Chisankho Sichibeledwa Tsiku Lovota Imakhala Process - Bon Kalindo

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 26. 06. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo asks opposition parties to be vigilant ahead of the 2025 Elections. He also asks UTM members to sit down and have a soul searching meeting to reflect on where they are coming from and where they would like to go.
    Ku Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo apempha zipani zotsutsa kuti zikhale tcheru pokonzekera zisankho za 2025. Apemphanso mamembala a UTM kuti akhale pansi nidkuganizira za komwe akuchokera ndi komwe akufuna kupita.
    #malawi

Komentáře • 7

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi Před 16 dny +2

    Kug'alulatu kumeneko ❤

  • @EnerstAcidAufi-to3bg
    @EnerstAcidAufi-to3bg Před 15 dny

    critical thinking

  • @lingsonmitunda293
    @lingsonmitunda293 Před 16 dny

    Ndipo kupanda SAULOS CHILIMA, sakanailawa state house a Chakwera awa.

  • @user-uk6xv3xe4p
    @user-uk6xv3xe4p Před 17 dny +1

    Big za azanu aja nde sumukamba avice pulesidenti

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 17 dny

    Galu yadpp yisiyeni yiziuwauwa utp sali nngati kalindo ndi anthu anzelu sangabwelele mmbuyo ngati chisilucho ayi munlungu atipatsa wina tisaopa tisabweiele mmbuyo akalindo utm msayikhuze tikadalila marilo ndiye akalindo mkukhala ngati mwasangalala kumwalila kwachilima simkulila ayi