A Chakwera Ndi A Mutharika Onse Ndi Olephela - Samuel Lwara

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 07. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara says neither His Excellency Dr Lazarus McCarthy Chakwera nor former president Prof Peter Mutharika are fit to rule this country. They are both failures.
    Pa Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara wati Olemekezeka Dr Lazarus McCarthy Chakwera kapena pulezidenti wakale Prof Peter Mutharika sayenera kulamulira dziko lino. Onsewo ndi olephera.
    #Malawi

Komentáře • 208

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 Před 26 dny +5

    Samuel you are right ✅ 👌....Chakwera ndi Muntharika...tiwaona zintchito zawo....Onsewa olephwera we.Need New Blood....Mkulu uyu akalankhula chilangamo....zoona zokhazokha......More Fire 🔥 Samuel...👍👍👍👏👏👏👏👏👏

  • @Mahmoodwargison-op2gm
    @Mahmoodwargison-op2gm Před 26 dny +10

    Vuto munthuu akalakhula ngamo mumamuda kma chilungamo chimawawa keep it up nr Rwala

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt Před 26 dny +9

    Ofcz munthalika failed somehow but these one eeeh aonjezaa

  • @OMEXTWAIBU
    @OMEXTWAIBU Před 26 dny +1

    I'm really agree with you Samuel , keep it up and don't fear. True true big.

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Před 26 dny +1

    Chilungamo chosatenga mbalin keep up the good job, zitseguleni mitu mbuli zimene zimavotera atsogoleri olephera, 80% ya anthu ovota ndi mabulutu, akufuna Chakwera olephera kubweretsa Mutharika olepheranso.

  • @MasterMwandira-q8v
    @MasterMwandira-q8v Před 26 dny +3

    Ndizoonadi. APM, CHAKWELA, awa ndi anthu olephela, bwanji tiyeseko afford nawoso tione kulephela kwao

  • @GiftPhiri-tt7nn
    @GiftPhiri-tt7nn Před 26 dny +6

    Chipani cha dpp bingu anapanga chitukuko kwambiri and ndimachikonda koma president amayenera kukhala wina ku dpp ko , sankhani president wachinyamata ife tikamuvotela , dpp bola singafanane ndichakwera koma ma president tiyese atsopano

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os Před 26 dny

      Mwayankhula bwino kwambiri, anthu amadana ndi chilungamo

    • @haneefmuyaya7472
      @haneefmuyaya7472 Před 26 dny

      I prefer, Muthalika ataimanso ndi Atupele,
      Zikhiza kukhala bwino, akazatopa, mwana azapitirize,
      Koma zomatenga anthu isaziwika bwinozi,
      5yrs it's not a joke guys

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki Před 26 dny +2

    Mr lwara you are number one! Apm and chakwera same what's up group both are fools. Malawi is a cursed country leader ship is worse.

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Před 26 dny +2

    Unaonako dpp ikugula fertilizer ku butchery,kwatsala iweyo akumange mpamene utadziweno kuti pakati pa awiriwa Pali kusiyana.

  • @BrightPhiri-bt6ev
    @BrightPhiri-bt6ev Před 26 dny +5

    Apa mwalankhulapo za nzelu lero.peter is not a solution to our problems tinamuyesa kale

  • @DIRECTORJARVMACK
    @DIRECTORJARVMACK Před 23 dny +1

    Ndizoona onse ndi olephela koma devaluation mmmmmmmm ndiyopweteka kwa achinyamata ogwila maganyu ife APM my vote

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Před 26 dny +4

    Pena pake nanuso Mr Lwara mumaganiza moperewera kwambiri,inuyo mungafanizire Peter ndi chakwera? Like seriously?

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Před 26 dny +1

    Pa Peter pokhapo ndie wapenga Peter sungamufanizilire ndi chakwera APM akufunika than any one

  • @anniedennis7127
    @anniedennis7127 Před 26 dny

    That's very true , only a patriotic Malawian cannot vote for failed leaders Chakwela and muthalika.

