NGC meeting

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 09. 2024

Komentáře • 163

  • @puremwSDAsongs
    @puremwSDAsongs Před 9 měsíci +2

    Mukuona ngati Peter muthalika angakonze mavuto a dziko lino. Izi zinayenera zichitike basi tili kumapeto adziko. Konzani moyo wanu lapani machimo, zonse mukuzionazi zikungosonyeza kuti wayandikila Yesu kubweranso

  • @user-nu7ng3un4t
    @user-nu7ng3un4t Před 9 měsíci +5

    Am happy for Malawi. We need strong parties to compete inorder for the best to emerge at polls not having only one strong party in a nation of 20 million people it's unhealthy. Bravo DPP.

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 Před 9 měsíci +4

    Am so proud ❤❤❤mwaitana onse koma...amene sanamvewo atengana kosayamba chake chipani monga gerezedar ndi mamuna wake nakhumwa andi owasatira awo budzi zonkha ...zonkha mene zikubebera izi zadongosolo azitulusa onkha namabodza pamenepo phati g

  • @user-nb7xr9vb4t
    @user-nb7xr9vb4t Před 9 měsíci +4

    Watching from south Africa Pretoria and I am very excited for this NGC MEETING ❤❤❤

  • @user-qv4ko6ps4j
    @user-qv4ko6ps4j Před 9 měsíci +3

    Am very glad to see you all attending a great NGC we have been waiting for a grace period of time and congratulations to you all in that wonderful room may God do wonderful things on behalf of your NGC services in order to come up with better results for the betterment of the candidates who will bring back Malawi's fruits to be fruitful to all Malawians,,,,,,,all the best guys.

  • @user-ee6be5kl5o
    @user-ee6be5kl5o Před 9 měsíci +2

    Im very happy indeed we need adai to rescue Malawian facing more challenges in this country pple suffering now than before more fire

  • @joemlelemba6572
    @joemlelemba6572 Před 9 měsíci +7

    I can't wait to see you back in the government boss , you deserve to be the boss

  • @user-xh1ve5ym3l
    @user-xh1ve5ym3l Před 9 měsíci +1

    Ine ndwakondwa kwambiri, mtima wanga wasangalala. Kuno ku Dedza anthu akuvutika kwambiri. Akugona ndinjala , ngakhale gaga akusowa , koma zimenezi kunalibe. Lero zakhala bwino anthu awone kusintha . God bless Malawi.

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll Před 9 měsíci +1

    Bravo to you newly appointed Dr clement Mwale indeed you know your description, you plead for these prodigal sons and daughters, you know that politics is game of numbers, this is not the time to loose anyone, when you are approaching convention, you need every member on endorsement, welcome nsonda,

  • @Yusufu-Daudi
    @Yusufu-Daudi Před 9 měsíci +3

    Iyi nde yakunganatu 💪💪💪💪

  • @franciscoduartie5762
    @franciscoduartie5762 Před 9 měsíci +3

    Bravo my believed DPP this is the way to go,2025 tikuyiphula infact let me make it clear that nnali mmodzi Ochoka ndi chilima koma pano nnabwerera and I vow not to leave DPP again😂😂😂❤❤

  • @leonardjika2100
    @leonardjika2100 Před 8 měsíci

    AM GOING TO GOVERN OUR NATION THE DAYS OF POLITICIANS ARE NUMBERED SO HELP ME GOD

  • @kenstonszulu4100
    @kenstonszulu4100 Před 9 měsíci +2

    Very colourful and fantastic. God Bless the DPP

  • @user-zc1mg5lj7p
    @user-zc1mg5lj7p Před 9 měsíci +2

    Adad omwewo sizinazo ai yanga voti pa adad from Maputo Mozambique

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 Před 9 měsíci +4

    My happiness has been restored 🔥🔥🔥🔥

  • @Malawian-q5f
    @Malawian-q5f Před 9 měsíci +1

    What a relief , finally my beloved party showing a sign of life. Congratulations

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 Před 9 měsíci +2

    The Father has Spoken and we love you So muchite Dad.

