A ZIKHALE NG'OMA UKU NDIYE KWATENTHA🙌🙌🙌 TAMVANI MFUNDO ZOMWE ABWELA NAZO

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 10. 07. 2024

Komentáře • 540

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi Před 22 dny +22

    Malawi chikangawa party

  • @ackimchindimba9912
    @ackimchindimba9912 Před 21 dnem +6

    Mudyeleni apapa ndalama ziyamba kuphweka bas ndi kampeniyi tiyeni tiwadyele koma tonse ndikudziwa kuti ndife APM

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 Před 21 dnem +11

    Nyama za mmanyumba mwanu. God is good and his eyes can see even in the heart of everyone. It will not work in the Name of Jesus

  • @anniedennis7127
    @anniedennis7127 Před 22 dny +11

    Ng'ona zodya anthu zingalamulire anthu

  • @user-wq3dh1ly2o
    @user-wq3dh1ly2o Před 20 dny +3

    Olo patavuta bwanji simungalamulileso dziko la malawi chifukwa munataya chipangano ambuye sangalole kuti mutilamulile anthu akupha inu

  • @Sammy-vb1ed
    @Sammy-vb1ed Před 21 dnem +2

    Mudzina la yesu krist ndikupemphera kut uone zowawawa zikhale

  • @MeleckDennis-vg3bv
    @MeleckDennis-vg3bv Před 22 dny +7

    Zopusa zokhazokha mfiti za anthu,kwanu kwathapo agalu inu

  • @JumaGadaff
    @JumaGadaff Před 14 dny

    Bwana kuvota tidzavota koma dziwani kuti muli ndi mulandu ku chikangawa zikomo mulungu ankhale Nanu amen 🙏🙏🙏🙏

  • @user-wu4tl2yn9e
    @user-wu4tl2yn9e Před 22 dny +5

    Before kuvota aliyense azizakumbuka kuchikangawa

  • @BrunoMbewe-xj1yy
    @BrunoMbewe-xj1yy Před 19 dny +1

    Ndangothokoza kuti mene mumampephelamo mu Mpephero lanu nonse simuna mutchulemo Yesu khristu.Zaoneka kuti inuyo mwazi wayesu simunauziwe mene munagwilira ntchito, pitilizani kugwira ntchito zakumidimazo.

  • @Gmtmphats124gy
    @Gmtmphats124gy Před 21 dnem +5

    Akanakhala kuti mulungu amalanga mpompo mpompo akanakuthilan moto pasokhano wanu omweo

  • @giftmaliwa2385
    @giftmaliwa2385 Před 21 dnem +6

    Za make Dzana this new generation

  • @spargomw
    @spargomw Před 21 dnem +5

    Zikhale Ng'oma😂😂😂😂 tsitsi muzipesako tisamakugemuleni zonse😂😂

  • @ephraimmbiza9727
    @ephraimmbiza9727 Před 19 dny

    Most important thing is that you know yourself that you will not come back in government

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y Před 21 dnem +1

    Dzigawenga dzawanthu anthu akupha inuuu ng'ona zomwe mwachita pakupha abale athu asanu ndi anayi aja kuchikangawa dziko lonse lapansi ladziwa choonadi chifukwa ma German aja anenana zonse kuti black box inali ku palace.Ndipo anenaso kuti ndichiwembu chomwe munakonza.Pomwe inu muli pheee kufuna kutiuza bodza, ife tadziwa kale ndipo muyaluka

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw Před 21 dnem +1

    Mukumbukeni chilima amene munamupha uja azikhale ng.oma ndipo zimu wake ukufinyeni ndipo khalira pomwe

  • @sanlakedickson6780
    @sanlakedickson6780 Před 21 dnem +3

    ana asatana awa Mzimu wa chilima ukuvutitsani

  • @juntoiman
    @juntoiman Před 21 dnem +7

    Pathako panu nonse Zikhale Ng'oma pantumbo pako wamva

  • @user-eg8wx8oi5z
    @user-eg8wx8oi5z Před 21 dnem +1

    Now it makes sense kod nkhumbai Nd mtumbuka eti😂😂

  • @kinggasperagain
    @kinggasperagain Před 21 dnem +1

    Kweni Malawi inasoka ivinthe kuwina waka nbwe chikurya waka ndalama

  • @PaulMwaona-kh1fj
    @PaulMwaona-kh1fj Před 21 dnem +1

    Ubwino wake achinyamata alipo ambili kunjaku,apapa pachulukana makolo otamba

  • @HassanMbalaka-gb5sv
    @HassanMbalaka-gb5sv Před 21 dnem +1

    Palinyimbo inayake amat paulendooo paulendooo aaaayeee paulendoooo. Awakwao kwantha

