KU HOT CURRENT KWATENTHERATU

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 6. 07. 2024

Komentáře • 45

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 8 dny +4

    Hee bwanji pamaliro achilima munalephela kusegula mlomo chochi bwanji simunena kuti chakwera ali ndi dyela loipa mpaka kupha munthu sure chifukwa cha 5years😢😢😢 machende ake

  • @user-lb6ek3ee6d
    @user-lb6ek3ee6d Před 8 dny +2

    Malawi ndi chitsazo chabwino cha kusauka koma zikukhala zovetsa choni kwambiri mpaka pano ma President adakalibelabe a Malawi ndi President yekhayo yemwe amandisangalatsa Professor Dingu wa Muthalika zimu wawo ukuse mu ntendere adasitha zithu kwambiri osati izi tikuziona panozi manyaka enieni the must go out stupid Government

  • @stevenchirwa5028
    @stevenchirwa5028 Před 8 dny +3

    Don't just talk we need action to change Malawi 🇲🇼

  • @yusufbakali
    @yusufbakali Před 8 dny +3

    Nduna zaboma zosezakuba zimangidwe it only one way katangale akhoza kuta akamangidwa no belo ndende basi akagwire

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Před 8 dny +2

    🙏🙏🙏🙏🙏🙏Anyamata lero muli bwino kwambili 🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @JustinChiwale
    @JustinChiwale Před 8 dny +1

    Khoswe akakhala pakhate sapheka Malawi we can't fight against corruption

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 8 dny +1

    Kkkkkk anyamata inu leroli ndakupatsani 100 pa 100 ❤❤❤ guys iyiyi ndiye hot current

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl Před 8 dny +1

    Talk guys we are together but don't eat baz from chakwera

  • @ahmedmsume1489
    @ahmedmsume1489 Před 8 dny

    Akuonesana zikwanje inu lero mwatasa 😂😂😂😂

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba Před 8 dny

    Vuto ndale zanthu zimapatsa mphanvu president.koma democracy parliament ndiyomwe imakhala ndi mphanvu yolemba ACB director azipanganso report Ku parliament basi

  • @g_forcemusician4242
    @g_forcemusician4242 Před 8 dny +2

    2025 we choose wisely

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 8 dny +1

    Abida mia wapelekera bwino kwachakwera😂tiona dzinthu yakumbuyo😂😂

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 8 dny +2

    Kuti katangale kuti athe muphe chakwera ndi chimbava choipa kuchokela kumpingo that's why he kill chilima

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 Před 8 dny +1

    Lelo mwayakhula zokomela athu osaukano. Osati zachamba zanu zinja.

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Před 8 dny +3

    We need to change this leadership

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Před 8 dny

    Ajona mwamvatu malango anga kkk cz ndeumabowa bolako lero ❤

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Před 7 dny

    Kumalawi tili ndivuto katangale sangathe. Chifukwa ndi culture. Katangale ngati mukufuna kuti athe choyamba president akhale oopa Mulungu komaso akhale osanama chachiwiri azikhala ndinthawi yotendera ma office mwazizuzi osawawuza anthu ogwira ntchito. Chachitatu a police a traffic army ikhale yachilungamo ndipo asavere boma pankhani za katangale. Simungathane ndikatamgale pamene oteteza ziko ndi amene akuchita katangale ndiye mukugani anthu angasiye katangale

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Před 7 dny

    Nkhani ya police kuti alibe uniform sapata zili bwino ngati akuvutika choncho chifukwa apolice wo ndi amene akumanga anthu akamazuzula boma so azivutika motero

  • @Moses51
    @Moses51 Před 8 dny

    Chakwela ndigalu kwabasi

  • @SaukaniMbiliyawanda-ur7zb

    Amene sanachimweko ayambe kumugenda miyala

  • @TarPoor-ye9jx
    @TarPoor-ye9jx Před 6 dny

    Lero ndaziwa kut anthu chilungamo akuchziwa koma mantha mcp ndi chakwera anthu atopa nawo kkkk 😂😂anthu amaba koma tonse yalepera pazonse kuba kuli pa high too much

