Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za IMFA YA OYIMBA M'malawi...

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 5. 09. 2024
  • Mverani kufotokoza kwa a Twaibu pa imfa ya oyimba nyimbo m'Malawi...

Komentáře • 68

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Před 10 měsíci +9

    100% agree, ndimakangana ndi ena pa imfa ya martin nkhana, ndimanena zimenezi kuti anyamata akwathu atha chifukwa chofuna kutchuka,
    Iiiiiiiiiii Ndinayipalamula kwa ena Amalawi, lero ndi izi apululukabe kukonda kutchuka. thank you brother Twaibu. Zimene akuyimba zaziiiiiiii

  • @user-up5wp2hp3f
    @user-up5wp2hp3f Před 3 měsíci +2

    Liwu la ofuula mchipululu kuyesesa mtumiki kulira achinyamata km ayi ndithu vuto kukana kutchipa,ngati kut kugahenako tizikanjoyaso ngat tikuchitiramu.God have mercy

    • @RyleChole
      @RyleChole Před měsícem

      Kuchita chilugamo ndidongosolo la Mulungu m'bale

  • @user-en8bk1hm7z
    @user-en8bk1hm7z Před 10 měsíci +3

    Mr Twaibu maso auzimu mulungu apirize zivumbuluso zake pa inu. Ambuye akudalitseni

  • @PetroKachingwe-jf7dh
    @PetroKachingwe-jf7dh Před 10 měsíci +4

    Amen mtumiki Twaibu
    Yehova Mulungu wamphavu zonse apitilize kutisamalira
    Amen

  • @melaku6264
    @melaku6264 Před 10 měsíci +6

    Mr twaibu mulungu apitilize kukudalitsani ndikukusungilani moyo wautali mukutitsegula maso amen

  • @user-xh4bu5he9r
    @user-xh4bu5he9r Před 10 měsíci +3

    Keep on posting more plz, we are being blessed with your massages😂. from Zambia

  • @romanmanjolo1991
    @romanmanjolo1991 Před 10 měsíci +2

    So blessed by these messages
    Keep doing this great work
    And almighty God of the most high be with you always to protect.

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi Před 10 měsíci +2

    Zikomo kwambiri shek twaibu ndipo mwafotokoza modekha komanso momveka bwino Mulungu aonjezere mpweya womwe mumagwilisa ntchito polondoloza anthu muchifuniro chake

  • @user-xh4bu5he9r
    @user-xh4bu5he9r Před 10 měsíci +2

    From Zambia,pitirizani osaleka mpaka kumapeto

  • @dennismwenifumno994
    @dennismwenifumno994 Před 10 měsíci +1

    I know you man of God and all what you say I believe because is what you went through and you was doing it before.. may God help us in this end time as you continue telling us the truth....

  • @gracemotta7818
    @gracemotta7818 Před 10 měsíci +3

    Thanks now tadziwa

  • @albertkambuwa1329
    @albertkambuwa1329 Před 10 měsíci +4

    Sakubakila bushiri koma akuti imfa iyi sikumukhudza koma naye ana peleka mwana wake

  • @successngoma
    @successngoma Před 10 měsíci +2

    Mulungu akudise kwambiri man of God

  • @kennethnkosi55
    @kennethnkosi55 Před 10 měsíci +2

    Eshiiii.Mulungu alowererepo

  • @markbanda7434
    @markbanda7434 Před 10 měsíci +3

    Amen abusa zikomo potiziwisa komaso potiphuzisa my God continue to protect you

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo Před 7 dny

    Mulungu alemekezeke kumwamba mulungu azikudalitsani kutiwulilila ku mwamba

  • @isaackinod1256
    @isaackinod1256 Před 10 měsíci +1

    Amen mtumik tiyen tithawile Kwa Ambuye 🙏

  • @fwasanishaba
    @fwasanishaba Před 10 měsíci

    Izi ndithu ndi zinthu zomwe anthu tikamamvetsera zimakhala ngati nkhambakamwa koma kuno kudziko kuli zambiri zomwe zimachitika. Zikutengera mzimu woyera ndi Yesu atalowererapo. Yesu atichitire chifundo. Zikomo chifukwa cha mau amenewo