  • @mkhulukinyata5198
    @mkhulukinyata5198 Před 9 měsíci +3

    This is what we have been wairing for", I like the way how He's Excellency shouted Mr Nsonda , Yes I agreed with He's Excellency for what ever he has said concerning Nsonda ..Mr Nsonda he is untrustworthy man n' he is hypocrisy.
    Much love to my Country watching from SOUTH CENTRAL L.A USA

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Před 9 měsíci +3

    Imeneyo ndie NGC timadikila ifeyo,osati ya MCP ija ai!!!achina Dausi,,Nakhumwa zitsilu zawanthu

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 9 měsíci +2

    Muwasamale anthira kuwiri alimommowo, msonda and his friends, they're not for DPP party, they belong to mcp cruel party

  • @emmanuelsambo1158
    @emmanuelsambo1158 Před 9 měsíci +2

    Respect leaders, that's very true. All the best DPP NGC meeting

  • @DICKSY-kz1qd
    @DICKSY-kz1qd Před 9 měsíci +2

    Koma chipililo penganjira ndi wa Zeru

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g Před 9 měsíci +2

    Adandi kuwonda mwatha mukalowa boma mumadya bwino kwambiri kwabela amalawi mukufuna munenepeso sizitheka mungoyamba business yasomba kunyanjako bas akolo 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @leveltrapper4322
    @leveltrapper4322 Před 9 měsíci +3

    Am happy that chisare is out

  • @georgejamali
    @georgejamali Před 9 měsíci +2

    Congratulations you guys appreciate you for that fantastic NGC meeting ❤❤❤

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 Před 9 měsíci +4

    Nkhope zopanda mantha

  • @leveltrapper4322
    @leveltrapper4322 Před 9 měsíci +3

    Adadi is lukng gud

  • @user-cp4gt4pw7j
    @user-cp4gt4pw7j Před 9 měsíci +2

    I am very very happy to the strong meeting l never see in my life

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v Před 9 měsíci +4

    Peter is mature enough, about Ken Msonda and Nankhumwa shame

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw Před 9 měsíci +3

    Ken Sonda ukutaniko kumeneko kape iweyo kwambiri

  • @user-jj7oz4lo9t
    @user-jj7oz4lo9t Před 9 měsíci +2

    Adadi moto kuti buuu🎉🎉

  • @lyiemax
    @lyiemax Před 9 měsíci +1

    Proud of you guys, 2025 DPP Bomaaaaa!!!!!

  • @macdonaldchifupa7458
    @macdonaldchifupa7458 Před 9 měsíci +2

    Ine ndamva kukoma kwambili ndi msonkhano umeneu ❤

  • @johnniemvula3479
    @johnniemvula3479 Před 9 měsíci +2

    Thanks APM that's the way to go

  • @George-zd5le
    @George-zd5le Před 9 měsíci +1

    I'm from Northern living here in South Africa, to my side I love Dpp and I want to see the part untied

  • @joemlelemba6572
    @joemlelemba6572 Před 9 měsíci +2

    Nankhumwa galu wa chebe chabe usabvutike

  • @petermasenti2084
    @petermasenti2084 Před 9 měsíci +4

    Watching from south africa imeneyo ndiye dpp osati za a Nakhumwa ndi azawo anja a mcp ndipo sakufunika ku dpp achoke basi muthu kukhala leader of opposition Koma kumakanika kutsutsa ku parliament he is useless

  • @bellemagoldenwalk7767
    @bellemagoldenwalk7767 Před 8 měsíci

    bomaa iloo adady woyeeeeee dpp woyeeeeee ❤❤❤

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 9 měsíci +2

    Kha ngc siimeneyo aaaaaa🥳🥳🥳🥳🥳

  • @hopeskafumbi2246
    @hopeskafumbi2246 Před 9 měsíci +2

    I'm very happy with this NGC meeting osati zosokoneza zija

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před 9 měsíci +3

    Iam very very happy with this meeting .....we are behind apm

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 Před 9 měsíci +1

    NGC koma iyi osati ijayi ya zifwamba yachitika last week ya anyamata Malawi Young Pioneer ija!!!??

