Omwalira apezeka wa moyo

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 2. 09. 2023

Komentáře • 66

  • @SaidShop-nf3qu
    @SaidShop-nf3qu Před 3 měsíci +3

    Abare Kodi busayo ndingapeze bwanji abare ndiarogo mwaambuye chonde ndithandizeni

  • @nimrodkapingatheu5475

    Anthu awawa anazonzedwa ndi ukulu wa Mulungu.. si azibusa ongofuna kunjoya mmacarpet wa....

  • @user-eu9xe6wl8b
    @user-eu9xe6wl8b Před 9 měsíci +1

    Great work prophet❤🎉

  • @user-yy6rj5lc4i
    @user-yy6rj5lc4i Před 10 měsíci +3

    Pano zithu sizili bwino ndimakhala ndikuva nkhani zimenezi kwambiri chomwe chimandipasa kulimba mtima kuti ndizoona ndithu ndipo satana akugwilisa ntchito anthu oipa mtima awa kumaononga miyoyo ya anthu kumalimisa muminda.Ambuye atichitire chifundo kwambiri

  • @IvvyMakuluni
    @IvvyMakuluni Před 10 měsíci +1

    Mpimpimpi!!!!!mwabisapo chani a Zulanga....mesa mufuna anthu tidzidziwa chilungamo 😅😅😂

    • @user-lc7ji1gn9w
      @user-lc7ji1gn9w Před 10 měsíci

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 kma ndaseka

  • @user-lz1ry1sm4j
    @user-lz1ry1sm4j Před 7 měsíci +1

    Too bad. The name of the Lord is a strong tower

  • @hawabanda-xs5fx
    @hawabanda-xs5fx Před 9 měsíci +2

    Anakakhala azibusa ena bwezi Ali pa screen mulungu apitilize kuwakhuza abusa in Jesus Christ

  • @BdhfbHdhe-pd7nh
    @BdhfbHdhe-pd7nh Před 10 měsíci +3

    Ukulu wa Mulungu tauona

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Před 10 měsíci +3

    Adzibale anga.nsanje to chitipa kwainu nonse mukumapanga masalamusi amenewa kodi mumafuna kuti mupedze chani ? Kodi umakhala umphawi ? kapena kukhwima ? Tiyeni tiyike chikhulupiliro chathu pa mulungu tiyeni tigwire ntchito ndikumapempha kwa mulungu zomwe tikufuna koma tisamafike mpaka pomapha nzanthu muchifukwa chofuna kukhupuka kodi zimenezi kwainu mwapanga idzi zikanakhala kuti mwachitidwa inu kapena mwana wanu mukanamva bwanji ? Nchitidwe uwu utheretu kumalawi inu mukupha anzanu inuyo ndiye mudzapita kuti ? 😂😂😂😂

    • @josephnanyanga2012
      @josephnanyanga2012 Před 7 měsíci

      koma akutipweteka anthu wokupha azawowo because amatitengera anthu wotitimawadalira andipaseko namba prophet please

    • @user-zc9ku5fw4n
      @user-zc9ku5fw4n Před 5 měsíci

      Ndipo ineyo ndipemphero Langa Kwa onse akupanga nchiiiitidwe opha anzawou adzafe mozinzika.ndili munyengo zomwezi nane Ambuye andochitire chifundo Mwana wanga azauke,🙏

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před 11 dny

    Ndingampedzeko bwanji mbusa amenei?

  • @MadalitsoHope
    @MadalitsoHope Před 8 měsíci

    Zamphavu 🙏👏 prophet

  • @richsambakusi424
    @richsambakusi424 Před 9 měsíci +1

    Azibusa ngat awa mulungu azipitiliza kuwadalisa

  • @collinstrevor
    @collinstrevor Před 10 měsíci +1

    Ukulu wambuye uwonekere afiti ayaluke sambitu kumampha makolo anzawo

  • @esthermakwinja3207
    @esthermakwinja3207 Před 10 měsíci +1

    Ambuye akantheni afiti on se dziko lilongosoke

  • @JosophineSolobala-hp5ds
    @JosophineSolobala-hp5ds Před 4 měsíci

    So sad alot of our relatives akugwilitsidwa ukapolo somewhere ife kumat anamwalila😢😢

  • @rachealphiri3416
    @rachealphiri3416 Před 9 měsíci +3

    It happened in Zambia twice

    • @ephraimphiri5789
      @ephraimphiri5789 Před 9 měsíci

      Nope, it's happened in Zambia more than seven times 'just on TV' about 5-7 years ago...and many more times in the rural areas...

  • @MussaIbla
    @MussaIbla Před 10 měsíci +1

    Eish zovesa chisoni kwambiri

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Před 10 měsíci +3

    Ndi zoona wanthu ambiri sakufa akuma phedwa ndi asatanic m'modzi wa iwo ndi INE inenso ndinaphedwa koma ndina zuka koma munali mu 2015 moti m'mene ndina zukira kunyumba kwa achibale ku Malawiko sindinabwere ndikuopa Kuti mwina achibale sangandirandire koma panopa ndiri ndi Wana awiri chidzukire ineyo ambuye yesu akandithandiza ndizafika kunyumba chifukwa ndina chosedwa kumeneko ndi Wanthu wena awiri woyera mpakana pano wa nthu anandi chosa kumeneko amabwera mpakana pano ndimacheza nawo dziko Lino lapansi likudabwisa kwambiri pempherani kwambiri ambuye yesu afika nthawi iriyonse nanga m'mene ndiriri ine munga ndiziwe kuti ndine odzuka panopa ndiri ku Mozambique malire ndi zimbabwe kunyumba ndiku Mulanje kwa nkanda ku kambenje

