Zifukwa Zomwe Zingapangitse MCP Kuchoka M'Boma - Concerned Citizen

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 09. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, A Concerned Citizen, outlines the reason why MCP will not win the Next Election.
    Pa Nyasa VoiceBox, Mzika Yokhudzidwa, ikufotokoza zifukwa zomwe MCP sichidzapambana pachisankho Chotsatira.
    #malawi

Komentáře • 42

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Před 2 měsíci +5

    Zoonadi chidule akuluwa ndi kupha apambuyo pawo chomcho sibwino ntchito za satana kumaoneka ngati abusa.

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Před 2 měsíci +4

    Komatu Iwe Chakwela Mmene Unapha Chilima Muja Usazitenge Opambana Iyayi. Udindo Uliwo Pangafupike Pangatalike Umatha, Iyi Si one Party System.
    Chitsiru

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 2 měsíci +2

    Mukunena zoona abro kupanga mugwirizano ndi MCP zikungofanana kuti wuli pa wubwezi ndi mkango mukangosemphana pang' ono basi iwe ndi wulendo

  • @JunaKananji
    @JunaKananji Před 2 měsíci +1

    ❤❤❤❤❤❤waganisa bho Love you ❤❤

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Před 2 měsíci +1

    Koma ndizoona ndithu... Azitolankhan panopa akuopa kwambir, sakuyankhura tchutchu ai... Bodza anthuwatu amayenera achoke mdzina la mulungu please 🙏

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před 2 měsíci +4

    Dzowona anthu akudziwa chilungamo pano

  • @user-qg4it7my9n
    @user-qg4it7my9n Před měsícem

    I agree with you Mr😍😍

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf Před 2 měsíci +1

    Good Speach

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před měsícem +1

    Ndipo achmwene inu mumasanthula bwino kwambiri, zomwe mwanena zoona zokha zokha. 100%.

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy Před 2 měsíci +2

    MCP ku moto 🔥🥵 izikakukuta mano

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Před 2 měsíci

    You are 100 percent right

  • @GoodsonLindani-gf8pn
    @GoodsonLindani-gf8pn Před 2 měsíci +2

    Zoonadi big chakwela akumamvera anthu oipa awa,chimwendo banda, h mkaka, z ng'oma, mkukuyu, gotani hara, ndianthu okupha, oyambisa kusankhana mitundu ndi zonse zonyasaamenewa ndiagalu.

  • @lyiemax
    @lyiemax Před 2 měsíci

    I salute you big man ❤❤❤

  • @dontreybanda278
    @dontreybanda278 Před 2 měsíci

    Good massage boss

  • @user-gg9hw4oj2v
    @user-gg9hw4oj2v Před 2 měsíci

    That's facts bro

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Před 2 měsíci +1

    Bakili Muluzi mu 1994, Ndi kamenya kwaya Ana imba nyimbo nthawi imeneyo ndiri kalasi 7.Anati MCP,eeeee, MCP,Anthu aja Ndi akuphààaaà,Abale MCP,eeeee, MCP Anthu aja Ndi A kubaaaa, MCP wakupha Chakwera woyeeeee wakupha aaaaa,aku Phani Nonse kumeneko oooo,thamangisani mimbulu yoooo

  • @joykhonje
    @joykhonje Před měsícem

    U T M please pangani mgwilizano ndi zipanizina

  • @tuzijachaba-zl6pm
    @tuzijachaba-zl6pm Před měsícem

    Mwanena mfundo za phindu zokha zokha ifenso tikuwona choncho palibe kuwina

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 2 měsíci

    Uchitsilu ukabvota wekha ndi tiyana tako ndiwe mbuzi yamunthu

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 2 měsíci

    Mbuzi yamunthu mbuli yosapita ku school

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe Před 2 měsíci

    Ndipo or kumudziko munthu amene Sali pa You tube kumufunsa angoti bola Pete yemweuja chimanga chimkapezeka mu admark. soap timkakwanitsa kugula😢

  • @RCFAKI-mx4dv
    @RCFAKI-mx4dv Před 2 měsíci

    Hello

  • @tuzijachaba-zl6pm
    @tuzijachaba-zl6pm Před měsícem

    Muli ndi mfundo zabo!

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 2 měsíci

    Sukudziwa chomwe ukunena and zikuoneka kuti iweyo mcp sukuidziwa dikila 2025 ndipamene mcp udzidiwe galu wachabe chabe

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Před 2 měsíci

    Manganya ndi chipani chake chija odya zake alibe mulandu ndi amene atapange ngwilizano ndi MCP

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx Před 2 měsíci

    Kumeneko nde kukamba tchutchutchu

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Před 2 měsíci

    18 to 35achinyamata awa

  • @JoshuaJumbo-mp3ze
    @JoshuaJumbo-mp3ze Před 2 měsíci

    😅😅😅😅

  • @eliasmpita3916
    @eliasmpita3916 Před 2 měsíci

    Ndikuvomereza kwambiri zinthu zadula. Mafuta ophikila, mafuta agalimoto, fetereza, zopindulira anthu.

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před 2 měsíci

    Iweyo nkulu umadziwa kuyankhula mbambande inuyo

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před 2 měsíci

    Nayenso chakwera ndi oipanso osati omuzungulira okha akanakhalakuti si oipa sibwenzi akumvera zopusa achoke basi

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os Před měsícem

      Indeeeee Chakwera ndi chimunthu choyipa kwambiri ku ubusa kuja amangobisalirako chabe basi. Anthu tikudziwa kuti ndi munthu oyipa kwambiri.

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere Před 2 měsíci

    Koma mukuvutika ndi CZcams pamene ovotera MCP sali pa CZcams ndipo alibe nthawi yokuyankhani

    • @LamieTiger
      @LamieTiger Před 2 měsíci

      Palibe amakonda MCP asadzakunamizen bwana athu angodyanawo tindalamato athu kuvotera tonse ija anavotera kwen kwen chifukwa cha mfundo dza chilima mu tonse muja mukanakhala opanda chilima akanaluza and ikanakhala one on one amene akanavotera MCP anali akubanja kwachakwera ndiiweyo ndiathu amuchipaniwo bas coz ngakhale azigogo athu amaziwa Kut MCP ndikaleromwe inali yokupha yokuba yoononga

    • @PhillspicJere
      @PhillspicJere Před 2 měsíci

      @@LamieTiger wabadwa mochedwa iwe palibe chomwe ukudziwa ukungoona kuyankhira nkhani za akulu akulu,

    • @CHIWIKAJUNIORNYAMBOSE
      @CHIWIKAJUNIORNYAMBOSE Před 2 měsíci

      😅😅😅 akulu akulu zigawenga😢

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr Před 2 měsíci

      ​@@LamieTigerndizoona anthu ammidzimu samveradi Koma ndizomwe zachitika panozi adana nayo mcp ndizokaikitsa kuwina munchoonadi. Adzaberatu awa,, Ine ndechokavotanso ndizandichoka cz palibe yemwe nkumuona okamuvotelanso apart from malemu Chilima 😢

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r Před 2 měsíci

      Nde ngati samakhala pa CZcams why did they arrest Bon Kalindo over the CZcams audios?? Musavutike a MCP wo amakhalapo pa CZcams