I think president Chakwera is right to announce that he will stand as per term mandates. Regarding to the alliance wording that has been read by Mr Pamkuku, it means that the two parties will hold their electives and their leaders are re-elected, then the two presidents will have to revert to the agreement just read
chilimatu apa anaputsa ...zoona munthu unali president nde ukakhareso vp ... nde ife porankhura tizizati former president and vice president chakwera kkkkkkkk chamba eti
It is really possible to have a good president leading wrong people... I personally love Chilima....being humble to be the vise president for two consecutive terms after kumulangiza, church leaders, we people telling him kulowa alliance, pano tikumunenenso...
Inuyo mumakodwa anthu akamatukwana chakwera y umagokamba chithu chimodzi always utm ndi chipani mcp ndi chipani onsr ayenera kupita ku conversation then akasakha munthu owadzamilira mu 2025 inuyo nonse ndi a utm kodi Bingu sanatuluke mu udf ndikuyambitsa dpp bwanji thawi zina kumakambapo imrneyi adakhoza kaprna ai thawi zonsr mngwilizano wa utm ndi mcp anthu tu adaleka kulimbikila chifukwa cha atola nkhani inuyo
a chakwela akulephela kubwela poyela chifukwa chipani cha MCP sichao ai koma chimene ndikuona ine ndichoti achakwela akuopa a ku MCP koma chimene ndikuona ine achakwela akudikilila kuti asakhidwe kaye ku MCP ndipamene azapange chiganizo and azatenga wachiwili wao ndi kupita nae ku convention ya tonse kukampasa phavu
Chakwera adalankhula bwino momveka kuti mphamvu zowapasa udindo a chilima zili ndi MCP osati a chakwera chifukwa choti a chakwera wo adalembedwa ntchito ndichipani asati Chilima. Mwachisanso ngati MCP itayimisa a mKaka pa utsogoleri wa upulesidenti musepitemba muno utm izaloza chala ndani
Well said by @badanidube. Apa palibe nkhani apa, I even wonder why the three analysts see it something to discuss. The constitution is very clear that the president can vie for a second term. Who has the agreement because even you analysts have not seen the agreement, I wonder on what basis is this analysis! There is no issue here. Follow the constitution, that’s the answer. Each party is free to feature a candidate, let them go to the conventions. There is no issue here, if people agree kuseli, where is the agreement?
I think president Chakwera is right to announce that he will stand as per term mandates. Regarding to the alliance wording that has been read by Mr Pamkuku, it means that the two parties will hold their electives and their leaders are re-elected, then the two presidents will have to revert to the agreement just read
Adzipitiriza kuti chimanga tidzagule 350,000=00 kwacha sukuwamvera chisoni amalawi Mac-Hendie Chakwera?
This is dramatic issue,lets wait 2025
Chilima ndiwopupuluma,lelo ndi izo aziona,utm yatha basi, ndi ya pa face book. All the way from johannesburg cbd.
chilimatu apa anaputsa ...zoona munthu unali president nde ukakhareso vp ... nde ife porankhura tizizati former president and vice president chakwera kkkkkkkk chamba eti
sizinachitikepo T/A ndikukondwera kubwerera kukhala group ndapita
kkkkkkkkk
Timpweteka ndife anthu asaonengat ochenjela
Chilima ndi Mac-Hende
😂 akuti akungothandizila amfumu kulezela
Kkkkkkkk😂 apa kunku kkkk😂😂😂 Ina aliladi
Ngati tili ndi mbuzi yamunthu mdziko lino la Malawi ndiye ndi Chilima.Iyeyu Wakhala 10 years kumangodya ndalama zathu zosagwilira ntchito
Chilima amaziona ngati Dolo Ali kape ndiwaphuma
Koma Mac-Hendie Chakwera akufuna life presidency
It is really possible to have a good president leading wrong people...
I personally love Chilima....being humble to be the vise president for two consecutive terms after kumulangiza, church leaders, we people telling him kulowa alliance, pano tikumunenenso...
