Msilikali wawopseza zowulula chilichonse pa kuphedwa kwa chilima

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 12. 06. 2024
  • Towards the goal channel

Komentáře • 536

  • @binosjoseph142
    @binosjoseph142 Před 14 dny +64

    We need such brave soldiers in Malawi

    • @allankumwenda47
      @allankumwenda47 Před 13 dny +1

      He is a liar

    • @thewnoc
      @thewnoc Před 13 dny +1

      Uyuyu si brave ndichitsilu akuonesa kuti anali ndi information yokwanila koma sanayigwikise ntchito ndikumadikila pa khoti
      Iyeyu ngati amawava anthu akulila and kudziwa mbali imene anali osanena or palediyo kuti ngati aboma akubisa koma team ina yofuna kufufuza mwachilungamo ipite ikapulumuse anthuwa😢
      Anthu ambiri akuonesa kuti amadziwa komwe kunagwera ndege koma osalankhula mpaka tsiku kutha kudzayambilaso mawa lake

    • @OTILEJOHN
      @OTILEJOHN Před 13 dny

      Amalawi anzanga tiyen tisaloleso kulamulidwa ndi mfiti chakwelayu

    • @user-nt8bd4yl7b
      @user-nt8bd4yl7b Před 13 dny

      Are you sure ndi soldier di

  • @user-ne7rn4ki3c
    @user-ne7rn4ki3c Před 13 dny +30

    Mulungu akuteteze fearless soldier for the first time to reveal the truth about chilima's and eight others death once again may Allah protect you all the time 🙏🙏 amen

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e Před 13 dny +19

    Yesu adafela kuyankhula chilungamo My God protect you Sargent

  • @MebleNgulinga-hi6rg
    @MebleNgulinga-hi6rg Před 14 dny +20

    Mzimu wa munthu osalakwa ngovutaaaaa Ichi nchiyambiii ziululika ndithuuu ñdipo nonse mwapanga izi mubweza one by one.......God he is watching

  • @user-er7ub4ug7y
    @user-er7ub4ug7y Před 14 dny +17

    Sitikuopa sitifooka dziko ndi latose ili ndipo tidzafera mbendera yake imenei 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼 very powerful word😢😢😢

  • @DIRECTORJARVMACK
    @DIRECTORJARVMACK Před 13 dny +34

    Zomwe zayakhulidwa apazi chimodzi modzi zomwe wayakhula wa bakili muluzi,nkhani iyi musayitenge ngati yabodza

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Před 14 dny +72

    Msilikari wabwino olimba mtima uyu tiyeni tigwire naye ntchito yothana ndi Chakwera

    • @OTILEJOHN
      @OTILEJOHN Před 13 dny +1

      Tinthana nae chakwela ameneyu

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 Před 13 dny +1

      Dat's true bro

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x Před 13 dny +1

      @@harrisbanda5891 Brother tigwirane Manja tonse ndimunthu m'modzi asatikwaneyi kumangoswa mitima yathu tiyeni timukodze

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 Před 13 dny

      @@user-uc1pd1tc2x I agree with you bro, zikufunika mademo adziko lonse kuti ng'onazi zituluke m'bomamu, tikupempha amabungwe kuti ayitanitse mademo ochosela asatana amenewa👉 👹👉👹👺👉👹👉👿👉☻👉👽👉👹

  • @user-gd2kl1fx1q
    @user-gd2kl1fx1q Před 14 dny +23

    Wonderful wankhondo

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 14 dny +18

    Good Messnge Chakwela achoke ndi galu

  • @ZondoChirwa
    @ZondoChirwa Před 14 dny +19

    A real soldier is like this man now deal with chakwera a Malawi don't leave him live.

