Video není dostupné.
Omlouváme se.

Nkhanga zaona Chakwera watumiza Asilikali kuti Akamuphe Peter Muthalika lero.

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 12. 07. 2024

Komentáře • 436

  • @johnmpatama1461
    @johnmpatama1461 Před 27 dny +25

    This is the beginning of the end of Chakwera government.

    • @user-mr2mh4gq8w
      @user-mr2mh4gq8w Před 26 dny

      AMbuye mutisogolere Peter ndi salimo 91 ambuye mupase I mzimu wachiziwitso

  • @user-ev6bi7jr7g
    @user-ev6bi7jr7g Před 27 dny +25

    Ndiye MCP tikuidziwa ife ndimeneyo ndale zake ndi zakupha

  • @stephankamyata3862
    @stephankamyata3862 Před 26 dny +19

    Achisale pls motsongozedwa ndambuye protect our APM

  • @augustMag
    @augustMag Před 26 dny +18

    Kwa APM yekhayo ndiye sangamukwanise dinner and dance ndi imeneyo koma Peter Muthalika yekhayo ku dinnerko Peter Muthalika akudziwa zokachita ifa ya Bingu Muthalika ndi ifa za anthu padege ukumupasa phunziro Peter amandisangalasa ndi omvera malangizo awanthu ngati Inu Amtanyiwa ndi Bakili Muluzi TV 🔥

  • @BrownMainje-sh7hj
    @BrownMainje-sh7hj Před 26 dny +14

    Shame on MCP

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb Před 26 dny +14

    Ngati iyeyo akuphanso Pieter nayenso ayenera kusogozana naye.

  • @MayamikoBanda-jh8bn
    @MayamikoBanda-jh8bn Před 26 dny +29

    I love the way momwe mumachenjeza Malawi kwa zigawenga . Ndiye nimamutsatilani kwambiri pa CZcams Kono ku Zambia

    • @MaggieMujuma
      @MaggieMujuma Před 26 dny +1

      Eeeee mayo ndalama yanga ine Peter munthalika iwe ndi Wilson msemanjira iwe anthu okuba inu

    • @chimeraJonathan
      @chimeraJonathan Před 24 dny

      L

  • @AiameAdamo-su1nt
    @AiameAdamo-su1nt Před 27 dny +12

    I'm here following you step by step each and everyday.

  • @PhilipMatolino
    @PhilipMatolino Před 27 dny +15

    Kom guyz chakwera khani ndiyotu wina kungofanso kukhala ma demo anyooo!! Mwatitola mcp kwambiri

  • @KhalideNerve-mu1eq
    @KhalideNerve-mu1eq Před 27 dny +10

    Mission impossible God is watching 😢

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Před 26 dny +3

    Thanks for your information Mr Limpopo FM 🙏 we always with you

  • @louisgolden
    @louisgolden Před 26 dny +6

    May Allah protect APM

  • @user-ew4dm8yy3b
    @user-ew4dm8yy3b Před 26 dny +8

    Achisale motsogozedwa nd mulungu please protect apm

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 Před 26 dny +6

    That's end of mcp in this country again.....God ll protect Amp

  • @lovenessmuthiya3513
    @lovenessmuthiya3513 Před 26 dny +6

    May God protect APM

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i Před 26 dny +3

    Nyimbo imeneyo ntanyiwa ukamabwera pa Limpopo FM usayisiye chonde Limpopo FM moto kuti buuu 🔥🔥 🔥🔥🔥

  • @JosephyMakunganya
    @JosephyMakunganya Před 27 dny +9

    Apa ndiye alimbana ndi achina chisale 🔥🔥 Malawi wafika posauzana

  • @CharlesMaloya
    @CharlesMaloya Před 26 dny +5

    Chakwela and Rwanda foreigner based in Malawi you will get what you want warning to Rwanda you will see

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw

    APM SANGAPITE NGATI CHIWETO .YEMWE UJA MUNAPANGA UJA BANSI .. APM ATUPELE CHIHANA ANTHU AWAWA SANGAPANFIDWE NTINTINI NEVER

