A Gadama ndi anzawo analowa mmanda lero pa 21 May. Kodi analakwanji kuti aphedwe?

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 20. 05. 2023

Komentáře • 157

  • @georgemsangu
    @georgemsangu Před rokem +7

    Ine ine Ngati George Msangu from Mzimba centre.ndizaferamo sindingavoter McP.okhao ana osadziwa kanthu ndiomwe mavotera zopuzmsa. Reporting from South Africa

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x Před 20 dny

      True big inenso i won't vote for chipani chokuphachi ndiine mwana wa Adad mpakana kale

  • @chiyenangomba3330
    @chiyenangomba3330 Před rokem +8

    Innocent blood was shed, malawi silizatukuka chifukw Cha mwazi wa athu osalakwa koma I know the judgement day is coming soon

  • @petermitambo9257
    @petermitambo9257 Před rokem +6

    Ndikamava, izi zimandikwezeletsa kidzakhala chigawenga chowukila boma. Or kudzajoina magulu amtopola. Zimandiwawa. Andale ndi wanthu oyipa😭😭🤞🤞🤞

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Před rokem +3

    Brother timakunyadila kwambila mumalakhula chilongamo mulungu apitilize kukutetezani chifukwatu tikuziwakuti pali anthu ena samafuna chilungamo kutichiziwike mwainuyo taziwachilungamo and we still upgrading muma stories anuwa may all mighty allah bless you and protect u as you stand for the truth

  • @luciascharles4345
    @luciascharles4345 Před rokem +7

    A mcp kuyambila kale ndiya galu awa

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Před rokem +2

    Here we go! Thanks bakili muluzi CZcams channel!! We need some more teachings kuti tidziwe za anthu oyipa amenewa a mcp, agalu amenewa!! Akupha onyasa and opanda chikondi !!

  • @Ndinenjani
    @Ndinenjani Před rokem +3

    Very sad Malawi where murderers are hero’s and victims are villains. The truth must be told.

  • @rodwellmwenekitete8974
    @rodwellmwenekitete8974 Před rokem +4

    Abakili muluzi anali nawo limodzi chifukwa thawi yimeneyo anali wankulu wa yangi payaniya,,,bakili ndiwakupha asabitsale

  • @innocentliyawo3943
    @innocentliyawo3943 Před rokem +2

    He was a freemason sent to our country for sacrifices. He was not a Malawian as well.

  • @charlesmpiyama-js4gy
    @charlesmpiyama-js4gy Před rokem +3

    Komadi 21 may chaka chilichonse boma likanaika nthawi yokumbukira anthu amenewa, instead timapereka ulemu kwa mbava yotchedwa kamuzu, shame!!!!

  • @user-st6bt5vv9c
    @user-st6bt5vv9c Před 9 měsíci +1

    Inu mcp was and is the bad party because some of you youngsters you don't know it that's why you are following and to say fact there were many people who were killed well MAN KEEP ON GIVING US THE TRUTH thanks may God bless you and their souls must REST IN PEACE

  • @amisichiphiri8227
    @amisichiphiri8227 Před rokem +2

    Zachisoni ife a Malawi 🇲🇼 kwambiri pokumbukila kamuzu day ,munthu amene adapha anthu osalakwa,ndi chifukwa chake sititukuka mulungu anatifulatila

  • @bobkenneth2947
    @bobkenneth2947 Před rokem +4

    I'll never praise KAMUZU and if I've done it before it was because of not knowing the truth about him but honestly he was a wicked man and thief in fact MCP wasn't supposed to be ruling today,Rest in hell KAMUZU
    😡😡

  • @marychipofya4945
    @marychipofya4945 Před rokem +3

    koma zinthu zake please..nkhani zomvetsa chisoni kwabasi ndipo zopweteketsa mitima. Amapha anzao ngati iwo ndi amuyaya. Lero naonso ndi mbiri chabe. Anthu awa anawamvetsa anzao zowawa kwabasi. So sad. May their souls rest in peace.

  • @Razarusmbavachakwera
    @Razarusmbavachakwera Před rokem +9

    Awa ndimachine opangila machine azake pankhani yazofuvuzafuvuza

  • @Bushiriderick811
    @Bushiriderick811 Před rokem +3

    Am wondering why up to date the state gvn called mcp still praising kamuzu and hournering that kamuz while he was foreign, killer and destroyed on top of that he didn't do anything for Malawi as development but just to brainwash our parents

    • @tingo3155
      @tingo3155 Před rokem

      Nkhanza it means good to them, MCP is rotten to the core

  • @charliepoulaliecky1893
    @charliepoulaliecky1893 Před rokem +3

    Nchifukwa chiyani ndalama zathu za ku Malawi amayika nkhophe ya mfiti imeneyi???

