CRUISE 5 WITH JOHN ZENAS UNGAPAKE TEMBO
Vložit
- čas přidán 21. 01. 2018
- JZU Tembo, one of the most seasoned politicians in Malawi opens up about his past. Tackling issues of the cruelty associated with his party, Malawi Congress Party, why Dr. Hastings Kamuzu Banda needed a translator, whether he hated Gwanda Chakuamba and his views on the bickering going on in the MCP.
Great chigawenga this guy Mr kan'gono anaphapo mbalame ndi anthu
This was one of the best interviews Joab did, very interesting and making anyone listening to complete it all. May the soul of bwana Tembo, rest in eternity
Kkkkkkkkk mau omwe ndawakonda koposa mu program imeneyi ndi oti azungu ndi oyipa ndizoonadi mau achiwiri atolankhani osamaonjedzera nkhani those are great and good words from JZU Tembo thanks
Thanks cruize 5 for the nice programme.Tadziwako zambiri.
Very fascinating I love this interview
This is becoming my favourite channel
May your soul rest in peace father JZU Tembo
Brilliant interview knew him when he was governor of reserve bank of Malawi.Interesting to hear Kamuzu spoke with his ministers casually in Chichewa not in English which he did in public.
Your legacy will live forever 💛
ZODIAK BIG UP GUYS FOR THIS PROGRAM CRUISE 5, PITIRIZANI NDITHU
BIG UP MAN I HAVE ENJOYED THIS AND I HAVE LAUGHED
Great man JZU
A Tembo kukulatu uku. I like the way he answers the questions
Salute !!!
Munthu wamkulu tsopano(JOHN Tembo)..... Special thanks should go to Zodiac.....Timakudalirani ....Aliyense mMalawi wachilungamo ayenera kunyadira Zodiak for the Programme
I revisited this Cruise 5 program, what an epic. John Tembo remains one of the most shrewd politicians to date
Amazing
VERY interesting
Enjoyed it 👍
Kapumeni bwino baba ife chisoni njeeeh kamba kankhanza zanu🙌🙌🙌🙌
Koma bambo John tembo ,sanathe kulongosola bwino bwino za kamuzu bwanji ,munthu sungaiwale , mother's tongue, akunamapo mbabo tembo
Òoooh! Woow! Zingayambe kuyiwalika za borodi zimenezi! Opposition started long time ago!
Mwalowetsa zibwana mmalawimo
Ngati kuli Kotheka mudzacheze ndi a chair, kamdala kamakani tidzaseke apa, adzafotokoze mmene anasokonezera dziko lamalawi.
Sadali m'malawi😁😁😁😁😁😕😕😕😕😕😕 muthu wam'kulu ngatiuyu akulakhula mabodza😯😯😯 khalamba yabodza iyi
RIP Baba John Zenus Ungapake Tembo #MCP Legend & Veteran Politician 🕊️
São fazes da vida
Big man😍😍😍
I think Tembo anali SPY wa Kamuzu,,,,,
my suggestion is that since he is still alive on he needed is to come out and apologize for almighty God in heaven and those people of that country still today the government of Malawian has not compensate this people so John tembo he is killer and a plunder of resources of Malawi and his sister mama kazamila
Joseph Phiri. Anapha ndani?
Yes.. He should be tried
Very interesting
Gadama-chiwanga-sangala-matenje-there-waiting-for-you
Mr Joab, this question of who allowed and or said Dr kamuzu Banda should be the life president, i think we should also know that, that time there was no multiparty system, therefore we should all agree that Kamuzu would be the life president because panalibe wina aliyese amene akanatenga udindo wa upulezident. And on top of that Malawi was like any other countries where we fought ndi azungu. So i don't see it kuti it was one person who said Kamuzu should be the life President.
Nice one
This interview is Iconic, and DR Tembo the composure in him
Watching this now!!! Rest in Jah eternal glory Baba JZU!!!!
Anaamuna JZU
Notice how he says "discipline" yachipani amapanga ndi anthu lol if he wasn't responsible for that he wouldn't have called it "discipline". He recognized that as discipline not oppression.
Indeed seasoned politician. JZU Tembo.
Rest in Eternal Peace gogo JZU Tembo agreat son of Dedza 😭😭😭💔💔💔
Sir John Tembo akuoneka ngati akanakwanitsa kutumikira dziko lathuli
Atembo analakwachiyani mr Gadama mr chiwanga mr matenje mr sangala yr evil
i like this political gurus kkkk
Wow nice
Big man
May His Soul rest in peace
Amakwana JZU Tembo
Rest in peace Sir.
joab timatsata program imenei kuno Ku Pretoria
Munthu okupha uya , mukumuchemelera chani😢
Wakapeza a achina gadama, matenje,sangala ndi chiwanga omwe anapha iyeyo ali kumoto
May his soul rest in peace
Why
Rest well gogo ungapake John Tembo
Hamba kahle our Legend
Can you imagine he's still defending 🙄 😳 kamuzu now while he's in the grave
Liar!