  • @user-zq5ob7xz4l
    @user-zq5ob7xz4l Před 9 měsíci +3

    Very happy

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 9 měsíci +3

    Ayambaditu kale kunjenjemela kkkkkkkkkkk

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Před 9 měsíci +2

    Wow!!!45 Family member's DPP..thats very good numbers..God is Good

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Před 9 měsíci +3

    Apm 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @patiencetebulo
    @patiencetebulo Před 9 měsíci +2

    Am so proud of you guys keep it up

  • @user-xn5lo3wb4z
    @user-xn5lo3wb4z Před 9 měsíci +1

    A dad ndi machine 2025 awina kle

  • @TwaibuZilale
    @TwaibuZilale Před 9 měsíci +2

    Guys Msonda Akita akutaniko kumeneko yudasi

  • @user-hd6xc5ud2b
    @user-hd6xc5ud2b Před 9 měsíci

    Timakunyadiraa kwambiri Mr apre

  • @user-zj1xx1ic2m
    @user-zj1xx1ic2m Před 9 měsíci

    Aliyense Adad, Adad, Adad,,,,,our father APM 100%❤❤❤❤ 2025

  • @user-gv2pf4ju9r
    @user-gv2pf4ju9r Před 9 měsíci

    Amalawi ataphunzira kuti nsanje simapindula chiyembekezo chao chili mwa inu adad koma osamuiwala atupere muluzi ndi mnyamata odekha

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Před 9 měsíci +3

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤A P M 🔥

  • @patiencetebulo
    @patiencetebulo Před 9 měsíci +1

    Watching from South Africa

  • @leveltrapper4322
    @leveltrapper4322 Před 9 měsíci +1

    Koma mbali ya ana ija akuva bwanjii

  • @user-ng9xy3bs3v
    @user-ng9xy3bs3v Před 9 měsíci +1

    Nice

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Před 9 měsíci +2

    #viva DPP #viva....viva ADAD....Viva DPP Family..

  • @user-xe9hp2tc4t
    @user-xe9hp2tc4t Před 9 měsíci +2

    This is most loved meeting

  • @christopherstosherchimbuwi676
    @christopherstosherchimbuwi676 Před 9 měsíci +1

    Live from Durban South Africa ❤❤❤❤

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Před 9 měsíci

    I'm glad to see DPP comes together again adady woyeeeeee ❤❤❤❤❤

  • @user-ti2ct8ts8d
    @user-ti2ct8ts8d Před 9 měsíci +1

    Welcome back DPP🔥🔥🔥🔥

  • @MisterBanda-pl8ct
    @MisterBanda-pl8ct Před 9 měsíci +2

    More fire Dpp

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Před 9 měsíci

    Adadi mumusamale mfiti nsondayo ndigalu kwambiri

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg Před 9 měsíci +3

    ❤❤❤❤

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w Před 9 měsíci +2

    Tikudikira inu adad

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Před 9 měsíci

    Happy to hear this

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 Před 9 měsíci

    Nice for Malawi 🇲🇼..........long live AMP

  • @user-pw4hf5sz4x
    @user-pw4hf5sz4x Před 9 měsíci +2

    Zoona adad omwewo

  • @user-ii9ch7oz8n
    @user-ii9ch7oz8n Před 8 měsíci

    Paline chazeru apa mumalo mopanga chimozi kutukula Malawi mulibbusy zaukape panyapano😊

  • @user-fy1td2hf8j
    @user-fy1td2hf8j Před 9 měsíci

    Nankhumwa & grezerder shame, anthu osafunila dziko zabwino manyazi bwa?

  • @user-ku5fs6lv4n
    @user-ku5fs6lv4n Před 9 měsíci

    That's what we were expecting ❤

  • @elsonthangwi8010
    @elsonthangwi8010 Před 9 měsíci +1

    Watching live from Paramaribo Suriname

  • @ibrahimjackson-cg6tc
    @ibrahimjackson-cg6tc Před 9 měsíci +3

    🙏🙏🙏

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před 9 měsíci +2

    Chisale pa ntchito yake

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 9 měsíci +2

    Mitu ya dpp nde imenei

  • @juniornkhata2518
    @juniornkhata2518 Před 9 měsíci +2

    Heavyweights All de best.

