UTM YATHETSA MGWILIZANO LIVE LIVE MOTI ZOMWE AYANKHULA NDI IZI

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 11. 07. 2024

Komentáře • 453

  • @ChrissMike-ws9lf
    @ChrissMike-ws9lf Před 23 dny +91

    Ma followers a UTM tilipo?? Ngat tilipo manja mmwamba 🙋‍♂️

  • @kettiemkweu4528
    @kettiemkweu4528 Před 23 dny +10

    My UTM fellow let’s gather here. Ndikuti 2025 I will be in Malawi all the way from America just to vote for my UTM
    UTM you got my Vote ❤

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Před 23 dny +35

    Great move UTM family. Koma going forward tiyeni tidzipanga ma decision mofulumira, kunjaku nkwa mvula.

  • @LeganNyirenda
    @LeganNyirenda Před 23 dny +11

    Applause ❤mama for standing film against this alliance.

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em Před 23 dny +25

    Tiri pa mbuyo panu mama osaopa osatopa osafooka, ine sindinavoteko koma next year ndikavota, viva UTM viva mai kaliyati viva SKC

    • @user-rx1dj7kg8k
      @user-rx1dj7kg8k Před 23 dny +2

      Inenso ndukavota🎉

    • @RachelDongolosi
      @RachelDongolosi Před 23 dny +1

      Amen 🙏

    • @user-uf4hp6lu8t
      @user-uf4hp6lu8t Před 23 dny

      Am following you ❤❤

    • @paulmgombebanda-mr19sate
      @paulmgombebanda-mr19sate Před 22 dny

      Well done

    • @user-tk6qh9zs7h
      @user-tk6qh9zs7h Před 22 dny

      @@MariamJohn-dg4em palitu kusiyana pakati pa UTM ndi Malemu SKC.
      CHILIMA anapeza mavote okwana 1 million pomwe UTM ngati Chipani inapeza Aphungu Anayi okha basi.Ngakhale Kaliati anakanidwa kwawo pa Udindo wa u MP kamba koimira utm ndiye kumachangamuka pochita zinthu.
      Fame ya Malemu SKC si fame ya UTM as a political party.

  • @user-ri8em6my2e
    @user-ri8em6my2e Před 23 dny +15

    Boom !🔥🔥inuyo mwabwera ngati coming 💃💃

  • @fahadwalipeya8656
    @fahadwalipeya8656 Před 23 dny +5

    Well done ife ndale zanu zopusazo zophanazo ayi UTM in our hearts forever 💕💕💯💪

  • @petermark6591
    @petermark6591 Před 23 dny +3

    Ifeyo monga a UTM tasangalala kwambiri coz chotuluka mu tonse Kuti mzimu wa president athu achilima ukhale osangalala, glory to Jesus.

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Před 23 dny +6

    Great news,I am so happy you have made an excellent decision

  • @user-sm8gx4vf1v
    @user-sm8gx4vf1v Před 23 dny +11

    Amen and Amen kumwamba kulemekeze

  • @EmmanuelNkosi-ts8bn
    @EmmanuelNkosi-ts8bn Před 22 dny +1

    Politics will never build Malawi its all about tilowe Boma tikatape basi, listen to Mkasa song very carefully

  • @burtonjere-wn3qu
    @burtonjere-wn3qu Před 23 dny +3

    🔥 🔥 .. well done .. Bravo UTM !! U have my vote

  • @louismagongwa
    @louismagongwa Před 23 dny +8

    mwaitha akwenei mukakamila za tonse allince mutha nose psiti

  • @isaacchagwa2917
    @isaacchagwa2917 Před 23 dny +5

    Hono. kaliat you lead this political party,for its survival

  • @EvaDzimkambani
    @EvaDzimkambani Před 23 dny +11

    Well done UTM tili pambuyo panupo

  • @TressLuka
    @TressLuka Před 23 dny +7

    Khaaaa UTM kuti buuuu. Wafwaaaa Chakweraaaa !

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 23 dny +3

    Well done akweni may the almighty God continue to protect you❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @constancemkandawire7378
    @constancemkandawire7378 Před 23 dny +1

    Very good akweni mmakwana, will be waiting from you.May God go before us (UTM)

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Před 23 dny +3

    Akweni osayiwala kuti ndalama inapha yesu remember that

  • @user-ks3uw8gj8h
    @user-ks3uw8gj8h Před 23 dny +5

    2025 am going home only to vote for UTM well done guys hope our President Is smiling for the great decision which has been made🎉🎉🎉🎉🎉

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi Před 23 dny +3

    Yehova alemekezake.., Mzimu wa Chilima use mumtendele❤❤❤

  • @augustMag
    @augustMag Před 23 dny +3

    Mau amphamvu Mai Kaliati UTM meayitha🔥🔥🔥🔥💪💪♥️♥️

  • @user-dm2fs6hf1b
    @user-dm2fs6hf1b Před 23 dny +1

    Well done my sister they is no way to keep on going with these monsters, we the followers shall never give up. UTM wozaaaa munya achule a mcp zombalangondo inu.

