Bukhu la Enoki analichotsa m'baibulo chifukwa chani

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 6. 09. 2024

Komentáře • 340

  • @Josephmwangosi
    @Josephmwangosi Před měsícem +10

    In Malawi we are lucky to have this man he is the best Man. Who else in Malawi is at tho far with history. He is special to us guys. This man ndi bomba kudos Bakili muluzi Tv

    • @user-qq1uj7ct6n
      @user-qq1uj7ct6n Před měsícem +1

      Yes ndipo ndizoona ndithu.
      we're blessed sure

    • @aaronkondowe1590
      @aaronkondowe1590 Před měsícem

      This is very great man

    • @yowasschitsosa5348
      @yowasschitsosa5348 Před měsícem

      Alomwe munachita mwai kulamulapo dzikoli chifukwa cha ayawo kma mumatumbwa ngat kut panokha mukanatha kuwina, achiyawo ali chete mumadziva chani

    • @yowasschitsosa5348
      @yowasschitsosa5348 Před měsícem

      ​@@user-qq1uj7ct6nshame on you

    • @PaulMkandawire-oo7by
      @PaulMkandawire-oo7by Před měsícem

      Its not only for Malawian but world level

  • @user-yb3se6vi7m
    @user-yb3se6vi7m Před měsícem +3

    You are best Historian in the World God bless you all the time in order that God can reward you at the end of this good work from RSA we learn more from You Brother Thanks very much

  • @PaulMkandawire-oo7by
    @PaulMkandawire-oo7by Před měsícem +2

    I like this man continue telling things that some people hiding

  • @Addih_calyx_music
    @Addih_calyx_music Před měsícem +2

    Your the genius journalist in whole world #Bakilii TV👀💥💣💫

  • @kotking-xg7pp
    @kotking-xg7pp Před měsícem +1

    inu mulungu anadalitsa mumaiika bwino nkhani nkumvekanso bwino kwambir mmmm God bless you.

  • @user-qs2bp8rh7z
    @user-qs2bp8rh7z Před měsícem +6

    Kuzunguliratu inali yothera mwa achakwera eti. 😂😂😂

    • @JohnConar-kq4hi
      @JohnConar-kq4hi Před měsícem

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂

    • @patriciacraiton-sf5vu
      @patriciacraiton-sf5vu Před měsícem

      😂😂😂😂😂🎉

    • @user-km2js5nq9k
      @user-km2js5nq9k Před měsícem

      😂😂😂😂 akulu amenewa kkkkkkk komab amatha

    • @patriciacraiton-sf5vu
      @patriciacraiton-sf5vu Před měsícem

      @@user-km2js5nq9k kkkkkkk ndipo iiiiiii kkkkkk

    • @user-jl6sq3ph1b
      @user-jl6sq3ph1b Před měsícem +1

      Chikangawa km ngat akufuna kuti azilandilabe ulemu anakangotula pasi udindo cz tikazamuchosa ndi votes ndie tizakamuvesaso nyekhwe kumumanga ndi.mbamva zizakezo cnanga sakufuna kuvomeleza kulakwa kwake chikangawa ndi wa mutu wawukulu uja ngat gumba gumba

  • @joeldaniel-pc3ij
    @joeldaniel-pc3ij Před 18 dny

    Luke serious i love your history telling

  • @cephasnkhoma2301
    @cephasnkhoma2301 Před měsícem +1

    Sir come with more. Dzifukwa zenizeni amakhanila buku'li. I Thanks.

  • @user-qq1uj7ct6n
    @user-qq1uj7ct6n Před měsícem +1

    ineyo nde sindimakumvesan sir.
    nzeru zimenezi bwanji??
    Ku Malawi ndife odalitaika potipasa inu.
    long life bro..

