![MALAWI TODAY](/img/default-banner.jpg)
- 7
- 213 717
MALAWI TODAY
South Africa
Registrace 18. 09. 2022
This Channel aims to inform, educate, Entertain and help Malawians.
Zoona A President Tizikhalira Kukukuwani? Wonder Akutero. 8 Oct 2023
Zoona A President Tizikhalira Kukukuwani? Wonder Akutero. 8 Oct 2023
zhlédnutí: 12 158
Video
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke// PART 2
zhlédnutí 46KPřed 8 měsíci
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke// PART 2
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
zhlédnutí 153KPřed 8 měsíci
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
Kkkk koma ndaseka mokweza atagwilana ndi nzungu 😅😅😅😂😂😂
Thanks for sharing us about our wickedness in Malawi in my opinion is Mr Chikwara is not nice president of Malawi he is after money laundering and killing innocent people x
Reality is needed to make something right
Stay safe Mr Kapito
Mukanakhara Ku UTM tikanasithisa mukalumbire mukatituluse pamoto
Ineyo I don't say much kuopa wat am saying is may the good Lord in heaven protect U in his wings be safe my father it's my prayer eeeesh real man for Ur own parents who is U exactly heeee God save my father his real
God bless you Mr Kapito wayankhula mfundo zenizeni❤
iam agree with you big kapito you are talking truely but dpp was tried than this
This man has leadership qualities right away from secondary school days at Mulanje Secondary school . Malawi needs leaders of Kapitos cariber.
Mpaka zizukulu
Nthawi imeneyi dpp imalamula otsutsa amatsutsa zimene iwowo akhoza kukonza zinthu koma zinthu sizinasithe ndiye lero kuti dpp azitsutsa a mcp akhoza kumati munali m'boma momwemu mumatani ndiye izi ndi zandale zozuta kumalawi bas
What i don't understand is that if Malawi is a democratic country....i believe that the cabinet sits down to table programs of how to run a nation..now blaming the president only is wrong ....all in the boat are rotten.... don't deceive us.....
Mr president where ever you are....us in South Africa and all over the world are suffering..No passports... expired passports.... sought immigration please 🙏
We don't need to come home to corrupt immigration officials to have a passport... it's our citizen right.....we paid but we can't get our passports 😢😢😢
Mr kapito well said as far as you not talking on behalf of someone....
Then don't comment if you don't trust him
Malawi needs the young leadership with vision...all old people please sit down....u have not done our country any good
Thought out immigration....we are outside the country No passports.....suck corrupt officials... this is unacceptable
From kamuzu banda ...up to now no real leadership only stealing.. corruption.. nepotism and bringing down the country....
thank you sir kapito for your explanation
Mr kapito keep going
Panopa ndawamvesa a DPP chimene amakhalira chete President uyu ndi wamagazi ifeyo tikuziwonela kunja koma anzathuwa akuziwonela pafupi President uyu si munthu wabwino a DPP akhalebe chete mpaka campaign iyambe
Koma apapa mwayankhula chilungamo ngakhale msogoleli alindimaganizo amenewa likhoza kukhala boma mkhoza kuyendesa boma bwino ❤❤❤❤
Bravo kapito 100% agree 👍
Ur a man full of wisdom.
Mmakwana inuo mulibho
koma boma ndi ndale zinayandikana kwambir mpake dziko silitukuka ku malawi. thanks mr kapita❤❤❤❤
Chifwamba chimenechi chinawina chifukwa cha nfundo za chilima
Mr Kapito tikupempheni mubwere ku UTM muzatiyimilire u president ine ndimafuna munthu wosatila zama Reform ngati inu bwana
Bwana kapito kuzang"alula khokhooo
Good Mr kapito
Mr Kapito a man himself he doesn't fear nothing .He is so intelligent
Good explanation without taking politics but only justice ⚖ landilani ulemu Mr John Kapito😊😊😊
He is agreat man
Mr kapito mumakwana mukunena zoona
True son of malawi kapito
Good explanation posatengela ndale ❤ koma chilungamo chokhachokha
Time to say truth has come
Ndilibe mau mbili bwana kapito you're good man you're a m'dala 😂😂😂😂😂😂😂😂
Akungomva za azikhale ng'oma za maganizo akhupha basi
Zoonadi,kudzikonda. Zimandiwawa zomayambitsa chitukuko ndie chikawina chipani china,nkusiya chitukuko chija osachipitiliza chifukwa anayambitsa ndi achipani china. Chitukuko chimakhala cha chipani kapena chotukula dziko lathu and a people as Malawians?
This man is speaks the truth
That's talking mr kapito, tell them n open the eyes for Malawians ❤
Good one
Mr John kapito keep on trying to assist the blind
Mr Kapito katswiri
Big up
Carry.on.bwana.kapito
Kuyankhula momveka bwino mr
Kodi Kapito ndi life president wa Consumers Association? Munthu wanji osasiiira udindo anthu ena? Kapito is irrelevant and wasn't he there when Peter Mutharika messed things up? Alomwe musatinyase ndipo musatibowe. Kagweleni uko ndi Peter Mutharika wanuyo. In this 21st century, basi kumafuna kulamuliridwa ndi munthu wa zaka zoposera 80? Are you people normal? I guess not.
Well said kapito 🔥🔥🔥🔥
Well said kapito🔥🔥🔥🔥🔥
Bakili tv we miss u😢