Hello Zikhale Ng'oma! Kunali anzanu a nkhanza kuposa inu, anamwalira.

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 11. 12. 2023

Komentáře • 114

  • @SameKaposa
    @SameKaposa Před 6 měsíci +2

    Big mumatiyankhulira zakhosi I hope uthengau umufika zikhale yo maonekedwe akeonso ngat wamkulu wa asing'anga

  • @HAROONEASHIRAFF-ht9jt
    @HAROONEASHIRAFF-ht9jt Před 6 měsíci +1

    Ndizofunaka kwambiri kumaudza chilungamo tili munthawi yakuswa kuswa😂😂😂 BAMBO ZIKHALE

  • @EnockDoice32
    @EnockDoice32 Před 6 měsíci +4

    Powerful voice

  • @stanleykaludzu-bm4pm
    @stanleykaludzu-bm4pm Před 6 měsíci +1

    Bring him back Bon kalindo the DC we want to see him walking freely in the Streets of Malawi

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs Před 6 měsíci +2

    Koma abale chaaaaa kd zikhale ng,oma watan watching from mawalian

  • @Shaabann
    @Shaabann Před 6 měsíci +1

    Ulemu wanu big man God bless you tikuziwa zambiri because of you

  • @georgeabigailmaseko-ts3fq
    @georgeabigailmaseko-ts3fq Před 6 měsíci +1

    Following from Western Cape South Africa

  • @PRECIOUSMKUTE
    @PRECIOUSMKUTE Před 26 dny

    Long live this channel 🎉

  • @sweeneykamwendo6251
    @sweeneykamwendo6251 Před 6 měsíci +1

    It's content that people love...keep it up Bro. We're learning more about your vids

  • @user-Grant260
    @user-Grant260 Před 6 měsíci +4

    Always you stand for us elder ❤Watching from Venezuela in Caracas 🇻🇪

    • @user-nj4ob8jw6y
      @user-nj4ob8jw6y Před 6 měsíci +1

      Iweyo bvuto lako umadana ndi MCP, that's why ngakhale udzinena zoti zikumveka, wanthu a ku Malawi, they don't take you seriously. Bvuto lako, u are too obsessed with MCP

    • @user-nj4ob8jw6y
      @user-nj4ob8jw6y Před 6 měsíci +1

      Remember, palibe chipani Cha ndale Cha ku Malawi chimene sichidaphe wanthu . Iwe mchawa nzanga , kwathu ku Malawi , amalamulira ndi aka tolika, ufune usafune, ife a Chawa, tilibe chance. Ngakhale ukuwe pa channel yakoyo, do you think Bakili Muluzi has got an impact? Ukunamatu iweyo

    • @user-ew8lf7zd7u
      @user-ew8lf7zd7u Před 6 měsíci

      ​@@user-nj4ob8jw6y😢❤😢❤❤ ❤❤😮😮😮😮😮😮😮😮😮

  • @MateyuMandera-en5ih
    @MateyuMandera-en5ih Před 6 měsíci +2

    Always you stand 4 us 💗💗💗🌏🌏

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg Před 17 dny

    Ndpo muuzen zikhale ng'oma galu ameneyo watikwana

  • @user-qq3ip1od6i
    @user-qq3ip1od6i Před 6 měsíci

    Keep on doing great job

  • @williammenard48
    @williammenard48 Před 6 měsíci +1

    Sad news about Kalindo

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Před 5 měsíci

    Akulu mukunama zikhale ngoma adzamwalire adzasiye dzikoli nanga udindo womwe ali adzamusiyira ndani zikhale ngoma ndi wamuyaya sadzafa namga ati adzikalandira ndalama kwakagame ndani zijhale ngoma nduna yamalawi yamuyaya mpaka yesu adzabwere

