Press Conference ya a peter munhtarika

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 09. 2024

Komentáře • 170

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg Před 9 měsíci +11

    Mutalika akuwoneka bwino kwambiri timangomunyoza akadali ndi nzeru

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula4937 Před 9 měsíci +8

    One of the best assuring speeches from the true servant leadership...mabodza a boma onse ali pa mbalambanda...boma lanji lodana ndi REFORMS...Apa a Malawi 🇲🇼 mwazimvera nokha utsogoleri wabwino after Bingu ndiye ndi APM basi...anatiphula mu cash gate apaso atha kutiombola mu 3 months only! Apapa ndayamba DPP 2024 camping 🏕 basi...

    • @maxwellntungama2003
      @maxwellntungama2003 Před 9 měsíci

      Politics is a profession where people venture in to sustain their families.

  • @user-dk6yc8pl2m
    @user-dk6yc8pl2m Před 9 měsíci +2

    Respected to you thanks for coming and to talk Tu your people thanks

  • @jafaranusa503
    @jafaranusa503 Před 9 měsíci +4

    I'm gonna fasting for you to win in 2025
    May almighty God continue to grant you knowledge ❤mr.
    President

  • @rashidsaid2232
    @rashidsaid2232 Před 9 měsíci

    Kukhala Chete sikupusa DPP is greatest democracy in Malawi God bless DR president Mthalika Mthalika

  • @rechealbracia-vk7np
    @rechealbracia-vk7np Před 9 měsíci +2

    Chakwela ndiwe bb ndipo kungonva kuti wafa tsiku la Christmas lisitha kuzakumbukira dzana la chilombo iwe! Ndizako Chilima munve kut anthu akupephera kut bola miyoyo yanu isakhalepo kt anthu 17 million apulumuke. God munve kulira kwathu😢😢

  • @IbrahimWezely-qd4vj
    @IbrahimWezely-qd4vj Před 9 měsíci +4

    Kabambeyu ndiyemwe ine ndimamuona kuti ndi solution ya malawi

  • @mabletungande349
    @mabletungande349 Před 9 měsíci

    Only chilima wud change our country.Chilima has my vote

  • @chippiephiri4505
    @chippiephiri4505 Před 9 měsíci +5

    I love this speech may the good Lord keep blessing Mr munthalika

  • @DamianoKapachika-ft1ye
    @DamianoKapachika-ft1ye Před 9 měsíci +3

    Ilove dpp

  • @user-xe7zi8pr2l
    @user-xe7zi8pr2l Před 9 měsíci +2

    Pls Mr APM may God bless you all the time we're waiting for you to rescue us in aur loved Malawi country agaruwa atikwana ife tanchona mumaiko ano ayeni because of those people who call them self tonse alliance the don't know anything about running the country wht the know ndikuba basi in fact ndika group kamamafiya akuba komaso kwawo ndikupha

  • @user-dv5dv8je9t
    @user-dv5dv8je9t Před 9 měsíci

    Madala team, zinthu zimayenda ndi nthawi, kukwera mtengo wa zinthu ndi nthawi basi, osamnamiza anthu

  • @user-vq9if2ep5q
    @user-vq9if2ep5q Před 9 měsíci

    Adad....Boma iro❤❤Ife tili pa Mbuyo panu.....osaopa ...more fr🔥🔥🔥

  • @noelmunthali3516
    @noelmunthali3516 Před 9 měsíci +1

    Bright Msaka you are very bright

  • @user-lt5ir6od2f
    @user-lt5ir6od2f Před 9 měsíci

    We are doomed, are these the choices we have. Who is less evil to the citizens. Come on dpp, you have a great Economist ,make him president for you party and let's get rid of the Nonsense not tonse , government

  • @user-xq5ju2uo9h
    @user-xq5ju2uo9h Před 9 měsíci +1

    Tabwezani matayi mwazimanga kwambiri mukulempela kuyankhula maka amsaka 😂😂😂😂😂😂

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 Před 9 měsíci +2

    That's my vote ❤❤❤❤Yes indeed APM can change this Government only for 90 days very true, but Chakwera even titampatsa 20 years nothing can change only ana ake ndi mkazi wake plus azipongozi ake.

