This is 100% true Ndevu zamwai. Look they talked about Balaka Road, up until to now nothing happen. Dr chakweni is a good person but not being a president, maybe Chilima could be a good president.
You have said everything that agood Presdential advisor could say to the Presdent, and they have heard it all in 2023...but they do not listen.....tel them for the last time this 2024! Timakuyamikani
Andevu zamwai ndikupezeni mumapanga ma program anu muli ndi A Banda please muziwapasako mpata a Banda kut azitha kumalizisa mfundo yawo coz sometimes mumawadula koma umakhala issue yabwinonso ndiye zipasanani mpata but to be honest belu lanu limakuwa kuposa laku Vatican ndipo chakachi mwalakhula osanva ankhale choncho timuonesa 2025😂😂
Vuto la president wa Malawi wapanoyi ndi mulendo ku chipani Cha Malawi congress party anangomupanga kalibu nde Anthu amenewo amazimva mphamvu kuposa president eg a Mkaka komaso Chimwendo Banda ndichifukwa amatha kumuuza president kuti aimaso koma akudziwa kuti kuli mgwirizano wa tonse ogawana ma udindo,that is why president angoonda ndimubalalika osadziwa chochita his good person koma anamubalalitsa a chipani chake chofunika iyeyu yekha adzuke apo biiii wautali chifukwa azasowa chowilingula
Si kusintha apange resign finish apo bii ife sitikumva bodza lililose munganene achakwela ndi chilima tatopa nanu ife si zitsilu zanu. Zikutiwawatu tikumva kuwawatu oky iwe iwe chilima vs chakwela mumadziwa mulungu km????
Olo akamapanga speech ngati nthawi yonyera yakwana, no energy no power when he speaks how can the nation be energised to develop when a president is slow in speech, leaders who want things to be done speak like a young kamuzu, a bakili muluzi before power turned him into thinking he was a god, chakwera should speak with power and energy and the nation will wake up .
Njala ku Malwi kulibe koma anthu alibe njiranzopezwra ndalamam chifukwa panopa almost all trading centres tradera are selling sourced within Malawi. So what is their problem. They do not have means of having money. Sonwe need to work on this. This problem.has been there for so long and handouts its not the answer to this issue. There is no reason for thw government to farmers. A real farmer muat feed himself first. Anybody failing to feed himself doesn't qualify to be a farmer. So let's make our ciztizen become farmers. For more than twenty years government has been supporting citizens but not change so where are we missing.
Brian banda you're the king mumayankhula zoona zenizen I'm so proud of you brother❤
This is 100% true Ndevu zamwai.
Look they talked about Balaka Road, up until to now nothing happen.
Dr chakweni is a good person but not being a president, maybe Chilima could be a good president.
Mbambande
Abanda ndi abwana akowo mumakwana ine ndimakunyadilani
Chakwela chilima nonse munya
Malawi on fire 🔥🔥🔥🔥
but to be honest mutharika was more better than chakwera
Very true
Pakalipano ku Malawi kulibe television yoposera pa times TV ndipo I'm very proud of the times media group
Obanda and Ondemvu your the true servant
brian ndi ndevu zamwayi please don't worry we know wat we are going to deal with this mcp government
I like kwagwanji makamaka akabwela anthu atutuwa yes ndimava kukoma
Brian en Mr ndemvu za mwayi tayambisani chipani wina president en his vice mutha kuyendetsatu boma Inu mutamazapanga zomwe muyakhulazi
You have said everything that agood Presdential advisor could say to the Presdent, and they have heard it all in 2023...but they do not listen.....tel them for the last time this 2024! Timakuyamikani
Wonder n Brian pa min of agriculture Po mwaswa mwaswa.
I really much appreciate, u said it well an2 aona achtaz . Maudindo ndithu amatha khalan osamala ku palace ko plz.