    • @MuhaShaibu
      @MuhaShaibu Před měsícem

      😢 Koma ul bhobho aise kk mutuwo sulbho hope so

  • @user-uf1tz7bp5q
    @user-uf1tz7bp5q Před 6 měsíci +2

    How do you know history from moçambique ine nde moçambique ndipo zomwe ukunenazo zoona zokha-zokha livro De historia Vai contrar todos

  • @user-nx8gy8lq4q
    @user-nx8gy8lq4q Před 6 měsíci

    Big up bro we r following you

  • @user-fp3dt1sz8j
    @user-fp3dt1sz8j Před 6 měsíci +2

    Your the best

  • @victormaulika6523
    @victormaulika6523 Před 6 měsíci +1

    You are the best

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před 6 měsíci

    We have been waiting for this boss

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev Před 6 měsíci

    Big up broh, following

  • @user-oy2bu8vm4t
    @user-oy2bu8vm4t Před 6 měsíci

    The best tv inded

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 Před 6 měsíci

    Koma zoti winiko amene akumumanga sichakwera koma zikhale ng'oma sizowona, zikhale ng'omayo ali pansi pa ulamuliro wa chakwera so chakwerayo ndi yemwe akumutuma ng'omayo.

  • @user-xy4hq6sx7v
    @user-xy4hq6sx7v Před 6 měsíci +1

    Zikhale ng'oma musiyeni azatha ndi anzake aku mcp omwewo ingotini phe mcp ndi mcp mnkango ukanyowa sikuti ndi kambuku ayi

  • @raffickaffick
    @raffickaffick Před 6 měsíci

    Super voice

  • @user-sh4jz7hs3x
    @user-sh4jz7hs3x Před 6 měsíci

    Thanks bro mumatiyimilila

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Před 6 měsíci

    Big love brother ❤❤❤

  • @ibrahimmeemzy9754
    @ibrahimmeemzy9754 Před 6 měsíci +1

    We love you too much ❤❤❤

  • @alfredbanda886
    @alfredbanda886 Před 6 měsíci

    Bulutu Chakwela Nyawuuuu Gule Wankulu masanziiiiiiiiii Enieni Bwantasaaaa,Walisaukitsa Dziko Lamalawi Mwalitenga anga Zakubanja Kwanu Agalu inu .Come 2025 Out and Jailed

  • @user-kg4mh4uu2g
    @user-kg4mh4uu2g Před 6 měsíci +6

    Respect you big brother, keep it up. Watching you from muscat Oman.

  • @alicehananiya
    @alicehananiya Před 6 měsíci

    Azikhale kumwamba kuli mulungu siku Lina mudzasowa chowilingula Bon kalindo ndi munthu osalakwa mukupangilanji? Zotele ndi moyo wake

  • @user-us8dn8ff7b
    @user-us8dn8ff7b Před 6 měsíci

    Wishing you moyo wautali bro mumatimilila

  • @user-qb6ej7jj1d
    @user-qb6ej7jj1d Před 3 měsíci

    Bon kalindo mmmmm alibe maso mphenya awo

  • @japhethjeremulimba
    @japhethjeremulimba Před 6 měsíci +3

    Let's pray for Bon Kalindo

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před měsícem

    Atsogoleri ambiri a mu Africa sakalowa ufumu wakumwamba

  • @jamestsabola1376
    @jamestsabola1376 Před 6 měsíci +1

    Siku likubwela azamwalila ndithu kufuna osafuna

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Před 6 měsíci

    Zikhale ng'oma ndi wamuyaya sadzaona IfA komanso pampando pomwe alipo anayamba po ndiiyeyo sadzacoka zikhale ng'oma wasatanic nkhope ngati usiku wapha mabrund lero ukudzudza prezdent wathu chisiru kwambiri khope yoopsayo ngati mdima

  • @user-gg6uh2wo4x
    @user-gg6uh2wo4x Před 4 měsíci

    Ulemu wanu mr

  • @petermasenti2084
    @petermasenti2084 Před 6 měsíci

    Ndi chifukwa chiyani chakwera sakumuchotsa zikhale ngati ministry of homeland? Ukakwera pa msana pa njovu usamati pansi palibe mame, tsiku likubwera limene a zikhale mulungu azakulangani be warned

