NGC meeting ya Dpp

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 09. 2024

Komentáře • 173

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula4937 Před 9 měsíci +5

    Matsoka a DPP anayamba poyamba kumusala SKC...Bingu anladziwa kuti chipani ichi chinkafunika new minds....

  • @sweeneykamwendo6251
    @sweeneykamwendo6251 Před 9 měsíci +7

    Anthu awa alibe mzimu kkkk

  • @ShemMwale
    @ShemMwale Před 9 měsíci +7

    This is Democracy country. Others are in Dpp to affect rights and freedom. We are Dpp we will never allow as blood party.

    • @patrickmacheso5062
      @patrickmacheso5062 Před 9 měsíci +4

      Tell your people to form their own party not this nonsense, DPP is belongs to APM not Nkhumbwa, Dausi and other useless people.

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 Před 9 měsíci

      Mukanangolemba chichewa boss, chingerezi chanuchi eeeee olo graduate akhoza kulira.

    • @kaitanokagalu
      @kaitanokagalu Před 9 měsíci

      @@Littlefair7 mwatero Kodi? Midziwa bwanji olembawo si a graduate?

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 Před 9 měsíci

      @@kaitanokagalu
      Koma chingerezi chomwe chalembedwa apa ngati amakakamizidwatu, tiyeni tizilemba language yathu momasuka basi.

    • @kaitanokagalu
      @kaitanokagalu Před 9 měsíci

      @@Littlefair7 kikkkkkk ndiye anthu oterowo amakhala amakanitu osati masewela hahahahahahah!

  • @Slyvia-uu3wc
    @Slyvia-uu3wc Před 9 měsíci +1

    Yambitsani chipani chanu adausi,,,bingu wa muthalika atawona kuti akupangana over take ndi muluzi anapanga chipani chake ,,,ine zavotera adad ❤❤❤ ,,,dausi akufuna kufa atsanalape

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll Před 9 měsíci +3

    This NGC meeting has been sponsored by MCP gurus, and atola nkhani ogulidwanu tikukuziwani

    • @kaitanokagalu
      @kaitanokagalu Před 9 měsíci

      MCP ilibe nthawi ya zopusazo m'phwanga ilibe Ndalama zogula anthu a DPP,kuti adzitani anthuwo?

    • @user-ko9ht2pj8d
      @user-ko9ht2pj8d Před 9 měsíci

      Game zikwanje tsopano poti mwawadziwa osaiwala yanu ija tili kuma stand

  • @EmercianahKasiku-en6hl
    @EmercianahKasiku-en6hl Před 9 měsíci +2

    This is Democracy chipani sichikhala Cha munthu mmodzi or banja ai zinathetsa chipani changa UDF zokakamiza chipani kukhala zakubanja meeting ya chipani kupangira ku Page house munyumba ya munthu kkkk go go Nankhumwa umatha iweyo

  • @user-oo5bx1rl3j
    @user-oo5bx1rl3j Před 9 měsíci +1

    Iyi si AGC meeting ndipo zimene mukukambilana si za chipani Cha DPP koma inuyo mukungogalukila chipani cha original DPP tsogoleri wake ndi ownable Peter Mutharika. Ndipo pemphelo lanu ndi lopanda ntchito ndipo Mulungu sangavomeleze pemphelo ili ndipo Dausi ndi wakupha olo Mulungu akudziwa za Dausi wapha anthu ambili ali ku Mcp ndipo musamamunvele ndi chokupha chimunthu ichi

  • @giftkanjuchi-qm8hf
    @giftkanjuchi-qm8hf Před 9 měsíci

    Bravo nakumwa ndi Jeff wa feff. Ana a chabe osafuna kusekerera zopusa. Ana inuyo musazafe

  • @SavicoJastin-vj7pt
    @SavicoJastin-vj7pt Před 9 měsíci +1

    Dausi pepan ngat unayamwa belelamako choonde mwayes mwana wa mulungu akuyendere ndith zomwe mwakonza tazimva kale sizomwe uku fotokozazo ayiiiii booza ambuye ambuye talila ameen

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 Před 9 měsíci

      Uku ndiye kuyankhula kopusa, mwana wa Mulungu akulowa pati pamenepa? Kupusa bwanji kodi?

