ZOMWE WAYANKHULA DALITSO KABAMBE PAMENE AMALANDILIDWA KU UTM LERO ZIYAMBITSA MAPOKOSO NDIPO KUCHEMA

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 6. 09. 2024

Komentáře • 59

  • @lyiemax
    @lyiemax Před měsícem +6

    Welcome to UTM Bwana kabambe , the only beloved and trusted party, thanks for choosing wisely 🔥🔥🔥🔥

  • @RachelNkhoma-vn2jo
    @RachelNkhoma-vn2jo Před měsícem +6

    Munthu osankhidwa ndi Mulungu amampatsa nzeru zakuya zoyendetsera dziko koma so amakhala ndi maso mphenya losamalira anthu m'dziko tipelekeso ulemu kwambiri inu mayi kaliyati mlelankhugwa amayi osategeka ndi dziko kuti zili uku ,Mulungu akuonjezeleni madalitso ochuluka pantchito yomwe mwaidwira koma so mwasankha mtsongoleni oyenelera

    • @GeraldChisamba
      @GeraldChisamba Před měsícem

      😂😂😂😂😂😂 mwabadwa liti kod inu

    • @PeterMoffat-jg2bb
      @PeterMoffat-jg2bb Před měsícem

      Ok​@@GeraldChisamba

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Před měsícem

      ​@@GeraldChisambamusiyeni sakudiwa kanthu za kaliyati kusintha zipani koseko sikutengeka kodi 😅😅😅😅😅

  • @jeremiahmalikebu2393
    @jeremiahmalikebu2393 Před měsícem +3

    Welcome to the family Dr Kabambe

  • @ZonneckChikondi-q4l
    @ZonneckChikondi-q4l Před měsícem +3

    Kod amadikila kt achilima atisiye kaye kenako azibwela nkuzapanga join UTM,bodzatu ili akusaka mpando onona mkuluyu,akuluakulu a UTM mukapanda kusamala muononga chipani

    • @jameshuwanzulu
      @jameshuwanzulu Před měsícem

      Ku utm timapitatu ku conversation musayiwale sitipeleka mpando pa tebulo

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o Před měsícem

      Zaziii izo mukukamba utm si ya masavechi kuti ingangopereka mpando mophweka

  • @ChimmsRichardOrden
    @ChimmsRichardOrden Před měsícem +3

    Achimwene anga ndasangalala kwambiri chifukwa cha chisankho chanu choyenera nanenso ndili m, mbuyomo ndikupezani

  • @RobertCosmas-bo1uo
    @RobertCosmas-bo1uo Před měsícem +1

    Dpp ndiyochenjera kutumiza nyambo ku utm cholinga asavute kupanga alliance kabambe skut wongobwera tiziona kothera .

  • @user-zy5cc4zx4k
    @user-zy5cc4zx4k Před měsícem +1

    Amalawi tidatani Kabambe wakhalapo Reserve Bank Governor osathandiza zeruzo zaoneka Lero Amalawi ndi otemberedwa Kaliyati yemweyu wanyoza akulu enandiena lero akuchuluka zeru. U T M Ndiya olemekezeka a vice president a Dr Usi komanso olemekezeka Akambala omwe mophatikizana ndi okondedwa athu Dr SKC mzimuwawo uuse muntendere ana panga United Transformation Movement (UTM ) asakunamizeni a Kabambe abwera Kuti DPP isavutike kupanga mgwirizano NDI UTM. Kuba mbava izo a Malawi osanamizidwa.

    • @MpogoroMwikoko
      @MpogoroMwikoko Před měsícem

      Exactly 💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯

  • @user-zf7lh1py7u
    @user-zf7lh1py7u Před měsícem +2

    Anybody joining UTM should go to the branch and area and constituency. Nobody should enter at Central executive level.
    Ngati uli umphawi ndi wanu. UTM youth should not accept corruption, mediocrity and rubbish.. The UTM youth should protect the party for greedy leaders.

  • @danmbuzi
    @danmbuzi Před měsícem +2

    Umakwana katswiri engineer bk tv

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo Před měsícem +3

    Dzikomo a Kabambe chifukwa chokumbutsa bodza lomwe tinalandira pomwe UTM inali limodzi ndi Mcp. Anthu azadya katatu pa tsiku Koma anthu kusowa ndi phara lomwe. Kulemba anthu 1.000.000 pa Chaka, Koma anthu amaphunziro awo kukharira maganyu m'ma Town ndi m'minda ya anthu.
    Chonde Manfestar amenewo chotsaniponi angationongele Chipani chathuchi. Amenewo ndi amene alepheleka kale. Bodza limenelo tiyeni tiwasiyile Eni ake a Mcp

    • @williamsalexmbonga
      @williamsalexmbonga Před měsícem

      Man inu simukudziwa kuti zimenezo angalonjeza ndi kathyali wa Miyambi uja zonsezo

    • @joyceellis9045
      @joyceellis9045 Před měsícem

      Koditu manifesto mwanenadi idali yathu ife a Utm . Koma tiziti siidatheke chifukwa kum'phika sikudali ife.
      😂

  • @JamesMasina
    @JamesMasina Před měsícem +1

    Mwagulitsa chipan kwa kabambe

  • @user-zh9kb2sj2i
    @user-zh9kb2sj2i Před měsícem +1

    Koma mr kabambe dzalemekezeni mzimuwachilima pls mubwelendintima ofuna kudzathandiza dziko kuti kuwala kwachilima kudzapitilile

  • @Mary-lb4ce
    @Mary-lb4ce Před měsícem +1

    You r welcome bwana Kabambe.