  • @user-nn9mx5tt6d
    @user-nn9mx5tt6d Před 6 měsíci

    Always respect u big

  • @humairamalombe295
    @humairamalombe295 Před 6 měsíci

    Atsogoleli a MCP onse ndimasatana afiti anthu okupha

  • @user-om7ol2mp6z
    @user-om7ol2mp6z Před 6 měsíci

    Auzeni zoona zikhale ng'oma chi ndi munthu osaphuzira

  • @TONYJUSTIN-cx7yt
    @TONYJUSTIN-cx7yt Před 6 měsíci

    Best history ❤

  • @HildatoweraMhango-et4mz
    @HildatoweraMhango-et4mz Před 6 měsíci

    Nthawi ikwana ya zikhale mulungu akuonaso asiyeni atase nthawi yawo kuipa kwa chakwera kotenga ma big fish kukhala nduma munthu wakupha ameneyo

  • @user-md5uv2cg6i
    @user-md5uv2cg6i Před 6 měsíci

    Amalawi vuto ndi kuiwalansanga mwaona lero zikhale mutu ngati zungu

  • @siphoshabangu9465
    @siphoshabangu9465 Před 6 měsíci

    I love you brother

  • @ishakatimbe7341
    @ishakatimbe7341 Před 6 měsíci

    Bwana

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Před 6 měsíci

    I really hate MCP zikhale ng'oma azayankha mulando tsiku lina MULUNGU simunthu.
    Koma samora machelo anapha anthu ambili ngati Kamuzu kuno kwathu ndikhulupila tikunena pano ali ku gahena wosewa.

  • @user-xc1xt2qd7t
    @user-xc1xt2qd7t Před 6 měsíci

    Dolo wa madolo ndwe 1 💥🔥💯

  • @user-mz4tk1pw3f
    @user-mz4tk1pw3f Před 6 měsíci

    Zikhala ng'oma uziopa mulungu zimene ukupanga sizabwino

  • @harrymicah6140
    @harrymicah6140 Před 6 měsíci

    😂😂😂😂😂 azikhare ng'oma mwanva komwe muliko

  • @irenechirwa9710
    @irenechirwa9710 Před 6 měsíci +4

    Zikhale ng'oma typing and deleting😂😂

  • @SolomonBewula
    @SolomonBewula Před 14 dny

    Wasala pangono kufa alibe masiku onsewo

  • @ngindechikalodza8051
    @ngindechikalodza8051 Před 6 měsíci

    Zikhale ng'oma akukhala akukhala Ku rwanda

  • @alickchiumia2616
    @alickchiumia2616 Před 6 měsíci

    Kukhala ku opposition ndikowawa😂😂😂😂😂😂

  • @user-qi8xe7qh1e
    @user-qi8xe7qh1e Před 6 měsíci

    Komanso zikhale ng'oma akuyiwala kuti pompano taika chigawenga cha mcp John tembo amene amaona ngati sazafa lero alikuti ndipo wasa sisiliya kadzamila zigawenga zokhazokha zimenezi zazimuna ndizazikazi

  • @BinuelFranqueLamussiLamussi
    @BinuelFranqueLamussiLamussi Před 6 měsíci

    Inuyo ndi big, ndine mozabique, inuyo mumanena zowona zenizeni pitilizani tchito yabwino big.