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 26 dny +2

    Ndinu achitsilu alwara sungafanizile MCP ndi DPP aaaaa anyamata alipo muboma akupanga chani

  • @user-fm8ed7eo3i
    @user-fm8ed7eo3i Před 26 dny +1

    Inu ndiye mu kuwona owina ndi ndani, plz musapange zoti wina mungomuioitsa mbiri koma mudzilankhula kuti zinthu zisinthe. Pano tikufuna kuti tisinthe dziko ndiye osinthayo ndi APM zisiyeni zikhale chonho

  • @spargomw
    @spargomw Před 26 dny +1

    Akulu ngat Mfundo zakutheran ndibwino kukhala osayankhula kalikonse, inuyo pangan Alliance nd Lyton Mangochi muyambitse chipani chanu coz apapa mwaonetsaso uchitsiru ofanana nd Lyton Mangochi.

  • @QueneteCatundulo
    @QueneteCatundulo Před 26 dny +3

    Asowa choyankhula awa

  • @user-ti2ct8ts8d
    @user-ti2ct8ts8d Před 26 dny +3

    Iwe mutharika ungafanize mbudzi ngati chakwela? Iwenso ndi kape kwambiri

  • @YNOTGEORGE8
    @YNOTGEORGE8 Před 26 dny +3

    Yes Mr Lwarwa thus fact APM thus not a solution

  • @user-ee6be5kl5o
    @user-ee6be5kl5o Před 26 dny +1

    Lwala Mutu wako sakugwila waoneka kale omwe amasankha ndi anthu iweyo sungafanizile Mutharika ndi chakwera , Mutharika anthu amasangalala kwambili kuposa pano ndi chifukwa anakuthamangitsa mnyumba ya Malawi housing, iweyo ziyankukula zako zopusazo amalawi Peter Mutharika wooyee

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe Před 26 dny +1

    Naweso larwa izi ife ai. chifukwa a Peter mutharika sungafanizire chakwera never. Pali zambiri zomwe simungafananitse

  • @user-iu6mr5xu6r
    @user-iu6mr5xu6r Před 26 dny +1

    Kodi bambo Lwara, amene afuna nzake pakati pa Peter ndi Saulosi ndani? Khalani ndi cipani canuco. Kuposa kunena zopusa ngati cidakwa. Kodi wanzeru? Nanga ulikuti ndipo ukutani?

  • @JumaKachala
    @JumaKachala Před 26 dny +1

    Koma.lero ndee mwayankhula zopepelatu
    Peter angafanane ndi chakwera

  • @user-iu6mr5xu6r
    @user-iu6mr5xu6r Před 26 dny +1

    Inu ndi munthu amene amanena zinthu zimene sadzidziwa. Munapha zipani 9 kukhala ndi kusunga MCP. Lero mulalata?

  • @OweniMalokooweni-es9qx
    @OweniMalokooweni-es9qx Před 26 dny +3

    Ndipo kwambii timufuna atupele mulunzi😊

  • @AlfredSteven-v9m
    @AlfredSteven-v9m Před 19 dny

    Yes ur right koma mukananena oyenera muzipanimo

  • @user-st6bt5vv9c
    @user-st6bt5vv9c Před 26 dny +1

    Lawala is looking for chihana but AFORD alone can't win how old was mandera both are candidates let them exercise their freedom

  • @BertharrySecurity
    @BertharrySecurity Před 26 dny +1

    Mnthalika inde analephela Koma anayesesa, kusiyana ndiwomwe alipowa

  • @PeterPhiri-di1ux
    @PeterPhiri-di1ux Před 26 dny +2

    ndimakupanga follow koma lero wangomunyoza muthalika panya pako ndipo ndakutuluka

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 26 dny +1

    Bola APM kusiyana ndi chakwera, nthawi ya APM zinthu zinaliko bwino kusiyana ndi chakwera.