  • @user-mw6lr9sm2q
    @user-mw6lr9sm2q Před 9 měsíci +2

    Dawus ndiwosokoneza Kodi osangoyambitsa chipanichanu bwanji iyi ndi DPP yakhothi

  • @timothymphwina
    @timothymphwina Před 9 měsíci +3

    Koma Inu ndalama mwadyazo musanza ndithu anthu achabe inu

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 Před 9 měsíci +2

    Ma Court akulamulidwa ndi MCP ndiye nzachidziwikile kuti akumuopa APM and akufuna Nankhumwa kuti akhale President cholinga adzadutse moyera.

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 Před 9 měsíci

      MCP pamenepa ikulowa pati? Umbuli bwanji kodi?

    • @kaitanokagalu
      @kaitanokagalu Před 9 měsíci

      @@Littlefair7 Kodi mukamnvatu kuti ku Malawi kulimbuli,amatanthauzati zimenezi, ndipo, ukamziona ngati zinalowa mkalasi koma zinabwelako mmutu muli zimamina thooooo! Kikkkkk ma form form okhaokha kikkkkkkkk!!!!

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 Před 9 měsíci +2

    Pungwe pungwe uwu bwezi akulandila Ali bomawa Koma mukupangana Nokha Nokha anakhumwa Ku paliamenti mumangogonako kod amalawi minyama yathu yatunduwanji 😢😢😢😢😢

  • @gospelnetworktv5585
    @gospelnetworktv5585 Před 9 měsíci +1

    These people are patrotic to the party, they are the ones who are willing to preserve the party not Za NAmalomba ndi APM za misala basi. big up people mwachititsa manyazi a ku page hausiii

  • @onester4946
    @onester4946 Před 9 měsíci +2

    All blame to Nankhumwa. He will never be president

    • @patrickmacheso5062
      @patrickmacheso5062 Před 9 měsíci +1

      Nankhumwa mbuzi ya munthu and akuona ngati angalamulire dziko la Malawi, kukhala President si ntchito yophweka amufunse Chakwera mmene akulephelera.

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 Před 9 měsíci +3

    MCP iyi.Onse amene asankhidwawa ndi a MCP in DPP uniform.
    That's why mu comment section mu mwadzadza a MCP

  • @earnestkavuta2721
    @earnestkavuta2721 Před 9 měsíci +1

    😂😂😂😂 chisakho chakunyumba Kwanu chani😅😅

  • @francistonysanena5349
    @francistonysanena5349 Před 9 měsíci +3

    Amene wakhala akusatila khaniyi bwino bwino kuchokela pa chiyambi akuziwa kuti Anthu awa akupanga zolondola

    • @kaitanokagalu
      @kaitanokagalu Před 9 měsíci +1

      Ndizoona mukunenazi koma eni ake a DPP sakuzilondola ndipo ndi anthu onvetsa chisoni,I think they are ignorant by nature

  • @DoYouKnow3838
    @DoYouKnow3838 Před 9 měsíci +3

    This is absolutely not a DPP I used to know and like.

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Před 9 měsíci

    Koma ziliko ndalama I apha yesu koma usanza sure🔥🔥🔥

  • @mariumkuyerbarak3691
    @mariumkuyerbarak3691 Před 9 měsíci +1

    Chinthu chomwe chikundidabwitsa ndi chakuti misonkhano ya gulu ili zikumaulutsidwa ndi ma TV station wodziwika bwino Zodiak, Times MBC. Pamene misonkhano ya ADAD yikumakhala pa Bakili Muluzi Tv kapena pa Ngaliba TV.