  • @AjibuTwalibu
    @AjibuTwalibu Před 26 dny +6

    Mwachita bwino
    Comrade mtanyiwa
    Tili nawenawe sitingakutaye

  • @RobertNedson
    @RobertNedson Před 15 hodinami

    Ambuye apitilize kukudalitsani 🙏🙏🙏🙏musafooke chonde chonde mulungu ali mbali yanu ndi ife ofuna mtendere ndiochitila chifundo malawi aliyese amen!🙏🙏🙏🙏

  • @AlexMbewe-p7y
    @AlexMbewe-p7y Před 26 dny +6

    NDIPO SIZITHEKA AYI MULUNGU ALI KOMWEKO AMENEUJA SANGAKWANISE CHAKWERA KWAKE KWATHA NDIPO ALI NDI THAWI YOCHEPA MULUNGU AMULANGA ANANGOKHALA BUSA KOMA NDICHIGAWENGA CHACHABECHABE BUT I BELIEVE GOD IS THERE TO PROTECT PETER WA MUTHALIKA

    • @macdonaldkorea2928
      @macdonaldkorea2928 Před 26 dny

      Or nkhope ya Chakwerayo ikuchitakuonetsa kut ndinkhandwe yoopsa....asapotilidze.konse aidya malawi yonse

    • @StelliaSangaya
      @StelliaSangaya Před 22 dny

      Zoonad

  • @Emmanuelisraelsimbi
    @Emmanuelisraelsimbi Před 26 dny +2

    Koma ngati mgwirizano watha ndiye tikhale chisankho tu coz utsogoleri wu unasankhidwa pansi pa mgwirizano wa Tonse. Lets vote guys

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y Před 27 dny +8

    Kumeneko ndiye ku mafelano kuja sopano koma anthu awa akuti bwanji ndi dziko lathu cholinga chawo ndi chani? Komaso asilikali athu angoti ziiiii kumangowonelela dziko likuwinengeka koma zoti abale awo ndi makolo awo ku mamamidziku akuvutika iwowo sakuziwa kodi? Nanga chomwe akumakhalila chete ndi chani ? Chakwela kwake kwatha ife tikufuna mtendele mu dziko musakomedwe ndi ndalama komaso omwe akudya ndalama za magazizi si asikali onse pali omwe akumadya enanu dzukani kutha ndi boma lopusali lakupha la mabodza komaso pa katangale azathu aku mangochi tetedzani PM kumeneko akaziwika anthuwo apondeni or kuwapha kumene np afela zintchito zawo

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os Před 26 dny

      Asilikali a Malawi amawoneka kuti ndi opepera safuna kuthandiza Zika za Malawi akowopa kuyimbira anthu akulemekeza zigawenga zi Achina Chakwera

  • @HamzaMkwanda-bh8dc
    @HamzaMkwanda-bh8dc Před 26 dny +4

    We don't have any police in our country

  • @ChifundoNinje
    @ChifundoNinje Před 26 dny +4

    Plz plz achisale amunkhitho plz maso ndinu kt amene mumapeleka chitetezo Kwa Pam

  • @preciouskadembo1932
    @preciouskadembo1932 Před 26 dny +2

    Dr Bakili Muluzi amkatuza koma ife aMalawi kusamva

  • @user-tw2zf7bj3e
    @user-tw2zf7bj3e Před 27 dny +13

    May Allah almighty protect Apm 🤲 amiina

  • @ephraimphalawala4720
    @ephraimphalawala4720 Před 26 dny +9

    In Jesus name, God protect APM

  • @PeterJames-i8y
    @PeterJames-i8y Před 26 dny +6

    Mulungu amene anapulumutsa shadrec ,Mishec ndi abitinego kuphatikiza Daniel mudzenje lamikango apulumutsenso azitsogoleri amene atsalawa. kuti kudziwike kuti kumwamba kuli mulungu wamoyo amene sagona komaso saphethira amawona chilichose cha pasi pa thambo. mulungu apitilize kuulula zisisi pa ana ake amen.