  • @user-xd1cm7tm7t
    @user-xd1cm7tm7t Před 26 dny +2

    2020 mumanenaso Chocho kut alowe anyamata lelo bwanji

  • @StevenDastan
    @StevenDastan Před 26 dny +1

    Apm ndimunthu wankulu kwambili kuliphika dziko lino

  • @user-nd9cm3yl7e
    @user-nd9cm3yl7e Před 25 dny +1

    Muthalika satukwana muthu olomodzi ndiwante ndele zd

  • @EllahChikwatu
    @EllahChikwatu Před 26 dny +1

    Iweyo suzakalamba omwe anakubala nd sikana wina nyamata sibwino kwanu kulibe agogo

  • @marcuswalker2613
    @marcuswalker2613 Před 26 dny

    Mbuli iwe Mtumbuka opanda mfundo atakulanda nyumba ndiye wowowoooo. Ndale zako zilibe tsogolo "mark my word"

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w Před 26 dny +1

    As itikut peter alibwino koma tikut apm alikobwino kusiyana ndi chakwera basi

  • @VuyolwethuMbabani
    @VuyolwethuMbabani Před 26 dny +1

    Iwe uzilimbana ndi chakwela otsati Peter ngati wapasidwa ndalama ukazibwedze uyaluka komanso uchita manyanzi 2025

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7e Před 26 dny +1

    Apm amalize term yake munamulandila nsanje upresident l support Dpp 100%

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s Před 26 dny +1

    Alwala mwayamwa tikutulukani mwayambaz,inu nthawi ya DPP mungayerekezere ndinthawi inu.
    Inu nthawi ya DPP anthu amamangidwa chonchi or kukwera kwazinthu zinafika apa?
    Njara,kusowa kwamankhwala mzipatala,kukwera kwa zinthu mungayelekeze ndinthawi ya DPP

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di Před 26 dny +1

    Mulilanaye APM chomwe timadziwa APM sanaluzepo ndewu akamamenyana 1 to 1 kukanikana ndiye mubweletse 1 to 5 ndiye 5 a wine muziti m'modziyo walephela? Anthu adyela Inu tandiyankheni alwara komanso kamenyedye ka m'modzi uyo sikanasithe 40 pelesenti ndiyomweyo anapezanso pa 1 to 1 mulila ndi APM 2025 APM boma

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di Před 26 dny +1

    Lwara ndi wa ganyu sasamala za amalawi akungifuna kuti amupatse ndalama koma APM sangamupatse ndalama n'gooooo ozavotela APM ndife amalawi akumudzi amene tikudziwa ubwino wa APM tikufuna feteleza ontchipa ife

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma Před 26 dny +1

    Galu nzimayiiwe athu anzeru avotera dppp pitamuthalika amayesetsa kuti athu tizidya chakwera anabwera kudzaba njara yavuta km muthalika zakudya zimatsika ntengo

  • @user-zx3pz2wy1j
    @user-zx3pz2wy1j Před 26 dny +1

    Kodi osalephela ndi ndani ngati ukutiso peter ndiwolephela iweyo wachitapo chiyani ?

  • @HendresonLubano
    @HendresonLubano Před 26 dny +1

    Kuyambila pano usazanyozeso muthalika ndimunthu watendele

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před 26 dny +5

    Kodi a lwara muli mbali iti
    President wanu pano ndi mdani
    ....jnutu mwasowa kolowera ..
    .mmene chakwera waonongela zikoli mungayerekeze ndi apm....inuyo mukukhala ngati mbuli bwanji
    Mmene peter amasiya upresident katundu anali pati.....iweyo lwara wangosowa kolowera .....osachita support Enock chihana bwanji monga wakwanu.....usiletu kuyankhula za peter......amalawi chiyembekezo chimene tasala nawo ndi peter

  • @retirementtoafrica
    @retirementtoafrica Před 26 dny +1

    Nkhani yodya mabanzi ndiyovuta, chilungamo chimasowa ndikumagoyankhula mozungulira opanda solution.

