Velikost videa: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Zobrazit ovladače přehrávání
Automatické přehrávání
Přehrát
Only one of the best channel never wanna miss everyday
Keep it up. You make us to understand some issues which happening all over the world ❤❤
You are number one my brother ❤❤❤❤❤❤❤❤
You are quite right man, I'm here in South Africa for decade and it's true
Tipasen part 2 as soon as possible plzzz brother we will always appreciate what u doing to us❤
Waiting for part 2 u r no 1 my brother that's why l like this channel
Keep it up
Eeeeee abwana inuyo ulemuwanu 😮😮😮 eee mumandi gometsa heavy
Very well explained indeed, you 're doing a great job
Waiting patiently for next part
That's true my brother palibe apolice achinyengo ngati aku RSA. Koma ntembo anagwilisawu anachita kupanga kidnap nyamata wina pano DNA yinapanga match.
Big up and keep it up bro.
More fire muluzi channel 🔥💯👍👍
Thank bro for updating us South Africa ndiyo Sodom ndi Gomorra.Thanks again bro for all update you give us here, pitilizani
Bg ndinu dolo bc apapa ndipomwe anthu ambili axiyambani kukusatilani bwino bwino
So interesting story keep it up you're so great ,so what is next for this story 😀 😄
Mumandisangalasa mwanva apartir de Moçambique malawi is my neighbor 😍
Wow ,,,,, that's was my request
I salute you brother you're number one
Waiting for part 2
Your the top one ! Ndinu munthu wamkuludi brazah! Palibe angadutse pa inu mwayitha ndikudyadirani man! Top channel palinso wina bwana pilizani man!
Following boss
big up boss
But please don't forget to give us update of Ukraine war and sudan civil war tikamva mau timamva kukoma olo tikhale nd njala
Well explained bro
Well explained 👏 👌
Best tv
Mumakwana ❤
Zikomo brother tayisatila nkhaniyi
Kkkkkkk eish nkhani iyi ndiyodabwitsa kwambiri , G4S idathawitsa Thabo Bester.
Big Mumakwana Ulemu wanu . Koma kodi zaku Ucrânia simuponya masiku wano, kodi pano zilipati ?
I like you so much bro timakunyadilani kwambili love you ❤❤❤❤
Part 2 changu boss
Kkkkkkkkkk anayasa chi fire anthutu anazama heavy
Eish !! Brother inuyo ayi ndithu mumakwana heavy ndimakunyadirani koopsa
Nkhani yamkulu uyu yavuta kwambiri paMzansi pano ndipo uyuyu aaaah ndimunthu oipa eeh
Man mumayitha
Timadikira imeneyi mumaitha big
This is true that's why I like u
You are no one brother keep it up ❤❤
Eee bro nkhani ya Thabo sindimaitolela apa mwaitha bro
Anthu amazama patali 😂😂😂😂😂zangondikomela
Chonde chonde tikudikila part 2,,, live in Johannesburg south Africa
Inuyo a BM tv ulemu wanu kukupangani hirer munthu utha kukhoza history ndithu ok BK pitilizani nkhaniyi mpaka pamapeto
First to comment this is nice
Kodi sopano akulu mumatha kupanga ma history, bwanji history yanu sumulengeza
❤️❤️❤️
Waiting part 2
I need Oliver mtukudzi History bro
Here in Africa south Africa too much clooks ever
Bakili muluzi Tv 🎉🎉🎉🎉
Thanks polongosola bwino
Hahaha anakathawira Ku Russia or America... But thanks for good expiation
Kom inuyo big smunama.
Zoopsa
Kodi zoona akuti thabo uja si thabo maligana mene anakaonekela pa court akuti asiyana kwambiri ??
Amaba mitembo ndi kupanga demand insurance pamtembo omoz ankapindulapo 2 milion rand
Respect 🙏 brother
BIG 👍
Ayaya akufunika alowelelepo pomuthawisatso pamasengano
You forgot to start with why he was there in the first place
Let's grow🔥🔥
Yinuyo ndiwakulu basi yife pheeee kunvesela mumakwana
Ngat Kuli Kotheka kupatula za ndale zija muzitipatsila patsilaso mbilizi bwana ife timakondwa tikamamva zimenez
South Africa ndi dziko lachinyengo
Kod iyeyu anamangidwa chifukwa chan? Nanga kulemera kumeneku amatani?
I like you brother koma ku rasha n uklean zili pat?
USA 🇺🇸 🇺🇸🇺🇸🇺🇸🇺🇸🇺🇸
First comment 😊first comment
Thabo Bester ameneyu anakwa chani mpaka zaka 10 ku prison
Ndi chigawenga choopsa komanso ogwiririra
ulemu wanu wanu
Apapa ndimanvela ngati ndikuwonelatu movie brother inuyo anakhonza
Tiuzeni zoona abro
Okay so what ur plan
True
💪💪💪👍
Kodi adalakwa cha
Kupha azimayi kuwagona kuwaphanso
Mwayita wakulu
amwene inuyo ndimakunyadilani kwambili
This guy ndi Dolo heavy and atathawa anayamba kusunga tsitsi ndi ndevu itakhala movie ndi kawawa
kkkkkk ndimakuvan captain ulemu wanu slut
Bravo
Only one of the best channel never wanna miss everyday
Keep it up. You make us to understand some issues which happening all over the world ❤❤
You are number one my brother ❤❤❤❤❤❤❤❤
You are quite right man, I'm here in South Africa for decade and it's true
Tipasen part 2 as soon as possible plzzz brother we will always appreciate what u doing to us❤
Waiting for part 2 u r no 1 my brother that's why l like this channel
Keep it up
Eeeeee abwana inuyo ulemuwanu 😮😮😮 eee mumandi gometsa heavy
Very well explained indeed, you 're doing a great job
Waiting patiently for next part
That's true my brother palibe apolice achinyengo ngati aku RSA.
Koma ntembo anagwilisawu anachita kupanga kidnap nyamata wina pano DNA yinapanga match.
Big up and keep it up bro.
More fire muluzi channel 🔥💯👍👍
Thank bro for updating us
South Africa ndiyo Sodom ndi Gomorra.
Thanks again bro for all update you give us here, pitilizani