  • @user-cm3pl3pb9u
    @user-cm3pl3pb9u Před 10 měsíci

    😢😢 zovuta kwambuli. Pastor Twaibu mulungu akuyang'anileni

  • @user-hy1kl8bj8b
    @user-hy1kl8bj8b Před 11 měsíci +3

    mulungu atilanditse kwa oyipayo

  • @KeffasSimion
    @KeffasSimion Před 10 měsíci +1

    Ameeen zoona Mr Twaibu mwasitha moyo wanga Mulungu thandizani moyo wanga

  • @maclearjass8389
    @maclearjass8389 Před 11 měsíci +5

    Uthenga wa mphamvu tikasowa chowilingula ambuye akudalitseni bale

  • @MemoryLanga-eb4vm
    @MemoryLanga-eb4vm Před 10 měsíci

    Amen powerful message

  • @user-lc3dk9jc4x
    @user-lc3dk9jc4x Před 10 měsíci +1

    Muzidalisidwa mtumiki

  • @Phinifolo-mm4hh
    @Phinifolo-mm4hh Před 10 měsíci +1

    Atwaibu mulungu nafe atikhudze

  • @user-ez1dt2zh1m
    @user-ez1dt2zh1m Před 10 měsíci +1

    Amen mwatusegula maso

  • @user-jw5rx9ze8k
    @user-jw5rx9ze8k Před 10 měsíci +2

    May almighty God, help us in Jesus name, Amen.

  • @AlfredStingMw
    @AlfredStingMw Před 7 měsíci

    Help us Lord

  • @user-mc8gk4xv3f
    @user-mc8gk4xv3f Před 10 měsíci +3

    Chemwali ake ndani abale atisiyawonso?

  • @user-oz3sj7yc9y
    @user-oz3sj7yc9y Před 11 měsíci +2

    Ambuye atitsogolele

  • @user-mi3sf7it8n
    @user-mi3sf7it8n Před 10 měsíci +1

    Amen

  • @FrankChikhadzu
    @FrankChikhadzu Před 10 měsíci +1

    Oimbaw ufit

  • @user-ph3zy9ox7d
    @user-ph3zy9ox7d Před 10 měsíci +3

    Mwainu ndikondwera maso anga akutsekuka muuzimu ambuye akudalitseni

  • @shakiraameen8001
    @shakiraameen8001 Před 10 měsíci +1

    May our living God continue blessing you

  • @ashikalam8616
    @ashikalam8616 Před 11 měsíci +3

    Zomvesa chisoni

  • @user-jo6kw4ni2x
    @user-jo6kw4ni2x Před 10 měsíci +2

  • @user-md5uv2cg6i
    @user-md5uv2cg6i Před 10 měsíci +1

    Asiyeni azipita vuto ndi kuchulukidwa

  • @user-zh2jq8tu1w
    @user-zh2jq8tu1w Před 9 měsíci

    Powerful

  • @user-ib6wr7pw6n
    @user-ib6wr7pw6n Před 10 měsíci

    God have mercy upon us😢😢😢😢

  • @KinziwindassoniKinzi
    @KinziwindassoniKinzi Před 10 měsíci

    Apa ndiye mwakamba mwa tchutchu .....wakumva wamva osamva adzakhalabe osamva .sitikukana tonse tidzafa koma izi zokha zawonjeza ....satanic is too much

  • @SurprisedKomodoDragon-jb5yb
    @SurprisedKomodoDragon-jb5yb Před 7 měsíci

    Ndinthu munthu samavetsa anena kuti malo amene amaveka sound mulungu samakondwera nawo

  • @jorohbee8750
    @jorohbee8750 Před 10 měsíci +3

    Mulungu azikiludalitsa ndikukusamaliran maka potipasira zobisikadzi

  • @WanangwaShammah
    @WanangwaShammah Před 8 měsíci

    Ndiliko ndi funso koma kodi kulibe oimba onse omwe akutchuka amapita kwa Satana?
    Mufotokoze bwino chifukwa tikhodza kumachita mantha kumaimba....komano Ambuye anatipatsa utumiki enafe oimba kuti tutembenuzire anthu kwa Mulungu...tutani nanga kuti tikhoze,?