  • @preciousmaononga
    @preciousmaononga Před 9 měsíci +1

    We need you back, sorry kusamva kwa2 pano tkulra nako

  • @madalitsosingle744
    @madalitsosingle744 Před 9 měsíci +1

    This is wat we call a leadership ❤

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před 9 měsíci +2

    Yes there is need for muthalika to come in and dialogue the chakwera

  • @Maggiemarket-wx5wu
    @Maggiemarket-wx5wu Před 9 měsíci

    May almighty God continue to protecting you and gives you more yrs tinkaona ngat mukutisocheresa koma pano taziwa kut munalidi munthu wolungama mwa chimwenecho mutikhululikire pa zomwe amalawi tinkalankhula pa ulamuliro
    Lero alimi ife akumudzi tikusowa chichita tilibe ndalama zogulira fertilizer sitingakwanise kugula thumba limodzi 110 0000 mpamene mu nthawi yanu inali 17 to 18
    Kulima ndiy tinalima koma mbewu tilibe ma ID athu Anatipasa koma mulibemo kalikonse anatinamiza kut muli mbeu komaso fertilizer komati bwana kukapangisa scan kupezeka kut ma ID aja ndiya Empty kotèro bwana ndi kugwada pamapazi anu bwana kutula nkhawa zathu monga ife akumudzi tikuvutika msima tikumadya ka wili pa week chifukwa chakapezedwe ka zakudya kakugisowa tikusowa mtengo wogwira pano bwana

  • @leviticusbonfancio
    @leviticusbonfancio Před 9 měsíci

    Kunena chilungamo we were blinded pomuchotsa Peter pa mpando zilibwino chifukwa zafikapa ndipa usandiuze naneso ndunvutika 😢, eeetu 2025 Dpp ikalowa m'boma ikonza ma mistake ake akale aja poti adali wochepa osati izizi.

  • @LameckMagona
    @LameckMagona Před 9 měsíci

    Go on dpp we need to change

  • @idrisssaladie5078
    @idrisssaladie5078 Před 9 měsíci +1

    zeru mumakhla nazo when you are out of government. mukalowa ubongo ose umathawiria kuchinena.

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Před 9 měsíci +2

    Dpp chipani chosamalira anthu osauka

  • @kelvinmalola-ui2kq
    @kelvinmalola-ui2kq Před 9 měsíci +3

    Dr Kabambe muli masomphenya😮

  • @user-kr1kg5hy9l
    @user-kr1kg5hy9l Před 9 měsíci

    Bravo my president.you deserve another chance

  • @suzgonyirongo3067
    @suzgonyirongo3067 Před 9 měsíci +2

    kodi mulibe office? Basi anthu akulu akulu peya peya kunyumba ya munthu?

  • @user-ko9ht2pj8d
    @user-ko9ht2pj8d Před 9 měsíci +1

    Munali muboma munalephera inu kozani kaye mavuto akuchipani then mutiuze solutio ya dziko

  • @user-no4km7yz8p
    @user-no4km7yz8p Před 9 měsíci +1

    That's great

  • @alinanegulumba8277
    @alinanegulumba8277 Před 9 měsíci +1

    I Like how blind we are as Malawians 😅😅😅😅 timayiwala mmmmmmmm

  • @user-yn9ky7gj7v
    @user-yn9ky7gj7v Před 9 měsíci

    Peter yemweyo 2025 bas mbanva zichoke chakwela ndi chilima chokani mwaulemu

  • @user-bq3xk1dg5y
    @user-bq3xk1dg5y Před 9 měsíci

    Sitikufunaso mzukwa uwu wa ku Thyolo udzatilamuleso.

  • @user-rv8vq3kl2z
    @user-rv8vq3kl2z Před 9 měsíci

    I love u fadah God may bless u ❤❤❤❤

  • @user-yn9ky7gj7v
    @user-yn9ky7gj7v Před 9 měsíci

    Achakwera tangosanzikani mwaulemu pitani kunyumba mukalele zizukulu asiyeni ena apitilize mutengane nda chilima chonde ndichokereni mwaulemu

  • @user-ko9ht2pj8d
    @user-ko9ht2pj8d Před 9 měsíci +1

    Amai awa 120000 feteleza shop itiyo a navicha kupanga rent minda musaiwale kwanu kulibe minda ili mmanja mwa ma estate tisanyozeke kuti mukupanga rent minda kwathu kuno uzani a Malawi chilungamo

  • @user-jz1fb5hj9g
    @user-jz1fb5hj9g Před 9 měsíci +1

    Aaa Aaa Aaa ndie chani

  • @macdonaldmunthali9895
    @macdonaldmunthali9895 Před 9 měsíci +1

    Yes Malawi is in bad shape but dpp is not a solution,too much tribalism

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Před 9 měsíci +1

    Pemphero la mtundu wanji ili? Ku malawi kulibe opposition.
    Boma lolephera nayonso Opposition mbola.
    Atolankhani athu mbola, amafunsa mafunso opusa ndi opanda phindu.
    Tinali ndi Eunice Chipangula pa dzana, ankadziwa kufunsa mafunso osati izizi, Kaya ma school ake anapita kuti. Mbola

