CRUISE 5 ELIYA NZERU WILLIAM
Vložit
- čas přidán 4. 05. 2021
- Anthu ena amakhulupilira kuti ufiti kulibe - anthu amenewa sanakumane ndi a Eliya William. Iwe amatsimikiza kuti adatambako komanso adapangako using'anga. A Eliya anali mkulu wa bungwe la asing'anga ku Malawi kuyambila 1986 mpaka 1996.
Iwo siabisa kuti achita zinthu zoopsya komanso aona zambiri kudzela mmatsenga. Iwo akutsindika kuti zambiri zimene timamva zokhudza amfiti ndizoona; amfiti amauluka kugwilitsa ntchito lichelo kapena tsache, ndondocha ndi anthu akufa amene amawathila mankhwala kuti achepe akatelo amawagwilitsa ntchito mmatsenga kuti azikaba ndalama kapena kulima kumunda, anthu amalodzana munjira zosiyanasiyana kuti wina afe kapena azikumana ndi matsoka.
Nkhani yabwino ndiyakuti a Eliya zaufiti komanso using'anga adasiya ndipo pano adayamba kupemphela ku mpingo wa Zioni komwe adakwela mpaka kufika pa udindo wa Bishop. - Zábava
Am leaving this comment here so after a month or a year when someone likes it, I get reminded of watch. ELIYA ❤again and again🤣😂
Ive liked your comment its a reminder kuti udzamvere music ya Amulungu inu. Kkkkkk
Watch it again kkkk
Watch it
Watch now hahahahaha
Hey!
Whose here 2024😂
Ine pano😂
I like this and I will watch whenever someone come and comment Kaya padzatha zaka zingati 😂😂
It's the song for me " Amulungu aaah, Amulungu nomwenu inu. Inu aah eeh, munatuma oyesu koma oyesu nkufa aaah, omulingu aah 🎉😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂
2024 anyone?? 🇲🇼
Ife tikubwera kumene
Ayi tamva nawo zambiri kuli zinthu kunjaku thanks joab for bringing this guy
Lemme rewatch this interview in 2024😂
Am watching now 😂😂😂😂😂
Me 3
The Best Interview Ever 😂😂😂😂😂
Am watching it
❤Ndimayisaka cruse 5 ya Eliya God bless you both
These are kind of people we need when stressed.Please Mr Joab bring more like him.
Absolutely right sir.
🤣🤣🤣
Hello
😅😅😅😅😅koma awa anyanyq aaa ndi stress siingachokenso koma kuopsya kwa munthu
Kkkk I just liked the way Joab was composed the moment Eliya was singing
Akut nyimbo ndiyimba ndekha kkkkk ine koma lero ndanjoya
Can’t get enough of watching this interview..bravo Mr chakhadza😂😂😂😂😂
I just got this video today. The guy is humble. Malawi needs to address this issue of witchcraft.
The best interview ever on cruise 5😂😂😂😂
Joab umatha kunena zoona l like and love the way umakhalila serious on your job. ❤❤
How Joab remains composed in this 🙌🏾🙌🏾🙌🏾🙌🏾and then Eliya keeps looking back anga ngati afiti anZake akumuona 😂
ndpo angoti maso mwa mwa ngati akumuwuzila zonena athakati anzakewo
Et et kkkkk
🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣
Kkkkkkk
Great interview. Love your composure, I am on the floor🤣🤣🤣
Joab...... how you compose yourself not to burst into laughter is beyond me. Good job 👍🏻
Koma A Chakhaza mumakumana ndi zinthu. Keep up good work
Tadzipo zina zomwe sitinkazidziwa , Thanks to you JOAB FRANK CHAKHAZA
wow Mr joab frank Chakhaza tasangalala ndi program imeneyi ...akufukika azabwerenso abambowa ayiwala zina sadandifotokonzere bwino lomwe😅😅😅😅
Joab ndiwe legend I would have collapsed with laughter atangoyamba kuyimba nyimbo
Nyimbo ayimba live,koma the guy has 100% confidence ayaya this world
😂🤣😂🤣😂this interview is therapy session already
Waiting for his album to come out 😂😂😂😂😂
😂😂😂
Amulungu inu 😂
Muwauze, we need air Malawi back in the air space. Kaya idziyenda usiku okha okha, bola idziyenda basi. Apapa solutions to our problems are already at hand
Tamvako zambiri ndithu. Bravo Joab...