  • @wayneivanmacadam
    @wayneivanmacadam Před 9 měsíci +1

    Useless immature politicians

  • @fctv7161
    @fctv7161 Před 9 měsíci +1

    Anthu opanda nzelu inu simungaone 😢momwe anthu akuvutikira mdziko muno??? ....zitsiru kwambiri

  • @user-dk6yc8pl2m
    @user-dk6yc8pl2m Před 9 měsíci

    Mungoyamba Chan ndye tiwone Kut mufkanazo pat Koma DPP singawono ngeke Nd makape ngat inu

  • @user-eu1qs1eu5q
    @user-eu1qs1eu5q Před 9 měsíci +1

    Ambuye ake ati amene akudaliseni lusifala dausi ndinu munthu wakulu muzikhala ndi zeru zofuna kuthandiza amalawi simuzawina

  • @jilanifaluku6301
    @jilanifaluku6301 Před 9 měsíci +1

    Akuwona ngati kulanda chipani ndi izee akulephela kumupha penter mapeto ake abalalika akugwilisa tchito makhothi sopano mukuzinamiza tikuwonelani kuti mukafika kuti

  • @godfreylumbalo6249
    @godfreylumbalo6249 Před 9 měsíci +2

    They're doing in accordance to Court orde 😅😅😅😅

  • @giftkanjuchi-qm8hf
    @giftkanjuchi-qm8hf Před 9 měsíci

    Dpp yeni yeni ndi iyiyi. Osati zankharamba yakumangochiyi

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Před 9 měsíci +5

    We ignore all your plans and secrets but just wait for the response from heaven mark my. Words. You are cheating yourself.

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 Před 9 měsíci

      Please you cannot mention heaven so cheaply, heaven is not a weapon of threatening others. Withdraw your nonsense please.

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole Před 9 měsíci

      I know what am talking about and God is withstand for everyone so why you are feeling pain with that word heaven is expensive and wait for the outcomes

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 Před 9 měsíci

      @@SolomonNjolomole
      Stop your holier than thou mentality, God is not a politician, stop mentioning God so cheaply.

  • @nditumenichagunda4192
    @nditumenichagunda4192 Před 9 měsíci +2

    Peter or ataima independent azawina

    • @tasmania527
      @tasmania527 Před 9 měsíci

      Adzawina ku Thyolotu kkkkk. Keep dreaming

    • @kaitanokagalu
      @kaitanokagalu Před 9 měsíci

      @@tasmania527 kikkkkkk hahahahahahaha koma abale ku Thyolo kokha Kodi? Ayesle kuima payekhapo aone dziko mmene limakhalira.

  • @user-dp3fo7tl8c
    @user-dp3fo7tl8c Před 9 měsíci

    Koma nde kuyalukatu, komatu iwe Nankhumwa, route yomwe watenga iwe wasochela ndipo sizikuthandiza Kodi unaganiza kuti anthu angakusankhe iwe kukhala mtsogoleri wa dziko?

  • @stanleymatolabanda5460
    @stanleymatolabanda5460 Před 9 měsíci

    Tiona zithu 😂 dpp once a mighty party now in shambles.

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll Před 9 měsíci +3

    MCP is hiding behinde these gungstars

    • @peterbakuwo1249
      @peterbakuwo1249 Před 9 měsíci

      Proofs please!

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 Před 9 měsíci

      For sure ndalama azitenga kuti akulephera kulongosola

    • @kaitanokagalu
      @kaitanokagalu Před 9 měsíci

      @@eliffagondewe8214 Ndalama za chinaso tsopano? Kodi you think MCP can be so low like your DPP? Sponsoring what? Hahahaha! Shame on you, by the way,this is normal when you are in opposition! Tangokhalani kaye choncho and wait the next level your division muthawa nokha

    • @josiahgarley3824
      @josiahgarley3824 Před 9 měsíci

      Zabodza

  • @user-bc1zi6hz7g
    @user-bc1zi6hz7g Před 9 měsíci

    Ajefu osadanda muchila

  • @user-ie4ci3zh7j
    @user-ie4ci3zh7j Před 9 měsíci +1

    Mesa adausi analowa muchipani mcp?

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Před 9 měsíci

    Daus Ndi wa mcp siwa dpp ndalama zikucokera kwa chakwera iwe daus ndi nakhumwa yambitsa chisoni chanu Osati ndi d pp prezdent ndi Peter bas daus ufune usafune

  • @user-ty7mc9mg1f
    @user-ty7mc9mg1f Před 9 měsíci

    Zindikirani kuti ,ndinu aNGC, koma okuba ndithu zandinyatsa.Mukufuna kugulitsa chipani,ku MCP.

