Mr.Kamulepo and this man Bon Kalindo,we don’t need Chakwera to proceed ruling this country up to November 2024.Please let’s organise tough strategies for him to step down.Bravo Kamulepo,Bravo Bon Kalindo
To be honest Malawi is going backwards people voted for Tonse alliance for hoping better life but federal system of government is the only way enough is enough.
Take that word .they will not manage what is coming , i believe something big is coming i say it again something big is coming anyamata soon azuka ndipo it will be like Kenya 🇰🇪 anthu akatopa amatopa kuti topi kungotopa basi
Inu a Nonse Alliance ndinu mwaba cilungamo CA a Malawi . Leromukamaphedwa, nokha mukudabwa! Mumanena kuti Peter wadaba vote za Chilima ndi za Chakwera. Za Atupere ndi ena Peter sanabe. Bwanji bwalo lamirandu linalola zipani 9 zikhale pamodzi? Tsono lero mukuti mukubwerera ku Cipani cimodzi? Pamenepa opusa ndani?
Mr. Kamlepo Kaluwa, ndine Mponda kuno, ndidakali kuno ku Soweto, but a'm taking my pension next year, I will be meeting you next year. I think u remember, Japheth Nkhoma, Mr. Kanyongolo, Mr. Maseko all from Soweto
Mcp yapalamula chitedze,,, when you pray for the rain deal with the mad too,, Chakwera umva madzi chaka chino ine Mulungu anandiyankhula momveka bwino kuti akuvupula kowopsya,uyaluka,, ngati ungathe umupatse makobili Mulunguyo tiwone, my God is exposing you this year you are finished,, awa ma prophet mwawapatsa ndalamawa akukunamizani ask me i will tell you what the Mighty Lord God said,, your judgement has just begun enjoy it
Once an eagle always an eagle. We believe in you the real freedom fighter legend Kamulepo Kaluwa. We're going to vote without their stupid ID'S protocol
The Dangerous Freedom Fighter of Malawi Nation, Kamulepo Kalua.. Our trust is on you Mr Kamulepo. Long live our freedom fighter
Mr.Kamulepo and this man Bon Kalindo,we don’t need Chakwera to proceed ruling this country up to November 2024.Please let’s organise tough strategies for him to step down.Bravo Kamulepo,Bravo Bon Kalindo
Ana asatana amakomenta zodana ndichilungamo ife pambuyo panu mr kamlepo ❤❤❤❤❤❤❤
Bravo Mr Kaluwa . Timadziwa Mr Kaluwa simunthu wamba kuti angamayankhe mafunso opepera ndipo wamuphu nzitsa kafunsidwe mtolankhani wa DPP yu . Siungamuthe Kamulepo wachepa
Good Messnge Mr kamulepo kaluwa, Chakwela you mast go watikwana
Well said, Commander. People don't know that you are a Field Marshal
a veteran freedom fighter,, a comrade, last man standing
A mr. Kamlepo Kalua munayamba kale kumenyela ufulu, ndipo sitilola a Malawi. Alephera achoke basi. A Malawi ndi okwiya kale ndi ulamuliro wa chakwera.
Malawian majority is Malawian s not achewa, big up kamlepo no divisions in Malawi, Malawi is 1
Mr unable kamulepo kaluwa you are a hero thanks dad for speaking the truth we know as anew generation
Munthu wankulu kuyankhula mosaopa ngat mene amayankhula nthawi ya kamuzu nde chakwera ndindaniso pano anthu anachenjera kusiyana ndi nthawi ya kamuzu
God bless mr kamulepo ❤❤❤❤
Powerful Mr kamlepo ❤❤❤
Mukusewela ndi kamlepo munthu amene amatha kupanga mabomba wanya chakwera
A MCP aputa Munthu wolakwika.
Nzeru zikacuruka Zina zimataika Cifukwa ninji munapanga zipani 9 kukhala Nonsa Alliance mukudziwa za ufulu wa zipani zambiri?
A kamlepo mulungu adzikudalitsani ❤🎉🎉🎉🎉
God bless you.
Good news Limpopo makwana💪💪
Well spoken loud and clear 🔥🔥🔥🔥
Tnauzidwa kt tizawuzidwa pakadutsa masiku 10, koma mpaka pano kuli ziiii!
I love your speech bwana Kamlepo
Atapezeka awiri atatu olimba mtima ngati Mr. Kaluwa ndithu things can change koma vuto ndi mantha amalawi😢😢😢
To be honest Malawi is going backwards people voted for Tonse alliance for hoping better life but federal system of government is the only way enough is enough.