    • @JoshuaMbale
      @JoshuaMbale Před 9 měsíci

      Chipani chongodzadza ndi nyambaro.....nanga achina big joe akutaniko kumeneko

  • @user-oo5bx1rl3j
    @user-oo5bx1rl3j Před 9 měsíci +1

    Ineyo monga mr Raphael Katimba ndikungofuna kuwathokoza a president a chipani cha DPP ndipo zaonetselatu kuti a Peter Mutharika democracy yathu kuno ku Malawi amailemekezadi . and why i am saying this? Choyamba amudzudzula Nsonda poyela kuti iyeyu akakhala kumbali amawanyoza kwambili komanso Nsonda simembala wa DPP koma iyeyu anachita kubwela kuchokela ku chipani cha PP ndiye ayankhunso kuti Nsonda ali ndi ufulu kubwelera ku chipani chawo komanso ayankhula kuti iwowa monga president wa chipani sakukwiila wina aliyense ai. Komanso ayankhula kuti anthu onse amene amatengela chipanichi ku Court adziwe kuti aonongetsa ma million ambili ku chipanichi. ndanena dziko kuti mafiya ndichifukwa chake akuonda ndi mutu omwe. DPP oyeeee 2025 ikulowanso boma

  • @user-ch4kb9ku7f
    @user-ch4kb9ku7f Před 8 měsíci

    Best ever ❤❤❤❤❤

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 Před 9 měsíci +1

    But better kumayankhula zomanga kaya...choncho mugwirizana?

  • @MarkManyowa
    @MarkManyowa Před 9 měsíci +1

    I love you Guys Viva DPP

  • @AronLuka-ue5hl
    @AronLuka-ue5hl Před 9 měsíci +1

    APM ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-ki9ui2wn3w
    @user-ki9ui2wn3w Před 9 měsíci +1

    A.P.M more fire

  • @chitsanzomafupa4877
    @chitsanzomafupa4877 Před 9 měsíci +2

    Chi combination cha ma....... 😂

  • @MbendelaDyson-ep6cx
    @MbendelaDyson-ep6cx Před 9 měsíci +1

    This is what we call corrum

  • @user-tp6nw4ym9x
    @user-tp6nw4ym9x Před 9 měsíci

    Boma ilo ana achepa🤣🤣🤣

  • @haroon-qp8mp
    @haroon-qp8mp Před 9 měsíci +2

    ❤dpp

  • @user-qq9oj6si2g
    @user-qq9oj6si2g Před 9 měsíci +2

    tikudikira inuyo

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před 9 měsíci

    Tsongolo la malawi 🇲🇼🎉

  • @juniortsegula3847
    @juniortsegula3847 Před 9 měsíci

    Viva Dpp viva apm

  • @Chexum99
    @Chexum99 Před 9 měsíci

    I wish DPP gave the best Opposition than the nonsense have right now Otherwise Strong opposition results into good governance. Stop The nonsense disagreements

  • @user-vc4kz3yk8p
    @user-vc4kz3yk8p Před 9 měsíci

    Mwangisowa chonena Inu zinakusangalatsani ndizijazi zadzana

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula4937 Před 9 měsíci

    Make sure united you stand, no camp has any significant chances of success

  • @user-hs5xv6bk2f
    @user-hs5xv6bk2f Před 9 měsíci

    Timadikilila mau Ngati amenewa apita Kodi mumachedwa Kuti ndimauwa nsonda ndiwoipa kuipa ndinkhope yomwe Mutu Ngati mbeza yowezela achule

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 Před 9 měsíci +1

    Live from Sandton Gauteng

  • @Yahiya-wm8nd
    @Yahiya-wm8nd Před 9 měsíci

    Koma nsonda ndi akamuna eeeeeee ayi ndithu

  • @user-qc1el4km5l
    @user-qc1el4km5l Před 9 měsíci

    More fire❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-yz1fk1dx1m
    @user-yz1fk1dx1m Před 9 měsíci

    Zosagalatsa

  • @PeterPhiri-nd6op
    @PeterPhiri-nd6op Před 9 měsíci +1

    A peter hoeeeeee❤❤🎉

  • @francisvisage2705
    @francisvisage2705 Před 9 měsíci

    I'm hearing only Tumbuka names here

  • @MuhammadSamson-yz1kl
    @MuhammadSamson-yz1kl Před 9 měsíci

    Adad anafe timaikonda DPP chifukwa chainuyo adad osati anakhumwa magulu wachabe chabe