance Meleka sung (adzakuiwala,
    Utasanduka nyatsi
    Adzathamanga nawe kumanda kokakutaya, bwanji udzipemphera)

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi Před 6 dny +2

    M c p zomwe imafuna zatheka,,, mmmmh koma ifah😢

  • @RobertJosias
    @RobertJosias Před 6 dny +1

    I wishing you all the best vice president

  • @ChisomoKandikole
    @ChisomoKandikole Před 6 dny +4

    Xoopsa masiku otsirixa 😢😢😢😢😢😢

    • @DuniaMalinga-gw7of
      @DuniaMalinga-gw7of Před 6 dny +1

      Pa dzana nyumba yomweyi timalila lelo zomsezija taiwala we don't focus on here after 😢

    • @bernaphiri
      @bernaphiri Před 6 dny +2

      Athu amamuiwala muthu ngat sanali naye limodzi kuvesa chison 😢 mzimu wachilima uziusabe nd mtendere

    • @ChisomoKandikole
      @ChisomoKandikole Před 6 dny +2

      Ndipo inu week osantha aiwara Kare eee miximu yao anthu amene anja ibweze in the name of Father, son and the horysprit

  • @user-jc7qg6cz2k
    @user-jc7qg6cz2k Před 6 dny +1

    Congratulations to Dr Michael usi

  • @chimwemwekamwana787
    @chimwemwekamwana787 Před 6 dny +2

    Mzimu wa chilima upume mwamtendere

  • @JusticeBornNdhlamini-fp7ic

    Kuchokera ku masewera lero akukathera as Vice president koma moyo uwu

  • @stevenkaombe8737
    @stevenkaombe8737 Před 6 dny +4

    Congratulations Dr Michael Usi. You are a blessing!

  • @user-ef7hq3wu4p
    @user-ef7hq3wu4p Před 4 dny

    The speech is very fine congratulations Michael usi

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona Před 6 dny

    Lord have Mercy .
    " Mulingati Abwino😭😭😭
    Malawi wangaaaaa 😭😭😭

  • @JamesWandari
    @JamesWandari Před dnem

    All the best my vice

  • @Nya-Jeka
    @Nya-Jeka Před 6 dny +1

    Pepa Saulos. Mzimu wanu uwuse mu mtendele 😢

  • @Jerry-vm6mo
    @Jerry-vm6mo Před 6 dny +2

    Amalawi palibe chomwe mwapanga ameneyo sathandizapo

  • @amonfriday630
    @amonfriday630 Před 4 dny

    Great speech boss

  • @user-nr8kx4hb7c
    @user-nr8kx4hb7c Před 5 dny

    Congratulations from Nairobi Kenya.
    Take over from where Chilima left.

  • @OwenDoctor
    @OwenDoctor Před 4 dny

    Amighty God please help Malawi and put your mercy in Malawi chilima may your soul rest perfect in peace 🙏

  • @user-mz8nw6nx6p
    @user-mz8nw6nx6p Před 6 dny +2

    Kodi Bible mumalumbililayi,,,ndilomweli linabwela ndi Mtumiki Yesuli kapena lina lakumidima??chifukwatu zochitazanu andalenu sizifanana ndi Bible

  • @JamecPhiri
    @JamecPhiri Před dnem

    U deserve it Michael

  • @wilsonchampopa7408
    @wilsonchampopa7408 Před 4 dny

    Big up Dr usi

  • @wilsonfelix6559
    @wilsonfelix6559 Před 6 dny +2

    Moto upita kwasala tchile

  • @AndersonAnusah
    @AndersonAnusah Před 5 dny +1

    Sitikukondwa ifeeee

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx Před 5 dny

    UTM yomwe tikufuna strong leadership ngat chilima apo biiii 2025 "mugwa nonse

  • @eunicemacdonaldkaipsa9705

    Continue resting well chilima

  • @TrizaMakocha-un4pi
    @TrizaMakocha-un4pi Před 5 dny

    Congratulations Mr Usi

  • @user-es4jt6ds8m
    @user-es4jt6ds8m Před 6 dny +2

    Mulungu akuona pa zomwe mukuchita chilima munalakwira

  • @evaromeo1897
    @evaromeo1897 Před 5 dny

    Congrats Dr Michael Usi, wish you best

  • @alicejonny7990
    @alicejonny7990 Před 4 dny

    Do best all over Malawi not only kumwera. Even us we need chitukuko kumpoto

  • @chiccochimwaza4791
    @chiccochimwaza4791 Před 5 dny

    Big up Manga, umatha daily

  • @LeendaDeborah2005
    @LeendaDeborah2005 Před 6 dny +1

    Zokhudzatu kwabasi 😢😢

  • @AndersonAnusah
    @AndersonAnusah Před 5 dny +1

    Zopusa zonsezi

  • @PatrickMasiye-gs8es
    @PatrickMasiye-gs8es Před 6 dny +1

    Ndizomwe umafuna mulungu akulange iwe nzako ali manda iwe ukuyakhula ngati dolo pamenepa

  • @PhillipMaalo
    @PhillipMaalo Před 5 dny

    True African leader.... Chichewa

  • @charlokapalamula9299
    @charlokapalamula9299 Před 6 dny

    Congratulations Boss. Well deserving

  • @KomboJere
    @KomboJere Před 5 dny

    Izizi zifanana ndi nyimbo ya Evance Meleka adzakuibala utasanduka dothi

  • @StephenwMbuzi
    @StephenwMbuzi Před 5 dny

    May love and peace be with you all Malawians in this difficult time and may God continue blessing you Amen!

  • @user-zg6mn8qr4m
    @user-zg6mn8qr4m Před 6 dny

    All the best vp

  • @stewardmbele7385
    @stewardmbele7385 Před 5 dny

    Mmmm great speech by Dr Usi

  • @samcmusical2083
    @samcmusical2083 Před 5 dny

    Just like a dream ndthu 😢 ....Moyo supanganika

  • @user-cl3tu4oi8b
    @user-cl3tu4oi8b Před 5 dny

    Thanks Lord 🙏🏽🙏🏽🙏🏽🔥🔥🔥

  • @AOVERABABA
    @AOVERABABA Před 6 dny +1

    Mr jokes amenewo 😅😅😅

  • @moffatzgambo9722
    @moffatzgambo9722 Před 4 dny

    Mr usi do what God has direct you i love you sir

  • @LinahNgulube
    @LinahNgulube Před 5 dny

    Family ya chilima yikumva bwanji😭😭Malawi💔

  • @RosheensSPA
    @RosheensSPA Před 6 dny +1

    Km guys dzana anali vs wa chilima lero kwa chakwera eeee dziko kuwawa 😢

  • @joeljere4385
    @joeljere4385 Před 6 dny +1

    God bless you our Vice president

  • @IvyViyuyi
    @IvyViyuyi Před 5 dny

    Yes abwana mwayankhula. May auzimu ndipo kwanilisani chimene mulungu akulamulileni sitiziwa chimene mulungu akuitanilani

  • @davidnoel599
    @davidnoel599 Před 4 dny

    Chilima and other 8 people may God Rest your souls

  • @RobertJosias
    @RobertJosias Před 6 dny

    Good speech to Mr m

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli Před 6 dny +2

    Chakwera week yamawa ndimaliro pulezident ndimanganya week yamawa

  • @FavourThyangathyanga
    @FavourThyangathyanga Před 6 dny

    😊😊😊😊 yomweyo

  • @franksimonda9991
    @franksimonda9991 Před 5 hodinami

    Malawi is doomed. How could such a comedian be appointed as Vice President? He doesn't even have a speech for his inauguration.