  • @fefa2050
    @fefa2050 Před rokem +5

    Nice Job Brother GOD bless you

    • @jomochirwa
      @jomochirwa Před rokem

      Oooh nchifukwa chake adad adatsekeledwa account yawo etiiii

  • @Bushiriderick811
    @Bushiriderick811 Před rokem +9

    I wish Malawi as republic we could hournering these hero's in the name of heroes day not kamuzu day

  • @charlesmpiyama-js4gy
    @charlesmpiyama-js4gy Před rokem +5

    Awa ndi makina keep it up, I personally appreciate
    for the work tirelessly done,

  • @patrickbonongwe8569
    @patrickbonongwe8569 Před rokem +1

    Mulungu azipitiliza kumupasa chilango Kamuzu ankawona ngati sazafa wasala Tembo ndi Kazamila anthu oyipa mitima

    • @yusuffatch4146
      @yusuffatch4146 Před 9 měsíci

      Tembo mumanena uja wapita tu. Watsalandi wina uja

  • @user-ks3uw3pq7d
    @user-ks3uw3pq7d Před rokem +3

    Inshaallah 24 years sopano ndikukula guy's holiday anthu gati awa idzakhalampo inshaallah 😭😭😭😭

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk Před 8 měsíci

    A brilliant research, keep us updated, proud of you always 🔥🔥🔥🔥

  • @JacoboManeno-uc3lb
    @JacoboManeno-uc3lb Před 9 měsíci +1

    Born and living em😮 northern Mozambique, I noticed the language spoken is of origin 😅BANTU being a BANTU myself (makon😅de by tribe) I was able to understand what NG😅WAZI did to others in his times

  • @daviemafunga
    @daviemafunga Před rokem +2

    Inuyo ndikuchikweza brother palibenso angazafane ndiinu pankhani ngt izi kmw

  • @farookousmane715
    @farookousmane715 Před rokem +8

    Keep it up..may almighty grant you more years of blessings for your daily endeavors

  • @petermanMitambo
    @petermanMitambo Před 24 dny

    ❤ history is the best teacher long live BMTV ♥️

  • @haneefmuyaya7472
    @haneefmuyaya7472 Před 6 měsíci

    Bakili Muluzi TV channel:
    We proud of you guys, keep it up updating the hidden information,
    Mumatisekula mmaso, ndi inu vumbuluso ndithu, okwiya nanu
    Ndi Mfiti, Satan, Devil
    We follow you guys

  • @georgethole3813
    @georgethole3813 Před rokem +2

    This is so nice we are learning alot

  • @lestermaide-yy4xy
    @lestermaide-yy4xy Před rokem +1

    MCP nyasi ya chipan to me I can't vote for it

  • @ibrahimtutini5862
    @ibrahimtutini5862 Před rokem +1

    Koditu ena amati MCP inaliyabwino chifukwa chauchisilu mcp inali yoopsa kwambiri ndipo olo munthu nyumba yokhala yako sumagona ngati ndiyako unali ukuopa kuphuzira komweku kungoti ukuziwa bwino zinazake kuposa ena zinalitu zoopsa makolo amadandaula kuti uphedwa lusotu anthu amalibitsa kuopa kuphedwa olo ena akamati bola KAMUZU umakala ugalu kwambiri ngati munali ang'ono amukonda kumakala pasi ndi makolo akuluakulu kumawafusa mene zimakalila. Olo oluka Mikeka omwewa akalukatu okongola amalanda akuti akapeleke kwa KAMUZU ndiye mukamasewela uziziwa kuti olo elo mavuto aliko koma mtendele uliko phone, TV, kukala ndizimenezo unali mulandu kale 😢😢😢😢😢

  • @elishamael-shadai
    @elishamael-shadai Před 2 dny +1

    May these heroes rest in peace

  • @edsonjohnbakaimani
    @edsonjohnbakaimani Před rokem +2

    Would you kindly write a book on these four government officials who suffered under Kamuzu administration

  • @abdllahalie2633
    @abdllahalie2633 Před rokem +1

    Thanks brother mumayiyimilila koma tipasileni nkhani za nkhondo ya Russia ndi Ukraine tinve mene zayendela ku bankhmutu chifukwa pano mwati ziiii kutipasila

  • @johnman4619
    @johnman4619 Před rokem +1

    Timafuns mufufuze za karonga stambuli komanso fanikiso phiri .at bakili muluzi ruled

  • @ishakatimbe7341
    @ishakatimbe7341 Před 8 měsíci

    Kuli mulungu kunja kuno ndamene asunge moyo was big man Peter. Iweyo ndaimika manja🤗

  • @enerstmwitha392
    @enerstmwitha392 Před rokem

    Thanks my brother and we thanks all the time

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm Před rokem +1

    Katangaleyu adachokera patali ndi chifukwa maboma onse abwerawa akumakhala akatamgale .