  • @NedsonKanjira-qj2ig
    @NedsonKanjira-qj2ig Před 9 měsíci +1

    Zimayi walankhula kokwanila mfundo zenizeni

  • @kalimawandale7161
    @kalimawandale7161 Před 9 měsíci

    Did you accept defeat Mr APM?
    Kuvomeleza nkofunika kenaka mupepese kuti mutapasidwa mpata nanunso dziko munaliononga

  • @austinkadzuwa7273
    @austinkadzuwa7273 Před 8 měsíci

    IS THERE ANY CHANCE TO SPEAK WITH PRESIDENT PETER ? I HAVE SOTHIN G TO TELL HIM BUT IN PERSON .

  • @almonkamanga5990
    @almonkamanga5990 Před 9 měsíci

    Zazii, Mandala Team, yopanda ndi mtchere.

  • @austinkadzuwa7273
    @austinkadzuwa7273 Před 8 měsíci

    i wonder who typed the name of president wrongly without fixing it . that is very bad . anyway i wish president Peter can be a minister of finance not a country leader neither LAZALO .

  • @user-xq5ju2uo9h
    @user-xq5ju2uo9h Před 9 měsíci +1

    Chipani chot chalamulapo never my vote

  • @leonardwadi9148
    @leonardwadi9148 Před 9 měsíci +1

    Za ziii zokhazokha izi, mungokangana nokha nokha dyela,boma mukaliwinila kuti inuyo

    • @blandinabonaventure
      @blandinabonaventure Před 9 měsíci

      Mmmm Ona macoment inuyo zuyekuyenderani vuto kondwani ndi azake angofuna udindo not masomphenya

  • @user-bq3xk1dg5y
    @user-bq3xk1dg5y Před 9 měsíci

    Agogo mukukhalira nthawi yanzanu, kapumeni kumanda tioneko zina ife.

  • @user-ii8ux7pj7w
    @user-ii8ux7pj7w Před 9 měsíci

    Dad kutengeka kwathu pano tikulika# my vote 2025

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 Před 9 měsíci +2

    ❤❤❤❤

  • @Kayifa-ey8zm
    @Kayifa-ey8zm Před 9 měsíci

    Tiyeninazo please mutitandise ife kuno tikufa 🇲🇼😭😭😭

  • @user-pn2zx9ce5l
    @user-pn2zx9ce5l Před 9 měsíci +2

    Boma iloo❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉

  • @ChrisNtanga-do5hk
    @ChrisNtanga-do5hk Před 9 měsíci +1

    One love adad

  • @user-lh4nx4hw7x
    @user-lh4nx4hw7x Před 9 měsíci

    Inu zimenezi musatiwuze ife zimenezi mukamuwuze chakwela kuseliko ife palibe chomwe tingapange anthu okula mtima inu musangatithandize nonse ndi mbamva

  • @CharlesNambela
    @CharlesNambela Před 9 měsíci

    Zomvensa chisoni kwambili zipani 9 zoona kulephela kumanga chimodzi tikati dziko la Malawi mwina zithu tiona za chilendo koma mbuzi zeni zeni moni Steven maseya i hop uremember me I ❤ DPP
    A busa awa ngakuba Kwambili
    Pls tikupepha ma vote 2024 pls pls

  • @temwachikuse4747
    @temwachikuse4747 Před 9 měsíci +1

    5 advisors.... who do nothing. you had 5 of them.

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 Před 9 měsíci +2

    Vuto lomwe ine ndimskhumudwa ndi dpp ndilakut kosuts amazimvetsa chison kwambir kom akamalamulir amakhal anth amwano limandinyasa zina kt An adhat lelo mul kosotsa zakuvutan

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r Před 9 měsíci

    Zizii mbavaa inu dpp

  • @user-yn9ky7gj7v
    @user-yn9ky7gj7v Před 9 měsíci

    Eyetu nde udolowo nyumba izinkhala ndi office

  • @LuckyEmmie-ht1nk
    @LuckyEmmie-ht1nk Před 9 měsíci

    Wa nyau party ukumva bwanji ku dambweko 😊😊

  • @Yabwata
    @Yabwata Před 9 měsíci

    Everyone must vote for peter of course who else can Malawian vote for someone else except p.m , chakwela asazawone ndi vote imozi yomwe, pake wamubo lake iyaaa .😢 shameful on chakwela mufiti yomwe sakuva kulila kwa anthu