  • @InnohLukah.1998
    @InnohLukah.1998 Před 13 dny +12

    Timafuna asilikali ngat awa...zkuvuta pati kodi kungodzuka kumpanga zomwe znachitika ndi nthawi ya pioneers....mukuchedwetsa zinthu bwanji kodi General 😢

  • @wilsonfelix6559
    @wilsonfelix6559 Před 14 dny +14

    Yehova akhale mbali yako

  • @user-ee6be5kl5o
    @user-ee6be5kl5o Před 14 dny +14

    Impeachment ichike achoke chakwerayo ndi munthu oyipa kwambili MCP ichikoke mboma ndipo anthu onse anduna zaboma amenewa aoñe nyekhwe Chaka Chino osawasekerera ayi apa zafika athipja tionse chakwera Mai amphamvu ulemu wanu msilikali wa bwino ameneyu

  • @AmaduJuma
    @AmaduJuma Před 13 dny +7

    Brother, you are our hero,keep it up and may almighty God protect you,chakwera ndi galu kwabasi,watipweka,😢😢

  • @mengokumwenda3832
    @mengokumwenda3832 Před 13 dny +5

    soldier I salute you for the bravery. Loyalty is always to the nation and its citizens and those in that plane were the citizens of this nation who died without being given a chance to live again

  • @WassiThandiwa
    @WassiThandiwa Před 13 dny +8

    Excellent work soldier. That's what Malawians want light know. Keep us updated

  • @charlesmasauko4651
    @charlesmasauko4651 Před 13 dny +10

    Apapa tidikiranso umboni wina wotani, chakwera akusowekera kudulidwa pa khosi ndi mpeni

  • @user-gx3xc9lk8x
    @user-gx3xc9lk8x Před 14 dny +14

    Sindinamuonepo mtsilikali olimba mtima ngati uyu ndipo pamene ulipo landilan ulemu wanu. Ndipo tigwirane manja tipange zothekera kut chilungamo chonse chidziwike

  • @user-es4jt6ds8m
    @user-es4jt6ds8m Před 13 dny +3

    Komaso msilikali uyu chonde tisamusiye yekha pliz a Malawi timupange sapoti pa chilichose kaye apita ku court tisonkhe chilungamo chioneke and wose amene sikuwakhudza agwidweso osawaiya ndi moyo

  • @IvyBanda-xs6sq
    @IvyBanda-xs6sq Před 14 dny +16

    No peace for wicked pipo😭😭😭😭😭😭😭

  • @zondwayongoma9481
    @zondwayongoma9481 Před 14 dny +12

    Osawopo bro god will protect your Malawi akufuna chilungamo mau a dr chilima azitilipikiska ngatikulikufa tizafele 🇲🇼 koma ifa chalima ndi zawo wose ife Malawi sitizayiwala moyo wa2wose never 😭😭

  • @user-ok7bq9es3y
    @user-ok7bq9es3y Před 13 dny +10

    Koma mabodza a Malawi tisiye, dzikoli ndi losauka, ma Vn enawa atha kuyambisa nkhondo, bwanji zonse timusiire Mulungu basi, ili ndi boza akunena mkuluyi.

    • @DIRECTORJARVMACK
      @DIRECTORJARVMACK Před 13 dny +2

      Silikaliyi akunena zoona m'bale wanga ndi silikali ku moyale balacks wayakhulaso kuti ndegeyo inafika bwino bwino koma pilot anaopsedwa ndipamene imatembenuka muona nkhondo mene imakhalila ku malawi

    • @ChikondiNyirenda-ei3vu
      @ChikondiNyirenda-ei3vu Před 13 dny +1

      Ndpo nkhan zabodza kuyenda changu.macadet😊

    • @user-re7fo3be2z
      @user-re7fo3be2z Před 13 dny

      Malawi is not poor country but these greed politics

    • @ezekielmselembo
      @ezekielmselembo Před 13 dny +1

      Ndipo amene angakhulupilire VN iyiyi ndi osaganiza bwino

    • @ShazieWaya
      @ShazieWaya Před 13 dny

      Ndipo anthu angopekera nkhani zabodza chakwera

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Před 14 dny +21

    Chakwera ndi mfiti guys tibweze tisaloreyi

  • @angelamanda1343
    @angelamanda1343 Před 14 dny +19

    Ooh my beloved Malawi 😢. We've been robbed 😢

    • @emmamwale1106
      @emmamwale1106 Před 13 dny +1

      😢😢😢robbed a good promising leader.. ambuye atichitile chifundo❤

  • @user-kc6tq6hz1b
    @user-kc6tq6hz1b Před 14 dny +13

    Go ahead a real soldier 💪💪

    • @sylvesteralfred8355
      @sylvesteralfred8355 Před 14 dny +2

      That soldier needs our support
      Let's not hear and keep quiet action is what needed most
      Fellow Malawians let's woke up from our sleeping together we can