  • @JosephJosab
    @JosephJosab Před měsícem

    Amuna m'dala bambo

  • @davenchimadzi6529
    @davenchimadzi6529 Před 6 měsíci

  • @timothychilwe5231
    @timothychilwe5231 Před 6 měsíci

    MCP se Boma koma kupha Abale athu komaso kuba

  • @geee7672
    @geee7672 Před 6 měsíci +1

    ...on Bon Kalindo, I think he actuarrly challenges that he misses prison. We cannot defend people who call demonstrations out of political frustration and be paid by frustrated DPP. Kalindo has the bset interest on his stomach. 3 governments never gave him a position due to lack of education. But I also want to to mention that KZN is a savage. He was also involved in the 22 massacre and I would think he was an authority during Chasowa's murder. But even if it were Richard Chimwendo, or myself, I would make sure Kalindo is disciplined. The problem in Malawi cannot be fixed by burning, looting and marching by paying street kids.

    • @user-ld1js7dt3b
      @user-ld1js7dt3b Před 6 měsíci +2

      I can't see your face but I can see mbali yako and you know what we are tired and sick with is so Called mcp that's why anthu sangaiware what they have done to our parents and nthawi achisiru, and they can not take us back thank you

    • @Yahiya-wm8nd
      @Yahiya-wm8nd Před 6 měsíci

      Iweyo chisulu kwambiri

    • @geee7672
      @geee7672 Před 6 měsíci

      @@user-ld1js7dt3b I am equally disappointed with MCP. BUt as poor by choice as we are, we cannot continue sitting on the streets. If Kalindo had a good plan, he would engage the industry captains to create employment than creating looters. We all know that MCP is incapable of turning the tide, we rather remove them in 2025. But we run the risk of worsening the situation by disturbing the already non-existent economy. By the way, currently in Malawi, there's no party that can govern. They are all gangsters and thieves. So creating a nation of looters will never solve any problem beyond 2025.

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 Před 6 měsíci

    Amve ndithu amenewa

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 Před 6 měsíci

    Amalawi zofuna izii okamba odalipo kut namapwala uyu otchedwa chilimayi ndi mzake mfiti chakwera wa Amonika sangapange kanthu koma amalawi kusanva

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk Před 6 měsíci +7

    God is watching what MCP is doing and we are also watching, we have answers in 2025, may God continue taking care of our president, president for the poor

  • @georgechikafutwa1334
    @georgechikafutwa1334 Před 6 měsíci

    ❤❤❤❤

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Před 6 měsíci

    Ndiponso azalirira ching'ang'dza a MCP onse Iwo aku wona Ngati azawinanso panopa Dziko lapansi lonse ladziwa zoti chakwera ndi Tonse alliance ndi mbava zakuba dzitsiru za Wanthu

  • @TimothyJustin-nh6we
    @TimothyJustin-nh6we Před 6 měsíci

    Best hx

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw Před 6 měsíci

    vuto A malawife timangolilira mmimba .zoti tipange action ayi ...Anthu akummwera ife ndife zitsiru.tikungoyang,anira zathu akungomangidwa pasiku katatu . Lero nawo mafumu kumangochi ayamba kurankhura mwamanyi after kurandira Bazi. akuti kumangochi kuno mademo ayi how

  • @jaychikumbu5898
    @jaychikumbu5898 Před 6 měsíci

    akuonekadi oophya nkhope

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před 6 měsíci

    Anthu akadzavotera LAZARUS CHAWERA palibe chabwino. Dzina lamavuto okha. Lazaro wa mubaibulo anali mphawi. Zinthu zizidzakwera daily.
    👆Dzina la matemberero ili. Chonde tiganize bwino a Malawi.

  • @GiftMalawian-kc4cy
    @GiftMalawian-kc4cy Před 6 měsíci

    Eeee

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 Před 6 měsíci

    Oyipa zikhale

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Před 6 měsíci

    Akakhala paudindo kumaona azao ngati makape

  • @austinvincent773
    @austinvincent773 Před 6 měsíci

    Tafika

  • @user-bw2cv9sd7x
    @user-bw2cv9sd7x Před 6 měsíci

    bg tilipambuyo panu muuzeni chilungamo galuu ameneyii kuti sikaleso ayi udindo umenewo ukutha so tell him truth

