Komentáře •

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 4 dny +12

    Mau amphambvu ndithu Mulungu apitilirebe kukhala nanu kukutetezerani komanso akulitse malire amoyo wanu abusa Amen

  • @TamandaWekha
    @TamandaWekha Před 2 dny +2

    Awawa amalalika okunva wanva osanvaso akhale mosanva momwemo. Powerful preaching

  • @user-hi2rh8ks3r
    @user-hi2rh8ks3r Před dnem

    Very good preacher.very good preaching for everyone

  • @MosesPhiri-q7x
    @MosesPhiri-q7x Před dnem

    Wow great preaching man of God ❤❤

  • @namasawaninkhoma3856
    @namasawaninkhoma3856 Před 4 dny +5

    Zikomo Abusa Mau Achilimbikitso. To God be all the glory.

  • @user-vn2mz7qd5i
    @user-vn2mz7qd5i Před 2 dny

    Uyu ukuyenera kukhala mlangizi wa a president on religious affairs l ❤ you Rev Yasin Gama

  • @ernestjuniormbanga3370
    @ernestjuniormbanga3370 Před 4 dny +4

    Powerful preaching

  • @reubenphiri4907
    @reubenphiri4907 Před 4 dny +3

    2:08 Ambuye alemekezeke chifukwa cha uthenga umenewu. Ndikungoganizira kuti abusawa akanakhala ndi nthawi yokwanira, chachitatu chomwe Yobu anachichitabe modabwitsa tonse ndi chakuti, ngakhale anzake a mkulu ameneyi anamunyozanso kufikira kunena kuti analuza zonse chifukwa choti anachimwira Mulungu, koma iyeyu sanawamvere, koma analankhulabe zomutama Mulungu pa moyo wake. Yobu 13vs13-15

  • @davidngomaministry
    @davidngomaministry Před dnem

    Amen powerful message 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🔥🔥🔥

  • @benedictchiwaya3043
    @benedictchiwaya3043 Před 4 dny +1

    May God bless you&protect you in all aspects. Chakwera must listen &change

  • @DolicahGift
    @DolicahGift Před 22 hodinami

    Amen and amen Ambuye azikudaritsani abusa🙏💕🔥

  • @MaryNgwira-s5z
    @MaryNgwira-s5z Před 4 dny +1

    Inu nda busa weniweni osati akupha wanthu ambuye akuze malile amoyo wanu ndi masithika ndi ulaliki wanu amen and amen

  • @marydaka3207
    @marydaka3207 Před 4 dny

    Amen. Very powerful message!!

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx Před 4 dny +5

    A gama lalikirani amve a chakwera mau amvetsetse kuti mulungu ndiyankho nthawi zomse

  • @NoahChikweza-xn1fh
    @NoahChikweza-xn1fh Před 4 dny +3

    ❤m'busa kulalikira Kwa m'busa Zake😂😂

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly Před 4 dny +4

    Ndiye mumuone kunkuyu ndizikhaleyo kkkkkk ngat akudabwatu afiti kkkkk mukanthidwa kuli Mwari kudenga just wait chakwela ngat akumva nkhutukumve yeniyeni Mulungu akupeleka uthenga tiyenazoni

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 Před 4 dny

    You are blessed sir. God continue to bless you

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 Před 4 dny

    Very powerful preaching 👏 🙌 🙏

  • @vincentlamanmathebulamwana5697

    Mashallah 🙏 abusa,mau anu,nkhope yanu,thupi lanu likutipasa ma answers abwino,mulungu azikudalisani😢

  • @AkusankhaNkhoma
    @AkusankhaNkhoma Před 10 hodinami

    God bless pastor yasin

  • @CharlesFalakeza
    @CharlesFalakeza Před 2 dny

    Amen and amen Abusa uthenga wachilimbikitso Amen

  • @phillipmphanda2163
    @phillipmphanda2163 Před 4 dny +1

    Mawu ogwila ntima ambuye adalitse mawu amenewa Amen 🙏

  • @CosimassShyman
    @CosimassShyman Před 4 dny

    This is powerfully teaching that is affecting full life

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani Před 4 dny +1

    Ufulu wanokha a mcp umenewu mwatiphera Chilima ndiye nkumati tilimu ufulu?

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e Před 4 dny +8

    Amene koma asogoleli osaopa mulungu akumangobela a Malawi osauka kumangolemela amodzi modzi mulungu awayankhule mwapadela

  • @RachelNathan-yv5zc
    @RachelNathan-yv5zc Před 4 dny +1

    Ameni ameni ameeen . MULUNGU akudalitsen Abusa Amen

  • @MaryChihana-bm9jo
    @MaryChihana-bm9jo Před 4 dny

    Ambuye alemekezeke ,ndipo Mulungu apitilize kudalitsa ndikuchjitira chifundo Malawi AMEN.

