Ka Manganya Kakuona Ngati Kasewela Game Yovuta | Koma Ndikamunthu Koipa | Watelo Khad

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 20. 06. 2024
  • #manganya #chilima #malawi #trending #news #viral

Komentáře • 218

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Před 6 dny +17

    Amene akususa ni wa amcp.amumasure.boni karindo chakwera nisataniki wamupha chirima

  • @JustinLipipa
    @JustinLipipa Před 6 dny +13

    Mmmmm in politics palibe True friend, si game yonkhulupilirana

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 6 dny +16

    Good Messnge my brother

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před 6 dny +10

    I think it's wise to pick somebody from utm other than MCP

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI Před 6 dny +14

    Chakwela wamupha chilima manganya amupha chakwela tiyeni tiziyang ana mezi ikubwelayi

  • @DivineMercy-df2pu
    @DivineMercy-df2pu Před 5 dny +3

    Manganya his cup will b full soon ... imagine MPs shouting m'boma ilo when we have just barried Chilima n I'm sure those MPs are not Utm ,UDF or DPP it can only b MCP . Your down fall is near.

  • @VisianMw
    @VisianMw Před 6 dny +18

    Inu nde mangoyankhula zilungamo zokhazokha boss 💪💪💪

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před 6 dny +21

    We have to pray for Malawi to be free from MCP and "satanic politics".

    • @Luxemaven8686
      @Luxemaven8686 Před 5 dny

      Facts!!!

    • @emmammatsa1284
      @emmammatsa1284 Před 20 hodinami

      I am not a politician neither belong to any party, in Malawi every party belongs to someone besides MCP which is the party for everyone but lacks good leadership, MCP leaders now are weak, wicked and have tainted the party.

  • @IssaKapalamula
    @IssaKapalamula Před 5 dny +4

    Mwauponda, mumaganiza kuti asankha wa mcp cholinga mudzetse mpungwe pungwe pakati pa utm ndi mcp 😂😂😂😂

  • @RabiaOsman-wy1ud
    @RabiaOsman-wy1ud Před 5 dny +4

    Interview ya b.banda ndi manga'anya inanena yokha, he couldn't answer zogwira mtima, I was hoping to hear zogwira mtima. Koma palibe ananena. Anali atamugwiritsa buns . It makes sense now.

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe Před 6 dny +5

    Ndipo manganya ngochenjeladi mix nka school kuposa anzawowo nde ndizovuta wina akhonza kuona madzi angazime

  • @user-kh4qp1ji1i
    @user-kh4qp1ji1i Před 6 dny +4

    Iweyo ndi katundu olemera kwambiri. Your brain is sharp!

  • @IsaacsCapetown-hu8wh
    @IsaacsCapetown-hu8wh Před 6 dny +17

    Potengela ndimmene wafela chilima muja olo akasankhidwa wina aliyese kupatula manganya bwezi tikuti wapha ndiyeyo

  • @TracyMutesi
    @TracyMutesi Před 6 dny +8

    Zimene mwayankhulazo nde ndi zambola musiyeni manganya alamulire imeneyo ndi nsanje

    • @AchinaKellz
      @AchinaKellz Před 5 dny +4

      Kape iwe mfiti

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 Před 5 dny +3

      Alamulile ng'ona zimzake not amalawife, he betrayed his President chilima, even the vp itself doesn't suit him, udindo ukumukana😂😂😂😂😂

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 Před 5 dny +2

    Manganya ndiwa mcp ever since....ka spy

  • @user-sh5wq4uf6r
    @user-sh5wq4uf6r Před 5 dny +2

    Your massage is very straight thank you my brother

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Před 5 dny +2

    Manganya ndi oipa kwambiri waphesa chilima pofuna kukhala vice President

  • @OlgaChirezi-qt1pg
    @OlgaChirezi-qt1pg Před 5 dny +2

    l Congolese from USA🇺🇸 but so sad guys in Malawi muchenchele

  • @user-sh2hr2cw8b
    @user-sh2hr2cw8b Před 5 dny +2

    You don't know Michael Usi, Jelous sikuthandiza bwera ku Malawi iwe

  • @user-gg6uh2wo4x
    @user-gg6uh2wo4x Před 3 dny +1

    Respect mr man

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h Před 5 dny +2

    A Malawi chonde tiyeni tizuke chakwela watopesa, uyu satanic president

  • @ElonBlack1999
    @ElonBlack1999 Před 6 dny +4

    Thanks for your video

  • @ChisomoKandikole
    @ChisomoKandikole Před 6 dny +4

    Mmmm Mulungu tu a kuona ndipo mmm munthu oipa mmm amamusungira kampeni kumphasa kuti afe chirima, mwanxi wake ubwexera ndinthu mmm