  • @musaalani9113
    @musaalani9113 Před 14 dny +46

    The president must resign

    • @SameKaposa
      @SameKaposa Před 14 dny +2

      Exactly

    • @sylvesteralfred8355
      @sylvesteralfred8355 Před 14 dny +3

      That's true bro what is needed to be done is we all Malawians kuti tonse kugwilana manja basi izizi osaziziyilira ndithu let's woke up our force is what can make him resign soon 🤞💔

    • @user-jd9yz5hp7y
      @user-jd9yz5hp7y Před 13 dny +2

      That's for sure he must go the useless President ever in Malawi is Chakwera

    • @InnohLukah.1998
      @InnohLukah.1998 Před 13 dny +1

      Not even to resign komano angotichokera pakati pa amoyo

    • @zimmekapachika6784
      @zimmekapachika6784 Před 13 dny +1

      Kuyipa moyo

  • @shadraachshadinho
    @shadraachshadinho Před 13 dny +2

    That's my Nation kumangodziwa zophana kukakamira maudindo koma zinthu osayenda ayii eeh enafe nde tizangofera moyenda basi

  • @japhethjeremulimba
    @japhethjeremulimba Před 13 dny +4

    May the good Lord bless and be with you comrade, for sure God I'll protect you and cilungamo cioneka

  • @ThomChirwa-py8xo
    @ThomChirwa-py8xo Před 13 dny +3

    True brother chilima sanalakwedi

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před 14 dny +11

    Thanks so much God bless you silikali adzilimba mtima chilungamo chimamansula chakwela wawonje watibweletsela chitibwe wachilendo padzaka dzino koma pakale nthawi ya kamudzi tidziwona kunena chilungamo ayi mulungu alowelelepo ife tachepa nadzo 🙏🙏

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 Před 13 dny +3

    What a soldier!, continue braving up, tingoyika kaye malirowa ava kuyabwa Sangaphe tonse ,ukatambatamba look east😮

  • @chancyjuniormoleni9480
    @chancyjuniormoleni9480 Před 13 dny +6

    Pa kolona pokha paja, chilima knew kuti politics is dirty game and anapeleka moyo wake kwa mulungu. Mizimu ya anthu amfa ija those souls will never crossover into the light before chilungamo chidziwike

  • @DaveSitolo
    @DaveSitolo Před 14 dny +3

    Thanks very much Sargent James much appreciate for that God be with you at all times

  • @DivineMercy-df2pu
    @DivineMercy-df2pu Před 13 dny +2

    Expose them mfiti za MCP

  • @BartonMagaleta-be3dv
    @BartonMagaleta-be3dv Před 14 dny +6

    U r v chosen one by God to tell us v truth,bigup

  • @CHAKAKACHAKA-MANMW
    @CHAKAKACHAKA-MANMW Před 13 dny +2

    Fact Mr,Just KP your self safe apalibe chisisi pazikolapasi Mulungu alindinjila zake

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 Před 14 dny +9

    Go Go Soldier

  • @ManessMahuwa
    @ManessMahuwa Před 6 dny

    U can't even die,God is with you. And he will protect you, Go ahead and we will going to support you

  • @user-nz5jg5hv1m
    @user-nz5jg5hv1m Před 13 dny +2

    Awa ndi asilikali omwe dziko limafuna tiyeni tipange support chilungamo chifalikire paliponse aliyense achiwone

  • @user-zo1uz2uz9m
    @user-zo1uz2uz9m Před 7 dny

    🙌🏼🙌🏼🙌🏼 our mighty father protect you really soldier chilungamo chiyende ngt madzi mlungu atimenyela nkhondo zonse ziwoneka poyela I salute you chief ✊💪