Koma sitima yayamba kudutsa ku area 50 inatha njanje
Ekwendeni to Euthini anausiyizila pa T/A Mtwalo please wativwileko msewu wajimika chomene wula tikusuzgika pakuya kukaya ku Euthini mwee😢
Comrate kamulepo kalua he is great man,
Am listening ❤❤❤❤❤❤go deeper ❤❤
Tose tivota kuno
Mwayowoyako va zeruu mwahuno
Kandeu from south africa currently za ndengezi zisatidwe bohboh China chake sichilibwino
Federal system of government it's the best in Malawi, we wa development not to keep billions for Malawians in the pocket,
The message is clear
Mwatikondwesha dada kaluwa u president ukumuyanani not galu uyo walipo watikomera chilima
Good talking mr kamlepo
Fight for Malawians mr tivote tonse opanda ma ID basi fire eee
Inu wakwanatu chakwela 😢😢😢
Program yofunikira kwambiri
More fire kamplepo❤❤
Kamulepo❤❤
Ngt zili zomagendanazo muwaudze asayerekedze kufika ku southern region azaona nyekhwe
Kamlepo adang'aza uyu ha is not the one I was listening in those good old years, he is mad now, shame
Mudziko muno tikufuna anthu ngati awa oyankhula chilungamo, osaopa ife tikufuna dziko lathu aliyese asangalare osati akumipando okha ayi
A MALAWI TISALOLERE CHIPANI CHIMODZI CHOKUPHA ANTHU OSALAKWA. AMALAWI DZIKO LATHU SILACHIPANI CHIMODZI. AMALAWI TIYENI TILICHOSE DZIKO LATHU PA UMPHAWI WA MCP
Bola MCP isamuphe kamlepo. Anthu akupha awa. Mulungu chonde apengetseni misala a MCP
Take that word .they will not manage what is coming , i believe something big is coming i say it again something big is coming anyamata soon azuka ndipo it will be like Kenya 🇰🇪 anthu akatopa amatopa kuti topi kungotopa basi
Akuti ntolakhani , osadziwa kuti CENTRAL GOVERNMENT OR FEDERAL GOVERNMENT ndichyani kukhuta NAPWIRI basi
Let's violence now tawonelera nyasi nthawi yaitari
Bravo Mr Kamlepo Kaluwa
❤ the greatest chat
Powerful 👊
Powerful 👍 👍 👍
Bvuto ndi mcp administration umbuli wachuluka from the president down the line mbuli zokha zokha.
Chilungamo
Ofunika kwasumila amenewo a mcp
Chakwera pa thako pako kwizako Kuno Ku muponto Yai .kutikomera mubaliwinthu Yai
Kamulepo munthu mulala chomene
Ndamene anayambisa democracy mmalawi. Simunthu wamba uyu. Ali ndi history
✊✊✊✊✊l love your speech Kamulepo kaluwa
Live from south Africa
Inu a Nonse Alliance ndinu mwaba cilungamo CA a Malawi . Leromukamaphedwa, nokha mukudabwa! Mumanena kuti Peter wadaba vote za Chilima ndi za Chakwera. Za Atupere ndi ena Peter sanabe. Bwanji bwalo lamirandu linalola zipani 9 zikhale pamodzi? Tsono lero mukuti mukubwerera ku Cipani cimodzi? Pamenepa opusa ndani?
Mr. Kamlepo Kaluwa, ndine Mponda kuno, ndidakali kuno ku Soweto, but a'm taking my pension next year, I will be meeting you next year. I think u remember, Japheth Nkhoma, Mr. Kanyongolo, Mr. Maseko all from Soweto
Following
💪💪💪💪🔥🔥🔥
Achikule munthu wazeru
Mumanena chilungamo
2025 tikubwera komweko ife usilu ayi
Mcp yapalamula chitedze,,, when you pray for the rain deal with the mad too,, Chakwera umva madzi chaka chino ine Mulungu anandiyankhula momveka bwino kuti akuvupula kowopsya,uyaluka,, ngati ungathe umupatse makobili Mulunguyo tiwone, my God is exposing you this year you are finished,, awa ma prophet mwawapatsa ndalamawa akukunamizani ask me i will tell you what the Mighty Lord God said,, your judgement has just begun enjoy it
Zidze mzatonse
Mmm but this chipani mcp mmmm not good
Strong speech mr kamlepo ambuye akutetezen bwana
Koma ndiye za mowadi zaziiiiii 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Tiye uko mwana wa mcp iwe kupusa kwako
IQ zero
Pita kanyele uko mwana wa nyau iwe
Ngat manyi akugwiran kanyelereni musatinunkhise apa iya
Galu wachabe chabe
Let's learn from South Africa what H E Ramaphosa had done t o bring unity and patriotism bent on his genuine philanthropy. Long-live!
Mcp she is not going anywhere
😂😂😂😂 She is?
Chizungu cha mcp chimenecho kutathauza kuti onse ndi akazi wokhaokha Aku mcp ko 😂😂😂
Lol😂😂😂
Chizungu chaku gule😂😂😂😂
Aweeeeee 😂😂
Once an eagle always an eagle. We believe in you the real freedom fighter legend Kamulepo Kaluwa.
We're going to vote without their stupid ID'S protocol