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 Před 9 měsíci

    Malawian the can't vote for Nankhumwa forget it serious

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula4937 Před 9 měsíci +6

    Parties shouldn't be owned as an estate...case study ya UDF is pathetic versus MCP owned by people

  • @user-mx3rw2dt4z
    @user-mx3rw2dt4z Před 9 měsíci

    Zaugalu zimnezo mwasowa zochita

  • @MrcharsCollen-cy6cr
    @MrcharsCollen-cy6cr Před 9 měsíci

    Nankhumwayo ndiye ayitu masanje enieni

  • @WilsonLimited-mv7it
    @WilsonLimited-mv7it Před 9 měsíci

    Koma akuluakulu nankhumwa ali mchimutu eeeee simwangodzadza mamina mmenemu

  • @user-kr1kg5hy9l
    @user-kr1kg5hy9l Před 9 měsíci +1

    Zanu izo,nthawi ikakwana mulapa.

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw Před 9 měsíci +1

    Ndikuona kuti iyi ndi mcp Reserve not DPP party awa akabwedza ndalama zonse zomwe apasidwa

  • @user-lc3sw8iz2g
    @user-lc3sw8iz2g Před 9 měsíci

    A DPP menyani nkhondo yolowa boma
    Mukawina zathane nawoni adani anuwa.

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Před 9 měsíci

    Kutereku amenewa ndi osaukanso kwambiri kumalawiko ofuna kudya nawo kuchokera ku MCP

  • @bernardchithumba6040
    @bernardchithumba6040 Před 9 měsíci +1

    Iwe kadausi ukuima ngati mndani ku NGC, yet you're mcp member, and that party is not mcp party but DPP ,,,,,,,,koma ya! Mcp ilowadi m'boma mogulidwa azipani Zina,koma Mulungu si munthu mudziwaso ukulu wa Mulungu,, ........bodza ndalama apatsidwa ndi mcp

  • @user-ku5fs6lv4n
    @user-ku5fs6lv4n Před 9 měsíci +1

    Maina onse apa ndiongoeserera zaziiiii

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Před 9 měsíci +1

    Dausi chonde usamati amalawi amalawi ake atiwo aaaaa kkkkk

  • @user-lh4nx4hw7x
    @user-lh4nx4hw7x Před 9 měsíci

    Thi is the buttle,Who can seiz the fire

  • @MaxwellMustafa-ec8fc
    @MaxwellMustafa-ec8fc Před 9 měsíci

    Mbamva izii muwoneni dausi mayakhudwe ake ayenera kuziwa kuti mulungu simunthu

  • @user-yb8we7tl2q
    @user-yb8we7tl2q Před 9 měsíci

    Nankhumwa woyeeeeee

  • @user-ty7mc9mg1f
    @user-ty7mc9mg1f Před 9 měsíci

    Nanu a Dausa, tadzinenani chilungamo.ndiye a Presidentiwo anakuchitani ok?Ndiye mmene mwatelo mukawauza chani,a Peter.KuBA uku

  • @user-ie4ci3zh7j
    @user-ie4ci3zh7j Před 9 měsíci

    Akuononga dziko akufunaso awononge chipani cha ddp, akathidwaso ndi mulili winatu? Kkkk

  • @user-uf1tz7bp5q
    @user-uf1tz7bp5q Před 9 měsíci

    Inu kd ndinu upusa eeeti inu mukuona gt angavotele nakhomwa ndi ndani koma inu mukupusa bwanji nakhomwa angakhale president mwapenga

  • @lewisdicksonmlozi130
    @lewisdicksonmlozi130 Před 9 měsíci

    Uyoyo lafu jumayo zaka zosezi wakhara aliboma wapangako chiyani akumanga ma ronge kwawo kuno kumachita kusowa mseu anthu woipa nokha nokha wopanda chisoni ndiamalawi womvutika simungavomereze kuti mwakura agalu inu