  • @user-xd1cm7tm7t
    @user-xd1cm7tm7t Před 14 dny +18

    Tiphana asapite kumalilo

  • @user-dy4gc2hr5e
    @user-dy4gc2hr5e Před 13 dny +1

    Good move chakwera akuyenera kubwera 0yera apo bii akuyenera kuphedwaso sangaphe osalakwa

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v Před 13 dny +2

    Ndipo usaope aliyese azamfa yakhula basi chilungamo chiyende ngati madZi anyapala achabe chabe awa akupha azawo ngati khuku

  • @rosebychikopa9660
    @rosebychikopa9660 Před 12 dny +1

    May God protect you General Wasili

  • @PaulMunukwa
    @PaulMunukwa Před 13 dny +1

    Mtsilikali Okonda,dziko lake chilungamo Chiyende
    ngati madzi Malawi wake up

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 14 dny +5

    Mulungu akutetezereni inuyo biggy zombvesa chisoni kwabasi yohhh

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos Před 14 dny +18

    Bola asakuphe ase uyu ndi Satan weniweni chakwera wapha chilima 😭😭😭😭😭😭 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 Why Why. Chakwera Why 😢😢😢

  • @dominicmphepo-jk8lk
    @dominicmphepo-jk8lk Před 13 dny +6

    God bless and protect you dear brother a true son of the land Malawi,
    Ayaluka amenewa

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 9 dny +1

    Chakwela you mast go

  • @FrankLyford-fe2tf
    @FrankLyford-fe2tf Před 13 dny +2

    Pangani zomwezo bwana chilungamo chidziwike basi thank you mr

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 Před 13 dny +2

    My heavenly Father, perform wonders in Malawi especially in the minds of our callous political and religious leaders so that they know You in Truth and in Spirit as opposed to hypocrisy(Matthew 23:1-)

  • @BreezyRoben
    @BreezyRoben Před 13 dny +3

    We need people like you bru keep going we are not afraid

  • @3UBAWANJI
    @3UBAWANJI Před 11 dny

    We need soldier like you in this country

  • @CharlesTambala-zn2bd
    @CharlesTambala-zn2bd Před 12 dny +1

    We need people like you, boss

  • @George-zd5le
    @George-zd5le Před 14 dny +18

    Ana a muma 2000,simumadziwa za mcp singasinthe ndichipani chankhaza si iziiii

    • @Okalekale
      @Okalekale Před 14 dny +1

      Ine ndinabadwa m'ma 70s Koma maonedwe athu ndi osiyana.
      Democracy inaononga,economically komanso chikhalidwe cha a Malawi chinaora.Malawi anapenga mwachidule.
      Ma politician ndimbava zokha-zokha,Ali busy kusintha-sintha zipani chifukwa aliyense target ndi ndalama osati kutukula miyoyo ya a Malawi ayi.Komanso ndi ma puppets,amauzidwa zochita ndi azungu osati Ife amene tinawayika ma udindo.

    • @jenipherbanda3303
      @jenipherbanda3303 Před 12 dny

      Kkkkk ndipo zoona taziwano

  • @rejoicewrld124
    @rejoicewrld124 Před 13 dny +2

    We are with you we need justice

  • @amossinoden60
    @amossinoden60 Před 14 dny +2

    Brave soldier ku malawi mulungu akhale nanu bro

  • @augustMag
    @augustMag Před 14 dny +3

    There is GOD in the world tell us truth ❤❤❤❤

  • @RabiaOsman-wy1ud
    @RabiaOsman-wy1ud Před 14 dny +3

    Brave man. We pray 4you

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w Před 13 dny +1

    Mulungu siwosewelesa zibwanakumapanga koma pazikhala malile apapa ngat nzoona tithana osat masewero

  • @EmilyTembo-zu4zy
    @EmilyTembo-zu4zy Před 13 dny

    I respect u mr sir may God will stand for u for ever

  • @aggiemlotha1208
    @aggiemlotha1208 Před 7 dny

    It's time for Dr Manga 🎉... bachedwani mmabodzawa apa

  • @PatrickMalaw
    @PatrickMalaw Před 14 dny +3

    May God bless and protect you

  • @thewnoc
    @thewnoc Před 13 dny +1

    Tisathe mawu wamoyo kulibe wabwino amakhala wabwino akamwalila amene tikuwanyoza lerowa mudikile akatichokela ubwino wawo mudzuona
    Komano tilhale ndi mzeru mdithu osangotsegula kukamwa ngati anthu amisala
    Ine sinaoneko mtsogoleri wabwino munthawi imene akulamulila maka kumalawi kuno koma timazindikila ubwino wake mbari ina akamwalila