  • @patricksamson4852
    @patricksamson4852 Před 5 dny +3

    Chakwera watenga slow poison coz of frustration

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI Před 6 dny +7

    Manganya ndi pulendeti chakwela akafa mezi ikubwelayi

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9ly Před 6 dny +3

    Nkhani ndi ya tonse Alliance asakha bwino, game imeneyiyi tiyimalize isathele panjila aaaaaaaaaaaaaa inu tiyimalize basi UTM WOYEEEEEEEEE osadanda timalize gameyi

  • @ellahmwams831
    @ellahmwams831 Před 5 dny +2

    😂😂😂 dziko lalowa chisawawa ili

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm

    Km akulu inu ndi munthu oganiza mumalankhura chilungamo ndpo simumaopa munthu ambuye akuze malire amoyo wanu timakunyadiran❤

  • @fazeerchisamia4371
    @fazeerchisamia4371 Před 6 dny +4

    Lero wabwera ndimbola heavy,vuto mukupanga za personal kwambiri kusiya 20 million people.Sopano umafuna asankhe ndani.
    Akuti kovuta munthu kundipha ineyo kkkkk childish

  • @user-kl9id7kx3m
    @user-kl9id7kx3m Před 6 dny +8

    Enough of the hate, bro! Get a life and try to be objective in your criticism of the leaders back here. You can't just be sitting there saying things that have no proof for the sake of the views. The leaders are not without flaws because they're only human but make sure your criticism has to be founded on truth and constructive enough.

  • @CharlesmakveliNyirenda
    @CharlesmakveliNyirenda Před 6 dny +8

    Kkkkk zoona bwana ka manganya ndikafiti 😂😂😂

  • @SangwaniKawawa
    @SangwaniKawawa Před 5 dny +1

    Only God will save us from the misery

  • @danielsaidi7230
    @danielsaidi7230 Před 5 dny +1

    Pitani muzangolima musamangokhalila zolandila. Timagwirantchito kuti zinthuzipezeke, ndiye pamenepo uzingotayapo nthawi, ulankhule usalankhule koma manganya akulamulilabe, chakwela akulamulilabe.

  • @PempheroKaunde
    @PempheroKaunde Před 2 dny

    Koma mukuti chan aaa zopanda mutu zokhazokha inu mukutani kutenga dzikoli mutilamulire bwanj😂😂😂😂😂😂

  • @jacksonmaliro
    @jacksonmaliro Před 6 dny +2

    Mmmm inayo ndi nsanje akulu inu, manganya walakwa chani? Komanso mukamatchula dzina la munthu mudzikhala ndi ulemu, osamakhala ngati ndinu olenga munthu

    • @DennisDonework
      @DennisDonework Před 5 dny +1

      Koma manganya nduichenjela atha kumulanga chakwera kumuonesa athakubweza imfa yachilima dekhani muone

  • @EdwinMabviko
    @EdwinMabviko Před 5 dny +1

    Kaduku,wudzafa choncho ndiye kuti iweso ukupatsidwaso ndalama, ukunama chilichose chimene chili ndi SIGNAL chikhoza kupangidwa hack,iwe akupeza!!!!

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9ly Před 6 dny +3

    Asakha bwino TSOPANO TIONERENO GAME APAPANO YANGOYAMBA KUMENE

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 Před 5 dny +2

    Chakwera naye mulungu akuwona sakhalitsa mulungu atilangira😢😢

  • @AlinafePililani
    @AlinafePililani Před 6 dny +3

    Nanuso ndinu achitsilu

  • @nancynyirenda6774
    @nancynyirenda6774 Před 5 dny +2

    Wopani Mulungu a chimwene kutukwana uku mukafa muzapita kuti? A siyeni anzanu ndi nthawi yawo. Cha nzeru mwachitapo inu ndi chiti?

  • @CholapitsaSamson
    @CholapitsaSamson Před 5 dny +1

    Iwe ndiye umangoying'alula uli phe umakwana

  • @IsaacsCapetown-hu8wh
    @IsaacsCapetown-hu8wh Před 6 dny +3

    Chintchito chilipo pa home pano tiyeni tizingong'ana mwina zinalembedwa kale

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 Před 5 dny +1

    Miya was not a malawian to run for a president....yes manga is a sellout....just look at the jacket mbuzi yakumuzi 😂😂

  • @johnman4619
    @johnman4619 Před 6 dny +3

    Ukunena zoona bloh chakwera inso asamale

  • @JTUPHIRI
    @JTUPHIRI Před 4 dny

    Ndiye titani kuti tikonze? Osamangotokota apa kumapeto no solution, kumpusa kumeneko tikunva kuwawa ife. Tokotani mukamaliza tipaseni solution zizitikanika tokha. Inunso ngati mMalawi okhuzidwa muzitenganso gawo mma solutions wooo.