Chakwera ndiwachidodo zoonadi kaya nayeso mkulu oganiza bhoo uja akutaniko kumeneku
Moyenda chingaipa chinyau chakwela ndiwe galu kwabansi watikwana mbuzi ya munthu tsiku transport pastor kamwendo njila walephela bakha iwe
Lipoko lachuluka .... zoti anthu akufa ndi njala uku sakuva...
Guys you are the best TV broadcast in Malawi,continue being unpartisan
Koma mwabandula guys. Brian and Wonder, you rock!
Ayi ntchito yabwino pitilizani
Mukunena zoona
this man he has all the time but what iknow about chakwera he came to still our taxpayer
I did say this long ago... Kuti ngati President sakudziwa ntchito yake nduna siingapange kanthu kolozeka chifukwa kotengela mphamvu mkwakufa
Mpakana boma lafika pa nkhanga likufunika likoko 😅😅😅
It seems the state of the country being in such a state, benefits these people, hence the lack of motivation for change.
Ndipo inuyo ndo one
Muma tiimilira Brian, ndimakusatani pa program imeneyi kuno South Africa.zikomo kwambiri more🔥 ,,!
Kuno ku Dedza south west, ngakhale pamaliro chakudya chikusowa. Ma mfumu afika ponena kuti maliro adzichotsa mofulumira kuti aliyense adzizionera yekha. Zinthu sizili bwino ndithu.
Eee uncle brian tathamangani mitiitanileko akulu aja munachezanawo pankhani yaanyamata opita ku kuizalayeli aja taona anyamata aja ayamba kukana zina zinene anakamba nthawi imeneija amati analandila mafoni aulele tamuitanani nkulu uja anthu amufunse mafunso pangono
Abanda chakwela ndi chosamva
Andevu zamwai ndikupezeni mumapanga ma program anu muli ndi A Banda please muziwapasako mpata a Banda kut azitha kumalizisa mfundo yawo coz sometimes mumawadula koma umakhala issue yabwinonso ndiye zipasanani mpata but to be honest belu lanu limakuwa kuposa laku Vatican ndipo chakachi mwalakhula osanva ankhale choncho timuonesa 2025😂😂
Mumakwana ipatseni moto
Mr ndevu zamwayi please bruff us chakwera can never change anything ryt now
Koma ndiye kuli chibwanadi ku bomako
ntchito mumagwira
This is true ❤
Mr brain timakunyadilani always agalu awa sangamve sinankha iwo zawo zili bwino agothi awa anthu alibe nawo tchito. Km kmtu la 40 likubwela
This is a true
Anthu awa amatiyilir samapwatir kuyankhul❤
Mumufunse Bakili akuuzeni za Malewezi,Mchewa amangovomera.ndatsimikizira kwa Chakwera ndinkaona ngati Bakili wabodza
Ma guys inuyo mumatiyimilila kwambili my Allah protecte u guys
Thanks u mmatiimilila
Kuyakhula mwanyonga
Chakwela ndichiwanda simunthu olo mutayankhula bwanji iye aliplan yowononga dziko
Ndawu oopsa yabuka pakati pa chakwela ndi chilima
Vuto la president wa Malawi wapanoyi ndi mulendo ku chipani Cha Malawi congress party anangomupanga kalibu nde Anthu amenewo amazimva mphamvu kuposa president eg a Mkaka komaso Chimwendo Banda ndichifukwa amatha kumuuza president kuti aimaso koma akudziwa kuti kuli mgwirizano wa tonse ogawana ma udindo,that is why president angoonda ndimubalalika osadziwa chochita his good person koma anamubalalitsa a chipani chake chofunika iyeyu yekha adzuke apo biiii wautali chifukwa azasowa chowilingula
brian and nsinziya gear up this position where u are please guy don't fear when u speaking because some times always mixing discussions
Chakwela ngti ukuzinamiza kt uli ndi mabodza ena owanamiza amalawi wanya palibe angakhhlupilile anthu zowatenga amalawi ngti zitsilu wanya.
