Mbiri ya Joyce Banda

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 20. 01. 2021
  • Joyce Banda ndi president wakale wa dziko la Malawi amene adalamulira dziko kuyambira pa 5 April 2012 nkudzafika pa 30 June 2014.

Komentáře • 44

  • @farooqkazembe6516
    @farooqkazembe6516 Před 3 lety +5

    My brother I thank you for this programme your the one who open my eyes of our lovely country Malawi keep it up bro almost every day I always wait to hear from you. Thanks bro

  • @imulandunkeni1226
    @imulandunkeni1226 Před 3 lety +3

    Next chilima please

  • @mohamedriazshreef8697

    watching from cape town south Africa ❤

  • @kalolokapanda5168
    @kalolokapanda5168 Před 3 lety +1

    Kunalibe "Kamuzu Academy " 1972. Sono sizingatheke kuti bambo a Mai Joyce anga punzitse music... I guess it's an error no?

  • @ririvilla1423
    @ririvilla1423 Před 3 lety +2

    As much as I like chanel yanuyi mwalakwitsa mamuna wa Joyce sanali Kachali koma Kachale ndipo amachokela ku Zomba. Please do your research bwino bwino ndipo Kachale anali mamuna wabwino Joyce anamulakwira pomusiya

    • @g_deonm5793
      @g_deonm5793 Před 3 lety +1

      That's a minor mistake that can be corrected with tipex...he is on point with the main story...

  • @BizweckMasamba-pe5bu
    @BizweckMasamba-pe5bu Před rokem +1

    Mumakwana, koma muzisazika pomaliza kkk

  • @jamesngalande4345
    @jamesngalande4345 Před 3 lety +2

    Ine mmayi ameneyi mfundo zake sizimandisangalasa ndizopusa

  • @TheZuluman7
    @TheZuluman7 Před 3 lety +1

    Scandalous she may be but still beautiful and elegant with age.

  • @dennisjohnkacheche5498

    Nzimayi ogulisa mandasi kani unathawa amunako then got married to Mr Banda, you are a true Jezebel...cash gate Joyce

  • @AubreyDymon
    @AubreyDymon Před 14 dny

    Mmakwana boss

  • @makiphiri3469
    @makiphiri3469 Před rokem

    Your always saying the truth keep it up

  • @onesichone
    @onesichone Před rokem

    Looking beautiful Mayi

  • @isaaclungu6109
    @isaaclungu6109 Před 2 lety +1

    Thanks boss

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 Před 3 lety

    Malawi mwadzinalako tili pa Malawi amoto basi 60 trucks ayiboo!!! 😯😯😱

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 Před 3 lety

    Ndimakunyadilani braz

  • @duncankamanga3461
    @duncankamanga3461 Před 3 lety

    Tikukutsatilani boss.

  • @mapatayusu4371
    @mapatayusu4371 Před 3 lety

    Ameneyo ndiye muyawo

  • @danielmaluwa7896
    @danielmaluwa7896 Před 3 lety

    Hule uyu ankachindananso ndi Bakili muluzi, Bingunso anampwala

  • @amosiphilimoni6599
    @amosiphilimoni6599 Před 3 lety

    Kumuthawa mwamuna 😂😂😂😂cash get anaiyamba banja kk kuzamalizira m'boma

  • @francismtawayatv5336
    @francismtawayatv5336 Před 3 lety

    Eeeish scandal yooopsa ndithu. Mulungu atithandize

  • @Seche204
    @Seche204 Před 3 lety +1

    Hule lachabechabe

  • @paulnkhama3621
    @paulnkhama3621 Před 3 lety

    Joyce Banda mbava

  • @alexanderkaunda9554
    @alexanderkaunda9554 Před 3 lety +1

    Chimbava icho

  • @francokaunga2653
    @francokaunga2653 Před 3 lety +1

    Jezebel indeed

  • @stanleydamalekani2398
    @stanleydamalekani2398 Před 3 lety +2

    Just question Sir mukafuna ku ulutsa mbili ya munthu mumachita chiyani? Mumamufikila munthu? Mumazipeza bwanji zimenezi ? Plz answer me :)

  • @Benty_Pro
    @Benty_Pro Před rokem

    No wonder she dumped her Husband for his best friend... Uyuyu si okhazikika

  • @mushai
    @mushai Před 2 lety +1

    I wish this was in English..Can someone interpret for us?

  • @amosiphilimoni6599
    @amosiphilimoni6599 Před 3 lety

    Mai oipa uyu😈

  • @alexanderkaunda9554
    @alexanderkaunda9554 Před 3 lety

    Kkkkkkkkkkk mlamu amaoneka kuti mwanoulimo

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Před 11 měsíci

    Chakuba kuposa amuna chimbava

  • @aminakafasiyanji1777
    @aminakafasiyanji1777 Před 3 lety

    😀😀😀😀😀😀🤣🤣🤣🤣🤣

  • @benimakenzi7198
    @benimakenzi7198 Před 2 lety

    Russia top no 2

  • @jameskamanga628
    @jameskamanga628 Před 3 lety

    Umakwana kkkkkk

  • @abasshussein6442
    @abasshussein6442 Před 3 lety

    Chikhomo chakwathu

  • @mphatsouledi3135
    @mphatsouledi3135 Před 2 lety

    Full of lies. You can do better.