  • @georgemsangu
    @georgemsangu Před rokem +1

    Am a Malawian watching from sa but kamuzu Mmmmm AI no comments

  • @yusufualidan238
    @yusufualidan238 Před rokem +1

    I learn more from this channel

  • @molicieeosama8877
    @molicieeosama8877 Před rokem +1

    You r very important man 🤝🤝💪

  • @ancientnkhata1137
    @ancientnkhata1137 Před rokem +1

    Kale eish kunali Cruelty osati masewera

  • @marychipofya4945
    @marychipofya4945 Před rokem +1

    Mpaka kuwaphwanya anthu maubongo awo...mpaka chinsomali kunkhongo mmmmmh zoopsa😫

  • @MaxwellMustafa-ec8fc
    @MaxwellMustafa-ec8fc Před rokem +1

    Zikomo abraz zosezi zikunena za MCP guys MCP sichipani

  • @DoYouKnow3838
    @DoYouKnow3838 Před rokem +2

    the man called Kamuzu(Richard Armstrong) Banda was a ruthless murder....

  • @yusufualidan238
    @yusufualidan238 Před rokem +3

    Can you take us to mangochi mudzi omwe udawotchedwa uja

  • @richardmadaka287
    @richardmadaka287 Před rokem +2

    Kulakwa kwambiri! These things are not mentioned on Kazumu Day

  • @EmmanuelThom2-xf6ij
    @EmmanuelThom2-xf6ij Před rokem +1

    We like u ...keep moving bro

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Před 20 dny

    MCP kwawo ndikupha basi afiti okhaokha 😢😢😢

  • @user-iv3do9vk3u
    @user-iv3do9vk3u Před 9 měsíci

    Bakili muluzi ndiye mbava yayikulu, wakupha wankulu. Anatiphera matafale. Anàpha anthu ochuluka kwabasi mbava ya chiyao nsilamu

  • @ruthtimothy9583
    @ruthtimothy9583 Před rokem +1

    I like this channel ❤❤

  • @emmanuelchilongo2171
    @emmanuelchilongo2171 Před rokem

    Loud and clear from Zambia

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 Před 24 dny

    Mudzatiuzenso za mmene anafera a Njaunju komanso banja la a Tambala ku Lilongwe.

  • @petermitambo9257
    @petermitambo9257 Před rokem +1

    Koma kamuzu ameneyu ikhala masiku wano eehe wallah wenafe tikadavala ma bomba la tinke nawe ehe

  • @gramnampuluma5797
    @gramnampuluma5797 Před rokem

    Continue rest well you four guys...mulungu ndamene atazaweluze😣

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs Před 7 měsíci

    Mcp sichipani watching from Mozambique never give up bg brother

  • @user-zg7it1es9p
    @user-zg7it1es9p Před 9 měsíci +1

    BIG. 🙏🙏🙏🙏

  • @rodwellmwenekitete8974
    @rodwellmwenekitete8974 Před rokem +2

    Funso lina,,,,kodi eveson matafale adafelanji

  • @eunicemoyo6024
    @eunicemoyo6024 Před rokem +2

    Kom abale anthu ambili adaphedwa mu nthawi yoipayi

  • @user-jy5sl8yr5n
    @user-jy5sl8yr5n Před měsícem

    I will tell this story my child .don't celebrate kamuzu day ,don't vote for mcp

  • @ancientnkhata1137
    @ancientnkhata1137 Před rokem +1

    Makina amenewa

  • @robertchikaonda-mu1bg
    @robertchikaonda-mu1bg Před rokem +1

    Kamuzu akuyankha milandu imeneyi munthu oipa.zedi

  • @timothyngulube545
    @timothyngulube545 Před rokem +1

    MCP inali yakupha

  • @davidkadyakapita8836
    @davidkadyakapita8836 Před rokem +1

    Uyu ndi katswiri pa zofufuza

  • @chrissygama8678
    @chrissygama8678 Před rokem +1

    Inali nthaw yowawitsa ndithu may their soul rest in peace

  • @honourablemcgregorysc97tv

    Am watching it

  • @molicieeosama8877
    @molicieeosama8877 Před rokem +1

    Padafunika pakhale filimu Ngati adachitila za yida Amin

  • @user-tl1jq2gc5b
    @user-tl1jq2gc5b Před rokem +1

    Koma zibwana tikupanga lerozi ena analimvera kuwawa dzikoli

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Před 9 měsíci

    Kunalibe kamuzu kalero ameneyu anali Richard wa ku Ghana chibwenzi Cha Cicilia ndi John Tembo, okupha anzao amoyo hiiii 😭😭😭