  • @thokozanichabwera5658
    @thokozanichabwera5658 Před 6 dny +2

    I used to see sense in your videos but today I have been let down 😢

    • @bwenguking3894
      @bwenguking3894 Před 6 dny

      He is on illegal drugs

    • @gladyschisomo4324
      @gladyschisomo4324 Před 5 dny

      😂😂😂😂😂​@@bwenguking3894

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr Před 5 dny

      Ndipo nane wandifoola sanaiganizile shape and wandikhumudwitsa. Manganya zapaimfa ya Chilima sikumukhudza, tiyeni timufunile zabwino mulungu salakwitsa atha kudzagwetsa mcp ndiwanzeru plus alibe 2koloko

    • @thokozanichabwera5658
      @thokozanichabwera5658 Před 5 dny

      Choosing manganya is the only right thing because ndi vice president wa UTM. Lamulo limati VP replacement should be done within 7 days so there is nothing to wrong to be considered as a traitor

  • @AlinafeMuleso
    @AlinafeMuleso Před dnem

    Big man continue to give us information

  • @MussaJohn-gt8ep
    @MussaJohn-gt8ep Před 4 dny

    mr khad always with you. may Allah guide you

  • @user-cs5dh3yl8w
    @user-cs5dh3yl8w Před 5 dny +1

    Keep it up My brother ♥️♥️

  • @ElizabethTrapens
    @ElizabethTrapens Před 4 dny

    Ndioipadi ndinthira kuwiri, wampeni kumphasa ndipo uyu imfa yachilima akudziwapo kanthu km iwowa siamuyaya zidzaululika ndipo adzafanso

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 Před 5 dny +1

    Ana a look sharp like inu ndamene mungatukule dziko come to Malawi

  • @HappyAutumnTrees-cd9ye

    Chonena ife tilibe adziwe ndimulungu 🙏🙏🙏🙏

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 4 dny

    Machende ao bwanji kupha anthu like that😢😢😢

  • @jonathankumalasa
    @jonathankumalasa Před 5 dny

    Aliyese wokhala vp bwezi tikuti wamupha chirima ndi iyeyo,ukunenazo tabweretsa tangible evidence

  • @DoraTembo
    @DoraTembo Před 5 dny

    Very very true bro

  • @ChifuniroChintengo
    @ChifuniroChintengo Před 2 dny

    Well said

  • @violetpotani
    @violetpotani Před 4 dny

    Ambuye kumwamba ko ife ana anu imvani kulira kwathu.. Kuno ku malawi zinthu sizili bwino

  • @MadaKanene
    @MadaKanene Před 5 dny

    Perfect 👌 said

  • @lytonmaseko4534
    @lytonmaseko4534 Před 5 dny

    Yaaa manganya is clever really clever ka kalulu

  • @FatsaniNgolomi-xn4mo
    @FatsaniNgolomi-xn4mo Před 5 dny

    Kape iwe Ufuna dziko ikhale lopanda president kudikila wina awole kae? Bingu Anamwalira jb anatenga malo ake bwanj simunalankhule

  • @user-nv3rf7bl7r
    @user-nv3rf7bl7r Před 4 dny

    Nsanje iyi musamayese ku joni kuno ndikwanu kutchuka ndiza ziiiii

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di Před 5 dny

    Abwana olo mwana akudziwa kuti zachitika pamenepo ndi mbola olo munve kayankhidwe ka mai kaliyati utm ikudziwa kale kuti ndi mbola yachitika apa abwana amalawife ndi mbuzi timawombela m"manja oti atimphe

  • @marvinhanke5520
    @marvinhanke5520 Před 6 dny +2

    Si zonse zomwe mumayankhula ndi zanzeru.

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Před 5 dny +1

    Charlie Chaplin at war comedy

  • @ethusiasts
    @ethusiasts Před 4 dny

    kamunthu koyipa😢😢

  • @SolokingChimzy-yt7dj
    @SolokingChimzy-yt7dj Před 5 dny

    U r very brave bro

  • @brianntonya5319
    @brianntonya5319 Před 5 dny

    Muli ndivuto mwene

  • @user-rt7ye1gt8x
    @user-rt7ye1gt8x Před 4 dny

    So u mean chilima sanali ochenjera...imfa sithawika....I think wina aliyese akapita kunja ndkuziwa chizungu amazitenga wanzeru..ngati muli ndi zeru kuno munachoka chifukwa chani...anthu anzeru amalemera konkuno Boss

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw Před 5 dny

    Big up

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim Před 6 dny

    We know that inu mukusapota chakwera ndiinu a mcp are u sure chakwera ndi manganya the lead malawi chakwera mbuli osaona manganya ndi wamadrama lero ndalama yanu ndi k10,000 to $1 next year $1 k50 000

  • @Jele-mk9ip
    @Jele-mk9ip Před 6 dny +1

    But its the construction. There is no basis of accusing Michael Usi.