  • @muhabaulen7912
    @muhabaulen7912 Před 13 dny

    Ooh my allah guide and protect you mr watsili your really good ma of allah 🤲🤲🤲

  • @user-hx6jl2jq9j
    @user-hx6jl2jq9j Před 14 dny +2

    Mmmm chakwera afunika umumangilira pa mtengo angathawe buzi ya munthu

  • @user-ql9sp9hc6o
    @user-ql9sp9hc6o Před 13 dny +1

    Ma God protect u until you accomplish your mission. Dziko sili bwino.

  • @MaxiesGurvysproductionKamunga

    Chilungamo chi mamasula ukuteteza ndi mulungu

  • @DoreenEmmanuelj
    @DoreenEmmanuelj Před 13 dny +1

    Zikomo msirikali kulimba kwako mtima Ambuye akudalisen mochuluka usazione kuchepa wanyamula amalawi ambiri ndakudalira msirikali dziko ndirathu palibe zoopyesana

  • @JohnKamanga-tu2il
    @JohnKamanga-tu2il Před 13 dny +2

    Keep it up

  • @DannieChimenya
    @DannieChimenya Před 14 dny +3

    ndiye wati abwanawa amakunyasa 🥲🥲🥲

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m Před 13 dny +2

    Apato apresedent atiuze choonadi chifukwa dzikoli lamunthu Wina aliyese silanu nonkha ayi no kuopse zana

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba Před 13 dny +1

    Vuto asilikali akumalawi tulo limakuzazani mmakhalangat simuziwa chomwe silikali amayenela kupanga enafe mwai unangotiphanya bwez tikuthana konko mafelano

  • @MarthaBanda-ye4pt
    @MarthaBanda-ye4pt Před 13 dny +1

    The problem we have Malawians we always say we need people like you but we don't support tilibe kugwilizana that's y things zikumkeramkera koonongeka ..........dziko la Democracy limeneri? ....ufulu wanthu ukuonongedwa ife tili chete ........DZUKA MALAWI PLEASE!!!!!!!!!!!!!!!!!!

  • @FatimaMsusa
    @FatimaMsusa Před 14 dny +2

    Kodi akuluakulu chakwelayu... Akuonangati ife ndizitsilu... Ife timaganizatu

  • @GloryMathungwe
    @GloryMathungwe Před 13 dny

    Ntchito ya mulungu nde imeneyo . Mulungu sakusiya wekha gwira ntchito molimbika strong soldier ✊

  • @PriscaArthur
    @PriscaArthur Před 13 dny +1

    Ameneyi aulule basi munthu wabwino iweyo tanena tiwone ponamila achakwela ku anena chiyan

  • @PililaniChipendo
    @PililaniChipendo Před 13 dny +1

    Chilungamo chibwera poyera God is watching

  • @StiveriaMisuli
    @StiveriaMisuli Před 13 dny +1

    Ndilitu mbali yanu ineyo ndipo 100% akufuna kuoneka ochenjela amalawi ake siapanowatu ayi muziwe kuti sife ogona ndipo muziwe kuti zomwe mwapangazi mulungu aliko muzafa imfa yowawa ndiyochitisa manyazi kwambili afisi azang'ambilana thupi lanu ndikulidya mosakupasaniso ulemu kuti munali ndani zowona chifukwa chani koma kumumpha zanu ngat chinyama 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @wilsonali7890
    @wilsonali7890 Před 13 dny +1

    Ameneyo ndiye Msilikali okonda dziko lake

  • @user-ei6ji9qj8u
    @user-ei6ji9qj8u Před 13 dny +3

    Mmmmmm awatu apupuluma ndipo awapha mpaka sitipeza uboni 😢 mukanadekha Kaye ndikuona ngati mwafulumura