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw

    Uthenga upite kwa Norman chisale .onesetsani kuti chitetedzo chakhwimisidwa pa gate

  • @harrietmkusangombe
    @harrietmkusangombe Před 26 dny +3

    God have mercy on our country

  • @AhmadShariff-bk3rr
    @AhmadShariff-bk3rr Před 27 dny +7

    Mission impossible

  • @OnenessLestas
    @OnenessLestas Před 26 dny +1

    Zamaboza basi mulungu akuwoneni

  • @ephraimphalawala4720
    @ephraimphalawala4720 Před 26 dny +4

    Prayer Malawi

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 26 dny +1

    End of chakwera and MCP, achepa, wapha uja Chilima wakwana basi. Thanks to Limpopo FM.

  • @IbrahimPhiri-ky5jk
    @IbrahimPhiri-ky5jk Před 26 dny +8

    Awili aziwika kale tikuimbolani kuti muziwe zosatila anafika pa asoko ndiye atawapo koma tikuwalondolola anyani amenewa komanso mangochi boys ili paliponse 💯

  • @FrankSpison-o7o
    @FrankSpison-o7o Před 26 dny +4

    Lord have mercy on us

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r Před 26 dny +3

    Koma apa pali anthu odwala amene amakhulilupilila social media dziko lathadi basi munthu kungodzuka kupanga plan yoyipitsa munthu basi the opposite is true inu ndi amene mukufuna chakwera ataphedwa mu nthawi ya DPP anthu amaphedwa ambili apa lero iliso layipa bndiyetu sankhani yesu osati satana mudzakondwa

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje Před 26 dny +2

    I love u mr khanga osawopa ngwilanani manja pls

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 26 dny +1

    Inu antanyiwa mwina inuyo ndinu mmapha anthu ndiye mzinamizila ena ndinu zizsilu ndi maboza anuwo

  • @GRACIOUSKENAN
    @GRACIOUSKENAN Před 25 dny

    Ntanyiwa ndiwe one, continue ,tilibe asilikali angakhale police, kulibe ndattttiii aaaaaaa !!!!!!
    Agalu alipowo ntchito ndi zigololo bas😰😭😭

  • @vituveggah7619
    @vituveggah7619 Před 26 dny +4

    Osazamuphwekesa comrade

  • @AndrewChilambo
    @AndrewChilambo Před 26 dny +2

    Antanyiwa pitilizani kuchenjeza amalawi zazigawenga za mcp

  • @AiwaMedia-sh6vx
    @AiwaMedia-sh6vx Před 27 dny +2

    Limpopo FM and BAKILI MULUZI TV mukuyesetsa ndithu kutitsegula mmaso koma amene alikutsogolo kwathu n'gokhumudwitsa. A Opposition aliko????

  • @GrinTemboh
    @GrinTemboh Před 26 dny +1

    Continue with good news we always listen u ukutimvetsa kukoma ntanyiwa

  • @benjaminjobo3525
    @benjaminjobo3525 Před 26 dny +1

    Nyimboyi ndaikonda Antanyiwa cain ndi abelo

  • @tiwongehojaney5873
    @tiwongehojaney5873 Před 26 dny +1

    God will protect Peter ❤❤❤😢😢

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson Před 26 dny +2

    Akangopha peter l tell you chakwela we come by the trip cross the country kukathana ndi iweyo alu continue.

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 Před 26 dny +5

    Can I come to Malawi and show my position to chakwera government?

  • @user-sw8bb3iz7x
    @user-sw8bb3iz7x Před 25 dny

    God protect APM

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 27 dny +5

    Yoo alipachintchito eti

  • @BlessMnyenyembe
    @BlessMnyenyembe Před 27 dny +2

    Thanks

  • @AllanKamphata
    @AllanKamphata Před 26 dny +1

    Mwasowa nkhani, akaphe nkhalamba ngati imeneyi

  • @user-vq5fe6mo6o
    @user-vq5fe6mo6o Před 21 dnem

    Nipamene wina akt chakwera 😢😢koma zowawa izi menyeren nkhondo Ambuye titan padziko pano

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Před 26 dny +1

    Mulungu ndiwamphavu yonse Nothing can happen to them in the name of Jesus

  • @MatemangaMoyo
    @MatemangaMoyo Před 26 dny +1

    Limpopo FM ndi bakili muluzi tv, mulungu akupaseni moyo wautali

  • @Janaphiri
    @Janaphiri Před 27 dny +3

    Munthalika wakuti sangalanulire Dziko la Malawi ali ndi ntchito yanji?
    Za fodya basi Kodi mwasiya za Tea mwayamba za chamba eti