  • @lightwelljamugondwe4213
    @lightwelljamugondwe4213 Před 10 měsíci

    Amen 🙏

  • @EmmanuelBatumeyo-pn7bc
    @EmmanuelBatumeyo-pn7bc Před 11 měsíci +3

    Mulungu wamoyo atimenyere nkhondo ndikutitsogolera

  • @Crysis25
    @Crysis25 Před 7 měsíci

    Amangotchula anthu aliphe 😂😂😂

  • @Crysis25
    @Crysis25 Před 7 měsíci

    😂😂😂so fun

  • @AlfredStingMw
    @AlfredStingMw Před 7 měsíci

    Mulungu atithandize

  • @YusufuMaundala-
    @YusufuMaundala- Před 9 měsíci

    Chisilamu ndi chikatolika chidapanga ubale kod nanga tingatsatire bwanji njira yolondola kapempheredwe, komanso mavuto akubwerawo kuchojera kwa satana tizazemba bwanji kuti chakudyacho tisadye?

  • @FostinaPhiri-yb7bb
    @FostinaPhiri-yb7bb Před 10 měsíci

    Zoonadi mulungu atithandizile.

  • @DanielKaliati
    @DanielKaliati Před 10 měsíci

    Eeee end time we need to repent

  • @moseschiphaliwari3598
    @moseschiphaliwari3598 Před 10 měsíci

    Cent

  • @alicechinyama4155
    @alicechinyama4155 Před 10 měsíci

    Atsogo,anthu akungogwa ENA kufa kumene tinene kuti ndi mipweya yoyipa yomwe yatumizidwa kapena ma side effects a vivid vaccines?

  • @user-sz2lv3xm9q
    @user-sz2lv3xm9q Před 10 měsíci

    Koma akumalowa bwanji illuminat poti ndi ya anthu aku america

  • @tasiyanakasalu6228
    @tasiyanakasalu6228 Před 10 měsíci

    Mr twaibu mulungu azikudalitsan

  • @Phinifolo-mm4hh
    @Phinifolo-mm4hh Před 10 měsíci

    Zovuta

  • @user-pe7pd8bg7j
    @user-pe7pd8bg7j Před 10 měsíci

    Thank you 🙏

  • @enelessdimba8122
    @enelessdimba8122 Před 10 měsíci

    😢😢😢😢😢

  • @mozykavalo7352
    @mozykavalo7352 Před 10 měsíci +1

    Ine ndamvela audio bwino bwino koma pali pomwe mwaonesa kuti mubakila bushiri and bushiri si munthu oti mkumu bakila he is the one who is giving money to young artist i have all the evidence he is the devil himsef

    • @livingforchrist-malawi9476
      @livingforchrist-malawi9476  Před 10 měsíci +7

      Zikomo chifukwa cha comment yanu. Mu audio imeneyi, mfundo ya a Twaibu ndiyakuti mapangano omwe oyimba akumalowamo okha kudzera m'magulu osiyanasiyana, ndi amene akupangitsa oyimbawo kukodwa mu zinthu za satana zomwe pamapeto pake akutaya nazo miyoyo.
      Mukamvera bwinobwino mupezanso kuti a Twaibu akunena kuti munthu yemwe mukuti akumubakilayo osati ndiwabwino ayi; iyeyo ali kale mu mapangano otumikira satana.
      Mwachidule, a Twaibu akuti: chomwe chikupititsa oyimba kumanda ndi mapangano a zomwe oyimbawo amalowamo, osati kwenikweni munthu yemwe akutchulidwayo.

    • @user-fg4dp9zc7h
      @user-fg4dp9zc7h Před 10 měsíci +5

      Gud explanation

  • @stevenfrancism3638
    @stevenfrancism3638 Před 10 měsíci

    Amen