  • @PatrickStevenFernando
    @PatrickStevenFernando Před 9 měsíci

    Moto kuti buuu

  • @francistsutsu4811
    @francistsutsu4811 Před 9 měsíci +1

    koma zoona zimene akunena a Bright Msaka? bwanji osauza a Malawi chilungamo. kodi mmatengera a Malawi kuntoso bwanji? you are just taking Malawians for granted. kodi chifukwa choti a Malawi ambiri ndiosazindikira? basi kufuna kuwazunza a Malawi ndi mitima yanu yongofuna kuzikundikira chuma basi? enafe tatopa nazo zamabodza zanuzo.

  • @MwenyeCheNsoma-gb2yz
    @MwenyeCheNsoma-gb2yz Před 9 měsíci

    Worthy watching osati zina zija

  • @PlanzaWisiki-cv2fs
    @PlanzaWisiki-cv2fs Před 9 měsíci +1

    Boma iloo 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @bsowani5645
    @bsowani5645 Před 9 měsíci

    Chaponda ekhayu kuyankhula ndiye kumamuvutilapo pan'gono

  • @user-bq3xk1dg5y
    @user-bq3xk1dg5y Před 9 měsíci

    Sorry Mr APM,you are in the shadows of incompetence. Your government did nothing to the development of Malawi. Today is not tomorrow.

  • @trynessmsowoya4187
    @trynessmsowoya4187 Před 9 měsíci

    Me kumastand following

  • @user-sh2ef4gs9p
    @user-sh2ef4gs9p Před 9 měsíci +1

    Adad omwewo 2025

  • @usseintomasbacar8612
    @usseintomasbacar8612 Před 9 měsíci

    Koma Maseya pa prayer NDE mwaiphatu

  • @HumblenessTafari-sc8xs
    @HumblenessTafari-sc8xs Před 9 měsíci

    He just said that the. Depreciation is man made

  • @user-yn9ky7gj7v
    @user-yn9ky7gj7v Před 9 měsíci

    Nthawi ya peter timadya kanayi osat uyu wa nyawuyu angoyendayenda munthu nkulukulu

  • @bobkubwalo7504
    @bobkubwalo7504 Před 9 měsíci

    Massive prayer. Amen❤

  • @DickMdala-pn4pd
    @DickMdala-pn4pd Před 9 měsíci +1

    Ati kaya munalodzedwa😸

  • @stankaphinde7259
    @stankaphinde7259 Před 9 měsíci +1

    Adadi 🔥🔥🔥

  • @user-vq9if2ep5q
    @user-vq9if2ep5q Před 9 měsíci

    Koma Amayi mwarankhula bwino... Ambuye Akudalitseni

  • @memorygondwe1635
    @memorygondwe1635 Před 9 měsíci +1

    Adad 2025 boma❤

  • @user-hq6bk9uv4m
    @user-hq6bk9uv4m Před 9 měsíci

    Inu tinakuonani kale nanu munalephera kale musatipusisepo boma lanu mumaliso ndi mavuto aakulu kwambiri. Bola tiyeseko ena amu dpp momwemo Koma usati inu madala ayi

  • @user-ip9vh4tq3z
    @user-ip9vh4tq3z Před 9 měsíci

    Zopanda ntchito izi inuso musakhale ngati abwino zinakuvutani kale izi ndi zizindikiloza masiku otsiliza mukawelenge bible muzinamiza anthu osazindikila omweo

  • @aliedausi9733
    @aliedausi9733 Před 9 měsíci

    Was Dausi present?

  • @IbrahimWezely-qd4vj
    @IbrahimWezely-qd4vj Před 9 měsíci +1

    Munthu mukumuzuziranji akudwala??? Komatu inu a dpp munthuyu mulibe naye chifundo

  • @user-ig7dv8rp7r
    @user-ig7dv8rp7r Před 9 měsíci

    True leadership

  • @muyabasamson
    @muyabasamson Před 9 měsíci

    Ineso nikuwona sogolo mwakabambe nakhumwayo ayi nakhumwa zikumulephera kulidaopuzishoni muchenjele posankha ameneanga zasamale chipani cha dpp nakhumwa akhoza sithachipani mukhalemaso

  • @jamestembo6724
    @jamestembo6724 Před 9 měsíci +1

    Munapha achalubino inu adpp

  • @goodvisionmedia2023
    @goodvisionmedia2023 Před 9 měsíci

    ❤❤❤❤❤❤ APM

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w Před 9 měsíci

    Apm ndi machine including their executive 💪

    • @user-ko9ht2pj8d
      @user-ko9ht2pj8d Před 9 měsíci

      Machine ogona mpaka tpin izigwilitsidwa ntchito ndi bodyguard memories still fresh

    • @user-ko9ht2pj8d
      @user-ko9ht2pj8d Před 9 měsíci

      Olembedwa ntchito mosaoneka bwino apose aku mombera University?