Koma anyamata inu 😂
Big up guys
Brian and wander, mumayesetsa kwa unikira atonse koma ndi onsamva ndagonthu mkutu chabe.
So much Dead wood 😂😂😂😂
Si kusintha apange resign finish apo bii ife sitikumva bodza lililose munganene achakwela ndi chilima tatopa nanu ife si zitsilu zanu. Zikutiwawatu tikumva kuwawatu oky iwe iwe chilima vs chakwela mumadziwa mulungu km????
Auzeni asazaname kuti panalimbe malagizo mukuchita bwino osamawaopa
Boma liluza mwangovutika kukamba
since this people came again into power everything went wrong
Pamenepakufunikakuyankhulachilungomo chiyankhulidwe wokwiya akwiye osaopa bomalakubaili.
Live
Brian timakunyadilani mumagwila tchito yotamandika kuntundu malawi
💪🏻💪🏻💪🏻💪🏻🙄
Banda, lanu lero dzina lapezeka, Thusawu.
Inuyo ndi deal
Chakwera is the best leader you can't compare him to Muntharika.
Iwe iwe
Usamakhale ndi mtima opanda chkond ND agogo Ako aja plus azibale Ako aja kumudzi kuja iwe
Ukunama Aise ndekuti ndiwe Mbuli , Osmangot chalowa Mchakwathu Manja M'mwanba mufunika kumaganiza Munthalika ndi M'banga Aise
Timakuydilani guys mumati imilila❤❤❤
Mau amphamvu pitilizani timakukondani azibàmbo inu ndizoona mukunenazo
who was promising as saying he is going to be better than mutharika
B banda awa asiyene samava
Apumbwawa atonseo ubongo ungwira alibizy kuzompha mapapaya muboma mo akuziwa kt 2025 azawa sosola nthenga
Ayi tichokoche kuyambila chakwela ndi group yake yonse finish pulezident wanji osamvela chisoni amene anvotela chimanga chakenya chija simungagule kupulumutsa anthu inu zoona bola mukukhuta inuyo?
he time is over
Powerful
Kunena kwa chindunji uku. Anthuwa alephera. President athu akugona kwambiiri.Palibe akuwaopa a Chakwera. Dzikomo Times polira mmalo mwa Malawi.
Nduna zinkadziwika ndi kugwila ntchito mu nthawi ya muluzi basi,nthawi ya muluzi nduna iliyonse ngakhale kuyifunsa nkhuku imatha kukuuza nduna iliyonse dzina lakee ntchito yake .
Andevu zamwayi mumadzola mafuta woyeresa?
Chakwela ndi galu
Bwanj
Malawi asogoleri ake ndi aupo sakonda ziko lawo.Tonse alliance yalephere Koma zoti izachoka pampando iwalani ndipo ndikunenesa ine mwazi uzakhesedwa Kuti azavomereze Za kuluza kwao.
Olo akamapanga speech ngati nthawi yonyera yakwana, no energy no power when he speaks how can the nation be energised to develop when a president is slow in speech, leaders who want things to be done speak like a young kamuzu, a bakili muluzi before power turned him into thinking he was a god, chakwera should speak with power and energy and the nation will wake up .
Satanic times tv party, dzitsilu dza anthu inu eti
Njala ku Malwi kulibe koma anthu alibe njiranzopezwra ndalamam chifukwa panopa almost all trading centres tradera are selling sourced within Malawi. So what is their problem. They do not have means of having money. Sonwe need to work on this. This problem.has been there for so long and handouts its not the answer to this issue. There is no reason for thw government to farmers. A real farmer muat feed himself first. Anybody failing to feed himself doesn't qualify to be a farmer. So let's make our ciztizen become farmers. For more than twenty years government has been supporting citizens but not change so where are we missing.
Njala ku malawi kulibe????? My friend u are mad
Nzeru ulibe
You're talking foolish.
Demon! you r fool brother and you don't know what you are talking about, I think you're becoming mad 😡 .
Iwe galu kwabasi