    • @BittonRashid
      @BittonRashid Před 20 dny +1

      Aye aye paulendo tulinkwaula tulinkwaula kkkkkkk mfundo

  • @user-sh1rj3ol3t
    @user-sh1rj3ol3t Před 22 dny +2

    But tu Laz has failed Malawians way more than APM

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Před 21 dnem +3

    Mukuzinamiza agalu Inu za kumachende, azimai nonse Nyini zanu zamanu,mugawane nonse phwala limodzi limodzi agalu okupha

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před 21 dnem

    Ndimamva chisoni ndi anthu apanda nzeru ndikumanamiza anthu, mwaba zakwana azikhale ng'oma 😮

  • @zondanitzulumusicfly.5202

    Adziwa kuti babiloni is falling.

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 Před 22 dny

    “Akuti kumabwera ndalama “ ndalama za misonkho yanu zomwe zija ndi zimenezo. M’malao momagura mankhwala mzipatalaa , akungotafuna ndi Ma families awo

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před 22 dny

    Amuna mutu wake ometa ngati chiboliwo Muthu osokonezayo zazi

  • @EphraimNaveya-hz1du
    @EphraimNaveya-hz1du Před 13 dny

    Za ziiiiiii afiti simungazawine muli ndi magazi kale

  • @ChilangoNdalama
    @ChilangoNdalama Před 21 dnem

    Suiona vote yanga Chaka chamawa ndangokudyera aise

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov Před 21 dnem

    Viskulu vinu kwacha ninkhuni mpakana kupemphela pamusonkhano apo naumo wanthu wakutambulila namwe kuzomelezganga kwacha chitima chikukolana kweni in fact Mose imwe mukukondwa na mcp Mavi yinu

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 Před 21 dnem

    Ine kunkhara iwe president bola ndifele kokuno ku south Africa wallah wosantha kuyankhura ngat iwe paliolo lenu mwenjo

  • @LekkttarKhembo-or1tx
    @LekkttarKhembo-or1tx Před 18 dny

    Zitsiru za Malawi zikhale chakwera nonse ndinu osadura ndipo mumanukha kabudula mwanumo mukutinyasa tu

  • @BeliLikhola
    @BeliLikhola Před 16 dny

    muuzeni chilungamo ameneyo, chigawenga ameneyo

  • @user-uc9qk7ci2v
    @user-uc9qk7ci2v Před 22 dny +1

    Taonani zinkhopezo ungokhala ngatinsonkhano wa afititu

  • @Fatima-f5c
    @Fatima-f5c Před 22 dny +7

    Misokhano yanuyo muzipangila m,manyumba mwanumo Koma kunjaku ndithu tikugendani 2025 iwa alia

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr Před 20 dny

    Mpake muzipangira munyumba campaign,,, chibadwireni mfiti sindinkaidziwa ,,koma Malawi tiona zithu.

  • @YohaneChitseko
    @YohaneChitseko Před 20 dny

    Manje mapephero amene chabe mulungu sangamve anthu okupha ngati inu

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 Před 21 dnem

    Umphawi ndi matenda Zoonadi ( ife kuno ku Ntcheu sitikupanga nawo zimenezi popeza ABIYENI ndi aja munatichotsera aja ...)

  • @ChikumbutsoDzukwa
    @ChikumbutsoDzukwa Před 21 dnem

    Munamizana udya Galu amawawa muziona this is new generation

  • @lucianogeoffrey4275
    @lucianogeoffrey4275 Před 22 dny

    Koma mzimu wa Chilima uli pambuyo panu muyambila kugwa ku convention komko agalu inuu😢😢

  • @user-wg8tp8in1v
    @user-wg8tp8in1v Před 21 dnem

    Apa ponkha ndikupempha Chonde Azikhale asasankhidwe pampandowo

  • @BrightNyoni-yd4ip
    @BrightNyoni-yd4ip Před 20 dny

    Gulu iwe usamaseweletsa dzina la yesu nkhumba iwe

  • @BashiruIbrahima-h6z
    @BashiruIbrahima-h6z Před 21 dnem +1

    Kodi awa udindo wawo uja akuwuona kuchepa?? I'm feel sorry kwa manganya

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 Před 21 dnem

      Manganya ndi mbuzi.amuthanso ngati saulos.nzeru za ma Rwanda amenewa nzoipa

  • @Sammy-vb1ed
    @Sammy-vb1ed Před 21 dnem

    The savage politicians, we as malawians we don't need you anymore. Anthu atsankho, kupha komanso katangale.

