KODI TINGAPHUNZIRE CHANI PA MOYO WA MALEMU SKC..hot current 23/06/24

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 22. 06. 2024

Komentáře • 20

  • @temwachaima817
    @temwachaima817 Před 6 dny +6

    Kodi bwanji wonder sikukubwela ma investigator osiyana siyana a independent from family or other groups we can't rely one side kodi ma citizens alibe kuthekela kutero

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 Před 6 dny +3

    Komano zakafukufuku ameneyu aaaaaa sayenda bwinoyi

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Před 4 dny

    Wonder msiska kikiki mpaka nthungululu😂😂

  • @MussaDisi
    @MussaDisi Před 4 dny

    Aaaaa muli limodzi inu

  • @takondwajamesdickson7917

    Aikiranji MDF momo

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl Před 5 dny

    Vuto si A U TM autsi ndi a mcp

  • @dumisanihara
    @dumisanihara Před 5 dny

    Who identify the investigators? That's a billion dollars question.

  • @user-to5of3ks3g
    @user-to5of3ks3g Před 5 dny

    Sound guys

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Před 6 dny

    Akanaitana ma Russian kapena ma Turkish even ma R.S.A koma ma Germany tambwita amalawi

  • @chachaamoah3592
    @chachaamoah3592 Před 6 dny

    Should we trust this ? Kafukufuka ameneyu zabodza

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 Před 4 dny

    The best way is for President to at least buy five aeroplanes which can be used internationally and two for domestic flights then at least buy 7 choppers / helicopters and use two as paramedics ambulances at least three of them and one on the standby for unseen immergency like it would have helped to identify ndege inagwa ku chikangawa. The president should for now stop buying expensive cars of suvs and focus on the main important things to put the lives of people at peace and safe. He has to do these exec orders and try to solve the problem problems first.

  • @godfreyzuze
    @godfreyzuze Před 5 dny +1

    Why not combining two or three different investigators from different countries inorder to deal with these other external interferences or influences either from the government or individuals?

  • @user-ri8em6my2e
    @user-ri8em6my2e Před 6 dny

    AUsiwa adasankhidwa kale ndiaChilima koma mkati mwaulendomu tamuwona Usi akusitha zochita zake kukhala ngati ndiwaMCP ndiye pamenepo aUTMwa ndizovutakuwakhulupilira ndikuwasapota aUsi

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 Před 4 dny

    Dyera la maudindo ndi covetousness and deception ndi zimene zikubvuta panopa. He is surrounded with Ana a Satana.

  • @violetnkhoma8535
    @violetnkhoma8535 Před 5 dny

    Kodi Chimulirenji sadali Vice President? 😂

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v Před 5 dny +1

    Kodi inu a times munthu amene amakuimbilani kumakuuzani za ndenge kuti ili kuno inu muli busy kunamiza anthu za live broadcast inu munalowaso ndale ndipo anthu anakutulukani

    • @GospelSoldiers-sr7np
      @GospelSoldiers-sr7np Před 5 dny

      Ndipo kwambili koma ziwani kuti Mulungu azaweluza tsiku lina,mukumakhala ndi mbali amalawi siwopusa ay

  • @godfreyzuze
    @godfreyzuze Před 5 dny +1

    Kodi amene awaitana kapena awapanga identify ma investigator wa ndi ndani?,,the government or the independent institution?