  • @oswardmwale216
    @oswardmwale216 Před 8 měsíci

    Aaaa bwanji simunafukule kumaliza mpaka kupeza bokosi kuti muone ngati mafupa alipo

  • @user-rv8gi4ro6r
    @user-rv8gi4ro6r Před 10 měsíci +2

    Nkhani ndi yakuti mulungu wakwiya

  • @user-lc7ji1gn9w
    @user-lc7ji1gn9w Před 10 měsíci

    Nde mabeluwo kut zinveke bwanji ukubisa chani aaaaa kangaude watani kod😮

  • @BlessingsBanda-qn7xr
    @BlessingsBanda-qn7xr Před 10 měsíci

    Koma anthu ndinu otamba Ana anjoka koma mulungu adzaweruza . Jehovah inu inu ndinu choonadi ndi moyo kazitikhululukirani machimo athu

  • @BaxterChipofya
    @BaxterChipofya Před měsícem

    Asakhale anyamata okhwima awa akanafukula mpaka pansi to prove that A = B

  • @BaxterChipofya
    @BaxterChipofya Před měsícem

    Akafukule manda akapange check ngati mafupa palibed

  • @mordecaikachale2497
    @mordecaikachale2497 Před 10 měsíci +2

    Abel siyani kuliza ma bell 🔔 kubisa mawu ena Pano ndinyengo zoti zibisika za anthu tiziziwa basi

  • @JusticeMakwinja
    @JusticeMakwinja Před 2 měsíci

    Tikufuna busayo ndithu

  • @AmusedSakura-dx1nw
    @AmusedSakura-dx1nw Před 5 měsíci

    Lord have mercy

  • @liki-likiladies---lilongwe6963
    @liki-likiladies---lilongwe6963 Před 10 měsíci +1

    Divine postmortem

  • @chimwemwemaquesuwell5841
    @chimwemwemaquesuwell5841 Před 10 měsíci +3

    Choonde tipatseniko nambala yá openphererawo

  • @ChisomoKapanda-jg2uf
    @ChisomoKapanda-jg2uf Před 10 měsíci

    Ati amangonda ngati edzi kulankhula kwabwanji uku

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před 11 dny

    Amenewa NDE adzibusa a Mlungu not a "can I prophecy!)a busa a receive receive,ma agent a satanic ulaliki ukhare wa ndrama otsati wachipulumutso?

  • @user-dt8nr1zx6e
    @user-dt8nr1zx6e Před 10 měsíci

    Taona nawo zikomo

  • @CostaCasimiro
    @CostaCasimiro Před 7 měsíci

    Blassa semanal agovati ndi agedo

  • @adamusaidih8570
    @adamusaidih8570 Před 10 měsíci

    Kkkkkkkkk km ku Malawi gyz kuli ufuti

  • @josephnanyanga2012
    @josephnanyanga2012 Před 7 měsíci +1

    ndikupephako namba ya pulofetiyo ndikupepha

  • @user-zk5nu5fh6l
    @user-zk5nu5fh6l Před 10 měsíci

    Izi ndi zowona ndinaziwonapo ndi maso anga

  • @user-ek7vg7ld8h
    @user-ek7vg7ld8h Před 9 měsíci

    chifukwa chan anthu akungozuka ku Malawi kokha?

  • @marthacassam
    @marthacassam Před 9 měsíci

    Zaulendo uno tiona zithu

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Před 10 měsíci

    Ndiye wina amvekele ufiti kulibe. Ur mad.

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 10 měsíci

    Shame😢

  • @KINGMANMAKALA-hb9gs
    @KINGMANMAKALA-hb9gs Před 10 měsíci

    😂😂😂😂

  • @YusufMolesi-vr4pn
    @YusufMolesi-vr4pn Před 10 měsíci

    Hy

  • @AriohChauluka-lm9oo
    @AriohChauluka-lm9oo Před 9 měsíci

    M

  • @user-ux8qz1tg7l
    @user-ux8qz1tg7l Před 10 měsíci +1

    Number ya abelo pls pls ol ya abusa

    • @SaidShop-nf3qu
      @SaidShop-nf3qu Před 3 měsíci

      Gati mwaipeza number chonde tigawireni number yabusawo

  • @hawabanda-xs5fx
    @hawabanda-xs5fx Před 9 měsíci

    Abusa achilungamo achochi akusowa tikungolimbana ndi ama jecket mtwn

  • @mbawabuliyan9704
    @mbawabuliyan9704 Před 10 měsíci

    Family imeneyi kuli Anthu ochepa pakufunika afufuze bwino kwambiri munthu akupanga zimenezo aziwike

  • @patrickjaenda8288
    @patrickjaenda8288 Před 10 měsíci +1

    Zomvesa chisoni kwambili

  • @user-fq3jz4hl4c
    @user-fq3jz4hl4c Před 10 měsíci +1

    Chonde chonde ine kwathu ku Mangochi ndikufuna phone number ya abusa wo please ndili ndi mavutho nso ine yo

  • @BdhfbHdhe-pd7nh
    @BdhfbHdhe-pd7nh Před 10 měsíci

    Abelo ukutiona kupusa