  • @user-vx5st6my8i
    @user-vx5st6my8i Před 9 měsíci

    Boma ili latipha koma adad adatiuza koma kusamba anthufe

  • @IbrahimWezely-qd4vj
    @IbrahimWezely-qd4vj Před 9 měsíci +1

    Ndiiiithu munthuyu mukadamuvera chisoni osabweretsa kabambe or nankhumwa adzalankhule bwanji???? Mukumulakwira mutharikayu

    • @Chiso2019
      @Chiso2019 Před 9 měsíci

      Akuluakulu ndi dambo mozimila moto a bro....even judges put on white hats meaning to say there's is wisdom in grey hairs

  • @user-pn7ek7wb7n
    @user-pn7ek7wb7n Před 9 měsíci

    Mukunamiza ana anu makadeti

  • @user-it7of3ns8z
    @user-it7of3ns8z Před 9 měsíci

    Zidakukanikani kale chipani cha family ichi munadya kunakwana palibe chachilendo pa zomwe odalawa ayankhura ukamakalamba umakhala ndi makani...siyilani ena achiteko mbali Yao za inu zinatikwana..

  • @MaxwellMustafa-ec8fc
    @MaxwellMustafa-ec8fc Před 9 měsíci

    I thought is my phone me too no sound, dpp is my trust.

  • @stanleykaludzu-bm4pm
    @stanleykaludzu-bm4pm Před 9 měsíci +1

    APM mbambande

  • @madalitsoyobex1642
    @madalitsoyobex1642 Před 9 měsíci

    True why devaluation comes when people are expected to buy agriculture inputs why why chakwera knows nothing

    • @user-ko9ht2pj8d
      @user-ko9ht2pj8d Před 9 měsíci

      Look at statistics from 90s kwacha imapanga gain only time ya tobacco tikamafika these months get affected and mind you tobacco selling seasons imafika November koma pano by August msika watha where do you expect it to gain?

    • @user-ko9ht2pj8d
      @user-ko9ht2pj8d Před 9 měsíci

      That's why Kabambe you had the audacity to grant your colleague loan ya 187 years eti ? Mumaononga chuma ndinudi you have come out in open kuti muli mu boma you were the ones enjoying

    • @tisuhmakhwah7085
      @tisuhmakhwah7085 Před 9 měsíci

      Cholinga musagule fertilizer njala ipitilire

  • @regnanosa8147
    @regnanosa8147 Před 9 měsíci

    We love u papa

  • @user-jd6do2wh6g
    @user-jd6do2wh6g Před 9 měsíci

    NOSENS AKUBA NDIA SANKHO INU

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg Před 9 měsíci +2

    Mcp nde panja penipeni mumalo moti akanaliphula ziko pamoto nde iwomso kuliteleka ndi nkhuni zikulu zikulu

  • @lloydmazengela
    @lloydmazengela Před 9 měsíci

    Zikuoneka ngati a DPP sakuziwa chomwe akulankhula akalankhula za kusowa kwa mankhwala zipatala ulamuliro wawo Ku chipatala sikumapezeka mankhwala,,, komaso ndi anthu ozikonda kwambiri,, ongoona zao zokha osati za antnu,,, lero muli busy kunamizatso amalawi ndizambiri zomwe munakanika

  • @AugstineManda-pl1dz
    @AugstineManda-pl1dz Před 9 měsíci

    You malawian why saying 2025 it's 5 years that's 2024 voting constitution ya dziko la malawi imatelo osati 6 years malawi wake uti?

  • @Vado507
    @Vado507 Před 9 měsíci +1

    Chokani apa

  • @user-lc1yv6kx9g
    @user-lc1yv6kx9g Před 9 měsíci

    Kkkkkkkkkk koma ndizoonadi chitsotso chimaoneka mchamzakodi tiyenazoni

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 9 měsíci +1

    100%❤