ZAYAMBIKA TSOPANO/ TIONA ZINTHU CHAKA CHINO.

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 6. 07. 2024

Komentáře • 29

  • @ShafieIdrissah
    @ShafieIdrissah Před 10 dny +2

    Chakwera tell Malawian gets money for rooting compain 2019 ngati simuulula anthuso zangaulule

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9d Před 9 dny +1

    Ambuye ndikupempha please mtengeni chakwera afe asanamalidze Malawi please please

  • @user-uh5ef4cr8d
    @user-uh5ef4cr8d Před 10 dny +2

    First MCP and chakwela where did he gets Money for rooting compain in 2019 he must tell Malawian

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms Před 9 dny

    Mr a chatsika 2025 chanu palibe samalani akulu

  • @user-ky8eq5ek1p
    @user-ky8eq5ek1p Před 10 dny

    Ok ndiyeoyambakuulula ankhale palipanoyo

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms Před 9 dny

    Boma kugula chimanga kwa alimi and then azigulisa kunja

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita Před 9 dny

    ndalama zomwe azikhale ng,oma Ritchard chimunthu kunkuyu chitchyola ndi apresident akumafupa anthu kuwatuma azipanga zosayenela akumazitenga kuti

  • @user-kg5lf6bd1g
    @user-kg5lf6bd1g Před 9 dny

    Mbewu zokhazo tengo ufike pa k1000

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Před 10 dny

    Aaaaaa zaka zingati zakapeni izi zoputsitsa athu

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 Před 9 dny

    Zimenezi zingathandize chani guyes?

  • @user-ii2sh1mz3r
    @user-ii2sh1mz3r Před 10 dny

    Ziwani Kuti mau amalenga , samalani ndi kamwa yanu iyo a Richard Chimwendo Banda ,

  • @GrantYohane-zd4qy
    @GrantYohane-zd4qy Před 9 dny

    Koma boma kagulidwe kake ka chimanga aaa ku admark amafunatu chotsuka. Koma mbewu sabweletsa ya chimanga chimene amafunachi.

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před 10 dny

    Wayankhula ndi chakwale opusa iweti a chaima ndi chakwera zikugwilizina

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo Před 9 dny +1

    Km Chakwera ndi anthu ako mukubweretsa mfundo zopanda Pake, iwe mmene umalowa m'boma ndalama unatenga kut?

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Před 10 dny

    Dziko achakwera lakanika 4 Yes palibe chimene apanga kusowaso kamba

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Před 10 dny

    Aaaaamugulila ndani chimanga palibe 2025 tikumanabe basi. Chimanga gulani

  • @user-ii2sh1mz3r
    @user-ii2sh1mz3r Před 10 dny

    Kodi uni ukuti tili pa ufulu wozilamulira , Koma bwanji nthawi zonse tikudalira chuma kuchokera Ku maiko akunja, economically we are still colonised, politically we are dependent, but full of witchcraft , instead of serving people political leaders are busy shouting at their fellow leaders , akuti ,ine mungandifanizire ndi a Kuti , ine ndi kumtunda , muona uja ndithana naye mmmmm

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 Před 7 dny

    Ku family ya sadc miya

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w Před 10 dny

    Kkkkkkk mbolo zanu

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef Před 10 dny

    😊😊😊😊😊

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Před 10 dny

    Chakwela Uchenjele Ndi Nzimu wachilima ndi Ena 8 unawapha aja ndicholinga uimenso 2025, Ndalamazo Zakoma Chotani Zochita Kuphela Nanzo Anzako.
    Amalawi Munapusa Kwambili Izi zinachita poyela simunapangepo kanthu Only Born Kalindo Amene Amaona Zinthu Ndikuyankhulapo Ena Nonse Zitsilu

  • @DavidMtambo-zm8ne
    @DavidMtambo-zm8ne Před 9 dny

    Ayambe kaye kuulura chakwera panthawwi ya campaign yake ya 2019, stupiet thinking

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b Před 10 dny

    😮😮😮😂😂😂

  • @FaressPatel
    @FaressPatel Před 10 dny

    Zoopsa kwabasi

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita Před 9 dny

    ndalama zomwe amaitanitsaila asilikali aku isalael ndi Rwanda akumazitenga kuti zomwe akumatumiza anyamata kokasaka atolankhani alimpopo fm ndi bakili muluzi tv akuzitenga kuti

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 Před 10 dny

    Iyyeyo chakwerayo ankazitenga kuti?

  • @user-nw6ie3xx8b
    @user-nw6ie3xx8b Před 9 dny

    Leave us alone as mcp ask dpp how norman chisale got rich

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Před 9 dny +1

      Mcp yanyanya mwa mmodzi ndiweyo wakuba iwe