ANTHU SANAGONE NDIPO TIKUNENA PANO CONVENTION YA MCP ILI MKATI ACHEZELA KUVOTA

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024

Komentáře • 41

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 Před měsícem +9

    Anthu sanagone koma mukutionesa zinthuzi za anthu akugona kkkkk koma atolankhani inu mufuna akutameni chani

  • @MrNthungama
    @MrNthungama Před měsícem +3

    I agree you've Said people they didn't sleep but we can see people sleeping

  • @user-qb4pj5yy5b
    @user-qb4pj5yy5b Před měsícem +2

    Mukanakapangira ku ofesi kwanu kuja, nanga kukwerakwera mipando chonchi!! Timapangiramotu graduation mmenemo

  • @CassimCawanga
    @CassimCawanga Před měsícem +2

    Sanagone anthu akuliza mkonono

  • @KamandaniNgwira
    @KamandaniNgwira Před měsícem +2

    Times pono munawina mitima yathu ine ndizavotera inu , more 🔥 Tim's

  • @SaffronJeka
    @SaffronJeka Před měsícem +1

    Thank you

  • @MalitaKapesi
    @MalitaKapesi Před měsícem +1

    Zitiuzani zoona anthu akuchita kuoneka kuti akugona, inu mukutinamiza kuti anthu sanagone.

  • @DucePerez
    @DucePerez Před měsícem +1

    Nokha mukuti sanagone koma ma pictures wo akuonesa kugona😂

  • @PrincesSofilet
    @PrincesSofilet Před měsícem

    🎉Awaso ayamba ndale anthu agona inu mkut sanagone😂😂

  • @TaniaMphalumo
    @TaniaMphalumo Před měsícem

    😂😂😂😂😂😂ndarama anakoza

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm Před měsícem

    Abale fisi Ali ndi bwenzi ,koma mpakana kutchula dzankabudula mwa apule ?

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 Před měsícem

    Za ziiii😊

  • @mayoh0074
    @mayoh0074 Před měsícem +2

    Yemwe uli uli mweeh

  • @LashidSnoten
    @LashidSnoten Před měsícem

    Zilibwinokwaiwowo

  • @EvelFrank
    @EvelFrank Před měsícem

    MCP motomoto ndili pambuopanu ACHAKWERA

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 Před měsícem +1

    Koma Zikhale Ng'oma wagwa nayo

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Před měsícem +1

    Malawi Television ill kuti

  • @JumaGadaff
    @JumaGadaff Před měsícem +1

    Alekeni mulungu alowelelapo aedzekana okha okha

  • @JasonMailos
    @JasonMailos Před měsícem

    kkkkk kkkkk kumwalila osat kugona,

  • @bamusilabana6423
    @bamusilabana6423 Před měsícem

    Abalimbana imeneyi ndiyapaubale wawo

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před měsícem

    Eishhhhhh koma abale

  • @MrJwjmvula1974
    @MrJwjmvula1974 Před měsícem

    Anyamata a Chipongwe inu amene mwamuona ndi Kumkuyu basi?

  • @EvelFrank
    @EvelFrank Před měsícem

    Zikuendabwino

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx Před měsícem

    Komatu anthu wo akuvutika mawa odya okha a siya ma nyumba awo kugona ngati akapolo zoona ndikuona enafe timakana ku voter tizikhala ngati akapollo

  • @stainkabinde4226
    @stainkabinde4226 Před měsícem

    Alendo akumuzimba agona

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Před měsícem

    Zuchita kuoneka kuti Mcp yathapo basi machende ako Chakwera galu kumtumbo kwako unapha Chilima umaona ngati uzawina mavote unyera manyi kumatako kwakoko fiti iwe

    • @user-nj4ob8jw6y
      @user-nj4ob8jw6y Před měsícem

      Nawenso pamtumbo pake Atupele Muluzi, m'nyamake , mbolo ya bambo wake. Bambo wake ndi mbuli sanaphunzire, sadzakhala president m'Malawi muno. Akungodikira DPP kuti imubeleke mwana wa kapolo

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d Před měsícem +1

      @@user-nj4ob8jw6y sizikuveka izi tukwanani bwinobwino Kkkkk

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 Před měsícem +1

      Anthu akupha inu

    • @user-nj4ob8jw6y
      @user-nj4ob8jw6y Před měsícem

      @@henryphiri6100 Takanyerani uko inu mumaganiza kuti kuyendetsa dziko ndizosewera? Adalephera a Bakili Muluzi

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 Před měsícem

      @@user-nj4ob8jw6y koma bola Muluzi osati nyikwi imene ikulamulira panoyi.