May GOD bless you all the time Father Nthalika, anatenga Boma kuti atizunze anthu awa, Mulungu awasegure mason awone momwe amalawi akuzunzikira, Nonse omwe mumalankhulira Boma muopen Mulungu musanalankhu zanuzo.
Lazalo munthu oyipa mtima kwambiri ndipo umunthu unachoka kale kale mwa iye,zoti ankatumikira nkachisi wamulungu ndakayika ndithu. Ambuye atichitire chifundo atichotsere chipsyinjo chimenechi,Lazalo ndi chiwanda. Tiimba bwanji nyimbo ya Chauta ku Bagamoyo.
I love FR Mthalika me my late brother Jackson Mapira.
I am so touched, Mulungu apitiridze kukudalitsani
Powerful massage
Good message our Catholic church you are standing the truth of Hall Malawian keep it up good work and don't lose your hopefully 🙏🙏
Wansembe uyuyu amandiwaza kwambili. May good Lord continue protecting you father Nthalika
Very powerful message ❤
Thank you father, you really preach, I silute you.
Mulungu apilidze kukupatsani utumiki wabwino❤ I love you Mr mthalika ❤❤❤
Amen Amen uthenga wamphamvu ❤❤
Thank you father may lord continue bless you with powerful massage
Powerful message
Powerful massage father
A LOUDER AMEN ❤
Powerful message, I feel sorry with Chakwela
Glory to the God❤
May GOD bless you all the time Father Nthalika, anatenga Boma kuti atizunze anthu awa, Mulungu awasegure mason awone momwe amalawi akuzunzikira, Nonse omwe mumalankhulira Boma muopen Mulungu musanalankhu zanuzo.
Amen, mwayankhula ndi moyo wanga komanso moyo wawo.
Apapa payankhulidwa za mzeru. Tsoka kwa iwe amene samamva mau ochokera kwa anthu ozodzedwa ndi Chauta
Feel you father ❤
Amen and amen 🎉🎉🎉
Powerful 🔥
Amen
Amen Amen
Ambuye atithandize 😢😢
Amen.
Emen my father muthalika
❤
Mpingo umakafikila munthu pakhomo Pake direct
God protect you kut mupitilize ntchito yake, don't fear at all
Tithokoze ma bishop anthu,,, ndizowona andale akuwononga dziko lathu lantendere ,,, pitani mukamedye ndi bayibulo chakwerayo
True
Kaya mnene bwani zanja lamulungu likalemba lalemba inu inu ansembe napeleka mwana wamlungu yesu koma kumapeto mnziwona zimene anachita mlungu mabibishopu simulungu khulupililani mlungu lye ndiye yankho
Eeee koma mcp 🙌
Mau kulimasula Kalata mwamvemvemve .
Kkkkkkkkkkklk olo nunkhila ndi mcp
Lazalo munthu oyipa mtima kwambiri ndipo umunthu unachoka kale kale mwa iye,zoti ankatumikira nkachisi wamulungu ndakayika ndithu. Ambuye atichitire chifundo atichotsere chipsyinjo chimenechi,Lazalo ndi chiwanda. Tiimba bwanji nyimbo ya Chauta ku Bagamoyo.
Anthu a Mulungu okhawo ali ndi chilungamo. Zikomo ambiye posankha ndikuzoza anthu anu.
Zoona zoona chilungamo chokhachokha tili kubagamoyodi
Tivotelanso DPP chifukwa zinthu zimatchipa Komanso Malawi amamudziwa Kuti ndiovutka lelo wina aliyense angadzule athane naye ATI Iwo Koma ndabusa
Zamphavu
Yankho la mwana okula mtima
Anthu awa ndi abodza agokhutisa mimba zao zomwe akugawazi nzopanda pake this is campain
Palibe chimene chingazasithe ndimavuto okha okha ena anali akhaza ena kumpha alibino pano kuwola ndalama zaboma osaganizila anthu
Usazinamize iwe kunkuyu n abare ako kuti ungawanyenge anthu ndikuwapasa chakudya n ndalama .Tonse n wa ku DPP ngakhale n ku baga moyo komabe bolako
Eeeee yankho awa anyanya kubakwake chilichonse chikuavuta Komanso usatana waonjeza
Mcp mulungu akulangani ndi mwanowanuwo anthu akamakulangixani mwanotho chifukwa ambili mwainu mulikale ndi ziwanda xaumbava
Kod ulalik kapena zandale tikafika zandale votelani dpp chifukwa iwowo amapha malbino njaunju robert chasowa ndi ena ambili sindinu mtumiki mlape mulungu safuna kumsakaniza
Ikapusa mcp zikoli 2025 lixakawikana pa 4 azizabelanawokha pachigawo chapakat akamapanga mwanowawo umatinyasa
Toooooooonse tagwirizana kaaaaaale...kuti 2025...ndi D .....P.....P.....baaaaaasi.....zinazi ndi manyaka enieni....ngakhale atapatsidwa zaka 50...palibe chimene chingachitike..😂😂😂😂😂😂😂
Chakwera ndi mtumiki WA satana
Nonsense
Boma ili ndiloipa kuposela maganizo asatana
Amen
Powerful
Zoonadi zimenezo mavuto okhaokha basi