  • @MarriamBakalie
    @MarriamBakalie Před 21 dnem

    Manganya beware upita ngati chilima those r the same people who killed chilima with the same position they r nt happy with u take care

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere Před 21 dnem

    Aaaa! Tadzingopani zanuzo zotchula Bible_zo ai siyani ndichibwana chachikulu

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma Před 21 dnem

    Chikangawa party, okupha Inu muganiza asakudziwa ndani

  • @Zamwano
    @Zamwano Před 21 dnem

    Ma suit ake amenewo chingawine ichoo 😅

  • @millionsenenje5010
    @millionsenenje5010 Před 21 dnem

    Mr Kamuyambeni ndiinu bambo wanga koma pena pake mhhhhhhh

  • @MusaKazembe-b1d
    @MusaKazembe-b1d Před 17 dny

    They are not even ashamed 😮

  • @CharlesMongola-jw7sk
    @CharlesMongola-jw7sk Před 20 dny

    Pepani mfundo zanu zopusazo musaphenso Manganya,afiti inu

  • @user-tw2zf7bj3e
    @user-tw2zf7bj3e Před 21 dnem

    Manganya waziwonera wekha kuti iweyo komanso utm sakufunani uziganizile

  • @RobertChisenga-ci2mq
    @RobertChisenga-ci2mq Před 21 dnem

    Do you think karonga's ndizitsilu?
    Poti kukaronga kuliso mbudzi ndizomwe zilikumenekozo

  • @IshumaliMakajunior
    @IshumaliMakajunior Před 21 dnem

    Ndipo lnu mukanadziwa mene tikuvera

  • @JackNagoli
    @JackNagoli Před 21 dnem

    Let them talk guys ndipo apange ma plan awowo km ubiwno wake malawi siwaathu atatu tiyeni tikakumane chaka chamawa basi khani ndi vote not to talk too much angochedwa nazo

  • @user-mq2or1lz8h
    @user-mq2or1lz8h Před 21 dnem

    😢😢😢😢oooh he has confirmed that this is serious business 😢😢😢rip SKS

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Před 21 dnem

    My pipo tiyenda bwanji 😢 koma able

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Před 22 dny +1

    Akulu awa ndi achitsilu kwambiri ndi azizawo onsewo kumeneko

  • @frankndawandawa6666
    @frankndawandawa6666 Před 21 dnem

    kutiseweretsatu Amalawi uku akuona ngat taiwala kale nthawi yomweyi

  • @pacharokoloviko1694
    @pacharokoloviko1694 Před 19 dny

    Mayankhulidwe ake amenewa anthu aphanako uku

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Před 21 dnem

    Mayo mayo chitumbuka sitikunva yankhurani chichewa

  • @CannyMpehla-d1s
    @CannyMpehla-d1s Před 21 dnem

    koma malawi waoladi ng'omaso ikhale vp kkkkkkkk

  • @user-mq2or1lz8h
    @user-mq2or1lz8h Před 21 dnem

    😢😢😢😢 mpakana kumutchula mulungu nyasi ngati?😢😢😢😢😢😢

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya Před 21 dnem

    Azimai opusa inu mxiew, kuziwachera achamanu ife tidakagonabe,
    Kuvotera MCP kuli ngati kuyenda maliseche koma utavala panti, mpakaso zikhale nkukhaka VP ndiye zamapipotu! Shupiti zanu

  • @user-ot8no9ex2z
    @user-ot8no9ex2z Před 21 dnem

    Azakuvoterani ndi ambuyanu ndithu nsonkhani umakhala ndi anthu awiliwo kuousatu uko bwanji manyazi zimvereni chisoni

  • @LindaNkwazi
    @LindaNkwazi Před 18 dny

    U r still remembering chikangawa

  • @user-ph3zy9ox7d
    @user-ph3zy9ox7d Před 21 dnem

    Inu munthuyu ngoopsa chonchi😮 is he a human being??

  • @TroubleKatsala-jp2li
    @TroubleKatsala-jp2li Před 21 dnem

    Anthuwa apengamisala simukuona zimene akuchita tiyeni tiwadyele koma vote osawapatsa

  • @georgemponda
    @georgemponda Před 21 dnem

    Mbuli izi😂😂😂😂 Zikhalebg'oma nde panja penipeni

  • @VictoriaWilly
    @VictoriaWilly Před 21 dnem

    Kunamizana ndi kosavuta, zinamizanani

  • @alexgweje8610
    @alexgweje8610 Před 21 dnem

    Mulibe manyanzi anthu okupha inu 😢

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana Před 18 dny

    Aaaa dzitsiru dza athu kunamizana kukhwapa kwanu nonse

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe7633 Před 21 dnem

    Uyu sikhale ngoma same like idi ameen

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 Před 17 dny

    Apa akunena zoona Zikhale Pali zambiri zakhara zuchitika, nde kusankha mwachibwana MCP pa mpando itha kuchokapo

  • @HopeMakoka
    @HopeMakoka Před 21 dnem

    Akabwerstsa ndalamazo landirani guys Koma zodzalamuliranso awa mmmmmm Kumwamba kudzatsika pansi

  • @Sammy-vb1ed
    @Sammy-vb1ed Před 21 dnem

    Azikhaleo kwaona nkhopeyo ngati muru wamanyi afisi 😂😂😂😂😂😂.

