conference ya dpp ya lero

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 09. 2024

Komentáře • 44

  • @user-zs9pl2kt7f
    @user-zs9pl2kt7f Před 6 měsíci +2

    Munatinamiza university ku mzimba andale mutipha amalawi

  • @user-xs3pk1vp8i
    @user-xs3pk1vp8i Před 6 měsíci +1

    Mwakhuta kachasu kkkkkk opposition yimawawa myiwona

  • @user-vu9rt8gj3o
    @user-vu9rt8gj3o Před 6 měsíci

    Apm my vote

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 Před 6 měsíci

    Ifeso tikuphempha mseu waku mzimba eswazini mzalangwe road, contractor anachokaso kumseu umenewu, please chonde tithandizeni kuwakumbutsa a president awa akuwudziwa mseu umenewu, mseu umenewu ukudutsa kafukule mpaka kufika ku ekwendeni. Mayendedwe akuvuta kwambiri kumseu umenewu.

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 6 měsíci +1

    Akulu akulu musaope mcp, tisabwerere ku one party system. Sitilola zimezo. Mavuto achuluka ku Malawi. Lichoke boma ili.

  • @user-qk2hw4ex3c
    @user-qk2hw4ex3c Před 6 měsíci +1

    Pano ndiyanu muyiwona dwambadzi a DPP munatasa kwambiri mudzikolo

  • @user-nc4vi1jt5g
    @user-nc4vi1jt5g Před 6 měsíci +3

    Dzitsilu inu adpp

  • @user-yf6yt5if1d
    @user-yf6yt5if1d Před 6 měsíci +2

    Inuyo mwayiwalira zomwe mudayichitira utm ku Mangochi ndi Machinga?
    Separation of Government arms meaning what? Inuyo munazichita?

  • @user-zs9pl2kt7f
    @user-zs9pl2kt7f Před 6 měsíci +1

    Akuphedwa anthu ku mzuzu siinali nthawi yanu?

  • @BrianManda-hb8co
    @BrianManda-hb8co Před 3 měsíci

    Miyakupa yophatikiza ndi nyekhwe ku dpp. Kkkkkkkk ku opposition si zinthu

  • @WillardChanza-qr5sc
    @WillardChanza-qr5sc Před 6 měsíci

    Why can't you go to court sort out your issues. Vacate the injunction remove Nankhumwa from the leader of opposition position, start afresh basi

  • @RonaldFunsani-ik1us
    @RonaldFunsani-ik1us Před 6 měsíci +1

    😂😂😂😂 inuyo guys mutenga Boma

  • @enipherphiri207
    @enipherphiri207 Před 6 měsíci

    Inu mukulankhula ngati wamsembe munali kuti dpp zigawenga achina japi akuzunza amalawi???

  • @JacksonNamakhwa-jp4mg
    @JacksonNamakhwa-jp4mg Před 6 měsíci

    Walephela kulamulila ameneyu osamuvela chisoni achoke busa wakhaza ngati ameneyu sindinamuwoneko ine ayi ati Phela ana athu uyu

  • @user-xh1ve5ym3l
    @user-xh1ve5ym3l Před 6 měsíci +1

    Ineyo lero ndinapita ndi mwana ku chipatala Cha Dedza central ,mwayo anathyoka m'kono dzana koma ndagula ndekha chikhakha olo mankhwala sanampatse komanso pomwepo mkutiuza kuti basi dzipitani . Zinthu kumalawi sizikuyenda .

    • @BraveNyirongo-xe5fg
      @BraveNyirongo-xe5fg Před 6 měsíci

      Dedza Central hospital nde yakuti? But very unfortunate if it happened

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 Před 6 měsíci

    DPP be careful mcp ndiaanthu oipa kwambiri, even nanu mupanga zanu zopusa zomwe zinakutulusani boma koma mcp chenjera nayoni ikuongerani chipani,,

  • @user-qk2hw4ex3c
    @user-qk2hw4ex3c Před 6 měsíci

    Mwaiwala zimene mumapanga ndi adzanu ndipang,Ono simunathe anthu angat mwavuta anthu a DPP