  • @WisdomMaseko-fi5sv
    @WisdomMaseko-fi5sv Před 27 dny +1

    Koma mtanyiwa ndi masewero ako ukuzuza anthu kwabasi ona ena ayamba kale kupempherera APM kkkkk

  • @kensonmbewe6692
    @kensonmbewe6692 Před 24 dny

    I think this is a sign that we have so many satanists in Malawi, we need God, anthu afika pongoyankhula zimene akugani as long as it will black mail Chakwera, how can you feel if that happens to your father. Too bad

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 Před 26 dny +1

    Anthu amenewo asamale mangochi sigawa ma sweet

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Před 26 dny +1

    MCp ndichigawenga kuchokela ma 90s nde wina iziti chakwera Alobwino walowa nzwiwanda wangofika pa misara

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f Před 26 dny +1

    Eeeee koma ma cadet muli pa ntchito. Kkkkkk

  • @adrianobrigida3402
    @adrianobrigida3402 Před 26 dny +1

    Chigawengacho Chichewa Chakwera chikutseweretsa miyoyo ya wanthu.

  • @kidneyblessingschilinguloj7292

    Keep it up

  • @piliranimalama6090
    @piliranimalama6090 Před 26 dny +3

    Anthu ndiye kuwadodatu ndi mabodza

  • @FamousJohnathan
    @FamousJohnathan Před 26 dny +2

    Yanjiru simatani..?

  • @JohnFrank-g6e
    @JohnFrank-g6e Před 14 dny

    Ndi Ana awa zomwe akufuna sizitheka komwe in the name of Jesus

  • @macdonaldkorea2928
    @macdonaldkorea2928 Před 26 dny

    Tiyamike kut okonda dziko ngati achina Mtanyiwa alipo ambiri....chifukwa chaichi choipa sichibweredzedwa....a Gadama, Matenje ndiena monga a Chilima ndiena aja akwana, pa Muthalika pokha usayerekedze ndithu iwe Chakwera (kungokhala anthu amagazi basi)
    Bakili Muluzi amkanenatu kut MCP siyoyanjana nayo lero ndiiyo itangolawa mpandowo basi kupha kwadzuka ASAAAAA

  • @cliftondad3816
    @cliftondad3816 Před 25 dny

    Zinazi zalowa fodya zinthu.. apa nde trust pa nkhani zanu ndachosa.... Maboza

  • @user-od6eo5zc4h
    @user-od6eo5zc4h Před 26 dny

    Mudzina la yesu christu mnazaleti mutetezelnini Peter mutalika kulikonse komwe kuli iye

  • @christophergibson72
    @christophergibson72 Před 26 dny +1

    Inu munthu watha kale uyu mufuna mudanitse basi

  • @JosephyMakunganya
    @JosephyMakunganya Před 27 dny +2

    Nkhope za Rwandans zimadziwika asalowe dara kumeneko

  • @EliasKawuwa
    @EliasKawuwa Před 27 dny +1

    A Ntanyiwa tengani ndi inuyo dzikoli,musawauze azanu kuti atenge koma inuyo, a Bon Kalindo, wa Bakili Muluzi TV,atenge dzikoli,kuti kunyoza,ndikutukwana kusiye, kumangonyoza basi, zambiri zimene mumanena ndizabodza kwambiri, zonse akunena za Peter Muntharika ndi zabodza zimenezo, kungofuna kudzionetsa kuti achina Peter Muntharika awaone kuti akupanga za iwowo,kuti DPP ikadzawina adzawatole,adzadyetse mimba zawo

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f Před 25 dny

    CHAKWERA tamachita manyazi zinazi popanga, nawenso Manganya ndiwe katukule, Mulungu wakumwamba, achite nanu mwapadera ndipo asakusiyani chonchi

  • @patrickkusailemp3769
    @patrickkusailemp3769 Před 26 dny

    Longlive APM ..God is in control !!

