Azisogoleli ameneqa onse alandile ma thembelelo kuyambila ana awo komanso zizukulu zawo za ana awo onse amene azadye ndalama zomwe akubasi za anath osauka alandile thembelelo ndibkhate mu zina la yesu....
God is speaking to the government of Malawi anayiwala kuti kunja kuno kuli Mulungu, akupembedza ndalama. Mulungu dzukani pa mpando wanu wachifumu mutimenyere nkhondoyi
Ameen ameen abusa. Apa boma palibe koma chizuzo basi kuononga dziko uku. Koma apa pakufunika nkhondo ambuye atithandize.chifukwa ngati afika pomupha chilima ife ationa ngati ndani.koma nkhondo ndimeneyatsala basi
😂😂😂😂😂😂😂Koma guys ine ubwino wake sindinavoterepo chipani chilichonse than DPP chibadwireni😂😂 Thalika eeeeee ai ndithu ubwino wake amakamba chilungamo 😂😂😂😂😂😂
A Bishop mwalitha bomali, ndipo kumene ali Chakwera sakugona ndi m'mene mwatulukila ma Bishop. Chakwera ndi boma lake la MCP lalephera tatopanalo.
Azisogoleli ameneqa onse alandile ma thembelelo kuyambila ana awo komanso zizukulu zawo za ana awo onse amene azadye ndalama zomwe akubasi za anath osauka alandile thembelelo ndibkhate mu zina la yesu....
Amen! Father Ambuye azikutetezani.
Anthu amulungu kugwa kwa munthu openphela amalandila nazo Themberelo.
Chilungamo chokhachoka. Zokhumudwitsa wina tinamusankha anali M'busa..koma lero anasanduka ..
Amen abusa inuyo mumatha
Amen and amen mulungu atithandiza kumeneya nkhondo imeneyu
God is speaking to the government of Malawi anayiwala kuti kunja kuno kuli Mulungu, akupembedza ndalama. Mulungu dzukani pa mpando wanu wachifumu mutimenyere nkhondoyi
Mawu amalenga. Amen Father
Ulemu wanu Abusa ❤❤❤❤❤❤
Father mumakwanisa ulaliki wanu wabwino kwambiri
Amen abshop
Chilichonse chili ndinthawi koma na apapa zafikapa Ambuye chitaponi kanthu mwasanga
Zowona ndithu, malawi akufunika ma demo kuti akozeke
Mau amphamvu zedi
True talking man of God
@@user-mj2te7vl6p Kung'alula
Amen father
Chakwela azindikile kuti akadzangotuluka boma akutengedwa komaso manganya ndi wa MCP asamatinamizepo apa
Amen father 🙌🙌🙌
Amen father Amen mau mau
Ifeso talanda bwana😂😂😂😂😂😂
Palibe zofuna kutchuka chilungamo chinenedwe achulewa a mcp anapha anthu pangoz ya ndege( chilima) ndi ena onse
Tikufuna anthu olimba mtima kumalawi kuno ngati fazzala awaa
Momwemo abishop
Wow this is charming
Menyani nkhondo ambuye
Emen ambuye achitepo kathu ndithu
Amen
Amen mau awa agwile ntchito kwa woipayo kuti Malawi apulumuke
Amen Amen
Amen 🙏
Ameeeeen Father
Uthenga uwuwu ukamufika woipa chikumbu mtima chimugwile
Ameen ameen abusa. Apa boma palibe koma chizuzo basi kuononga dziko uku. Koma apa pakufunika nkhondo ambuye atithandize.chifukwa ngati afika pomupha chilima ife ationa ngati ndani.koma nkhondo ndimeneyatsala basi
Abusa awawa MULUNGU awapatse moyo wautali.imfa ya chilima akatolika sakugona ndipo akati apemphere amakhala serious mcp bro apule samalani
Mulungu wanthu ndi lawyer basi
Munthu wamulungu walankhula apa
@@WilliamBandaWili Kung'alula
Ameeeen father
Ine aroma ndimayiziwa ndiyimeneyi kafuseni malemu kamuzu aroma sia mcp
Mau ogwila mtima zoona .
Mukatenge chinzukwa uko Kuti chilamulire Amalawi mwandilidza😢
Kuyakhula kumeko abusa
Abusa
🙏🙏🙏
Mau amphanvu 🙏
Akufuna kutchuka awo
Iwe osatchuka bwanji? Kapena umaweta ng' ona za mcp ati?
Iweyo tchuka panyo pako
Alleluia Abosa naneso ndi banja Langa ndaitengako mulungu afufute ndithu!!!!
😂😂😂😂😂😂😂Koma guys ine ubwino wake sindinavoterepo chipani chilichonse than DPP chibadwireni😂😂 Thalika eeeeee ai ndithu ubwino wake amakamba chilungamo 😂😂😂😂😂😂
@@user-uc1pd1tc2x 🤣🤣😂 akhale ndima lawyer 20 tu uyu
@@MalawianCamerachilungamo sichidzamangidwa chilungamo sichidzabitsidwa mpakana chidzaululika ndithu
@@MalawianCamerachilungamo sichidzamangidwa chilungamo sichidzabitsidwa mpakana chidzaululika ndithu
🎉🎉🎉🎉😅
@@patriciacraiton-sf5vu 😃😃😃😃😃Inee ndiwa APM mpakana kale Pat ukudziwanso iweyo ♥️♥️♥️♥️🤗🤗
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen