MAYI WINA WAGONANASO NDI DOCTOR WA PRESIDENT KU STATE HOUSE

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 23. 09. 2023

Komentáře • 88

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před měsícem +3

    Koma nde kuyalukatu boma la chisembwere ngati ili sinaliwonepo yohh
    Keep it up Mr ntanyiwa more fire

  • @fredalbert6998
    @fredalbert6998 Před 2 dny

    More fare🔥🔥🔥🔥 tili pambuyopanu

  • @user-ny1ml7ow6u
    @user-ny1ml7ow6u Před 6 dny

    Continue telling the truth

  • @alickalick6509
    @alickalick6509 Před 9 měsíci +2

    LIMPOPO FM moto kuti buuuuuuuu with Comrade MTANYIWA
    Awululeni ayaluke anthu oyipa a Mcp

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 Před 9 měsíci

    I like the song

  • @chiphalechima831
    @chiphalechima831 Před 9 měsíci

    Nice one song

  • @HassanantonyHaxy1
    @HassanantonyHaxy1 Před 21 dnem +1

    From nsanje boma Limpopo fm ❤❤❤❤🔥

  • @wilisonbornface4282
    @wilisonbornface4282 Před měsícem

    Watching form South Africa

  • @WakalalaMtiozi
    @WakalalaMtiozi Před 13 dny

    Ndiyakhepo pa mayi akunedwayo malemba akunena kut . Wawuze athu zomwe wawona ndimaso wosati zakuva ndiyena ayi kid chikakhala chabodza wukwanitsa kwawuza athu ones amen wawuzawo pepani baba yakhulani zowomwe mwawona ndimaso

  • @KondwaniMwasinga-rs6kv
    @KondwaniMwasinga-rs6kv Před měsícem +1

    Limpopo FM keep it up

  • @victoriabanda7828
    @victoriabanda7828 Před 9 měsíci +1

    I like Bakili muluz, amapeleka ma umboni, pankhani zake

  • @leonardjika2100
    @leonardjika2100 Před 8 měsíci

    A NEW THINKER WISE WILL GOVERN OUR LAND SO HELP ME GOD

  • @Mark.P1u3
    @Mark.P1u3 Před 2 dny

    Mark pastor 9:14

  • @MerryWayson
    @MerryWayson Před 19 dny

    Ai A Cormled Kunotu tadzuka bwino ndithu , Aaaa A MCP mama Mr Chakwera akusaka pofera awapeza amene wawasogozao Chakwera pompano

  • @blessingbanda6206
    @blessingbanda6206 Před dnem

    Usapelekele umboni wabonza Mulungu akuwona zonse

  • @argentchilanga3246
    @argentchilanga3246 Před 9 měsíci

    Takunvani a Limpopo FM nkhanga zaona poti mayi Wina wadyesa nyemba Kwa dotolo was apresident kkkk

  • @asivenathilitye7268
    @asivenathilitye7268 Před měsícem

    Continue is a good story

  • @agnesmkanthama5327
    @agnesmkanthama5327 Před 15 dny

    Mmmmm nanga mpachisanu, kwa a banje, cha MMA 4,😮

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r Před 3 měsíci +1

    Kkkkkkkkk km kwathu nkokoma umangovuta ndi umphawi basi

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll Před 9 měsíci +2

    Ameneyu kennako agona ndi a president 😅😂😂

  • @user-cy2db4fs7w
    @user-cy2db4fs7w Před 9 měsíci +1

    Ayaluse moto kuti boooo😊

  • @FloraRonard
    @FloraRonard Před 19 dny

    😢😢😢

  • @languitoneelias9972
    @languitoneelias9972 Před 11 hodinami

    Nde pali vuto lanji?mwaiwala kuti mkazi wa bakili muluzi anagonana ndi bodygurd inunso ukape bwanji

  • @user-zz1mf2li5s
    @user-zz1mf2li5s Před 5 měsíci

    Mmmmmm zamabodza izi ndinu macadet inu 16:40

  • @Kalumbijoyce-hb8gr
    @Kalumbijoyce-hb8gr Před 9 měsíci

    Usatanic wawowo 😂😂

  • @DalitsoKaunda
    @DalitsoKaunda Před 12 dny

    Kodi mayi ameneyo wabuyi buyi ndindani abale

  • @dianandove7031
    @dianandove7031 Před 16 dny

    You Malawias you need president like Kamuzu Banda .you dnt have respeck

  • @asivenathilitye7268
    @asivenathilitye7268 Před měsícem

    Thaulandndila moni

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Před měsícem +1

    Osawopa inu nde mumanena zoona
    Ndi aBakili mulizi TV

  • @blacksonpeshes5057
    @blacksonpeshes5057 Před 2 dny +1

    takudyadirani tizikupemperelani kut asakupezeni

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga Před 18 dny

    Awadiaziwada ofunikila motobasi ahebili 12:29

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 Před 9 měsíci

    Limpopo FM zikomo moni talandira koma mabvuto onsewa anthu ena oipa anachita kuwasankha

  • @user-pi8mz3bx9n
    @user-pi8mz3bx9n Před 9 měsíci +2

    Nkhanga zaona!!!!!

  • @Kalumbijoyce-hb8gr
    @Kalumbijoyce-hb8gr Před 9 měsíci +1

    Chiwandadi chimenecho

  • @ZinawZinawmulu
    @ZinawZinawmulu Před 16 dny

    Mumativesa kukoma amkanga zaona mupitilize kutelo ine Balakasi

  • @zacariasjoselemessonelemes9562
    @zacariasjoselemessonelemes9562 Před 9 měsíci +1

    Nkhanga zawona kkkkkk

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Před 9 měsíci +1

    Kustate kwasunduka ku ndagala chifukwa chotenga mahule osalimba nsalu nkumamagwira ntchito lero ndiidzi nyumba yolemekedzeka ikungomveka zausiru zokha zokha kodi nthawi zija simungamakambirane zosisa mitengo ya zinthu zomwe munkalonjedza zija kapena mwalephera kusisa ? 😂😂😂😂😂😂

  • @user-mb2sn3xv7p
    @user-mb2sn3xv7p Před dnem

    Koma yah

  • @ClementMushele
    @ClementMushele Před 20 dny

    Komano man ngati umanena zoona iweyo ndi katundu umakwanila

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před měsícem +1

    Achitsilu mulibe zochita mukufuna kumanamiza Malawi basi

  • @MillyKachepa
    @MillyKachepa Před 21 dnem

    Koma kuli zinthu 😮😮😮😮

  • @user-uw3sp6rq8m
    @user-uw3sp6rq8m Před 4 měsíci

    Chakwera ananyenga kale mkazi ameneyu chitsilu choke alone ena dzamuchima

  • @wellingtonmtoso2074
    @wellingtonmtoso2074 Před 9 měsíci

    Innnuu mwatani kodi pezani nthawi nanu mukaloweko kenako tidzamve za inuyooo mmmm

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z Před 22 dny

    Koma azibale ndichani kwenikweni agalu amenewa?

  • @user-dt8nr1zx6e
    @user-dt8nr1zx6e Před 9 měsíci +1

    Nkhanga zoona mumatiimilira

  • @stalickkafera3454
    @stalickkafera3454 Před 19 dny

    Za bodza
    Munthu wamkulu ngati iweyo pali nkhani yoseketsa
    Mau onyasawo

  • @user-tw2zf7bj3e
    @user-tw2zf7bj3e Před 9 měsíci +1

    La 40 limakwana

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw Před 4 měsíci

    Akatero ndinkazi wamweni wake uhule basi zisilu ziyanthu zaku paliyameti ko

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 9 měsíci +1

    Kwachema

  • @ImraanJafali-dk7rg
    @ImraanJafali-dk7rg Před 9 měsíci

    🤓🤓🤓🤓 Kwamvuta akutinyasa ife achakwela

  • @user-km3ek5pl3p
    @user-km3ek5pl3p Před 6 měsíci

    Nthawi yake iiiiiiiiiiiiiii

  • @KhefasKhembo
    @KhefasKhembo Před 18 dny

    Koma man mukunenadi zoona kuti anthu agonanadi aaaaa

  • @Kalumbijoyce-hb8gr
    @Kalumbijoyce-hb8gr Před 9 měsíci

    Ufitiwawo waonekera

  • @promisebanda8785
    @promisebanda8785 Před 9 měsíci

    Koma ngt irinyere😂😂😂😂

  • @judgeshonga
    @judgeshonga Před 17 dny

    Chonde muzifika pa point msanga pankhani osamachulutsa zolubwalubwa

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 Před 9 měsíci

    Abale zikuoneka kuti atsirikali athu sidzikudziwika mbali yeni yeni komanso ntchito yawo akuyenera kugwira chifukwa kale a Malawi timadalira atsirikali kuposa police popedza zonyansa zonsezi akuchitazi anayamba kale mogwiridzana ndi mbiri ikufotokodzera

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa Před 21 dnem

      Anawagura akulu akulu a boma nde ntchito zawo sizingaoneke komanso ovutika ndi apansiwa

  • @phillimonzgambo1663
    @phillimonzgambo1663 Před 9 měsíci

    Nkhanga zaona

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 9 měsíci +1

    Mulungu aliko atimenyere nkhondo 😜😜

  • @triza.kamwanjatalandira446
    @triza.kamwanjatalandira446 Před 9 měsíci

    Koma.abale misonkho yaamalawi ikungowonongeka

  • @RoseChinseu
    @RoseChinseu Před 15 dny

    😅😅😅😅

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 9 měsíci

    Alomwe namwe tikati panji mazelu muli vizeleza kuyowoya unenesko cha muli vindele

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 Před 9 měsíci

    Chakwela anamunyenga kale mai ameneyu

  • @NyirongoMexonyoba
    @NyirongoMexonyoba Před 22 dny

    Kkkkkkkk kuyaluka

  • @thomasnyasulu
    @thomasnyasulu Před 9 měsíci

    Koma boma la MCP imeneyi, laposa la Kamuzu.

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o Před měsícem

    Ma cadet a lomwe a khutukumve inu usatibowe mulibe zochita koma kupeka nkhani zabodza

  • @MaggieGondwe-vn2wx
    @MaggieGondwe-vn2wx Před 9 měsíci +1

    Mumativetsa kukoma ankhanga zaona

  • @AlinetMatewele-cp7ru
    @AlinetMatewele-cp7ru Před 9 měsíci

    Chofunika.mulungu.amukkhudze

  • @NoahJumbe-fi5hv
    @NoahJumbe-fi5hv Před 9 měsíci

    Izi SI zoona chifukwa simuonetsa zithuzi kuti ngati ndizoona muzionetsa zithuzi zao mkumalankhula nao

  • @Kalumbijoyce-hb8gr
    @Kalumbijoyce-hb8gr Před 9 měsíci

    Washing for south Africa 😂😂😂yomweyo galuwee

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 Před 3 měsíci

    Tiuze cadat

  • @ulemuchigoma4899
    @ulemuchigoma4899 Před 9 měsíci

    Fake channel i like Bakili Muluzi Tv he provides evidence

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před měsícem

    Bodza kufuna kutchuka awa

  • @user-pn7lx1oo1l
    @user-pn7lx1oo1l Před 9 měsíci

    😂😂😂😂😂 koma nde zovuta bwanji

  • @philimonstepe4795
    @philimonstepe4795 Před 18 dny

    Koma nkhani Zina muzitipatsako ma umboni osamayankhula ndiye pot a Malawi tazolowera kunamizidwa

  • @Brockbaby143
    @Brockbaby143 Před 8 měsíci

    Zikuchitika kuti zimenezi,propangand yake ndie yopanda umboni.

  • @GodfreyTsumba
    @GodfreyTsumba Před 9 měsíci

    Mmmm this is political propaganda, you are not a true journalist my friend but a politician

  • @SPAGHETTI313
    @SPAGHETTI313 Před měsícem

    😅😅😅😅