  • @NDHLOVULASTON
    @NDHLOVULASTON Před 12 hodinami

    Powerful message

  • @MarkManyowa
    @MarkManyowa Před 4 dny

    You're our own Prof Lumumba In Malawi
    Love you

  • @Chifundoaustin
    @Chifundoaustin Před 4 dny

    Amen. Powerful massage

  • @GeorgeKafaamveka
    @GeorgeKafaamveka Před 3 dny

    To I very sorry to those who didn't listen properly the preaching, it's not Chakwera, it was a general powerful preaching even to those in a opposition who chose not to attend the function. Those are real witches and thieves

  • @MaxwellChiwaya-tv7kn
    @MaxwellChiwaya-tv7kn Před 4 dny

    God bless you pastor Gamba

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e Před dnem

    Amen and Amen powerful 🙏 🙌 👏

  • @monicamatambo6969
    @monicamatambo6969 Před 4 dny

    Glory be to God. My faith is lifted up.

  • @Albertngwira-vy3th
    @Albertngwira-vy3th Před 3 dny

    Amen more wisdom

  • @user-gm3cx2xn9o
    @user-gm3cx2xn9o Před 4 dny +4

    Tikamati uyuyu anabwera kuzatumikira anthu ku umzimu ❤❤❤ amen

  • @user-js6xn9qj1r
    @user-js6xn9qj1r Před 4 dny

    Powerful man of God 🙏🙏 Amen

  • @user-di4ry5pi1e
    @user-di4ry5pi1e Před 3 dny

    Amen powerful message ❤

  • @fannyeric
    @fannyeric Před 2 dny

    So powerful 👏

  • @Sammy-vb1ed
    @Sammy-vb1ed Před 3 dny

    Amen abusa God bless you ❤❤❤❤.

  • @cathbertkadammanja3446
    @cathbertkadammanja3446 Před 4 dny +1

    Yobu had one wife and David had many wives but the commonly recognized wives were 8 Bible limodzi lomwelo lomwe timati buku lopatulika la mawu a Mulungu.
    I wonder why many people run away from that uncircumcised truth.
    Indirectly a Yasini Gama akuti kukhala nd akazi oposela mmodzi ndi ntchimo zomwe zili zosemphana ndi zomwe limafotokoza buku lopatulika.

  • @user-qz1jm5nm6d
    @user-qz1jm5nm6d Před 4 dny

    Powerful massage 💪💪💪

  • @NellyMasakatira
    @NellyMasakatira Před 3 dny

    Amen abusa mau amphamvu.

  • @user-wt5mf5kv6u
    @user-wt5mf5kv6u Před 3 dny

    Amen Abusa wakumva wamva

  • @VicterKumanda
    @VicterKumanda Před dnem

    Amen ndizowonadi

  • @user-fe7fb3nw5h
    @user-fe7fb3nw5h Před 4 dny +1

    Emeni auzeni mopanda matha mulungu awa Kathe zed

  • @user-lc4ll8td5f
    @user-lc4ll8td5f Před 4 dny

    Always God news is powerful big up of God!!!

  • @user-dz5go4dd8i
    @user-dz5go4dd8i Před 4 dny

    Great preaching

  • @Patricia_Chisankha
    @Patricia_Chisankha Před 4 dny

    Amen Pastor!

  • @moureenmolesi
    @moureenmolesi Před 3 dny

    amen papa

  • @GetrudeKambwazira
    @GetrudeKambwazira Před 3 dny

    Wow powerful

  • @EmilyKabaride
    @EmilyKabaride Před 4 dny

    Amen 🔥🔥🔥mwawuka amveka

  • @BenGravelNkhoma-tw4vu
    @BenGravelNkhoma-tw4vu Před 9 hodinami

    AMBUYE alemekezeke cifukwa cauthenga wabwino

  • @stelladolizyi
    @stelladolizyi Před dnem

    A yasin Gama kulalika mopanda mantha ngati akhalira mfuti

  • @user-uv3gm5bb8x
    @user-uv3gm5bb8x Před 4 dny

    0:42 Powerful massage Amen and Amen

  • @GladysKapasula-x6w
    @GladysKapasula-x6w Před 2 dny

    Amene abusa mumtidaritsa

  • @thokokankhunda7725
    @thokokankhunda7725 Před 4 dny

    ulendo uno i give salute ...amen osati kumalalika za ma buckets

  • @JMB804
    @JMB804 Před 4 dny

    Amen pastor

  • @John-to8gl
    @John-to8gl Před 4 dny

    Amen abusa ulaliki wamphamvu ❤❤

  • @SallamDishan
    @SallamDishan Před 4 dny

    amen mawu achilimbikitso may God be with you

  • @evelynmakhaya2756
    @evelynmakhaya2756 Před 4 dny

    powerful preaching

  • @user-el8to1te3l
    @user-el8to1te3l Před 3 dny

    Amen amen and amen

  • @AyandaJanga-fe7wp
    @AyandaJanga-fe7wp Před 3 dny

    Powerful man of God

  • @PempheroAlufandika
    @PempheroAlufandika Před 3 dny

    Mbusa uyo aaaaa Ali ndi ndi mulungu wapepheratu mwa maso a tsogoleri

  • @LytoneMwatibu-gk6il
    @LytoneMwatibu-gk6il Před 2 dny

    Alalikira bwino abusawa🙏

  • @wilfredgomba3362
    @wilfredgomba3362 Před 3 dny

    Good

  • @GeniusLloyd
    @GeniusLloyd Před 4 dny

    Powerful words

  • @IbrahimPhiri-ky5jk
    @IbrahimPhiri-ky5jk Před 4 dny

    Mulungu akudalinseni chifukwa chachinthunji kulinga ndi dziko lamalawi komanso ndimiyoyo yamansiku ano yomwe tilikudunsamo 🙏🙏🙏