  • @WillardChanza-qr5sc
    @WillardChanza-qr5sc Před 6 měsíci

    Beating individuals in full view of the police is similar to what DPP used to do while in power. They used to beat people while the police watched. These two political parties have similar colours: whether MCP or DPP palibe wabwino. DPP looks angelic now that they are out of government. Inuso munali amwano kwambiri muli M'boma you are not a necessary evil. However mnthawi yanu the economy inaliko bwino. Ndinu madolo you could see to it that a common man shouldn't suffer in the village, apo pokha nditha kukuvulirani chipewa, though munali ndi zofooka zanu

  • @user-kf1bv9om1k
    @user-kf1bv9om1k Před 6 měsíci

    APM anatuluka anthu ake omwewa

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 Před 6 měsíci +1

    Anthu akulu akulu ngati inuyo mavuto mukuwadziwa bwanji osapanga chiganizo koma anthu awa kugona amaonjeza

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 Před 6 měsíci

    Muyeso uja mumayesa nawo anzanu dzana lija ndi umenenso akukuyesa nawo inu lerowu

  • @davietembo7935
    @davietembo7935 Před 6 měsíci

    Amalawi tiyeni tipange analyse the actions of Mcp led government against the rule of law. Are you serious to say that Nankhumwa is eligible to be leader of opposition despite being mcp or dpp or utm? Guys tikamapanga comment be sober minded for mmawa zinthu zimasintha. Let's sustain our democracy.

  • @user-yf6yt5if1d
    @user-yf6yt5if1d Před 6 měsíci

    A Mhango muzingozivutha musaganize kuti mwina azakupasani u vice president was dziko,Mayazi

  • @jamesmsonkho4830
    @jamesmsonkho4830 Před 6 měsíci +1

    Zakukhoti tichedwa nazo

  • @user-kf1bv9om1k
    @user-kf1bv9om1k Před 6 měsíci

    Osatinamiza ife ayi. Munachita opusa kunatha basi.

  • @user-yo9rw8tr4s
    @user-yo9rw8tr4s Před 6 měsíci

    Chitsilu ndi chakwera wosalimbana ndi dpp cz muzalila 2025 mukuiwona ikulamulira

  • @user-dv6wy1sq8g
    @user-dv6wy1sq8g Před 6 měsíci

    Mukapitiliza kugona a DPP mupitilila kugona nyekhwe mukuenela kudzuka

  • @enipherphiri207
    @enipherphiri207 Před 6 měsíci

    Karma 😂😂😂😂

  • @user-kf1bv9om1k
    @user-kf1bv9om1k Před 6 měsíci

    Opusa anthu onsewa zimene amachita ali mboma ndizimene amachita.

  • @fraserluwemba6364
    @fraserluwemba6364 Před 6 měsíci

    DPP rise up again. DPP hungry lion now

  • @shotsfired588
    @shotsfired588 Před 6 měsíci

    Agalu awa alibe manyazi zedi, akuti chani zokhapidwa??

  • @BraveNyirongo-xe5fg
    @BraveNyirongo-xe5fg Před 6 měsíci

    Dpp you have failed us with your greed. Mikangano yakuchipani pano iyo yayamba kusokoneza parliament. We can all read and understand what is happening. So what about the injunction? Should the speaker be in contempt of court deliberately because of the immunity given to parliamentarians during their sitting? Or just to make dpp happy?
    You failed in government and you have failed in opposition. Inu amene mkulimbikira APM mkuononga DPP.

  • @miltonkanyamula9486
    @miltonkanyamula9486 Před 6 měsíci

    Kodi Inu lero zikukuwawani kuti anthu a chipani akumenya a chipani chitsutsa?
    Mwayiwala zomwe anyamata Anu amachitila muli mboma ?
    Inu mwaonetseratu kuti muli desperate kuti mukapitilize kuba kuja munkachita kuja.
    Munyopoka... Chakwera will continue.. Inu takhalani kaye ku opposition...

  • @driano763
    @driano763 Před 6 měsíci

    This useless party.

  • @francis12fombe54
    @francis12fombe54 Před 6 měsíci

    Kkk😂

  • @user-pb7ux9yw1r
    @user-pb7ux9yw1r Před 6 měsíci

    Corrupt mcp

  • @user-yf6yt5if1d
    @user-yf6yt5if1d Před 6 měsíci

    A Mhango muzingozivutha musaganize kuti mwina azakupasani u vice president was dziko,Mayazi