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 23 dny +4

    Well done my people wina apenga misara Chaka chake chino

  • @JenipherRapkani
    @JenipherRapkani Před 23 dny +1

    Congratulations akweni ambuye azikudalisan ndikulifunila ufulu dziko lanthu ❤❤❤

  • @chifundopatrickkamwiyo5784

    Keep the fire Burning.....utm 🔥

  • @John-to8gl
    @John-to8gl Před 23 dny

    That is what i was waiting to hear from you guys
    I wish the team all the best and keep going forward 🙏

  • @alomuddin8801
    @alomuddin8801 Před 23 dny +1

    A utm mwaganinza bwino 👍👍👍👍 osadya pamodzi ndi fiti ayi

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer Před 23 dny +4

    Mulungu akutsogolereni a utm akumenyeren nkhondo pamaganiz anu abwin✅❤️❤️❤️❤️❤️❤️🎉🎉🎉🎉

  • @MirriamKambale
    @MirriamKambale Před 23 dny +1

    ULemu wanu akweni osabwelera mbuyo pa tsogolo ndi Utm keep keeping the SKC manefesto and try hard kukwanilitsa mzimu wa SKC uzausa mumtendere.

  • @user-jh8tj5in3y
    @user-jh8tj5in3y Před 23 dny +3

    Gulu lonse lomwe layima apa munthu ndi Publicity Secretary yekhayo! Ena anthu aphindu ajomba! kutha kwa Chipani!

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 Před 23 dny

    I had never voted before but next year a’m definitely going to vote for utm

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma Před 23 dny +1

    Congratulations utm ndi nonse atsogoleri takunyadilani asakunamizeni ndi timaudindo mukachoka maliro kumeneko

  • @sinoadedza6231
    @sinoadedza6231 Před 23 dny +2

    Pambuyo pachipani Cha utm moto buuuu 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-cn3gi2vf5n
    @user-cn3gi2vf5n Před 23 dny +1

    That's great mama we are following you

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 Před 23 dny +1

    Amen indeed akweni mulungu azikudalitsani ndipo akutsogolereni mzonse

  • @SueWahna
    @SueWahna Před 23 dny +8

    At aliyese osunga ndevu ndi wa UTM anena anena akweni😂

  • @gracemaluwa4674
    @gracemaluwa4674 Před 23 dny +4

    Congrats Akweni❤

  • @peternashyo9850
    @peternashyo9850 Před 23 dny +1

    Great and wise decision, Viva UTM.

  • @user-gr5zt6kw3s
    @user-gr5zt6kw3s Před 23 dny +6

    Well done

  • @HarryYottam-ft1bo
    @HarryYottam-ft1bo Před 23 dny +1

    Keep it up ndazikonda koma ndipemphe nawo Kwa akulu akulu a utm kuti mukamayamba convention, don't forget miyambi mizu yathu inamera pamenepo please

  • @wizyrastah
    @wizyrastah Před 23 dny +6

    Tatuluka tatuluka anena anena basi

  • @Mwizaso
    @Mwizaso Před 23 dny

    I've been waiting for this speech yooo🥳🥳🥳 the best decision ever 🥳🥳🥳🔥UTM Boma🥳🥳

  • @mkandawirem610
    @mkandawirem610 Před 23 dny +1

    More fire bravo utm, apa zakhala bwino kwabasi

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 Před 23 dny +1

    A president akhale madam kaliyati,and tonse takinzeka ku ka vota UTM, burning the fire alive ya SKC MHSRIP 🌹

  • @HusseinAdamLidezo
    @HusseinAdamLidezo Před 23 dny

    Mwachitad bwino kuchoka mofulumila mukanatafunidwatu nonse, kuganiza modzama❤❤

  • @Vwalavwata
    @Vwalavwata Před 21 dnem

    Indeed ndinayamba kusata za ndale chifukwa Cha Dr SKC may his soul rest in peace

  • @MariaNkhata-i9q
    @MariaNkhata-i9q Před 23 dny +1

    Weldone mama that's a very good movie ❤

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn Před 23 dny

    AKWENI MOTOOOOO!❤ Mzimayi wathu okondeka olimba mtima wanthabwala ocheza ndi anthu bwino one ku mtima ziiii kumva bwino

  • @BlessMnyenyembe
    @BlessMnyenyembe Před 23 dny +4

    Ndanyadila, vote yangso mukhale nayo!!!

