NKHANGA ZAONA - YASALA MISIKA IWIRI KUTI A OTCHE ANYAMATA AKWA NSUNDWE

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 10. 10. 2023
  • Tidziwe tv

Komentáře • 32

  • @amadichembe4068
    @amadichembe4068 Před 2 měsíci +1

    Osatopa chonde . Mulungu akudaliseni nooooonse

  • @amadichembe4068
    @amadichembe4068 Před 2 měsíci

    Mwaswela bwanji abale anzanga apa pa nkhanga zaona ,Kodi nkhanga ziipo ?papita masiku sizikumveka ,kapena Zina gwidwa pakhosi kkkkkkk

  • @Jamesmwale-iz4ri
    @Jamesmwale-iz4ri Před měsícem

    Powerful words

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr Před 7 měsíci

    Anisha moosa Pretoria ludiam 😂😂😂

  • @alickalick6509
    @alickalick6509 Před 9 měsíci

    Osatopa Comrade MTANYIWA will stand up until to the end.
    Mcp apa ili pamatenda akulu ndipo akudziwa kuti there days are numbered

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr Před 7 měsíci

    Anisha moosa Pretoria l west

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve Před 9 měsíci

    Ise kwinthu kuno za uchisilu sitikufuna chakwera achoke basi ngati sakuchoka timuwombera

  • @CJAY-kx7eu
    @CJAY-kx7eu Před 9 měsíci +1

    Chilima ad Chakwel agul onseo tikundinkil atupele muluz ife come duz atupel

  • @user-mc8gk4xv3f
    @user-mc8gk4xv3f Před 9 měsíci

    Ntanyiwa more fire

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Před 9 měsíci

    Anthu kumangophedwa kuberedwa koma chakwera kungoti ziiii tiziti akutuma ndindani kuti zizichitika zotere akutuma ndi chakwera

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Před 9 měsíci

    Sondinamuonepo president Kuyenda pansewu osayimisidwa pansewu kuti apasidwe moni koma kuwowozedwa chisiru 😂😂😂😂😂

  • @amadichembe4068
    @amadichembe4068 Před 9 měsíci

    Kuno ku Zambia nimakonda kumvela nkhanga zaona ndi nkhani zam maboma

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 Před 9 měsíci

    Apolice wakwathu kuzolowera kunyera matumba mwalo mongwira tchinto komwe munalembendwa..pano mukunkhalila kupepha yambonya. Akakupasani inu zongo paseu kundikira kti atulukira kti . AChina munulo .. ndy azawo ndy lelo mwaona ziiii mwasowa osetela Poona kti born kalindo palimbe mwankhaula mwamva mawa poteniso kulipiran mupedza ya tea ..mawatso mupite ikamati 30:08 kunkhala mutafika kti moyo watsiku ndi tsiku ukukomereni inuyo mwamva ndikukutumani ine tsopano boss lady zakupedzani komweko olo dzuwa libandule...imani popo zabwerese ya mkaka kunyumba mayi akalandire mawa banja kti liyende bwino ndakuuzani tsinanga tchinto yongwire kulimbe ine ndy ndakupatsani imeneyo .

  • @alicechinyama4155
    @alicechinyama4155 Před 9 měsíci

    Nyimbozi nduzifuna ndingazipeze bwanji

  • @jessierodgers150
    @jessierodgers150 Před 9 měsíci

    MCP mbiri yake ndi yakupha basi nde zomwe mukunenazi ndizoona ndithu

  • @ibrahimjackson-cg6tc
    @ibrahimjackson-cg6tc Před 9 měsíci

    Nkhanga zaona

  • @amadichembe4068
    @amadichembe4068 Před 9 měsíci

    mwaswela bwanji achimwene wanga pa program ya nkhanga zaona amutanyuwa ndi enanso amene amamvesela pa program ya nkhanga zaona pempo yanga asakwiye mulungu azamasula zonse. ezafika nthawi

  • @user-xq3rt3ou7z
    @user-xq3rt3ou7z Před 9 měsíci

    🎉🎉🎉🎉🎉

  • @Yahiya-wm8nd
    @Yahiya-wm8nd Před 9 měsíci

    Koma hule ameneyu patricia eeeee wandichimwitsa ponganiza

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 9 měsíci

    Olo atapasidwa mfuti zokwana 10 malatayo, wapolice komanso wa army amaphedwa mfuti ilimmanja ena ilimuchiuno

  • @alicechinyama4155
    @alicechinyama4155 Před 9 měsíci

    Nsika wapsawo nde UTI ine ndiwamunsika momwemo,I do follow u koma izi mwanamatu a ntanyiwa

    • @user-mz1pp2su5v
      @user-mz1pp2su5v Před 9 měsíci

      Aaaaaaa iwe umakhala msika wake UTI?
      Msika wa Lilongwe unatamba kupsa ku gate yaku mtunda ku nsomba ndiwe iwe ukuti chani umakala kuti iwe usatpsenso myima pano

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 9 měsíci +1

    Comrade mtanyiwa sopanooo kkkkkkkk, ndigaileko ulbum ya nyimbo zomwe ukuponya pa limpopo fm' zi please, zimandidalisa kwambiri.
    Makamaka iyi yoti ACHAKWELA UFUMU WANU AKUBWERA AMEKI AZAUTENGE, just give de full ulbum please

  • @amadichembe4068
    @amadichembe4068 Před 9 měsíci

    Achimwene mumani kwana

  • @JamesChimera
    @JamesChimera Před 9 měsíci

    Gule ndipa ground asogoleri muzanyowa

  • @JamesChimera
    @JamesChimera Před 9 měsíci

    Bwanji muzitiuzako zomwe muzatichitile mukazatengaboma?

  • @blessingkamanga1781
    @blessingkamanga1781 Před 9 měsíci

    This is the person full of lies. Mabodza too much pa limpopo fm.

  • @MarkChundah
    @MarkChundah Před 9 měsíci

    Nkhanga zaona

  • @khalifacalvinajass9998
    @khalifacalvinajass9998 Před 9 měsíci

    Nkhanga zaona