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj Před 13 dny

      Ndiwabodza uyu sisilikari uyu ali ku South Africa uyu

    • @gilamwelekedwa4889
      @gilamwelekedwa4889 Před 13 dny +1

      If he knew about this he’d have done something right way before the plane took off because he knew the damage and danger ⛔️ that would happen why he didn’t stop it 😢he’s guilt too? He could have gone on and reported this before the flight ✈️ took off if he knew all this information. He played part too mxiii

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure Před 13 dny +1

    Oooh God, awonetseni kuti mumatha

  • @BlessingsNyirenda-ru7ss
    @BlessingsNyirenda-ru7ss Před 14 dny +8

    Asilikali wose akanakhala ngat uyu bwez zinthu zikusintha but we are sheem na president

  • @ZahirMatiya
    @ZahirMatiya Před 13 dny

    God bless you ,watching from Durban❤

  • @peterphir2250
    @peterphir2250 Před 14 dny +2

    Akulu ndikupempheni kuti information yonse muli nayo mugawire wina wachinsinsi kuti nayenso asunge chifukwa anthuwa akhoza kukukwenjani kuti muwapatse zonsezo kufafaniza umboni so please take my advice

  • @steventelfer8186
    @steventelfer8186 Před 13 dny

    Thank you sir. I’m with you.

  • @user-fb1eq3jg1e
    @user-fb1eq3jg1e Před 6 dny

    Wonderful wa nkhondo

  • @user-td6qe4gr6w
    @user-td6qe4gr6w Před 13 dny

    Bravo, the true, courageous soldier

  • @CharityPhiri-rl7sz
    @CharityPhiri-rl7sz Před 13 dny +1

    magazi amunthu osarakwa chilichonse chiziwika la 40 likakwana

  • @user-mi3fw1zg8b
    @user-mi3fw1zg8b Před 13 dny +1

    But why?! Why?! Why? Mr President Chakwera u are so wicked, Evil man kupha Anthu osakulakwira why?😭😭😭😭😭😭😭

  • @dingychirwah2701
    @dingychirwah2701 Před 13 dny +1

    I choose to mourn our VP and those other innocent lives without pointing fingures . If he has evidence let him bring it , but we cannot just believe speculation.

  • @LinesiKanzota-fw7sj
    @LinesiKanzota-fw7sj Před 13 dny +1

    Mulungu mutetezere ,msilikaliyo asamuphe chakwerayo NDI we otani kuyipa tima chomcho iweso chakwera sukhala NDI Moyo Ufa ndithu mulungu akutenga

  • @wickymalawi
    @wickymalawi Před 14 dny +1

    God protect you boss

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 Před 13 dny

    We need people like this Man is telling people the truth keep it up Chakwera is a killer

  • @user-fj7dy1hi2q
    @user-fj7dy1hi2q Před 13 dny +1

    Akanakhala hero akanapanga chothekela kuti ndege ya Chilima isanyamuke, apapa we can't yield anything zachitika munthu wapita basi

  • @SuzgoMunthali
    @SuzgoMunthali Před 14 dny +3

    Ana ma 2000 akuvuta

  • @Bthula
    @Bthula Před 13 dny

    AMALAWI IF YOU REALLY love chilima and your country you must rise up

  • @MaggieNgodwe
    @MaggieNgodwe Před 13 dny +1

    Amen brother

  • @OmegaChaula
    @OmegaChaula Před 8 dny

    Kupanga campaign paground pakuvutani aphumbwa ndiye mwalowela paimfa ya chilima, Blackbox itiuza zonse. Munatha ma albino inu. Ndipo mnalonjeza kuti muzathana naye chilima,

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Před 13 dny +1

    Ambuye akudalitseni bother ndipo akutetezeni koditu muthu umatha kunena kuti ndi kumupha uyu kuti ineyo mawa ndidzale papando sudziwa kuti mawa lako ndulotani ndipo uve kuwawa chakwela mulungu akupatse chilango uli moyo ukuzuza a Malawi munjila zambili chifukwa uli papando koma mulungu akuone iweyo