  • @MarriamBakalie
    @MarriamBakalie Před 26 dny +2

    Wayambatu ku khota tidana nawetu uziyankhula za chakwela nt APM wamva machende ako galu

    • @DeliaKaduya
      @DeliaKaduya Před 26 dny

      😂😂😂😂 yomweyo galu iweee

  • @samsonhavenoyayshonga2609

    Koma pa ma President onse mu Malawi yemwe aliko bwino kuposa onse ndi Mutalika.

    • @RitaDickson-ls7ol
      @RitaDickson-ls7ol Před 25 dny

      Palibe zabola apa change position peter and chakwela out 2025

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Před 26 dny +1

    Ndipo a samuel lwara mumandiwaza nsaname kkk everytime ndikamamvera ma audio anu ndimamva sugar 😂 ndimafuna ndikumvelani daily cz mumabudula mpunga wanyama, kamba simugawa. Izizi akunena apazi akutsutsa amadya thewera lamwana 😅😅😅

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o Před 24 dny +1

      Zoona ine munthu uyu ndimafuna kumamumvera daily fact ndiyomwe akunenayi😂😂😂😂

  • @DesmondKanguwe
    @DesmondKanguwe Před 24 dny

    Reality yowawa...odana ndzomwe ukunenazi sadziwa zomwe akufuna

  • @kondwanbanda2671
    @kondwanbanda2671 Před 26 dny +1

    Alekeni anthu akasakhe okha

  • @GRACIOUSKENAN
    @GRACIOUSKENAN Před 26 dny +8

    Ndiyambe chochi,Neleson mandela uja sanalamulire dziko ali otha msinkhu??
    chikhala kuti peter anthu akumuda bwezi kumaliro kuja anthu akumulira kut ayimile??
    so iwe ukamat peter ayi what do you mean so tayimilatu iweo tione ndi mkamwa modambanamo aaarrriii.
    iwe do you compare chakwela nd peter,chambaaa chani,ngat sukufuna khala usavote uzidya soya peices bass kumpotoko ndi atumbuka azakowo bwanji? pita ukooooo

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 Před 26 dny

      Akunena zoona, koma mbuli ngati inuyo simungaone.

    • @user-es4jt6ds8m
      @user-es4jt6ds8m Před 24 dny

      Ayi osanena Kuti stumbuka pliz zichepezo tseka Chikamwa icho

  • @user-nd9cm3yl7e
    @user-nd9cm3yl7e Před 25 dny +1

    Wanamaiwe sudziwa ndale

  • @MenciaMadex
    @MenciaMadex Před 26 dny +1

    Apm my vote 2025

  • @TypexTikita
    @TypexTikita Před 26 dny +1

    Lwara zopela zomwe walankhula za APM chifukwa munthu wanzeru sangayerekeze mavuto tilinawowa ndi APM

  • @ibrahimbamusi109
    @ibrahimbamusi109 Před 26 dny +1

    Lwara tikutulukatu ali ndi chibwana

  • @KennyPhiri-zg1kr
    @KennyPhiri-zg1kr Před 26 dny

    Peter anayendesapo analephera chakwera walephera you are true pezani wina

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 Před 26 dny +1

    Nyamata wa chilima wasowa kolowera kkkkk

  • @jonas-xh4hz
    @jonas-xh4hz Před 26 dny +1

    a rwara zikambani zanzeru musiye kuyankhula zopusa zanuzo

  • @OsmanPatrick
    @OsmanPatrick Před 26 dny +1

    Machende ako iwe abambo akowo

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Před 26 dny +1

    Ndichifukwa achichotsa ntchito ndiwamisala wakutumayo akupusitsa koopsa 😂😂😂

  • @SofiyanoMayuni
    @SofiyanoMayuni Před 26 dny +1

    Peter ndiwabwino

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Před 26 dny +9

    Lwala wayamba kukhumudwitsa wanthu chakwera ungafanizire ndi Apm?

