![Malawi Lovers 🇲🇼](/img/default-banner.jpg)
- 171
- 2 891 639
Malawi Lovers 🇲🇼
Registrace 25. 02. 2017
Welcome to Malawi Lovers ! We're here to show you all home series, commedy, vlogs and the beauty of the warm heart of africa Malawi 🇲🇼 and many more ♥.
Sounding up your alley? Hit that Suscribe button and we'll see you in the comments!
Sounding up your alley? Hit that Suscribe button and we'll see you in the comments!
Video
Kucheza ndi Mike's trading..900 interest loan
zhlédnutí 14KPřed 5 měsíci
Kucheza ndi Mike's trading..900 interest loan
Press Conference ya a peter munhtarika
zhlédnutí 31KPřed 8 měsíci
Press Conference ya a peter munhtarika
Chitsilu chimtora nkhanichi cha MCP kkkkk 😂😂😂😂 mbuzi kuonesera mbali
At nchani malawi
Chiphaso cha kuchipatala chigwire ntchito
Mkunkuyu Ndi Muthu oipa ndipo Mulungu amulange
Tifani umandisangalasa❤
Bwana chisale ineyo ndikuti pepani kwambili pa zomwe munazunzidwa Ifenso timamvanso kuwawa
Msiska is a problem and a party partisan. I am not surprised on the way he is behaving on the interview
Wn am the of them amene ndimamva kuwawa ndikamva kuti mwamangidwa,sinakumane nanu ,sitinayankhulako koma zimkandiwawa koopsa
Ngati dziko andale sangatipititse patsogolo,mbava izi,ngati ndalama zakunja zikutivuta ndichifukwa chakuti mumalola malonda afodya azichitika mma dollar pomwe ife timagwilitsa ntchito kwacha,bwanji ifeso tizigwilitsa ntchito dollars ngati ndalama yathu? Ndiye kuti vuto la folexs tathana nalo
Riah nd black beauty tu koma Ken nsonda at sikuti muzipopetu 😂
Mundi gugule 😂🤣
Kkkkkkkk Koma Joshua iweo umakwana nkhawa ulibe
Mtola nkhan uyuy he's unprofessional
Amen agapezek ndi # ya mbusa ameney anditumizir
Nkhani yogulisa ziwalo zinayamba kale kale ndipo ine ndikukumbukira boma likuopyeza anthu kuti anthu asiye kunena boza kuchitisa anthu anzao mantha. Pano anthu ngati Manjolo ndi a T/A ndi osowa. Nchitidwe umenewu uthe mulungu achite nao opha anthu . Zikomo a Ntola nkhani Ambuye akutsogolereni mu nchito imenei. Mwapulumusa ena.
You wasted time kucheza ndi a O.C
Bvuto a MCP ndi anthu osaweluzika ndi amakani kwambiri angoyang, Ana bora m, matumba mwawo muli bwino basi e,g ndalama akuseweresazi kumangogawa akuziwa ndi aphuzo akuziwa kuti ngongole akutengazo azabweze siiiwo
M, mabaketi osayenerera kudusa olamulira amawapasisa mosabvuta chifukwa ndi iwowa alindi aphungu ambiri bvuto ndalazo sazigwilisa bwino
Chisale athu ambili timakukondani kwambili mulungu azikhala mbaliyanu mumasamala ana amasiye andale ambili alindi chuma koma samawelenga ambuye akudalitseni
Majolo ofunika kukhala msitikali wathu I need his number
Nice one comedy
Apolice akufunika makofi onse
Mulungu muchitepo kanthu PA moyo WA mwanayu komanso langizo Kwa apolisi athu mmalawi muno mwachulusa kwambiri chinyengo mukuyenera kugwira ntchito yanu moopa mulungu
Where is the mother of that girl
Queen suzatheka
The leader has bad qualities. Ndi wodzimva. Sanayenera kutiwuza zonsezo hiyaaa. Zinazo nza kuchipinda.
Kunku you asatitayitse nthawi inu ndikaporo awa
Chisare amandiwaza amayakhul mopanda matha
All very wonderful Malawi what's going on?
Amalawi nzoopsa.
It's really fine
Koma guys mumayitha keep it up
t
Mbambande chisale
🔥🔥🔥🔥🔥♥️♥️
Mwana ndiwabambowo nanga akuwakakamila choncho bwanji ndekt wawaziwa abambo ake
😂😂😂😂😂akukakamiladitu ndikuona kut abambowa adagula kwasato
Mulungu ndi mwini chuma
Ofunsa mafunso ake okhala ndi mbali😂😂😂😂😂
Malawi
Bicc, phl, zitukuko izi zidzchitika pa nthawi ya Bingu osati Peter. Mmm, kkkk
Palibe chomwe akudziwa aNamalomba
Apadera mpaka kununkila nkuku tupilose mwakuta ndemukunsa kwachokela ndalama
Koma padziko pano pakuchitika zinthu eeh ndagoma
Eishhhh God have mercy upon Malawi😢
A chipatala ndiwo anganene zoona
Iwe ndie munthu iwe auzeni
Tolo Thoko😅
Nonse mumandiwaza ine Mai Banda ku Soche ku Kwale
Mega farms iyamba bwanji mutadya ndalama zake
May shokoshoko ndinu one