  • @mabletungande349
    @mabletungande349 Před 21 dnem

    Am utm n my vote .....Fredo kiss

  • @RodneySupply-tx3ul
    @RodneySupply-tx3ul Před 23 dny +1

    Thank you so much elder and akweni for well articulated speeches I am glad for taking this direction, God bless UTM, osatopa, osaopa osafooka!!

  • @mthawisakaunda
    @mthawisakaunda Před 23 dny +4

    Chakwera umamupheranji chilima taona zakuderatu akuthawa Kkkķk. Ovotera mcp panopa sanabadwe mwna coz mbr yanu yanyasa. UTM woyeeee🎉

  • @JosephHill-fy1bb
    @JosephHill-fy1bb Před 23 dny +3

    UTM,, DPP, AFFORD Mukagwilizana,, Dziko mulitenga basi...

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal Před 23 dny +1

    Zimangondisangalasa chifukwa sitimakonda chipani ichichi anthu ake ndi oganiza komanso ndi antendele ❤❤❤

  • @dicksonndire1857
    @dicksonndire1857 Před 23 dny +1

    God should be with the family of UTM,

  • @nafejonga972
    @nafejonga972 Před 23 dny +2

    UTM FOR REAL😂😂❤❤❤
    VAZE VAZE WOYEEE😅😅😅

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 Před 23 dny +4

    I wish Mai awawa alamule dziko ❤ndale anaziyamba kale

    • @nafejonga972
      @nafejonga972 Před 23 dny

      Me too dear❤❤❤

    • @gladyschisomo4324
      @gladyschisomo4324 Před 23 dny

      Vuto ndilakuti dziko lililose Lili ndi malamulo oyendetsela dzikolo ndiye munthu akasankhidwa kukhala president amakasainila kuti ndiyendetsa dzikoli malinga ndi malamulo ndiye zoipa amakaziona atasaina kale koma manja awo amakhala omangidwa chifukwa Cha malamulo aja ndiye nthawi zambili munthu amakhaladi wabwino asanakhale pampando koma akakhalapo zimavuta kukwanilitsa zija analonjeza Zina chifukwa Cha malamulo adziko
      Nde poti lamulo limapangidwa ndi munthu kusinthidwaso ndi munthu koma ndipovuta ndithu kukoza ma mistake omwe adapangidwa zaka 20 zapitazo iweyo ukoze mu zaka 5 zinthuzi nzovuta kuzivetsa nde vutoso akangolawa ndalama anthuwa zose zija amaziiwala ndalama ndi satana ndithu idapeleka mwana wamunthu osalakwa

  • @Jessica-pg6ep
    @Jessica-pg6ep Před 23 dny

    Mwachita bwino well done UTM Members Akweni umunthu mulinawo ❤timakukondani

  • @user-fm8ed7eo3i
    @user-fm8ed7eo3i Před 23 dny +1

    Mwakhwana guys uwo ndiye munthu ndipo maganidza booooh ngati Dr Chilima

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Před 23 dny +2

    Mwachita bwino akweni mwasiye agalu wokuphawo mbuzi za anthu

  • @macaleistkanjati-zw6cf
    @macaleistkanjati-zw6cf Před 23 dny +1

    Akusenda team ija kunooooo. YATHA TEAM!!!!

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 Před 23 dny +1

    Migwirizano ikumapha tizipani ting'ono ting'ono.Mukaona kuti simungapambane imani mwanokha ndi cholinga chakuti mupeze ma MP. Chipani chimalimba ndi ma MP ku parliament. Ndi 50+1 adzakufunani nthawi imeneyo

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js Před 23 dny +1

    Congratulations.Mulungu akuyanganileni.Light and darkness do not stay together

  • @BlessingsGondwe-v9u
    @BlessingsGondwe-v9u Před 23 dny

    Koma kumeneko,,, 🥳🥳🥳🥳🥳 mwat wina satsegula mmimba kuseli,, go UTM go my vote 🔥🔥🔥🔥🔥

    • @VungaQueen
      @VungaQueen Před 23 dny

      🔥🔥🔥tili pa mbuyo Panu a utm 🔥🔥

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Před 23 dny +1

    Mmmh mau amai kaliyati sakundipatsa chilimbikiso , pali china chake chikubisidwa , but it's ok let's look the way forward .
    But remember l'am not politician .

