BRIAN BANDA KUPHAPHALITSA ZIMAFUSO -🤔🤔🙌🙌21 July 2024

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 5. 09. 2024

Komentáře • 55

  • @JumaGadaff
    @JumaGadaff Před měsícem +15

    Akayamba choncho dziwani kuti mulungu wamakamu ayamba kuwakantha inu mulungu awavula zovala onse akuimila MCP ife chete ndi umasiye wanthu amen 🙏🙏

  • @MervinMwambinga
    @MervinMwambinga Před měsícem +1

    He can be a youth, well educated, good passions and visions but our constitution does not give power to Vp to decide and implement ideas. We have evidence, our lovely late VP SKC. He was our only hope for this country and no one else. Tiye tizinamizana chonchi basi.

  • @richardmadaka287
    @richardmadaka287 Před měsícem +1

    Mtsukuluzi simunampatse mpata kwambiri ngati mmene munachitira ndi Ndebvu za mwayi. Muzipanga balance a Brian Banda. Mwaonetsa tsankho

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn Před měsícem +4

    Skeffa chimoto wathadi eti mpaka afika apa kkkkk

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Před měsícem +7

    Mcp ndiyakupha

  • @PriscillaKhumbanyiwa-i1d
    @PriscillaKhumbanyiwa-i1d Před měsícem +3

    Satana amayenda ndi asatana azake amalawi wosazindikila kumasapota anthu akumpha amcp

  • @macmsiska2937
    @macmsiska2937 Před měsícem +3

    Mbava yayikulu iyo yikamayankhula m'maso muli gwaa

  • @user-wx5fq7gg7d
    @user-wx5fq7gg7d Před měsícem +1

    Mayi Chikata my neba from Mzuzu

  • @user-el8to1te3l
    @user-el8to1te3l Před měsícem +2

    N'gona zen zen

  • @NelsonMarley-m6p
    @NelsonMarley-m6p Před měsícem

    Zimayi opusa chinkhope ngati mtengo wamulambe mxiew

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 Před měsícem

    AAAAAAAAA nthawi Yotani monse muja??? Mumba ndi chakwera amabera limodzi agalu amenewa shupitiiiii

  • @user-un4pm4yt5i
    @user-un4pm4yt5i Před měsícem

    Dzitukuko dzompha anthudzo alamulira inuyo

  • @PriscillaKhumbanyiwa-i1d
    @PriscillaKhumbanyiwa-i1d Před měsícem +1

    Anthu andale makonda kumuchula mulungu pafupipafupi mulungu akukantheni bava za mcp

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi Před měsícem +3

    Koma siteniwe muganise bwino sachakwela muiwale

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Před měsícem

    Big up brother man!!

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2di Před měsícem +1

    Botolo la madzi okumwa muziliika kusogolo kwanu a Brian osati ku mbuyo or ku mohepete kwanu muziliona or mulibuzy

  • @user-el8to1te3l
    @user-el8to1te3l Před měsícem +2

    Mbava

  • @LloydMkula
    @LloydMkula Před měsícem

    Akufuna kutumikila a chakwera not a Malawi ma delegates mazimvelatu

  • @joeljere4385
    @joeljere4385 Před měsícem

    Onse aku North okhaokha

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před měsícem +2

    Nyero yako mzimai iwe ndithu

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Před měsícem +1

    😂😂😂 thiraspot paka 1 mita

  • @user-bi6pb5gc8t
    @user-bi6pb5gc8t Před měsícem

    Mwamvatu nokha akuti eyeyu akufuna azizatimikila achakwela osati amalawi

  • @CathrineBizza
    @CathrineBizza Před měsícem

    Ziyezekanani ku mcpkp uyaaa

  • @Betty-fe9ql
    @Betty-fe9ql Před měsícem +1

    Koma ma comment a Brian mpake pena amankhoma 😅

  • @stevemtambalika
    @stevemtambalika Před měsícem

    Chikangawayu watha basi kkkkk

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 Před měsícem +1

    Mukupikisana kwambiri because you are in government now,, fact osati zinazo aaaaaah. We have also heads to reason.

  • @LowanMasiye
    @LowanMasiye Před měsícem +1

    Boma ndilomweli

  • @FaheemChipojola
    @FaheemChipojola Před měsícem

    Amai awa nzeru alibe ndithu

  • @user-qd7sz1pf1i
    @user-qd7sz1pf1i Před měsícem

    Akunama amayiwotu 2025 mcp mulibepo😂

  • @NthambiInvestment
    @NthambiInvestment Před měsícem +1

    Ngati mukunamizana zowinaso muiwale,, vote ya 2025 tikavotela kuchikangawa ,, MCP Pachilani muzipita ,,,,,
    Nanunso a skeffa ndi a mlaka plz plz ziyalondolelani anthu koyenela pl

  • @giftmakoyo1441
    @giftmakoyo1441 Před měsícem

    Amayi inu mmmm😢

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 Před měsícem

    Akuba okha okha

  • @user-fm8ed7eo3i
    @user-fm8ed7eo3i Před měsícem

    Abambo idzoo za ku chipani kwanu siii zotandidza a Malawi

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před měsícem

    Zaziii

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr Před měsícem

    A Brian ndi a ndevu apatu tikudabwatu leroli kwabookatu Ku MCP money kkkkkk.eeeeee koma abaleeeee.

  • @andrewBwanaisa
    @andrewBwanaisa Před měsícem

    Mwagwa nayo nonse a mcp

  • @kingnavitcha6243
    @kingnavitcha6243 Před měsícem

    Angalephere kuchitsa chipani choti ndi chake

  • @alomuddin8801
    @alomuddin8801 Před měsícem

    Mcp ya khanza yabweletsa njala mu dziko la Malawi chilichonse chinakwera mtengo,

  • @DavieMoyo-pe8vn
    @DavieMoyo-pe8vn Před měsícem

    😂😂😂😂 nyamata WA vinyo Ku MCP Malawi ngosangaratsa

  • @samuelosman3215
    @samuelosman3215 Před měsícem

    Aaaa simulaka uyu?

  • @tisuhmakhwah7085
    @tisuhmakhwah7085 Před měsícem

    Woiphonya ati akufuna kutumikila chakwela not malawians.

  • @user-iq5xk6ju7y
    @user-iq5xk6ju7y Před měsícem

    A Mumba is very controversial, kudzikundikira too much. Ubwino wako amaudziwa ndi ena. Zikuonetsa kuti atasemphana nawo mwayi uwu atha kuukira chipani . He is too confident. He is not bigger than the party.

  • @user-rx1dj7kg8k
    @user-rx1dj7kg8k Před měsícem

    Amayi opusa

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Před měsícem

    Kamat uku sizitha bwino uku mungot phee

  • @lupakishomalangaelix6606
    @lupakishomalangaelix6606 Před měsícem

    Usi sakaimila uku?

  • @user-jk8sh7fh2d
    @user-jk8sh7fh2d Před měsícem

    Anthu akewa sizothandiza ziko

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw Před měsícem +1

    paja iwe dxina lako ndani

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn Před měsícem +1

    Kkkkkkk oyimba akumalawi

  • @hopembendela
    @hopembendela Před měsícem

    iwe wakhutatu kondole eti

  • @jamesmsonkho4830
    @jamesmsonkho4830 Před měsícem

    Kkkkkkkkkkkkkkk

  • @michaelzuze6516
    @michaelzuze6516 Před měsícem +1

    I regret watching this shit

  • @MarriamBakalie
    @MarriamBakalie Před měsícem

    Ndiwe galu pamodzi ndi akwanu ose stupid guy gud man for nothing.