  • @user-jj3oo6jh1l
    @user-jj3oo6jh1l Před 20 dny

    Mr samuel.pachimanga choola timasankhako.kt ichi ngankhale chili choola km.ndinkhonza kukazinga nde anthu tikuona kt bola peter

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b Před 26 dny

    ❤❤ zowona

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma Před 26 dny +1

    Ulibe mfundo nzimayi pachinyero chako dppp ikulowabe m,boma panyero pako

  • @AlfredSteven-v9m
    @AlfredSteven-v9m Před 19 dny

    Mwangolongolora 18 min osanenapo oyenera anthu tigwire ziti ndiye

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Před 26 dny +5

    Mr. Lwara is a chaotic person, he wants people to applaud whatever he says, Mr. Lwara learn to be quiet sometimes, you are missing the point

  • @charlesmasauko4651
    @charlesmasauko4651 Před 26 dny

    Woooozaaaaaaa sir Lwara

  • @Samu-q3z
    @Samu-q3z Před 26 dny

    Apm ❤❤❤❤

  • @VuyolwethuMbabani
    @VuyolwethuMbabani Před 26 dny

    Udani wako ndi a Peter usasokonedze nao anthu omukonda Peter Ife Peter ndi chiyembekezo chathu usiye kuyankhula manyi

  • @lucianogeoffrey4275
    @lucianogeoffrey4275 Před 26 dny

    Mwayambatu uchitsiru madala. Muthalika ndi Chakwera you cant put then together. Ya Chilima ija timakupangani support koma mwayamazi ayi

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Před 26 dny +1

    Peter mutalika ndi simungayerekeze ndi Chakwera. Vuto amalawi timaziwa kuyankhula koma mopanda zeru. Mcp udf ppp dpp mukhale pasi muone kuti kodi ndichipani chiti chimwe chapangapo zabwino muona kuti dpp inayesesa. Chinthu chimozi poti mutalika wakalamba koma still ali ndi zeru . Chilima sanawinise dpp. Dpp nditimene anayitana chilima. Chilima anawinisa mcp ndiyime isamanyade .

  • @MastonWatson-g7g
    @MastonWatson-g7g Před 26 dny +4

    Iwenso mmutu mwako nzeru mulibe nzeru chakwera ungamufanizile ndi mutharika? kape iwe wosowa chonena.

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov Před 26 dny

    Akulu mwayowoya makola chomene ineso palije uyo angasanga vote yane anthuwa palibedi munthu ofunikila Peter anapangitsa kut kuyambe ma dembo tisaiwale ulamuliro wao

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy Před 26 dny

    Lwala nde tivotere ndanino kulephera kulitu ma stage stage enawo nde ndi zero

  • @GiftMathewe-fr3kn
    @GiftMathewe-fr3kn Před 26 dny

    Inuyo mukufuna ndani mwalankhula2 zopoila lelo awotu ndimaganizo anu bwana takumvani koma uthengawo kapena mwayamba kampeni2 tizavotela inu

  • @JamesMalango
    @JamesMalango Před 26 dny +1

    Akulu awanso,,,,

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb

    Auzeni zoona bwana

  • @RitaDickson-ls7ol
    @RitaDickson-ls7ol Před 25 dny +1

    That is true Peter ngati anachoka pampando analephela tiwoneko zna asatinamize agogo l love your point keep it up mr🙏🙏🙏

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 26 dny

    Apeter ndiye ndiokanika bola namkhumwa osati peter aaaa ngati zili chotcho basi alipowa angopitiliza

  • @user-qg4it7my9n
    @user-qg4it7my9n Před 26 dny

    Akulu fodya tamazimisiraniko a peter simungafanizire ndi mbuzi ya mu2 ngat chakwera

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Před 26 dny

    Rwala ndi opusa
    Chisiru iwe...chitsiru kwabasi

  • @OMEXTWAIBU
    @OMEXTWAIBU Před 26 dny

    APM wakalamba akapume, akakhala akungozikodzela ndiye angalamule ndani? Kwake kunatha petulo tiwone zina, munthu osadziwa kulankhula kkkkkk akagwele ndi family party yakeyo, Tiyeni amalawi tiyese Atupele ❤

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer Před 26 dny

    Ndip or achakweratu sitikuwafuna ife ai akapume achakwer kwao tikufuna tionen Ena bas

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Před 26 dny +1

    Aaa inu mbuzi ndi nkhosa mungafanizire?