    • @Jele-mk9ip
      @Jele-mk9ip Před 6 dny

      Sorry l wanted to say constitution.

  • @MorrisMapiri
    @MorrisMapiri Před 5 dny

    Good lucky to chakwera for he has been warned.

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 Před 5 dny

    Amalawi Kusanva 😢😢😢

  • @AlinafeMuleso
    @AlinafeMuleso Před dnem

    Koma imfa yachilima ndi yosaiwalika ngakhale a MCP akufuna kuifuta nsanga chilima anafa ngati galu munthu oti anali olemekezeka koma kumupanga chinchija anthu inu ndi amfiti tikat kuipa ndiye kut tachepesa

  • @user-xi6sr7kd7p
    @user-xi6sr7kd7p Před 4 dny

    😂😂😂 fact ka munthu kameneka

  • @AminAbbass-xc4qk
    @AminAbbass-xc4qk Před 6 dny

    🎉🎉🎉👏👏👏👏

  • @NACNAC-fg5yd
    @NACNAC-fg5yd Před 5 dny

    Mumafuna akanasankha inuyo?
    Kuchita kuvalira jacket ndi tie kulankhula zopusaZo? Kodi akuluwa alibe zochita Zina za nzeru than kulankhula za ndale?

  • @wittinessnkhokwe
    @wittinessnkhokwe Před 5 dny

    Malawi akulamulidwa ndima Gamba ( mbava) kkkk

  • @user-nu3zg6pr1l
    @user-nu3zg6pr1l Před 5 dny

    God bless Malawi

  • @ulemujumbe8501
    @ulemujumbe8501 Před 5 dny

    😂😂😂kkkkk amn"gamba pompo mkokonda ndalama Ka judasi

  • @mavmsusa1310
    @mavmsusa1310 Před 5 dny

    Bwana, munayika sing’enge ndi sing’enge to surround you. Kkkkkkk

  • @WezzieNyasulu-cp7hy
    @WezzieNyasulu-cp7hy Před 6 dny +1

    This is funny kma experiencing someones life on other people so we can talk this is wrong

  • @Cathy-oc7vd
    @Cathy-oc7vd Před 5 dny

    Panu ndi pakamwa pompo... tachitani ng'oooo.. siyani mabodza awa

  • @user-dl2hs9mu2i
    @user-dl2hs9mu2i Před 5 dny

    Wabodza iwe ....... vuto lokhara kuja ndikumakolopa umalakhura zopanda zeru ngati izi

  • @mr_bsoc
    @mr_bsoc Před 3 dny

    Khad ndi dolo!

  • @HusseinAdamLidezo
    @HusseinAdamLidezo Před 5 dny

    Never give up

  • @joshuankata6967
    @joshuankata6967 Před 5 dny

    Woyipa ndiwe galu

  • @user-hw4yw7ex4j
    @user-hw4yw7ex4j Před 6 dny +2

    Mwati kamung'amba?😂😂😂😂😂

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Před 5 dny

    yes yes Comedy indeed

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Před 5 dny

    Zoonadi brother

  • @user-qq3ip1od6i
    @user-qq3ip1od6i Před 6 dny

    What's the ways forward,, now?

  • @user-vu9rt8gj3o
    @user-vu9rt8gj3o Před 5 dny

    Exactly

  • @jonathankumalasa
    @jonathankumalasa Před 5 dny

    Uyu ndi mbuzi heavy zomwe amakhulupilira anthu zopanda umboni wogwilika

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 6 dny +1

    away ndiozungulila mutu ndachisilu

  • @ChisomoKandikole
    @ChisomoKandikole Před 6 dny +1

    Odya naye mbare imodzi ndye amakupereka

  • @WisdomBlack-uu7zt
    @WisdomBlack-uu7zt Před 5 dny

    Mumatha boss inuyo ndi one

  • @LAKISSONEBINGOLOSSEMACUNHA

    Zovuta kwambili,malawi Sali bwino

  • @Simangalisiwe
    @Simangalisiwe Před 5 dny

    One thing that I know is politics is evil only God knows about Malawian

  • @user-wt9vb1vb5v
    @user-wt9vb1vb5v Před 4 dny

    Inuyo ndi ambuli amwene kulimbana ndima devo anzanu.bwanji?

  • @PidoMaganga
    @PidoMaganga Před 4 dny

    Kkkkk 😂😂😂😂 aaaa iweso uli molalo bwanji kkkkk 😂😂😂😂😂