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Před 8 dny

    we shall be singing like this for how long

  • @StevenMjMbama
    @StevenMjMbama Před 8 dny

    Guys big up kwinako muzitchulako mayina aaaanthu amene akumapanga katangale

  • @AustinNkhula-j6y
    @AustinNkhula-j6y Před 8 dny

    Ttv awunikileni anthu aziwe zenizeni tatopa ife ndianyapapiwa

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před 8 dny

    Chakwela akufunika kuti achoke ndimuthu wakuba komaso dzikoli linalo bwino koma chakwela waononga kwambili zedi koma 2025 aona nyekhwe

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 Před 8 dny

    Bon kalindo anayakhula kt aku prison akudandaula kt iwo palibe amapita muziwaganizila km mukati wamisala

  • @Austinyonah
    @Austinyonah Před 8 dny

    Kuyankhula kwabwino

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py Před 8 dny

    Ambuye mulungu wanga mudapereka mwana wanu modzi yekha yemweyo kufera ifeyo ochimwa kudzuzika yesu chifukwa chaife , kodi ngat mudalora mwana wanu modzi yekha kufera ife ,simungalore yehova wina osakhala mwana wanu kuti angofa yekha kutulo osadwara ai kuti afere ifeyo amalawi tatopa naye ndiy skhale Chakwerayu ambuye ndimvereni mbuye wanga Chakwerayi atifere ife chifukwa wanyañya tikumvutika musadzuze ndimatenda ai akangogona apitilirekonko kuti tipume mbuye wanga ndimvereni yehova chskwerat akutidxuza musakhare chete yehova akhoza kumayesa ngat mulibe phamvu ngat safera kutola koma afeeee chakwera kuti nduna zake ziziwe kuti inuyo mdinu owopsa yehova

  • @HarryMsudzula
    @HarryMsudzula Před 8 dny

    Sinanga ntchito zina akanatha kugwira aprison like kugadira mayeso ameneb anaipereka ku mdf omwe sizimayenera kutero malinga ndi nature yantchito yawo

  • @Moses51
    @Moses51 Před 8 dny

    Aphana 🤣🤣🤣🤣

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před 8 dny

    Aona nyekhwe 2025

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Před 8 dny

    Lelo maimatu pachilungamotu kunenachoona chomwe ngakhale ife akumudzi tikuziona masomu boma ili linangolowelamo Kuba basi, chifukwa chilima anangomunamizila kuti apeze mphata Obama bwino, after kuona kuti bodza anapangila chilima kunamizila Kuba, anaona kuti kubako otsogolela anali chakwela chifukwa anatetsa mulandu cholinga amuphe chifukwa anadziwa kuti chilima amadziwa zonse. Chakwela chakwela iweyo mulungu azikupangila za bwino

  • @KanjoIsaac-u1w
    @KanjoIsaac-u1w Před 8 dny

    Kkkkkkkkkkkk

  • @DalitsoulNchengah
    @DalitsoulNchengah Před 8 dny

    Ulemu wanu

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Před 8 dny

    Anthu ena anagontha ku makhutu chifukwa cha matemberero

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Před 8 dny +1

    Kikikikiki

  • @MusaManati-ho4zf
    @MusaManati-ho4zf Před 8 dny

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @SandramKambalame
    @SandramKambalame Před 8 dny

    Boma ilili ili ndi manyaka

  • @augustinechibbalazi8897

    In Malawi we consider corruption as a problem.It is not a problem but the result of something.Therefore,to end corruption in Malawi we must list down main causes of corruption and get rid of them.

  • @giftmwango3214
    @giftmwango3214 Před 7 dny

    You don't know what you are talking about

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před 8 dny

    Chakwela akufunika kuti achoke ndimuthu wakuba komaso dzikoli linalo bwino koma chakwela waononga kwambili zedi koma 2025 aona nyekhwe

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Před 8 dny

    Chakwela akufunika kuti achoke ndimuthu wakuba komaso dzikoli linalo bwino koma chakwela waononga kwambili zedi koma 2025 aona nyekhwe