  • @zotsatirabanda4438
    @zotsatirabanda4438 Před 23 dny

    Mukatha mukambenso za imfa ya MacDonald Masambuka tidziwenso zoooona

  • @isaacmussa2942
    @isaacmussa2942 Před rokem +1

    Kamuzu anari mfiti kwambiri ngat lyeyo sadzafa

  • @user-mv1er5zr7e
    @user-mv1er5zr7e Před 9 měsíci

    Kamudzu akaziwa Kuti sanali mumalawi ndichifukwa chake akapha aMalawi

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Před 8 měsíci

    Shem story I cry for this story very bad

  • @ishmaelmkuluma2013
    @ishmaelmkuluma2013 Před 10 měsíci

    Ndichifukwa sikoli silikuyenda bwino coz muli magaz ambir

  • @AfiyakazembeKazembe
    @AfiyakazembeKazembe Před rokem +1

    Mumatimasula mithu

  • @janenkhoma6447
    @janenkhoma6447 Před rokem +2

    Kumwamba tukalowa by favor

  • @user-qn2nu4xs9i
    @user-qn2nu4xs9i Před rokem +1

    Nsogoleri wa mtima ngati mvuu😂😂😂

  • @cassimmeleka40
    @cassimmeleka40 Před 9 měsíci

    Mumatisegula mmaso enafe sitimaziwa kuti tembo kamudzi cicilia adalipangira zotani malawi

  • @charliepoulaliecky1893
    @charliepoulaliecky1893 Před rokem +1

    Umakwana boss

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Před rokem +1

    BIG 👍

  • @gracetjomane-jj3ib
    @gracetjomane-jj3ib Před rokem

    Katundu nganga uyu💕💕💕

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Před rokem +1

    Zachisoni

  • @fraserluwemba6364
    @fraserluwemba6364 Před 9 měsíci

    Akumusakatu paja kkkkkkkkkk kudana ndi chilungamo eeeeeeeh

  • @SmithMwangulu
    @SmithMwangulu Před dnem

    Best tv

  • @leyydavido-qd9gv
    @leyydavido-qd9gv Před rokem

    Big up malume

  • @LouisAndrew-jr1yj
    @LouisAndrew-jr1yj Před měsícem

    The best TV ever

  • @chrispinebanda7080
    @chrispinebanda7080 Před 11 měsíci

    THESE WERE DICTATORS, WHEREVER THEY'RE GOD IS THE FINAL .

  • @mrsmoseskita9180
    @mrsmoseskita9180 Před měsícem

    14 may timakumbukira chigawenga chotchedwa kamuzu Ghana

  • @cassimmeleka40
    @cassimmeleka40 Před 9 měsíci

    Mulungu sangawasiye An2 oipawa

  • @evancedzungu2272
    @evancedzungu2272 Před 2 měsíci

    Chilungamo pa dziko pano plb so siyani kudandaula

  • @BdhfbHdhe-pd7nh
    @BdhfbHdhe-pd7nh Před 11 měsíci

    Kumanda kwakamuzu kulizithu akunya manyi

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před rokem

    I regret casting vote for MCP. Chilima, Mulungu akuone pondinamiza mpaka ine kuvotera MCP:Chipani choipitsitsa.

  • @husseinsamuson1704
    @husseinsamuson1704 Před rokem

    Wi need more

  • @user-bx8wu5pb2n
    @user-bx8wu5pb2n Před 9 měsíci

    Alipanjra kamunzu sanafike ayi

  • @user-cv7zg2gl3r
    @user-cv7zg2gl3r Před 5 měsíci

    Nanga Matafale? Komaso chasowa? Best tv

  • @roychiwaya
    @roychiwaya Před 8 měsíci

    Very ssd

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure Před 9 měsíci

    Kulibe wamuyaya kamuzu ndi mzako tembo mulungu akuoneni

  • @marthacassam
    @marthacassam Před 10 měsíci

    Zobvetsa chisoni ndithu bomali khazazi latengera atate awo akamudzu

  • @Satier47
    @Satier47 Před 10 měsíci

    😢 m'maitha big🎉🎉🎉

  • @user-sz2qz9kx1p
    @user-sz2qz9kx1p Před 5 měsíci

    nice