  • @user-yz1fk1dx1m
    @user-yz1fk1dx1m Před 9 měsíci +1

    Muyaluka inu mulungu akukathani ndithu athu osokemeza inu

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u Před 9 měsíci

    Anthu awa ndi anthu oyipa
    Ndipo sakumva chisoni ndi amalawi ndipo mulungu akuona

  • @felixmozile7513
    @felixmozile7513 Před 9 měsíci

    A dausi uzimu unawachokera,zaumphawi wa a malawi alibe nazo ntchito

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Před 9 měsíci

    Machende ako iwe dausi mulungu akulanga

  • @ChamboChange-pq1hd
    @ChamboChange-pq1hd Před 9 měsíci

    Jeffrey ndiwe hule loputsa kwabansi msonkhano umenewo ndiwanu ndi ma boyfriend ako ngati Ken msonda nankhomwa ndiwe mbuli sungakhare president wa dziko agalu inu,

  • @nosherwanshahbaz3906
    @nosherwanshahbaz3906 Před 9 měsíci

    NANYONGO WAMAKO GREZDA JEFRY

  • @SymonNamalomba-sh3fu
    @SymonNamalomba-sh3fu Před 8 měsíci

    Anthu omwe akupanga dzinthu koma osaziwa chobwera mawa

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u Před 9 měsíci

    Anthu awa sakumva chisoni kunena kuti ndi afiti sitikulakwitsa

  • @fedson2050
    @fedson2050 Před 9 měsíci +1

    Anthu oukira inu mulibe NZERU serious

  • @EnockNgombe-dg3wu
    @EnockNgombe-dg3wu Před 9 měsíci

    Powerful asogoleli

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Před 9 měsíci +1

    Kodi Nankhumwa wanuyo angamuvotere ndani kkkkk inu dzitsilu za ana?

  • @user-xq5ju2uo9h
    @user-xq5ju2uo9h Před 9 měsíci +1

    Pofikana kupasa undindo daus mu chipani chafelanthu bas🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @usumanidaudi
    @usumanidaudi Před 9 měsíci

    Jefure hure uzitenge bwino tikoza kuyendesa ma video ako orawura wava

  • @amoschataika1284
    @amoschataika1284 Před 9 měsíci +2

    Ku DPP mwayamba zopusa kwambiri, udindo sitikakamila amakusankha ndi Mulungu.

  • @PeterChikwakwa-xk1kr
    @PeterChikwakwa-xk1kr Před 9 měsíci +1

    I can't understand

  • @user-nu1dj3jh7b
    @user-nu1dj3jh7b Před 9 měsíci

    Anamalomba diwoipa, pamozi ndi peter wawoyo. Kodi chilima kaliat ndi ena aja anachokelanji ku dpp ?

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Před 9 měsíci

    Onsewo ndi amcp so app mukumana

  • @user-nm6qh9wy4b
    @user-nm6qh9wy4b Před 9 měsíci

    Anyani inu

  • @luckysichone7721
    @luckysichone7721 Před 9 měsíci +1

    Anthu awa aphana sure 😂😂😂

  • @ibrahimmeemzy9754
    @ibrahimmeemzy9754 Před 9 měsíci

    Nankhumwa ndi a scam 😂😂😂😂😂

  • @user-ri5wf6jx9r
    @user-ri5wf6jx9r Před 9 měsíci

    Osangoyambisa chipani chanu bwanji zisilu inu

  • @lazarousnamakhwa6549
    @lazarousnamakhwa6549 Před 9 měsíci

    Pa anthu 71 abwelako ndi 23
    Zikumgooneka kuti ndiinubuzi

  • @esthergweje4038
    @esthergweje4038 Před 9 měsíci

    Bwanji anthunu muyambitse chipani chanu than kumabisalira kumbuyo kwa Chipani cha Dpp mukufuna kusokoneza chipanichi ifetu tikufuna Peter Munthalika osati izi mmene tikuvutikiramo

  • @IbrahimWezely-qd4vj
    @IbrahimWezely-qd4vj Před 9 měsíci

    Koma chomanamizira MCP ndichiyani kwenikweni??? Aaaaaa kungokhala kamtundu kokonda nkhani zopeka