Bravo Bwana Eliya
Kkkkkkkkkk die ndagwa ine akuti pano ndinafiila koma kumeneko joab u r my day maker from SA
I've watched this C5 twice first on fb now I'm here again just to promote home industry despite being entertained ....
The fact that he’s wearing a Ralph Lauren shirt 🙌🏾🙌🏾😂Pali phindu 😂😂
🤣
hahahaha
ahahahaha
😂😂😂😂
Azungu otuluka mmazila kkkkkkkk mwatipatsa phwete! Kkkkkk Komatu achakhaza mumadziwa kusaka nkhani kkkk more fire!!!!!!! kkkkkkkkk
Lol 😂😂😂 this interview was funny. Joab, how did you remain calm sir. I was stressed but I've laughed out loud 😸
😂😂😂😂🤣🤣🤣
Nzibambo a meiyu ngo seketsa
Best program in the decade, laugh laugh and laugh. We need part 2
Uncle Joab mwandiwaza eti nanga nkhwanya, nanga mnkhwani,, ndondocha sikudya mnkhwani otendera???🤣🤣🤣🤣😂😂😂😂,,,, Mmaitha uncle Joe, respect
a Joab, serious mumafunsa bwino mafunso ndipo interview yanu imasangalatsa kwambiri. keep on it....we support
Hello
Joab you are professional, salute. How you remained composed in this eeeeee. With loosening of association ili umu🤣🤣🤣🤣mnkachimwa ndi kuseka iiii
😂😂😂
It never gets old 🤣🤣🤣🤣🙌Eliya anabwera kudzakhala
Ndipo live😂😂😂😂
Had to revisit this one. Oh My!
Seriously, I haven't laughed this much in ages. Interview more real Malawians, Joab. Wonder how you kept a straight face man!! Good work!
I will always come back here and rewatch this piece. Its the greatest ever
The best gospel artist of the year 😂😂😂😂😂😂😂😂
Kkkk
Upcoming artist of the year😂
Exactly
I had to watch this again 😂. Great job Joab 👏🏿
Mmmm...hilarious. Ba Joab ndimwe bapondo. Laughed so hard 🤣🤣🤣
My oh my,on a serious note...Elia rocks period!his sense of humour is beyond measure...I can watch this repeatedly...koma Joab amaoneka ngati akuopa kkkkkk!love the Ralph Lauren shirt bwana.
1
1
kept up Mr joab you did agreat job !!!!
Omg I know Eliya personally as I went to his house in area 25 ku Sungwi that was 2001. He was simple guy.
am looking for him so hw can I faind u or Mr man plz
I think this mzeru man is real.
Starting off the year with this hilarious interview.Mr Eliya ndi stress reliever
Who is watching this with me now in 2079
Kkkkk can't wait for part 2. Koma NDA Seka osati zibwana
😁😁😁😁😁fent
Koma amenewa angapweteke coz akuwoneka kuti ndi khang'a
Ulemu wanu Joab, good job 🙏🙏
Mmm muthu opatsa chidwi kuvetsela ndithu.wawulula zambili
Ndikafuna kuseka ndimaonera interview iyiyi Mr Joan mmakumana ndi zithu 😂 Eliya am still waiting for your Album😂
Last song kills everything 🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣
KOMA ELIYA, akupweteka anzakò ndithu. Apolice alikuti kodi.
I saw Joab was frightened, he really wanted to run away😂😂😂😂😂
Khala ngat mutu sukugwira bwino ntchito tuu a Eliya
I'm Watching This But I'm Just Cracking😂😂🤣🤣
Madala Joab Be Bringing More Pple Of This Kind🤣🤣😂😂...
Joab ndiwe katundu pa ntchito yako
Joab this guy must come back, collect questions from viewers and ask him
This is fascinating
How did I not watch this all this time
That shirt is nice, he has class
Akudura anyedzi ndani? Anzanu tikumvera nyimbo ya Amulungu bwinobwino apa! Tikusekelera inu anyedzi duledule. Aaah! Chiphwete cho Eliya aweee! Akati atsekelere ...