  • @Tabitha-gs3mt
    @Tabitha-gs3mt Před 17 dny

    United Transform Movement (UTM) 2025 my vote 🔥

  • @SamsonChafulumira-mv7og

    Chikangawa watsala ekha well done mama

  • @MercyChimaliro-fi6mv
    @MercyChimaliro-fi6mv Před 23 dny

    We are here for UTM. Let's gather here

  • @UssenNjirinah
    @UssenNjirinah Před 23 dny +1

    Kkkkkk koma utm ndikawawa kusonyeza kuti manganya asala ndi udindo wokha ngati mulamba utatjawidwa ndimadzi....nambo eeeeeee zandiwopsa kkkk

  • @BrianJoe-z7u
    @BrianJoe-z7u Před 23 dny +4

    Ndakondwa kwabasi

  • @ViserKabango-jt1hs
    @ViserKabango-jt1hs Před 23 dny

    Moreeee fireeee,go forward akweni, together we stand

  • @OsmanBakali-s5x
    @OsmanBakali-s5x Před 23 dny

    Kuzangoti khaaa🔥🔥 akasake ena oti awapatse .... Time over rise up Malawi

  • @OmexAkim-ww9nd
    @OmexAkim-ww9nd Před 23 dny +4

    Mumakwana inuyo Mesa

  • @margretsandey
    @margretsandey Před 23 dny +1

    Nkhaaaaa akwene mwabweratu mwa coming, my vote

  • @danielmsowoya9107
    @danielmsowoya9107 Před 23 dny

    Beautiful & bold decision!!! Bravo UTM 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @RaphaelMaunde
    @RaphaelMaunde Před 23 dny +1

    Viva mama Kaliati viva UTM viva SKC💪💪

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Před 23 dny +1

    Amen 🙏, mwazunzika enough

  • @OscarMkandawire-g1z
    @OscarMkandawire-g1z Před 23 dny +1

    Watching live from Mkwapasi Mbizi- St Augustine Mzuzu

  • @faustascjfronha34
    @faustascjfronha34 Před 23 dny +1

    Zikomo kwambiri UTM mupitireze ntchito za SKC

  • @aggiemlotha1208
    @aggiemlotha1208 Před 22 dny

    UTM ingomutenga chimulilenji basi otherwise Kaliyati sangakwanitse.😅😅

  • @MphatsoPemba
    @MphatsoPemba Před 23 dny +1

    Uthe ngwilizano umenewo tipiliza kusatila utm

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 Před 23 dny

    Akweni must be tsogoleri wa utm because she’s very clever

  • @charlesjimu6054
    @charlesjimu6054 Před 23 dny +1

    Yes you need to partways with mcp

  • @WilliamKude-oj4mi
    @WilliamKude-oj4mi Před 23 dny +2

    Tilinanu lomodzi mama more fire 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥 you open gate please

  • @GeorgeLipengaphiri
    @GeorgeLipengaphiri Před 23 dny +1

    Akweni timakunyadilani keep it up vote yanu ilipo basi

  • @JoshuaMkandawile
    @JoshuaMkandawile Před 22 dny

    Very good news a Malawi 😊

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg Před 23 dny +1

    Mwachita bwino kutuluka, koma ndikuuzeni kut musamachite kudikira kut pafe munthu kaye then nkumapanga chiganizo. Koma mukanatuluka nthawi yomwe Chilima anali moyo chikanavuta ndichani??? Padakafunda padadyiwitsa galu. I hope a lesson has been drawn.

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn Před 23 dny

    Ndipo maganizo a chipani ichi ndawakonda kwambiri ndipo mayi kaliyati ndi mutudi wadzelu pa wokha ndimamuna

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje Před 23 dny

    U ar strong woman keep up mah don't afraid God will be with u akufuna moyo wanu ayamba ndiyeyo poti anazolowela kupha koma pano pokha tikumuwona ife aa

  • @Andrew-nz9sh
    @Andrew-nz9sh Před 23 dny +1

    On by your side UTM 💪💪💪💪💪

  • @anniedennis7127
    @anniedennis7127 Před 23 dny

    Very well done my UTM family

  • @user-lj8ug5lq8c
    @user-lj8ug5lq8c Před 23 dny +3

    Congratulation kweni with your friends you are not a feg woman,I can say you are a man of integrity

  • @peterchiutsi
    @peterchiutsi Před 22 dny

    But when Choosing A president Candidate please let's Choose munthu wanzeru

  • @paulkalizangoma5904
    @paulkalizangoma5904 Před 23 dny +1

    That's a very matured decision.

  • @user-gd2kl1fx1q
    @user-gd2kl1fx1q Před 23 dny

    Utm forever God is in control may the soul of skc continue resting in peace

  • @MkandawireMadalitso
    @MkandawireMadalitso Před 23 dny

    Great decision UTM ....... Let's move forward

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 23 dny

    100% !, ndiye apa mupabge alliance ndi DPP, AFORD ndi UDF, basi mwamutha Chakwera ndi boma lake la MCP. Watizunza mokwana.

  • @manjakhosipatrick1299
    @manjakhosipatrick1299 Před 20 dny

    Good decision 🔥 UTM Rest in peace SKC

  • @ZondoChirwa
    @ZondoChirwa Před 23 dny +2

    As u.t.m you are thinking make them that you are not gallible