  • @user-ee6be5kl5o
    @user-ee6be5kl5o Před 21 dnem

    Ndiye. MCP aaaaa!!!!! Mwauponda ndithu2025 muziona kwanu kwatha anthu anakupatsani mpata koma mwalephera zinthu muzaka 4 amalawi sangapa
    nge misiteki kawiri

  • @user-fq4kv8dj4t
    @user-fq4kv8dj4t Před 22 dny +1

    Chikoka mulibemo olo nzozo mbola maturity mbola eeesh mudyeleni

    • @CatherineDesire
      @CatherineDesire Před 22 dny

      ,🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤸🤸🤸🤸🤸mama ine ndakomoka

  • @user-oq5rg5mz7q
    @user-oq5rg5mz7q Před 22 dny

    Kusawa zoveselatu nanuso, agalu eni eni

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v Před 21 dnem

    Kodi khope zimenezo zikuyakhula apazi pamodzi ndi zikhale ng,oma zamasana kapena zautsiku mmmmm anthu andalama olo kuwezuka

    • @user-hm9nc7lz6e
      @user-hm9nc7lz6e Před 21 dnem

      Ndi zausiku mumuone or zikhameyo khope yace ngati chidzukwa

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Před 20 dny

    Dziko linaola...nduna yosapesa😅😅😅😅😅😅

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Před 21 dnem

    Mmmmm izo ndi ng'ona zikuruzikuru zikudyani

  • @user-kh2bi8rk1d
    @user-kh2bi8rk1d Před 21 dnem

    Msonkhano wanji wopangira mnyumba?? 😂😂😂😂

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2fo Před 21 dnem

    Zikhale Ng'oma muti chani apaa tiyeni uko 😂😂😂

  • @WilliamblackvPaul
    @WilliamblackvPaul Před 21 dnem +2

    Kwinaku ndingatukwane

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda Před 21 dnem

    Kumpoto kulije development, kufuma kale awo wangazenga kumpoto nimbani? No dpp, no udf , no utm, pali vifukwa apo,

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 21 dnem

    Simudzawina mizimu yonse yomwe munayipha ija ili pakati panupo anthu oyipa inu

  • @lame8
    @lame8 Před 22 dny

    Alandila ma 20 pin zikuchita kuonesa. Kuwatengela anthu ku Hotel kobisika angolowobela manja chifukwa cha ndalama😢

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt Před 21 dnem

    Mbamva ndi afiti awa sangawine tangonani anthu ndi anthu amabanja mwawo okhaokha amenewo

  • @alfrededwinmadziataika5869

    Sapesa Adana ndimadzi..😮😮😮😮😮

  • @BrightNyoni-yd4ip
    @BrightNyoni-yd4ip Před 20 dny

    Anthu akupha inu mukungo Taya thawi yanu

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před 15 dny

    MBUZI ZAWANTHU ZAMANU PANSI MUNYERA MUONA

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 Před 21 dnem

    Kwachaaa! Wachani mulibe manyazi eti!!.

  • @thondoyaenterprise3795

    Chimphongo , chonenepa , cha kuda , chilibiiii chi ZIKHALE N'GOMA.

  • @KhalideNerve-mu1eq
    @KhalideNerve-mu1eq Před 21 dnem

    Manganya come and see what you have done ✅

  • @user-wd9yd1bg9n
    @user-wd9yd1bg9n Před 21 dnem +3

    Zikhareyo akutha kuona kuti mmmm apa pavuta , olo zikhaleyo sanafune kubwera

  • @wisdomwizzie9944Jahblessevery1

    Ngat u MP amugwesa gwesa ana zaka zambirimbiri lero nkumat Vp kkkkkk mudyeleni ameneyo ine olo ya u MP sazaiwonaso kuno

  • @user-lk3ki9hi3k
    @user-lk3ki9hi3k Před 21 dnem

    Anthu a Karonga amenewo.......mukupepusidwa ndichani

  • @lawrencekauwa8005
    @lawrencekauwa8005 Před 20 dny

    Kkkkkkk,,,, to be a supporter 🙌