  • @bobchola5083
    @bobchola5083 Před měsícem +6

    😂😂 how it changed to Chakwela 💃💃💃

  • @Concerned320
    @Concerned320 Před měsícem +1

    Number one channel...God's protection upon you

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v Před měsícem +4

    Ndinadziwa ine kuti chakwela imukhudzabe ndithu😂😂😂😂😂

    • @user-rp9wy6rd1q
      @user-rp9wy6rd1q Před měsícem

      😂😂😂😂😂

    • @IsmailKhuneya
      @IsmailKhuneya Před měsícem

      Kkkk sangakambe nkhani osachula chakwela ndi mcp ndye kut nkhaniyo siikoma 😂😂

    • @Chancenyangulu
      @Chancenyangulu Před měsícem

      😂😂😂😂 history is best teacher

  • @ImranWyson
    @ImranWyson Před měsícem +13

    Home of history 🎉🎉Best TV 📺

  • @yusufuhyman676
    @yusufuhyman676 Před měsícem +2

    Mbambande boss

  • @user-ex7jn2fh1g
    @user-ex7jn2fh1g Před měsícem +1

    Nice one dude

  • @ZainthwaSikelo
    @ZainthwaSikelo Před měsícem +2

    God bless and keep you my brother for letting us know about man of God Enock

  • @user-yx3ge5qu4z
    @user-yx3ge5qu4z Před měsícem +2

    Ziii ameneyu bwanj bg man

  • @UZIKASI
    @UZIKASI Před měsícem +1

    Best teacher

  • @Chisomo-dh2gq
    @Chisomo-dh2gq Před měsícem

    History is the best teacher

  • @frankfriday3141
    @frankfriday3141 Před měsícem +2

    Mr bakili muluzi TV pa media akuti mwaqwidwa usiku watawu please tell us worrying about you brother 😢

  • @OwenTembo-xq6ug
    @OwenTembo-xq6ug Před měsícem

    True big man Lai malawi ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela Před měsícem +1

    The best tv in malawi

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před měsícem +3

    Always remember history is a best teacher, big up bakili muluzi TV 🎉

  • @Penior265
    @Penior265 Před měsícem

    ❤ be with us until forever brother chipanda inu bwezi tisakutsata

  • @sheilamwalilino3738
    @sheilamwalilino3738 Před měsícem +1

    Inuyo muyambe kuyankhura nkhanizi muchizungu mupeze wotanthawuzira mu chichewa basi .Morefire🔥🔥

  • @ObvidinhoBalalasJnr
    @ObvidinhoBalalasJnr Před měsícem +1

    I w'll repeat thiz guy iz better than ZBS, Times, Mibawa n all Radiosn reporters....

  • @Moses51
    @Moses51 Před měsícem +3

    The best TV in Malawi keep up update 💪💪🇲🇼🇲🇼 osawopa

  • @IbrahimSakalan
    @IbrahimSakalan Před měsícem +1

    My best

  • @Thanthwemanufacturers265
    @Thanthwemanufacturers265 Před měsícem +1

    Tatulitsani yong'alura zomwe akumupanga CIA

  • @FreedomsazaNyangulu
    @FreedomsazaNyangulu Před měsícem +1

    waiting justice for CIA

  • @RonaldGama-gz9ug
    @RonaldGama-gz9ug Před měsícem +2

    Broz inuyo ndinu odalitsika mulungu anadzalamo mzeru zochuruka mwa inuyo..Best of the Best TV

  • @DalitsoSaidi-zm7yl
    @DalitsoSaidi-zm7yl Před měsícem +1

    kkkkk kod nkhani ija yakathera kwa chakwera , ine ndmati lero zingokhala za mu baibulo basi kkkkk

  • @InokeKimu
    @InokeKimu Před měsícem +1

    I like it but the TV I love you but the TV AI❤❤❤❤❤❤

  • @SolokingChimzy-yt7dj
    @SolokingChimzy-yt7dj Před měsícem

    I love you my brother...koma ndingoyankhula za Joe Biden kutula udindo wake pansi..the thing is Mulungu akukwanilisa ulosi wake omwe unayankhulidwa many yrs ago kut America izapanga mistake kuvotela munthu wa nkaz Harlot ndipo zikazatelo uko kuzakhala kutha kwa America...
    Remember ulosi uwu ukukwanilisidwa munthaw yathu ino mkaz uja Bible limamufotokoza kut ndi mzimai oipa yemwe azagwadilidwe ndi mafumu kapena kut maiko ochuluka..Hava anabwelesa kugwa kwa anthu kumapeto kwa nthaw Mkaziso akuyenela kugwesa Dziko

  • @JohnMilo
    @JohnMilo Před měsícem

    Ana amene angelo anabeleka padziko pano onse anafa pa chigumula cha nowa. Mulungu sanawafune.