Apa mwati bwanji pa nkhani yoyankhula Chichewa Kamuzu Banda? Mr Joel muzamufusenso wina pa izi
JZU Tembo is old hence his memory and articulation of ideas is distorted a liitle bit, therefore its not appropriate to take his words seriously. For instance he declined being in an alliance with UDF during 2009 elections, a scenario we all know happened. JZU Tembo shall remain mwana wa nkango and iconic politician Malawi has ever have. His contribution to national building by working in numerous reputable public institution can not be undermined. Viva JZU. Viva MCP. Viva Chakwera
stl in great validity
What kind of contribution did he do to this country,yokupha anthuyo!!! Kunzunza anthu basi,they did nothing including the fake Kamuzu Banda
RIP legend
I hate this guy with all my heart, why he's lying to us? He was kamuzu banda's right man.... he knew everything that was going on all the killings and brutal
Mulungu yekha akaweludza
Rest in peace JZU Tembo
🎉
Awa ndiye nzika za Malawi osati omwe akunkhala ma president aaaaaa or mbiri yamalawi sakuidziwa akungodziwa zolemba mmabuku
rest in peace
Iweso unari munthu oyipa kwambiri
Rest in peace
amazing
Rlp legend
Bodza kamuzu samalankhula Chichewa chomveka bwino (fluent). Munthuyu anali wa ku Ghana. Anagula anthu ku Kasungu kunamiza dziko kuti ndi abale ake. Atolankhani ankaletsedwa kufufuza kapena kufusa mafuso anthu onse amene Kamuzu amati ndi abale ake. Ndipo anthu amene Kamuzu anagula ngati abale ake samaloledwa kulankhulapo zaubale wao ndi Kamuzu.
Now l believe kut munthu wa ndale ngwabodza,, when did Kamuzu speak Chichewa?
Kamuzu used to speak chichewa the video are there on CZcams
Madala madala Jzu
Bodza Kamuzu sankalankhula chichewa.
Yep... He is lying
mxxxii, munthu oipa uyu joab adamufusa bwino koma akuthawathawa
Rip veteran
mkuluyu sadzatheka
RIP
Kip goin chakhaza nw waiting for winiko kkkkkkk
Tembo amafunika 2hrs interview, amalankhula chimozi chimodzi🤣🤣🤣🤣
May His Soul Rest In Peace. 14September 1932 to 27September 2023. Died at the age of 91.
Koma joaba umatha umandivetsa kukoma from Johannesburg
Rip jzU
munthu wamkulu kwabasi...machine opangila machine azake
Rip
Haaa 😂😂😂😂😂😂😂he is lying about kamuzu speaking chichewa. He is protecting kamuzu legacy
Kamuzu he was speaking chichewa very well, wabadwa dzulo iwe ingokhala phee or uzionera zingayambe kuiwalika
Kamuzu amayankhula Chichewa ndi chitumbuka chomwe
The long waited interview
Thanks Joab and Zodiak
Wow....that was really good conversation. Next time go to Dr bakili muluzi
Kamuzu Chichewa baba tembo mukunamatu
This guy looks like kamuzu banda
eekkkk
Ineso maganiza choncho
Ineso maganiza choncho
vutola amalaw mukucheza ndi mmalwi weni weni nyimbo mukuyika zaazungu aaaa sizoona
A Malawi siamvera nyimbo za azungu?
Iconic clap back!!!!
What a legacy!!
RIEP Baba Tembo
At kundale kulibe kufunsana maganizo😂😂😂 aise john tembo umakwana uyende bho😅
This man reminds the Mwanza four,Dick Matenje, Aaron Gadama and others
Amos Chisisi walking in unforgiveness spirit
+I Threes
only God could judge him
because nobody knows
how much God loves him
enani or ukalàmba simuzaulawa
Still living in the past dzuka Malawi dzuka
Amos Chisisi kkkkkkkkkk yes this gentleman I think that he tried at all cost to clear his way in order for him to become the successor of Kamuzu & a lot of innocent people fell victim to this gentleman koma Ambuye sanalole.
Gift Sululu that is very true God alone amakhala ndi cholinga ndi each & every individual. Mawu a Mulungu amanena kuti tchimo lingafiyire ngati Kapezi ngati Munthu atavomereza ndikulapa azayeletsedwa ngati Matalala. But this does not stop people to point out what people perceived to be ill. Judgement is reserved only for God.
Ulemu wanu a Tembo, tinakusowani
Kakkkkk kumamusowa alimoyo kikikiki
Kkkkkk
Ataaa pang'ono ataa kkkkk
MHSRIP
Koma John tembo experience inapweteka😂🤣
All satans have soft talk,to hide their evil
Mkulu ameneyu anali woopsezya wanthu.
Chakupha ichi 😞😞😞
Tembo
Ubale wantundu wanji? President wake adali ndan kkkkk
Kamuzu amatha Chichewa komaso chitumbuka amatha. Anaphunzira ku khondowe