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg Před 9 měsíci

    Choka dawusi machendiwako

  • @harrymgabu7239
    @harrymgabu7239 Před 9 měsíci

    Zitsilu zokha zokha zonse zimene zinali kumeneko mbuz za mcp zimenez daus ndi chitsilu

  • @user-yh4qx6xq7u
    @user-yh4qx6xq7u Před 9 měsíci

    Kkkkkkkkkkk koma y inu mukupanga ngt scpan cmoz aaaaa akuvotelen ndmbwyanu bx

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi Před 9 měsíci

    Mbuzi za anthu izi...agalu

  • @MaxwellMustafa-ec8fc
    @MaxwellMustafa-ec8fc Před 9 měsíci

    Amayi amenewa azatha katani believe me am giving her 4 months

  • @user-dt8nr1zx6e
    @user-dt8nr1zx6e Před 9 měsíci

    Nankhumwa ndi galu ,panyopako

  • @user-ie7ut3qb8v
    @user-ie7ut3qb8v Před 9 měsíci +1

    ufiti uwu

  • @felixmozile7513
    @felixmozile7513 Před 9 měsíci

    Ufiti ndiooopsadi,

  • @user-pe8dh1ks1y
    @user-pe8dh1ks1y Před 9 měsíci

    Njila ikachepa salinbilana zimafunika wina kupatuka ngt ndare ndi zabwino yambisani chipani chanu

  • @mabvutobanda9168
    @mabvutobanda9168 Před 9 měsíci +1

    Anthu adyela 🚮

  • @IbrahimWezely-qd4vj
    @IbrahimWezely-qd4vj Před 9 měsíci

    Kupanda kutere dpp ikatha 90 days atha kuithetsa

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Před 9 měsíci

    Mwatumidwa ndi Mcp anyapapi inu

  • @WilsonLimited-mv7it
    @WilsonLimited-mv7it Před 9 měsíci

    Agalu

  • @SavicoJastin-vj7pt
    @SavicoJastin-vj7pt Před 9 měsíci

    Mai uyu akapanga zausir azaona zomwe anaona Jen jefureyu basi pooooo9 dausi ndi was mcp ndith muzaziona ndithuuuuu yes mbon yakumwamba

  • @patricksamson4852
    @patricksamson4852 Před 9 měsíci

    Otsilu za anthu inu

  • @kadijachilwan967
    @kadijachilwan967 Před 9 měsíci

    Kwavuta ndale ndizachabechabe

  • @MadandoChannel
    @MadandoChannel Před 9 měsíci +4

    This is mcp kkkkkk

    • @kaitanokagalu
      @kaitanokagalu Před 9 měsíci

      Aaaaaaa MCP itiso tsopano? Kikkkkkkk Kodi DPP imathasonkukhalaso MCP chitani manyazi. Ndipo zikukhudzeni

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 Před 9 měsíci

      Mcp 2 iyiiii hummm

    • @kaitanokagalu
      @kaitanokagalu Před 9 měsíci

      @@eliffagondewe8214 palibepo MCP,tikuuzeni ndife ndipo muzinva, ku Opposition ndi mmene kumakhalira ndipo simunati. Kuteloko mwangoyamba apapa, nanga mukaluzaso ulendo uwu kikkkkkkkk hahahahahaha ambiri muthawa sure

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Před 9 měsíci

    Anthu akulu akulu opanda mzelu mudziti chipani cha mcp dpp yakutiko ubwino wake amalawi pano maso anayela simungawapusitse mpakana pemphelo hhhhhh

  • @Sandra-bz1tn
    @Sandra-bz1tn Před 9 měsíci

    Ukali wa usilu uwuuuu

  • @user-qi8xe7qh1e
    @user-qi8xe7qh1e Před 9 měsíci

    Kodi adausi anankhumwa ndi azanu simungayambitse chipani chanu before zisankho kuchitika mukufuna chani ku dpp tayambitsani chipani chanu ndipo anthu akusatani koma zoti muzingopa against sizikuthandizani ndipo simungawine chomwe mungachite tulukani dpp ndikuyamba chipani china kapena mu joine zipani zina komanso mudziwe kuti anthu akukuonani sangakulupilileni chimodzimodzi ngati saulosi chilima