  • @JosephGerman-bn8br
    @JosephGerman-bn8br Před měsícem +1

    Mukumangitsa osalakwatu kuno😅😅😅😅

  • @AndrewBuzz-kx2nr
    @AndrewBuzz-kx2nr Před měsícem

    Best of history ❤

  • @SmartNyaluu
    @SmartNyaluu Před měsícem

    Kkkkkkkkkkkkk nkhaniyi ndimaonangati siyifika Kwa ntumiki wamulungu-yotu kkkkkkkkkkkkk 😅😅

  • @ChikumbutsoMkwera
    @ChikumbutsoMkwera Před měsícem

    Amen 🎉🎉🎉🎉

  • @yusufmanusa441
    @yusufmanusa441 Před měsícem

    Big up to u brother

  • @yvonneuwera2661
    @yvonneuwera2661 Před měsícem

    Koma Enock ....I don't know but this week am finding this one everywhere.....Jesus is near

  • @user-ji4ed6dl3i
    @user-ji4ed6dl3i Před měsícem +1

    We appricciate u

  • @AlexanderMphalasa635
    @AlexanderMphalasa635 Před měsícem +1

    Malawian historian

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer Před měsícem

    Amen

  • @VinsentMwapabwe
    @VinsentMwapabwe Před měsícem

    Bakili muluzi TV pitilizani tchito yanu chifukwa mumatiziwisa zambiri ndipo AMUMBUYE akutete ZENI❤

  • @erickkadoh777
    @erickkadoh777 Před měsícem +3

    I was waiting this story

  • @AlexChizombwe
    @AlexChizombwe Před měsícem

    I love Bakili Muluzi TV

  • @user-pp3zd5zb2h
    @user-pp3zd5zb2h Před měsícem

    Ukhale mkhoswe wanga umatha kuyakhula iweyooo 😂😂😂

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs Před měsícem +1

    Watching from Mozambique ulemu wanu basi bg brother ❤❤❤

  • @user-yb1nt9te7f
    @user-yb1nt9te7f Před měsícem

    Juno president of Malawi grandchildren you can't get a piece forever for them

  • @petermanMitambo
    @petermanMitambo Před měsícem

    History is the best teacher long live BMTV ♥️

  • @SaidyKamala-jj7lo
    @SaidyKamala-jj7lo Před měsícem

    Ulemu upite kwa inu bwana wanga yeeeeeeeetu tili ndi kuzindikila kuti kunali chiyani kalelo actually history is best teacher 😂😂😂🎉🎉🎉🎉🎉

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga Před měsícem

    You are number one for everything God bless you bro

  • @johnmiselo2230
    @johnmiselo2230 Před měsícem +3

    Second comment from Zambia
    Tell us more about the bible we really enjoy

  • @augustMag
    @augustMag Před měsícem

    Mulungu apitilize kukusogolerani ndi kukupasani moyo wautali ndi nzeru zochuluka mumatimvesa kukoma Bakili Muluzi TV ndi no 1❤❤❤❤

  • @GrevazioManyozo
    @GrevazioManyozo Před měsícem

    Mulindivuto amwene zina cilungamo komano zina mmaonjeza kwambili, Mulungu akuyendereni..

  • @user-nb7dp6pr9n
    @user-nb7dp6pr9n Před měsícem

    Best TV in Malawi

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde Před měsícem

    U r the best ❤

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona Před měsícem

    Wonderful ✍️ Wedone Brother from BAKILI Muluzi TV.
    M' busa okomedwa ndi Chuma,wa dyera , kuba ndi kupha akuona kuluza kuti atule pansi Udindo chikhalirecho akudziwa Kuti Dziko la mulaka.
    Keep it up Brother from BAKILI Muluzi TV osasiya kuwadzudzula ndi kuwaunikira kowala Chifukwa ali mu m'dima mnyamata ameneyi ( L M C ) .
    History is the best teacher ✍️

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Před měsícem

    Keep it up brother man!!

  • @Jafaliwathombo
    @Jafaliwathombo Před měsícem

    You're the best teacher of history, keep it up!

  • @user-jy5sl8yr5n
    @user-jy5sl8yr5n Před měsícem +1

    Brother timafuna videos Ina ya haiti tawona apolice aku kenya alikumeneko akuwombera anthu please timafuna videos yaku 🇭🇹