Iyi mukuyiseka opanda mawu chifukwa
Mulungu aumitse mtima wa chakwera kuti adzagwe chagada. Chilima akangowatuluka ndiye kuti athera pompo.
Voice ya chakwela mukuyiopatu,ilikuti
Mbusa wa satanic uyu za padzuko zamumeza wagule wamkulu ndalama zakuba zamuzunguza bongo
Tokuononga thawi anntbuwa ndi amozi o
Kod mmesa mwati poyamba zinayamba kukambirana ndi zipani ndipo kenako zinauza kut asogoleli akakambirane kut amene ati aimire ndi ndani.. apapa ngti asongoleriwo anakambirana za 5-5 ndiye kut zipanizo zinagwirozana zazo.. apa ndikungoonapo dyera komanso kuzikonda ku mcp ku..
Wamufera mmanja joka Chilima
Muziika nkhani yonse osati kumadula
Anthu onsewa ngaboza awa kapena kuti oipa awa
thin voice yake kkkkk koma ndi president uyu
A chakwera ndi akuba basi lero akuyankhula ngati bilimangwi
Vuto ndiloti anthu amkapanga za pompo pompo sanaganize za nsogolo, cholinga kunali kuchosa DPP basi lero ndi izi phuma limaononga zinthu, Achakwela kumbukilani mene munakhalira pa mpandopo m'mawa muzafunanso anthu omwewa kuti ziyende
Clip ya chakwerayo sinamveke
Anthuwa anapusisana heavy😅
Clip ya chakwera sitinayive ife
Dyera chakwera limpwetekesa
Inuyo mumakodwa anthu akamatukwana chakwera y umagokamba chithu chimodzi always utm ndi chipani mcp ndi chipani onsr ayenera kupita ku conversation then akasakha munthu owadzamilira mu 2025 inuyo nonse ndi a utm kodi Bingu sanatuluke mu udf ndikuyambitsa dpp bwanji thawi zina kumakambapo imrneyi adakhoza kaprna ai thawi zonsr mngwilizano wa utm ndi mcp anthu tu adaleka kulimbikila chifukwa cha atola nkhani inuyo
Chakwera suzawina uyelekeze uzayeme
a chakwela akulephela kubwela poyela chifukwa chipani cha MCP sichao ai koma chimene ndikuona ine ndichoti achakwela akuopa a ku MCP koma chimene ndikuona ine achakwela akudikilila kuti asakhidwe kaye ku MCP ndipamene azapange chiganizo and azatenga wachiwili wao ndi kupita nae ku convention ya tonse kukampasa phavu
😂😂😂Atabwali sametana
Kodi ma station wanuwo mukusowa nkhani zokamba.kodi zoona muzingokhalila chilima ndi chakwela kuti adagwilizana chiyani?bwanji wosamayika ma polograme wothandiza anthu mdziko pa iwo wokha.ifetu palibe chipani kapena mtsogoleli amene adzatilongosolela malawi,tsopano mma tv mwanumo bwaji wosapeza ma polograme ena woti muzilimbikitsa anthu kudziyimila pawokha chifukwa palibe mtsogoleli wachikondi ndi dziko lathu.
Amwene mwalankhula mwamzeru zeedi
Chakwera adalankhula bwino momveka kuti mphamvu zowapasa udindo a chilima zili ndi MCP osati a chakwera chifukwa choti a chakwera wo adalembedwa ntchito ndichipani asati Chilima. Mwachisanso ngati MCP itayimisa a mKaka pa utsogoleri wa upulesidenti musepitemba muno utm izaloza chala ndani
Well said by @badanidube.
Apa palibe nkhani apa, I even wonder why the three analysts see it something to discuss. The constitution is very clear that the president can vie for a second term. Who has the agreement because even you analysts have not seen the agreement, I wonder on what basis is this analysis!
There is no issue here. Follow the constitution, that’s the answer. Each party is free to feature a candidate, let them go to the conventions.
There is no issue here, if people agree kuseli, where is the agreement?
bayana chunga adzingobwera atavala Tshirt ya MCP feel free man
Amalawi akubvutika kamba ka Chili a, and now Allah he is punishing him
Mbava
Sizikumveka