  • @ibrahimalex7137
    @ibrahimalex7137 Před 27 dny

    We're here my brother ❤

  • @MalawianMediafm97
    @MalawianMediafm97 Před 26 dny +1

    🤣🤣🤣🤣 this is Comred ntanyiwa on Lipompo FM

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj Před 26 dny +1

    🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏yomweyo chikangawa

  • @GodifureRifa
    @GodifureRifa Před 26 dny

    Mulungu mumutetezere peter muthalika kulikose komwe apita 🙏🙏🙏

  • @SmileMalanda
    @SmileMalanda Před 26 dny

    Akuluwa misala chani kapena mwaz wachilima nd anthu ena aja zikuwazunguza😂😂😂

  • @NDIZOTHEKABANDA
    @NDIZOTHEKABANDA Před 26 dny +1

    Mabozatu amenewo

  • @mellipherjohn7158
    @mellipherjohn7158 Před 26 dny

    mumakwana bwana wanthuu🎉🎉🎉

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 25 dny

    Shame you chakwera fiti Yopanda manyazi wunapha chilima Pano wayamba kusaka Peter wupha anthu angati iwe

  • @AgnessMita
    @AgnessMita Před 25 dny

    Ambuye akutetezeleni APM

  • @MaureenBanda-t2q
    @MaureenBanda-t2q Před 26 dny +1

    Asiyeni akafa ndiiwowo ili ndi dziko

  • @user-gm3cx2xn9o
    @user-gm3cx2xn9o Před 23 dny

    Inu anthu akungofuna kutchuka ndiye inu muli busy 😂😂😂😂😂

  • @BenjaminCharlie-md3fk
    @BenjaminCharlie-md3fk Před 22 dny

    Umakwana ntanyiwa koma akangopha muntalika nafe tipha ndimiyala chakwerayo

  • @GraceMbengo
    @GraceMbengo Před 25 dny

    We pray for God's intervention. Mission iyi Ambuye alowererepo.

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 Před 27 dny +1

    koma mmm ntanyiwa boza ngati mnthu wa nkazi aaaa mnthu oti si wa dpp akagula ticket mnthu wachilendo aaa

  • @kangungufoundation2020

    Kodi amalawi bingu anakulakwirani chani?? Munamuchotsa mwachipongwe, peter uyu mukuti peter ndimunthu amene munamuchotsa mwa chipongwe again kungoni peter ndi chitsiru akuloranso kuti azapangidwenso chipongwe, saulos chilima zana zanali mumamutukwana limodzi ndi chakwera nde poti lero wamwalira wasanduka wabwino amalawi mulibe nzeru you deserve what is happening and there is no way out until you change, you will reap what you sowing

  • @user-uk1tt7ho9t
    @user-uk1tt7ho9t Před 26 dny

    May Lord for everything please protect our beloved president

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před 22 dny

    Asilikali nanuso bwanji otsangomupha iyeyo wakutumani Kodi anzako sakufuna moyo

  • @JabiluWaiti
    @JabiluWaiti Před 25 dny

    Mmmm koma akachoka kwa Peter abwera kwa inu a UDF inunso mukuyenera kukhala osamala

  • @user-kc7sd3te3d
    @user-kc7sd3te3d Před 27 dny +1

    Kodi asirikali athu bwanji ku Malawi uko mwangokhala pheeee 😂😂😂

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 Před 27 dny +1

    Koma aPrasident opuma ananenatu kuti Doom sumafayira mkamwatu ndizitu pano tubwelera ku ulamuliro wa chipani chimodzi

  • @user-gm3cx2xn9o
    @user-gm3cx2xn9o Před 23 dny

    Anthu akamatenthedwa zolankhula zake zimakhala ngati zingatheke 😂😂😂😂 mulira simunati

  • @user-je6wk8ew6g
    @user-je6wk8ew6g Před 26 dny

    Moti chikangawa yalusa sikugawanso masweet 🤣🤣🤣🤣 atimaliza

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj Před 26 dny +1

    My bsst ladio station limpopo

  • @user-bh2ei4os8w
    @user-bh2ei4os8w Před 26 dny

    Iyiyi ndiye akufuna Kenya Kenya tsopano 🏹🏹🏹