Hahaha a eliya gosekesa kwambili 😂😂😂😂
This guy Elia needs a big help he has real demons but thanks to jaob for good work your amazing ❤ from south Africa cape town
This was the best exclusive ever my artist musician Eliya nzeru😅😅😅😅😅
This interview is captivating
Aaaah koma a Chakhadza chonena chikundisowa.
Kikiki koma ndiye I can't stop watching this
Ngiwa we miss you on ur channel
Ufiti siwabwinodi,look at this,ngati wamisala,wopepera ndi chamba
Kkkk thats y ku court amakanika kuweruza mirandu ya ufiti,
Chomwe akunena apa does not make sense-ku court antha kumangonena mbwelera ndithu!
But this is good for intertainment.
ndkubadwa kwake osat character yasintha NDI ufiti Kkkkkk NDI president tu awa
Mavuto amanjoti story, big brother wa papa Gopani.
Achimwenewa ofunika amulandile yesu chifukwa zomwe akulongosoladzi ndi mphavu yaziwanda
😂😂😂😂😂 my brother omar jangia likes this whenever u see this in the future
Lol 🤣 I can't stop watching this Dude! ...
Nafwa 🤣 great job Joab 👍🏾
Joab plz am waiting part two kkkkkkk ndakomoka kwambili
Eish!! Kuli zinthu kudzikoku🙌🙌
these are kind of people we need when stressed😂
God knew that I shouldn't do journalism, otherwise nkanapalamula😂😂😂. Thumbs up Joab, very professional and this interview is a therapy on its own😂😂😂
Chuma chochuluka zedi ,joab ee! Chochuluka zedi akuti chuma....dzindlama mipando mu tente 5'mu...kupeza ntendere koma
😂😂I think Mr. Elia is one of the realest, straight talk; despite his background there's so much sense it almost everything he said and it's just interesting....tipange za EP koma nyimbozo😂😂😂
Great interview joab ur the bast
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣No stand up comedian can top this
😂😂😂
i have to come back and watch Eliya 😂
Waiting patiently for part2😂
Joab ai zikomo kkk this interview is something else. Above witch craft is madness which is manifesting in here. God have mercy
Ndikucheza ndi Eliya yemwe ndi mfiti..😂😂😂😂😂😂😂😂
That killed me straight 😂😂😂
My favourite program
Never get exhausted 😂😂😂😂Joab umantha ,Nice Ralph Lauren Mr president
This was best Joab
🤣🤣🤣🤣koma joab umapilira ndinthu, interview imeneyi ndikanakhala ndimachititsa ine program ikakuthela pa njira, mkuseka 🤣🤣🤣
Ku Malawi sindidzasamuka🤣🤣🤣
The best interview ever on cruise 5 kukamba veveve🎉🎉🎉
Joab u are super
🤣🤣🤣🤣 ndondocha siyamaluzi imadya mpunga ndi nyama ada awawa eish
First time watching this 😂😂😂😂 so fascinating
🤣🤣🤣
This man has a vibe sure!
So dah ni mchewa tu wapa phata dala.😂😂😂
The great of all time .. Katakwe
I swear I enjoy watching this again and again 😂😂
High time we harness and commercialise black magic,here is a former herbalist with a house in area 47 and a 70 bedroom lodge,we shouldn't be 3rd poorest in the world
He took advantage of Malawians' beliefs and scammed them
@@bostersibande8457 then we can now look elsewhere find others to scam,turning white folks into ndondocha
Ndipo ine ndiye ndakomoka ndi phwete kona a Eliya amenewo mayimbidwe😂 ndipo ndajoya ndisaname ka stress konse kutheratu. Achakhadza mumakwana and mwatifunsira mafuso okhaokha ofunikira
I swear if I was Joab I'd have died with laughter... 😂😂😂😂😂
A Eliya mmm ayi zikomo😂😂😂😂😂up coming gospel musician ...koma joab umapilira or mkuseka😁😁😁
Ndipo😅😅
am frowning you here in Lusaka Zambia kip tup