  • @moureenmolesi
    @moureenmolesi Před 3 dny

    amen postar

  • @corneliusthindwa
    @corneliusthindwa Před 4 dny

    nice paster

  • @user-sy6sy9lg2b
    @user-sy6sy9lg2b Před 3 dny

    Muwuzeni chakwela aside khupa anthu wosalakwa

  • @JowasiMasina-fy8ji
    @JowasiMasina-fy8ji Před 4 dny

    Mau amphavu wakuva wamva osamvaso sanave koma ambuye adalitse mau amene

  • @user-yu9fe5nv1u
    @user-yu9fe5nv1u Před 2 dny

    Amen and amen 🙏

  • @spargomw
    @spargomw Před 4 dny

    Amen Abusa

  • @Nomsa77
    @Nomsa77 Před 4 dny +3

    Mwalalika wakumva wamva

  • @user-jx7of6op8i
    @user-jx7of6op8i Před 3 dny

    Mau ndamenewo mwanva

  • @EthelLikagwa
    @EthelLikagwa Před dnem

    Zikomo mulungu akuze moyo wanu

  • @BernardoHonorio-ir2io

    Amén!!!

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 Před 4 dny

    Azikazi aYobu onsewo analikumenekowo in men's suits wo

  • @AlepharMakawa
    @AlepharMakawa Před 4 dny

    Abusa mulungu akudalitseni osati Ena woyipawo

  • @KingNgOma
    @KingNgOma Před 4 dny

    Chirungam mwayankhura abusa amen

  • @user-ce4ee7fx2w
    @user-ce4ee7fx2w Před 2 dny

    Amen and Amen

  • @blessingmanda
    @blessingmanda Před 4 dny

    this was powerful

  • @fikiremussa5961
    @fikiremussa5961 Před dnem

    Mawu achilimbikitso. Ambuye adalitse mawu ake

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 4 dny

    Kodi inuso abusa mwaganidza kudya nao ndalama dzamagazi 😢😢

  • @hudycorex1893
    @hudycorex1893 Před 4 dny

    Powerful!!!

  • @user-rn7wv8ze3v
    @user-rn7wv8ze3v Před 4 dny +1

    Munthu ngati pakamwa pali Chibazi sasowa mubusa Yasin chabazi chamupweteka

    • @JoyceGondwe-ve1zu
      @JoyceGondwe-ve1zu Před 4 dny

      Maganizo inu. Inunso penanso akukudandaulani you're not 100% . God is the only judhe

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 Před 4 dny +2

    Chakwera mbole yamako mwana wasatana

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Před 4 dny

    Amen amen Mtumiki 🙏🙏🙏🙏🙏

  • @christophermkweza7313

    Chakwera wazimvera yekha

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Před 4 dny

    Zikomo kwambiri abusa anthu Mulungu azikudalisani ku nthawi zonse.
    Koma achakwera ndi nduna zawo sakuva mawu a Mulungu ali pompo koma mawu a Mulungu akupita ku nkhongo. Malawi siziko laumphawi bwanji azitsogoleri akulemera ndi mabanja awo. Malawi wakusowekera atsogoleri ngati inu abusa athu.

  • @JessicaManda-zm1ug
    @JessicaManda-zm1ug Před 4 dny

    Amen powerful

  • @JustinChinombo-dy6tp
    @JustinChinombo-dy6tp Před 4 dny

    Ambuye azipitiliza kukudalitsani abusa, mawu amphamvu kwambiri awa

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi Před 4 dny

    Masha Allah

  • @user-rh1pw4nt2r
    @user-rh1pw4nt2r Před 22 hodinami

    Amen

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv

    Mamvuto athu siwochokeka Kwa Mulungu ayi Koma ndiochita kupanga afisi ena Ake ,
    Ati kuzilemeletsa okha nde must mpaka liti pepeza simufika angakhale 150 years muli Moyo ,
    mukafika 100 years mwakhala Kona kuyika shugar mkamwa mwanumo osamumvayi kumangotuluka thofu ,mukankhanthidwayinu musiku lomaliza nde popeza simuopa hayi chabwino

  • @mervinchilunjika-cs9te
    @mervinchilunjika-cs9te Před 22 hodinami

    Awa nde odziwa kulalikira

  • @ZainabPhiri-g5c
    @ZainabPhiri-g5c Před 4 dny

    Ulaliki ogwila mtima 9:54

  • @samuelazumah1050
    @samuelazumah1050 Před 4 dny

    Chakwera ukunvakoma

  • @HarryChikandira
    @HarryChikandira Před 4 dny

    Uthenga wa mvemvemve tisiye kutembelera dziko lathu .timuone ,Malawi pamalo takhalapo osaloza kwina abale.Mulungu atidalitse tonse.