  • @chadreckchibwithala1493

    kkkk mwakalipa alomwe atanena za peter mnthalika kkkk chilungamo si mkuchifuna alomwe peter walalamba amazikozera pa mpando angalamule dziko aaaa peter wakalamba
    mandela msafanize ndi gogo peter ayi

  • @EmmanuelMaxon
    @EmmanuelMaxon Před 26 dny

    Panyapako iwe ukuona ngat popanda akukhoti achinyengo aja APM akanatuluka m'boma?

  • @EmmanuelMaxon
    @EmmanuelMaxon Před 26 dny +1

    Iwe aliyese akavota yekha usati nyase usamat amalawi sakufuna dpp uziti iweyo sukufuna koma ine ndikufuna zako zimenezo mesa chilima anadziwa ndale chifukwa cha apm

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko Před 26 dny

    Iwe ndichisiru kwambiri ukunena kiti mcp asankheko munthu wina oti ayimireso 2025 ukuganiza kuti angakhale ndani pa anthu onse okuba amene ali ku mcp kuja?? Ndiwe mbuzi kwambiri

  • @Emmanuelmw603
    @Emmanuelmw603 Před 26 dny +3

    mutharika akuwinaso mufune musafune.....APM my vote ✊

  • @PriscillaKhumbanyiwa-i1d

    Vuto siyiwe uyakhula, vuto ndi amako anakubelaka iwe

  • @OMEXTWAIBU
    @OMEXTWAIBU Před 26 dny

    Bola mwanva, mbavazi zomwe zidalamulilapo kale ndi nthawi yopuma zikadye ndalama zomwe zinabazo

  • @PetrusTlhokwane
    @PetrusTlhokwane Před 26 dny

    Ndipo ndizoona tinapanga mademo 2020 chifukwa cha APM analephera nde tiyeni ngati pali wina ku DPP angazawine not APM chonde tiyeni Anthu awiriwo apume km 😂😂😂😂

  • @user-ee6be5kl5o
    @user-ee6be5kl5o Před 26 dny

    Lwala akufuna udindo basi Kodi kukhala maudindo osiyasiyana ndi kusonyedza Kuti munthuyo Ali ndi experience osati chakwera amagwila ntchito Ku chipiku iweyo Wayamba kuyankhula ,opusa zopanda nzeru wasowa kolowera

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o Před 26 dny

    Ntumbuka opanda nzeru

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Před 23 dny

    100% light show ndi olephela.tiyetsele,utm UDF or afford.amagona,ali pa mpando.ziko,amayemdetsa,ndi chisale.ndi,amayi akunyumba kwao.just, remember akazi awo,amachita kupita ku reserve bank kumangotenga, ndalama kumeneko,atiudza za change for what corrupt our nation? that's sheet 'we can no sitting here watching this happen.amalawi,kodi,timadziwa akamati democracy?tili kutali,ndi chitukuko mu ziko lathu.

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 26 dny

    Lelo mwalakhulako mwazelu mosakhalila mbali

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před 26 dny

    Amene angavotere aford ndi ndani ....chipani cha atumbuka .....muzavoterana nokhanokha anthu oti sakukukwana 5000000 ndiye mukufuna upresident

    • @AbrahamTembo-z5k
      @AbrahamTembo-z5k Před 24 dny

      Yes, Nothern Region has got a low population BUT has a STRONG DYNAMIC POLITICAL IDELOGY. Satengera kt uyu ndi wakwathu koma PERSONALITY ya munthu.