  • @dicksoncassim1954
    @dicksoncassim1954 Před měsícem +1

    My vote

  • @Alinafe-s6o
    @Alinafe-s6o Před měsícem

    Amazwa ndale sangadabwe ife eni ake tkuzwana

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm Před 24 dny

    Mauwo nga UTM koma mtimawo ngwa DPP

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před měsícem +2

    Good mayi❤

  • @DominicNantowa-t4d
    @DominicNantowa-t4d Před měsícem +1

    😂😂😂😂 Tinabwela timasakasaka mpado wonona 😂😂

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 Před měsícem +1

    Foundation ya tsogolo lowala layambika

  • @joicemumba3608
    @joicemumba3608 Před měsícem

    Amen

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před měsícem +2

    Kutha chipani kumeneko 😂😂😂😂😂

  • @wonganinyirongo1887
    @wonganinyirongo1887 Před měsícem +1

    Welcome bwana

  • @GeraldChisamba
    @GeraldChisamba Před měsícem +1

    Inatha UDF kulibwanj UTM 😂😂😂😂😂

  • @user-st6bt5vv9c
    @user-st6bt5vv9c Před měsícem

    Fundoless ungobwera basi inuyo better be bank governor

  • @PhilomenaChikabadwa-dt6vy
    @PhilomenaChikabadwa-dt6vy Před měsícem

    Congratulations .

  • @CharlesKanyumba
    @CharlesKanyumba Před měsícem

    Welcome Mr kabambe

  • @manfredzalirabetha2440
    @manfredzalirabetha2440 Před měsícem

    U T M mpaka kale apa yanyamuka wina alira

  • @johnbauleni4108
    @johnbauleni4108 Před měsícem

    Vuto akusaka saka mpando wawu President osa komedwa

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 Před měsícem

    Anthu adpp anthu oipa kutereku mwasangalala ndiifa yachilima mpaka kutumana Kuti kabambe Jayenge utm

  • @KestonNGUBO
    @KestonNGUBO Před měsícem +1

    Apa mwaliwa chipan cho ganiza bho hev

  • @OsmanAnussa
    @OsmanAnussa Před měsícem

    Mr Kabambe mukulankhula ngat munthu wamayitu mwatan kod kkkk

    • @SueWahna
      @SueWahna Před měsícem

      Ndipo ineso ndimava ngat Joyce 😂😂

    • @user-ol1hf7ru1v
      @user-ol1hf7ru1v Před měsícem

      😂😂😂😂😂😂😂

  • @user-ol6uc7bj2w
    @user-ol6uc7bj2w Před měsícem

    Koma kabambe kkkkk. Anyway politics ndizovuta kuzitsatila bwino. Asamale a UTM akakomedwa APHA chipani mophweka in the name of kulemekeza nzimu WA skc

  • @NathanKhoza-t5b
    @NathanKhoza-t5b Před měsícem

    Ganizo lanzeru la munthu ozindikila osati mbuli zopita kusukuluzi

  • @pempheroraynnoxmpesi8713
    @pempheroraynnoxmpesi8713 Před měsícem

    Imposter... A good one though 😂

  • @Maria-i2p
    @Maria-i2p Před měsícem

    Zilibwino

  • @prestonkasito1815
    @prestonkasito1815 Před měsícem

    Koma ndiye kukakamulatu kkkkkkk

  • @OwenNyangu-nv1yt
    @OwenNyangu-nv1yt Před měsícem

    Manyazi DPP. Apa dpp watha

    • @MpogoroMwikoko
      @MpogoroMwikoko Před měsícem

      Apa ndiye yikhala ndi mphavu kaya ukuwona ngati kabambe wabwerera utm

  • @BrightZgambo-t4x
    @BrightZgambo-t4x Před měsícem

    Mai mumakwana inuyo

  • @pempheroraynnoxmpesi8713
    @pempheroraynnoxmpesi8713 Před měsícem

    Kabambe u need to polish up ur political speeches 😢

  • @emmanuelmtambo3040
    @emmanuelmtambo3040 Před měsícem +1

    Lol too much talk is unnecessary 😁

  • @RobertNyaude
    @RobertNyaude Před měsícem

    😂