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 Před 6 měsíci

    Zikhale ng'oma is wish he think police prison is the place to play with

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 Před 6 měsíci

    Ndiye kuti mmene wasowa chonchi, Zikhale Ng'oma akusewera yapansi koma ngati kuli Satana ku MCP Mmodzi mwa iwo ndi Zikhale Ng'oma osayiwala Chakwera

  • @IbrahimDailes
    @IbrahimDailes Před 6 měsíci

    Ka 40 lizakwana palibe wamuyaya iwe zikhale ng'oma ndi chakwela wakoyo

  • @user-rc1gg1yi4m
    @user-rc1gg1yi4m Před 6 měsíci

    Following

  • @kasupeowenpaul
    @kasupeowenpaul Před 6 měsíci

    First to comment

  • @abisalomchunga6695
    @abisalomchunga6695 Před 6 měsíci

    Zoon big man

  • @GenialaChalera
    @GenialaChalera Před 6 měsíci

    Akulu zimene zimakuyamikirani ndi mbuli zizanu bwanji osamafotokozako za kuphedwa kwa Isa njainju anthu azidziwa chilungamo inuyo mcp mumadananayo Ife timangokuvetserani cadet

    • @ibrahmdoka7486
      @ibrahmdoka7486 Před 6 měsíci

      Iweyo mbuzuwe osalongosola zimenezo bwanji...mphaka

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 Před 6 měsíci

    Zoonadi a ng'oma axaona zowawa

  • @KondieOne
    @KondieOne Před 6 měsíci +1

    Wati ziiii Zikhale pano kaya ali kuti

  • @AllieKaisi-je6rm
    @AllieKaisi-je6rm Před 6 měsíci

    Akamuna mumatiimilira koma letter BOM sindikuziwa kuti amapanga bwanji nanga BOM ingakwane mu invulopu?

  • @user-ti2ct8ts8d
    @user-ti2ct8ts8d Před 6 měsíci +1

    Zikhale ngo'ma paujeni pako wamva??? Ukuzuza kalindo tizaonesana ubwino wake mukutuluka mboma

  • @AYATU730
    @AYATU730 Před 6 měsíci

    Wachibwana zikgare yo

  • @williamchunga9398
    @williamchunga9398 Před 6 měsíci

    Munthu wapachifila Kona kuvuta too much

  • @allieyusufmtiwiliwi8498
    @allieyusufmtiwiliwi8498 Před 6 měsíci

    Wina chinsalu chankachisi chidzamung'ambikira pakati

  • @Goliath461
    @Goliath461 Před 6 měsíci

    Zoonadi tikumanatu ameneyo oky

  • @Razarusmbavachakwera
    @Razarusmbavachakwera Před 6 měsíci +1

    RIP zikhale ng'oma and chakwera

    • @CalistoRichard-it8ot
      @CalistoRichard-it8ot Před 6 měsíci +1

      Not RIP BT sndikuziwa chizungu chake km asaksuse mumtendele km wakumoto bas

  • @jahiemmusa8796
    @jahiemmusa8796 Před 6 měsíci

    asikale ng'oma ndgalu wamunthu

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 Před 6 měsíci

    Power of MCP Boma la MCP khalidwe lawo lakhaza bass but god is watching this

  • @user-oy2bu8vm4t
    @user-oy2bu8vm4t Před 6 měsíci

    The best tv inded

  • @user-lx5he8rv7n
    @user-lx5he8rv7n Před 16 dny

    Koma mfana iweyo!!!!

  • @williamchunga9398
    @williamchunga9398 Před 6 měsíci

    Munthu wapachifila Kona kuvuta too much

  • @GiftMalawian-kc4cy
    @GiftMalawian-kc4cy Před 6 měsíci

    Eeee

    • @user-de1mt5su8i
      @user-de1mt5su8i Před 6 měsíci

      Ngati kuli zitsiru za wanthu ndinu wanthu mumacomenter nonsense alomwe