  • @CHINDEBVU
    @CHINDEBVU Před měsícem +5

    Much appreciate 🙏 to you My Best journalist

  • @user-to5of3ks3g
    @user-to5of3ks3g Před měsícem

    nice history

  • @user-gg6uh2wo4x
    @user-gg6uh2wo4x Před měsícem

    Home of history BMT

  • @aaronmlowoka1269
    @aaronmlowoka1269 Před měsícem

    Proud of you brother may God continue blessing in Jesus christ name

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe7633 Před měsícem

    Nothing goodness big akuopa unyolo 😂😂😂

  • @PatrickFabiano-x1w
    @PatrickFabiano-x1w Před měsícem

    So great

  • @happybinali4673
    @happybinali4673 Před měsícem +2

    You are the best in history brother

  • @yamikanichipendo8754
    @yamikanichipendo8754 Před měsícem +1

    We shall know the truth and we will be set Free

  • @cictechnologies1091
    @cictechnologies1091 Před měsícem

    Kosekuja kunali karambira bwaro chabe khani imapita kwachakwera😂😂😂😂

  • @esaumwanza3524
    @esaumwanza3524 Před měsícem +1

    In 1 hour 560 likes the best channel in history ❤🇲🇼🇲🇼

  • @MiracleMalichi
    @MiracleMalichi Před měsícem

    Achakwera Thulani pansi ulamuliro adzukulu anthu asadzabvutike chonde chonde achakwera mwadyerera dzikoli ine ndikukhala mu dziko laiyiake chifukwa cha inu

  • @user-oq7ub3yg8x
    @user-oq7ub3yg8x Před měsícem

    inuyo munabwela kudzakhala big up 🔥🔥🔥🔥

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Před měsícem

    The best TV in southern Africa umatha ndiwe dolo kwambiri

  • @MuyaoComedies
    @MuyaoComedies Před měsícem

    Am following

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem +1

    Biden watula coz is too old why not peter to resign coz is too old than Biden chakwera yemweyo boma

  • @AbuduAjisa
    @AbuduAjisa Před měsícem

    Munabwela khuzakala keep 🚶‍♂️🚶‍♂️🚶‍♂️

  • @cosmasnkanda8193
    @cosmasnkanda8193 Před měsícem

    Much respect big man👏🏾👏🏾👏🏾

  • @happybetchbanda1669
    @happybetchbanda1669 Před měsícem

    ndinaziwilatu kuti kothera ndi chakwela kkkkkkkkk

  • @user-et5nz4vz2v
    @user-et5nz4vz2v Před měsícem

    Best TV ever

  • @user-dc5nm2ym6g
    @user-dc5nm2ym6g Před měsícem

    Kuopya koyangu zithu zamutu ndikoti mulungu patsiku lachiweluzo adzakhala ndi mkwiyo ndi ukali kwa muthu oteloyu, ndi dziwalo zamuthuyo zizayikila umboni kuti anali wonkambila mulungu bodza

  • @tsanzomwanya
    @tsanzomwanya Před měsícem

    God bless you

  • @Allieshaibu8612
    @Allieshaibu8612 Před měsícem +1

    Don't forget to subscribe plz

  • @Mohammed-sk1fy
    @Mohammed-sk1fy Před měsícem

    Number 1 TV history,, Enoch wake wa Chihana

  • @Henry-c2x
    @Henry-c2x Před měsícem

    My hero

  • @ChrispineTemuwa
    @ChrispineTemuwa Před měsícem

    Home of history

  • @user-Grant260
    @user-Grant260 Před měsícem +1

    Always you stand for us elder ❤❤

  • @danielkhinguirossejuliasse6106

    agadeço muito este tv me abre miuta visaõ mais força bakili tv

  • @christophermkhize1991
    @christophermkhize1991 Před měsícem

    Kodi bwanji mutangokhala president wa history in the world

  • @AnthonyMhango-e9q
    @AnthonyMhango-e9q Před měsícem +1

    Ur the best history teacher in the world 🎉🎉🎉❤❤❤ randilani ulemu wanu bro

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Před měsícem +1

    Best of the best tv and historic.

  • @LatifBeni-e6z
    @LatifBeni-e6z Před měsícem

    Proud to watch your videos,❤❤❤❤

  • @henztsopano7006
    @henztsopano7006 Před měsícem

    Ur the AKA Mr expart I like this journ

  • @user-nr1xo1nw3z
    @user-nr1xo1nw3z Před měsícem

    Mbambande kwambiri 🔥🔥🔥🔥🎤 eniwake microphone 🎙️🎉

  • @tesfachinomba4901
    @tesfachinomba4901 Před měsícem +1

    Bwana @bakili mulizi tv
    Tiyankheni ngati mulipo akuti akugwilani?

  • @walusunguvital6869
    @walusunguvital6869 Před měsícem

    Buku la enoch mpaka joe Biden ndi amalawi 😂😂😂v

  • @OSMANMWENDA
    @OSMANMWENDA Před měsícem

    boss mutifufuzireko chimene chapangisa kut biden asaimeso u president ku america ,timakunyadiran mumatisegula mumaso mu zambiri,, tikudziwa zambiri chifuwa cha inu MAY GOD BLESS you

  • @user-ww2il4wb8o
    @user-ww2il4wb8o Před měsícem

    Best TV koma ma minutes amachepa😊😊

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw Před měsícem

    My best TV